Пікірлер
@rashidadan2533
@rashidadan2533 12 сағат бұрын
Mcp inaphadi sidik mia ndi Saulo Claus Chilima basi , koma mcp mmmmm osapanganayo ubale
@fastMalawi
@fastMalawi 11 сағат бұрын
Zinthu zake😏
@PaulvinMhango
@PaulvinMhango 21 сағат бұрын
Aaah born kalindo ndi mbuzi kumangolongolola basi tiziluzaso bundle osapangisaso mademo
@fastMalawi
@fastMalawi 20 сағат бұрын
😅😅😅
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 21 сағат бұрын
Sopano munthu ndi wa mcp kare angasiyirenji kurowesapo ndare nanuso abon karindo zandare kare zimenezo ndithu
@fastMalawi
@fastMalawi 20 сағат бұрын
🫡🤝🤝
@JohnMkota-p2x
@JohnMkota-p2x 21 сағат бұрын
Ineo born kalindo umandisangalasa kwambiri umakamba chilungamo
@fastMalawi
@fastMalawi 20 сағат бұрын
Zoona🫡
@rashidadan2533
@rashidadan2533 4 күн бұрын
Kodi mwangodzuka kumene , mukuyankhula ngati tulo silinakuthelenitu
@fastMalawi
@fastMalawi 4 күн бұрын
Pepani tikonza 🙏
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l 4 күн бұрын
Tanva koma simudziwa kufotokoza bwino
@fastMalawi
@fastMalawi 4 күн бұрын
Pepani tikonza 🙏
@Jacqueline-b4x
@Jacqueline-b4x 5 күн бұрын
Why simukunena number ya asilikali omwe aphedwa a ku Malawi?
@fastMalawi
@fastMalawi 5 күн бұрын
Atatu🇲🇼
@MariaDandazaraJSDmoio2024e
@MariaDandazaraJSDmoio2024e 5 күн бұрын
Kulimba azake chifukwa chiyan
@fastMalawi
@fastMalawi 5 күн бұрын
Eti eti
@JosephyMakunganya
@JosephyMakunganya 6 күн бұрын
Sometimes I don't understand why We Malawians( we )go there,this is not only peacekeeping there is something Behind 🤔
@fastMalawi
@fastMalawi 6 күн бұрын
Kwambiri 🤝
@BernardKalongah
@BernardKalongah 6 күн бұрын
Chakwera , pamodzi ndi azimzake akulimbana ndi kufuna kukhala olemera kwambir padziko lonse la Malawi, osati kuthandiza anthu / dziko , Koma kuthandiza mimba zawo komanso mabanja awo okha ,chimene tikudira apa ife ndi anthu angat omwe Angapezeke pa top ten ya anthu olemera pamalawi, I am show kwangangotsala chabe kanthawi kochepa kwambir ,tiwaonetse agalu amenewa,mbava, alesi ,
@fastMalawi
@fastMalawi 6 күн бұрын
Kwambiri 🤝
@rashidadan2533
@rashidadan2533 6 күн бұрын
Ntchito ya usilikali ndiyomweyo palibe kuthawa
@fastMalawi
@fastMalawi 6 күн бұрын
Ndipo kwambiri 🤝
@BernardChikopa
@BernardChikopa 7 күн бұрын
Zooona anthu andale kaya akalowa kimenekunja kaya amamwa magazi achani chifukwa onse saganiza za anthu....koma mimba zao eeeee,,tikapuma kumwamba...
@fastMalawi
@fastMalawi 7 күн бұрын
😅kodi?
