I feel sorry for these guys big time. Mmh basi koma angopilirabe .
@MarthaFrazer-um7yz3 ай бұрын
A day to remember 🔥💯
@AfroZaxxi3 ай бұрын
ukuku kunabhebha 👏
@IsaacNamulu3 ай бұрын
wow...send more
@Studetnurse3 ай бұрын
Ma uniforms akusiyana ena akuvala brown ena white. Wina atafotokoza why ma uniforms aliosiyana
@malawiprisonsservice3 ай бұрын
Awala white wo ndi a prison brass band
@Studetnurse3 ай бұрын
Alright. So ndifuseso apa ineyo I hold a diploma in nursing and midwifery. So I wanted to work ku prison. Can you please explain momwe zimayendera ngati wina unapanga zachipatala then ndikupita kumeneku