Palibe anganvomele choyipa, koma chabwino aliyese amachithamangila,,,
@MphatsoTolaniTolani5 күн бұрын
Koma Brian mafuso Ake akut kuyankhula moshashalika 🤣🤣🤣
@Andesite-M.Y.B6 күн бұрын
May,2024
@BrianZenengeya6 күн бұрын
Ati mpaka phephelere phephelere mwambamu kuti mutamike
@DoshenSulan7 күн бұрын
Kkk padela waung'alula🤣🤣🤣
@PeterMakaika8 күн бұрын
Akulu awa ndi a chitsiru bwanji nthawi ya Kamuzu kukakhala njala ya zaoneni ...wandinyasa bwanji mega farm yamanyi nthawi ya Bingu chimanga chikapezeka kunali ma mega farm iwe usandiyakhulile pa mbali chitsiru iwe
@user-dz4bc3mu3h9 күн бұрын
😂
@PaulChaleka-lb4vx10 күн бұрын
Brian Banda eeeee umakwana kufunsa zomwe amaliwi amadzifunsa mcp 2025 ichoke ndi yathamo
@thewnoc10 күн бұрын
Beautiful woman the former president of the republic of Malawi, very proud of you