Ma fund aja akat azifikila mmanja mwa anthu ngat awa bwez anthu ambiri atathandizidwa
@CharlesKapwanya-r2x2 сағат бұрын
Zonsezi chakwela bc moyo ukuzuza kwambili
@HalimaBwanali-f4g3 сағат бұрын
Azinena chilungamo lelo alipoyera
@MalliamAli3 сағат бұрын
Mulungu azikudalitsani bwana
@raytavares22563 сағат бұрын
First lady mai busa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Hilarious indeed calling ndidza pafupi poo
@MasankhoKausi-b2j4 сағат бұрын
Mbambande
@TamUs-u2h9 сағат бұрын
My vote to Chalakwe , president opandadi tsankho, ene akuti akazolowa m"Boma azasamutsa ma office from LL to BT kkkkk, Tele si tsankho ili? Koma ma cadets ndinu otembeleledwa
@chiefmitengo9 сағат бұрын
Nkhani yabwino ya ma school ngati iyi, Tele munthu obadwa Kwa amake ndithu ndikumadana ndi izi? Ma cadets chitani manyazi msanje si sikuthandizani, ndale sitidya AI koma chitukuko. Ndipo musazinamize kuti DPP izalowaso M'boma ng'oooooo
@EnockMpaha10 сағат бұрын
Ama mwafika apa down thawi yomweyo kkkkkkkk
@LimbikaniHaulesi13 сағат бұрын
Katundu
@Malani4115 сағат бұрын
This a joke. No need for leaders!!!
@PaulKambalame-l2e15 сағат бұрын
Kukhala ndimunthu ngati uyuyu ndichinthu chonyaditsa ku dziko ndipo tikuyenela kumuchita cover monga mdalitso wathu koma ife ndiameneso tilipatsogolo kumuipitsila mbili tsono tikamati anayenda bwanji kuchokela ku south Africa timafuna aphedwe? eshiiiii amalawi tilindimsanje ameneyi anathawila kwawo ndipo Kaya anthu akuluakulu aboma anathandizilapo zakuchoka kwake kuchokela ku south Africa anthu amenewo sanalakwitse ndipo mulungu awadalitse anachita zotamandika komatu Steven kayuni anthu amakudandaulani mulindi khalidwe lolakwika sinthani please 🙏🙏 achisaleso anakudandaulani kobasi apa ndiuyuso man of God akukudandaulani inutu mwazi wamwana wa prophet shepherd bushiri ulipa mutu panu😭😭😭mau anga nawa kwa man of God pitilizani kukhala munthu olimba mtima vuto munabadwila dziko la anthu amsanje inu musabwelele mbuyo Kaya nkhani zachifundo pitilizani kugwila ndithu osafoka tizazindikila koma mochedwa mulungu akadzathana nanu padziko lino lapasi 🙏🙏🙏
@GrecianKamwendo-s4l17 сағат бұрын
Kkkkkkkk chiphwanya watani zimayi
@PeterBendeka17 сағат бұрын
Watch ING From jouberg mulibo guy's
@JamesMachunga18 сағат бұрын
Koma umphawi ndiwovutadi president ndi duna zake zigoba ndalama za Malawi inu mukuchoka pamenepo kumagona ndidyala anthu Inu womvesa chisoni ndithu
@noriesingini18 сағат бұрын
Watching from Lilongwe kawale 2 nanjati
@Georgejames-d4z18 сағат бұрын
Kkkkkkkk koma chuma
@noriesingini18 сағат бұрын
Prophet mulelemba big man he is a talent man
@ShillahYohan19 сағат бұрын
Madoba doba sopano mwatbiliwa mbuya
@AlicksonMakata19 сағат бұрын
Koma eeeeee anthu inu mwafatsapo.
@GeorgeKhonje-q3u19 сағат бұрын
Mwana wamkango😊😊
@MaxwellNamwela19 сағат бұрын
Ine watching from lower shire-chikwawa mmalawi Momuno!!
@KelvinBandah-o5v19 сағат бұрын
Lies of kasakula
@StoreRoom-j7u20 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂
@ShadreckEsauh20 сағат бұрын
HKkkkkkkkk
@GreyGrant-jr4fs20 сағат бұрын
Adah awawa kkkkk
@langsonmndalanga20 сағат бұрын
Maka ifee kuno ku Northern gate what's ever kulibe chitukuko tingoona ma tunker akutidusa kuno ku Karonga koma sitiziwa kumene akupita
@YunusFikra20 сағат бұрын
Jelousy basi? Ochewa sazatheka😂😂😂😂
@geofreydzinyemba610721 сағат бұрын
Ulemu wanu guys
@LawrenceBelson21 сағат бұрын
Mpaka kuonesa chimimba koma namachende iwe
@MaggieGirl-n6b21 сағат бұрын
Koma mumandivesa kukoma anthu inu
@AlefaKhumalo22 сағат бұрын
Nde agan azionatu kkkkkkk😂😂😂😂
@kumbusemu944622 сағат бұрын
Eee koma mercy uli ndimwano iii
@kumbusemu944623 сағат бұрын
Watching from Groenkloof Pretoria
@Littlefair723 сағат бұрын
Funso lokuti anatuluka bwanji ku south africa ndi lopanda phindu, nditakhala ine sindingabwerenso ku ma interview anuwa.