@sautsochingoli7878
@sautsochingoli7878 7 күн бұрын
Mzimu wawo uuse mumtendere mesa amapita ndi mfuti kumeneko amadziwa njat nsilikali kut ngat sakaphedwa ndiye kut akapha nod iwowo ndiye ntchito ya usilikali mmene imayendera
@fastMalawi
@fastMalawi 7 күн бұрын
Ndipo kwambiri 🤝
@UsumanUsumanwillo
@UsumanUsumanwillo 6 күн бұрын
​@@fastMalawiDRC ndiyomwe asilikali amabwela ndi mamilion enawo ankhoza kupita kunkhondo koma akusakako gold
@fastMalawi
@fastMalawi 6 күн бұрын
@UsumanUsumanwillo zosaendatu
@UsumanUsumanwillo
@UsumanUsumanwillo 6 күн бұрын
@@fastMalawi kwambili
@UsumanUsumanwillo
@UsumanUsumanwillo 6 күн бұрын
Eyetu nkhondo sangangonyamuka amalawi ndi ma South Africa kuli ma Uganda ,Rwanda American zonsezo chifukwa cha kuluna boys mupange vedio ya kuluna boys machete muone mmene amakhapila anthu sakulakwisa koma ndilamulo la military
@Alexchinangwa-k2q
@Alexchinangwa-k2q 7 күн бұрын
mulungu adzikhalakumbuyo kwako❤
@fastMalawi
@fastMalawi 7 күн бұрын
🙏 amen
@CharlesJames-f1w
@CharlesJames-f1w 8 күн бұрын
Makolo.usi.nyamata.opanda.maganiso.chipani..chake.chasatana.mumapa
@fastMalawi
@fastMalawi 7 күн бұрын
Kodi?😅
@BeatriceChibwana-g6n
@BeatriceChibwana-g6n 9 күн бұрын
Ambuye mutichitile chifundo dziko lapasi lavuta
@fastMalawi
@fastMalawi 9 күн бұрын
Ndipo kwambiri 🙏
@UsumanUsumanwillo
@UsumanUsumanwillo 6 күн бұрын
​@@fastMalawikumapephelela ana tikubelekawa chifukwa zinazi akumazionela ma movie nkuyamba kusatizila kuluna boys ndiyomwe yabalalisa ku DRC kumalawi kungoti ayambe zomwe achita anyamata amenewo inuyo muona mmene asilikali ataigwilile ntchito machete kubwelesa mudela lanu mungave bwanji
@ThomasMGamah
@ThomasMGamah 9 күн бұрын
Point yanu ndiyotani akulu Mesa ndi asilikali ana signertu si uphunzitsitu iyi ndi military
@fastMalawi
@fastMalawi 9 күн бұрын
Mmangofotokoza pepani 🙏
@UsumanUsumanwillo
@UsumanUsumanwillo 6 күн бұрын
Kumene tayesan kumaona video nkumva zifukwa zomwe atumizila asilikali DRC munthu kubwela wamoyo ndimamilion kale si malawi ndi south african yokha ili kumeneko kwalowa ambili osiyanasiyana osaiwala kuti kuli gold kumenekuja kumalowa live chat muziona kenako kulowa kuma comment
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 9 күн бұрын
Akulephera kuteteza dziko lawo kumapita dala kumeneko zofuna awakutumule kumene anapha chilima agalu awa
@fastMalawi
@fastMalawi 9 күн бұрын
😅 kodi?
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 9 күн бұрын
@fastMalawi onse afele komweko akanamutenganso chakwera akamudyese
@SusanaMakanga
@SusanaMakanga 9 күн бұрын
Kurankhura kopusa azanu ataya miyoyo yawo azibare awo akulira Inu basi kumarankhura kopusa kuteroko enanu Chirima mumamukonda kuposa Mulungu eti?Ofa lero safa mawa Oro iweyo ukhoza kusowa ngati Mulungu angafune cz Miyoyo yathu iri m'manja mwa Yahweh
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 9 күн бұрын
@@SusanaMakanga ndiye iwe chakupweteka ndichani zautsilu basi awatibule kumene onse athere komweko ntchito zake zolembana pachibalezo,,, tachokani apa nanu fokofu,😏
@UsumanUsumanwillo
@UsumanUsumanwillo 6 күн бұрын
​@@SusanaMakangasukulu ndiyofunikatu akanalowa nkalasi anthu akutelowo sakanayakhula nkhondo ya military ndiyovuta kupanda asilikali mwinaso anthu akuitanidwa kuti kuluna boys bwezi atatipeza mu africa
@SailotaSamuel
@SailotaSamuel 9 күн бұрын
Tune your voice please 😮
@fastMalawi
@fastMalawi 9 күн бұрын
🙏 I'll Try
@DicksonKamwendo
@DicksonKamwendo 9 күн бұрын
Rip our Sodiers u have done ur best trying to bring peace in Africa.
