Ken Msonda nayenso nd tambwali kathyali otheratu kuteroku nde kuti zake apaa akudya ndithu ndipo ali after ndalama basi. Siyemweyu ankanena zoipa za mcp lero ndi uyu wasintha mawanga, muzinamiza ana osati ife.
DPP or utm ikangowina pasazapezeke Ochoka ku mcp kuzalowa ai mudyeretu ndalamazo agalu inu
@SiphamandlaNcaphayi38 минут бұрын
Muwina chipani cha moyo chili kuti
@Dan44-x5b2 сағат бұрын
Hot air
@presciouscarlos9165 сағат бұрын
Money ruin even kings
@JosephCompan5 сағат бұрын
ichi chimatha kuimba koma vuto lopita ku mcp
@Homeofpeace3215 сағат бұрын
Anamupha Chilima utakoma Ulemelelo
@wongiewongie6 сағат бұрын
Ine ndi waku Northen km awa akunena zoona achakwera alibe plan yoyendesera dziko
@wongiewongie6 сағат бұрын
Ine ndi waku Northen km awa akunena zoona achakwera alibe plan yoyendesera dziko
@PatrickMuronya-c7r7 сағат бұрын
Munthu akaba zinthu monga ndalama wakubayo samadziwa kugwiritsa ntchito zinthu zija. They said they would clear the rubble. Have they cleared it or tripled it?
@McfishMathumba15 сағат бұрын
apa gibho piason ndakufiraso
@WilliamKandani15 сағат бұрын
Achakwera alibe nzeru iliyonse .church ndi kulamulira dziko ndizosiyana.
@MathewsMpanga17 сағат бұрын
It takes a shallow minded person to listen and believe to what these outdated politicians say. Politics is the most profitable business.Hence these speeches.
Mmmm awa asatinamize he is a confused person and he is a crazy person and DPP is better off without him.
@RaphealKwelaniКүн бұрын
Ife tivotola dpp bas
@RaymondKaumbaКүн бұрын
No substance
@TimothyKamanga-t2zКүн бұрын
Pa nkhani ya ziwawa please tiyeni tipewe a Malawi ndeu simamga mudzi
@JimmyWChibweКүн бұрын
Chakwera moto kuti buu!
@memorychirambo4869Күн бұрын
Powerful message
@JanetZeenatKarim2 күн бұрын
This is a very untrue reflection of the history of Malawi. President Chakwera joined former VP Chilima in a court case to dispute the 2019 elections in Malawi. The special constitution court nullified the elections and the Chakwera/Chilima To se Alliance won the 2020 elections. Had party zealots allowed the alliance to operate properly, the Tonse government could have survived. ‘Nuff said.🙆🏾♀️ Oh God bless our land of Malawi!!!
@JanetZeenatKarim2 күн бұрын
Tonse Alliance
2 күн бұрын
Sibweni, let me comment on 2 facts. DPP brought cash gate,and during Bingu world bank and IMF forgave us all the loans,why was the kwacha loosing value?
@HarrisonMwanga-xy4sc2 күн бұрын
Ndipo,inu mcp yalelo ikupanga zosiyana ndi mwambo ya chikhalidwe chathu, achakwela sindikudziwa ngati ndi mmalawi.
@ChrissyBhima2 күн бұрын
Mau,mulungu akudaliseni achimwene
@AdamAhamad-k2i2 күн бұрын
Kumtumbo kwake President okupha angatiuze chani namachende ameneyu
@StevenDastan-f5y2 күн бұрын
Thats true
@omarajibu8602 күн бұрын
Ndipo ndiye zoona zake, lero mchewa akutengedwa ngati munthu wachabe chifukwa cha mmene zilipozi zikuwagwiritsira ntchito achewa. Mwachita bwino kulankhula. Mindset ya anthu a mitundu yina ndi yoti achewa si anthu abwino. Mwachita bwino kulankhula amwene.
@MonijaKataika2 күн бұрын
Will all rest in heaven...if we are to hear the last trumpet that is...
@DerlinNyirenda2 күн бұрын
Kkkkkkk
@DorothyKamanga-l9j2 күн бұрын
Umakwanana ntanyiwaa 😂😂
@JohnSaimala2 күн бұрын
Bwana mukuyakhula mwadzelu ndithu
@jameschidafumbwa10392 күн бұрын
😂😂😂😂😂 Mr msonda you said , politicians don't tell the true, so which side are you?
@NaphiChiwaya2 күн бұрын
Ulemu wanu mafumu a ku nchisi
@Mavuto-b4f2 күн бұрын
Mukulankhula zoona,amene mukutuma anthu kumagulila zikwanje nafenso tilinazo ndalama zoti tikhonza kugulila anthu a kumwera,koma mmalo mwake ndalama zathu tikuthandiza anthu kuti adzipeza chakudya,osati Minister kukhala busy kugulila anthu zikwanje ,komanso l follow up nkhani ya sata ,ndalama zimenezo muthu amene anasainla kutsegulanso ma bank account ameneyo akatenge ndalama zimenezo ndipo athu agulile chimanga ,mankhwala,ma umbulance athu akufa kusowa maambulnce pomwe wina anathawitsa ndalama za boma mabilions,zikufunika zibwelele ndalama zimenezo .Amalawi mwatola mokwanila.
@zayedmitawa83452 күн бұрын
Zautsiru zokhazokha. Iwe uli ku MCP and you're telling us this nonsense. Zomwe Namiwa akunena sakunama ngakhale ukuti ali payroll ya DPP koma mavuto omwe MCP yabweletsa ikupangitsa Namiwa kukhala munthu wa nzeru kuposa MCP. Nthawi zambiri chipani cholamura musamantenge otsutsa ngati mdani wanu.Otsutsa amatsegura maso boma kuti lichite zabwino Kwa anthu ake kuti masiku olamula dziko achuluke instead mumaona ngati it's a political fight. Iweyo Nsonda unali kutiko,pano uli kutiko?
@Homeofpeace3212 күн бұрын
Patricia Kaliati ndamene anaphetsa saulos chilima ku MCP. Don't vote for Patricia Kaliati pau Mp, it's sad kuti she's decided kulowa MCP