@fastMalawi
@fastMalawi 9 күн бұрын
🥺🇲🇼
@UsumanUsumanwillo
@UsumanUsumanwillo 6 күн бұрын
@@fastMalawi tikanakhala kuti nthawi yakongelesi tinalipo bwezi ifeso tikukumbusana apa Congo ilibe ufulu izi sizingathe
@MariaHarry-j7r
@MariaHarry-j7r 10 күн бұрын
Muthu sungamuvetse timaoneka abwino pa maso koma tiku semelana zinyawu
@fastMalawi
@fastMalawi 10 күн бұрын
Ndipo kwambiri 🤝
@MariaHarry-j7r
@MariaHarry-j7r 10 күн бұрын
Muthh sungamuvetse
@fastMalawi
@fastMalawi 10 күн бұрын
Zoona🤝
@JaneKadzuwa
@JaneKadzuwa 10 күн бұрын
Pamenepa mukufuna kuti timvera nyimboyo kapena xomwe mukulankhulazo?
@fastMalawi
@fastMalawi 10 күн бұрын
Tipepese 🙏
@JaneKadzuwa
@JaneKadzuwa 10 күн бұрын
@fastMalawi welcom
@franknsomba
@franknsomba 11 күн бұрын
Kkkk
@fastMalawi
@fastMalawi 11 күн бұрын
😅
@FernadoalbertodaimoneDaimo-d4u
@FernadoalbertodaimoneDaimo-d4u 11 күн бұрын
Zoona big the DC,
@FernadoalbertodaimoneDaimo-d4u
@FernadoalbertodaimoneDaimo-d4u 11 күн бұрын
The DC munthu wankulu
@fastMalawi
@fastMalawi 11 күн бұрын
Ndipo kwambiri
@fastMalawi
@fastMalawi 11 күн бұрын
😅
@FathimaMhlongo
@FathimaMhlongo 12 күн бұрын
Mumangoduliratu mutu
@fastMalawi
@fastMalawi 12 күн бұрын
Chitani subscribe basi❤️😊
@FathimaMhlongo
@FathimaMhlongo 12 күн бұрын
Ulemu wanu mmafika pondisowetsa zokamba
@fastMalawi
@fastMalawi 12 күн бұрын
Tiyamikire😊❤️
@rashidadan2533
@rashidadan2533 13 күн бұрын
Ngati wakhululukila akaidi 1500 , that means ameneo ndima Dollars , kuli kwathukuno ndim'mene yagwela kwacha ndiye kuti wakhululukila akaidi 23000, 100 m'makwacha . Trump wabwela mwasopano
@fastMalawi
@fastMalawi 12 күн бұрын
😅😅😅 kodi?
@fastMalawi
@fastMalawi 12 күн бұрын
😅😅 kodi?
@rashidadan2533
@rashidadan2533 13 күн бұрын
Ndiye muziyesesa kuti mukamayankhula soundyo muzichepesa kwambili kuti tizitha kukumbeselani bro
@fastMalawi
@fastMalawi 12 күн бұрын
Ndipo ndiye zitheka musakaike🤝🤝
@FathimaMhlongo
@FathimaMhlongo 13 күн бұрын
Zachita bwinot America imadelera
@fastMalawi
@fastMalawi 13 күн бұрын
😅😅 kodi?
@fastMalawi
@fastMalawi 13 күн бұрын
😅😅 kodi?
@FathimaMhlongo
@FathimaMhlongo 13 күн бұрын
@fastMalawi yes ndi dziko komwe ndi la evil
@LevieLinya
@LevieLinya 13 күн бұрын
Welcome pitilizani bas koma tandigileni nyimbo ikunveka pansi pansi
@fastMalawi
@fastMalawi 13 күн бұрын
😊 whatsap Number
@Wizzirabsoni
@Wizzirabsoni 13 күн бұрын
Kunena mosambisa inuyo mumagima pachilungamo
@fastMalawi
@fastMalawi 13 күн бұрын
Ndipo tikukhulupilira kuti mupanga subscribe 😊♥️♥️
@Happiness-xf7zl
@Happiness-xf7zl 14 күн бұрын
We are a sick national indeed