BON KALINDO WA LERO FRIDAY 27 SEPTEMBER
16:47
BON KALINDO THE DC 25 SEPTEMBER 2024
17:52
9 сағат бұрын
WAPHA MAMUNA WAKE CHIFUKWA CHA UHULE
18:13
14 сағат бұрын
MCP YAVOMELEZA KUTI DPP IWINA 2025
5:31
19 сағат бұрын
DAN LU ,, NDATULUKA DPP
2:50
Күн бұрын
DJ MUNYANANE 17 SEPTEMBER 2024
23:20
Пікірлер
@EmertonNsato
@EmertonNsato 6 сағат бұрын
Watumidwa ndi mcp galu iwe eti
@JogaJoseph
@JogaJoseph 10 сағат бұрын
This is limpopo fm with comrade mtanyiwa chaka chake ndi chino wina ayalukaaa
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 13 сағат бұрын
Ntanyiwa mwana wakwathu umwa chani broh umakonda thobwa ndikudziwa zaiwe
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 13 сағат бұрын
Chakwera ndi oipa mtima kwambiri
@RosemaryMponda-p9h
@RosemaryMponda-p9h 7 сағат бұрын
Ndipo zowona galu nyani ameneyi
@NoorRasheed-re5vh
@NoorRasheed-re5vh 15 сағат бұрын
100%
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 19 сағат бұрын
Mr Ntanyiwa....inu Ambuye Azikutetezani.....pamozi....ndi team yañu yose tofunila....za bwino A malawi❤
@EmanuelPaul-io2hk
@EmanuelPaul-io2hk 19 сағат бұрын
Pamtumbo wachepetsa koma mumtumbo mwao ana amahulewa
@PetroMatias
@PetroMatias 19 сағат бұрын
Charakwe Ariira😢😮😅🎉🎉
@PetroMatias
@PetroMatias 19 сағат бұрын
Cha ah
@PetroMatias
@PetroMatias 19 сағат бұрын
Vesizir 🎉🎉😢😢🎉
@mahamudufakeri9007
@mahamudufakeri9007 19 сағат бұрын
Big ntanyiwa mulungu azikupasan Moyo wawutali
@LameckNgwangwa
@LameckNgwangwa 20 сағат бұрын
Mangochi m" bomamo !! More fire bro Sallo
@AdamPetro-v2q
@AdamPetro-v2q Күн бұрын
MCP muli pa ma vuto Iwe Atupele ndi bambo akowo ngati mwatopa nayo UDF ingotulukani
@martinkazembe6221
@martinkazembe6221 Күн бұрын
majolite rule ku democrase atsatidwe ndi zoona koma sindekuti ndi chilungamo.
@MphatsoMahata
@MphatsoMahata Күн бұрын
Ndalama zamagazi zitipha Malawi tiyeni tilolerr kukhala osauka for the better of poor Malawi as
@MphatsoMahata
@MphatsoMahata Күн бұрын
Keep on educating Malawi,we love
@BensonMaleza
@BensonMaleza Күн бұрын
Inde ndemanga akulu awa alandila ndalama nanga MCP inayitana UDF nanga akulu awa akuzembayisa nkhani chifukwa DPP inapanga mgwirizano chifukwa imkafuna kuti mgwirizano koma ngati zili choncho ndizachotsa chilichonse no DPP no UDF ndizapanga wipe out wina aliyense mangochi empire wina aliyense asunge mau amenewo ndine Benson Maleza Saidi ndipo dziko ndizalisintha lizakhala Nyasaland tsiku lomwelo from shire highland Yao tribe the dominant tribe of the shire highland into Nyasaland
@ClementsKamanga
@ClementsKamanga Күн бұрын
Akulu muuzen atupele alimbike kampen adzakhala vpc akatelo walowa adadiwo angofuna achotse mcp bas
@amosphakira7936
@amosphakira7936 Күн бұрын
Udf ndi chipani cha MCP Mudxiwe ximenexo
@danmbuzi
@danmbuzi Күн бұрын
Umakwana engineer
@NosiphoMazwai
@NosiphoMazwai Күн бұрын
Zoonadi
@imranhopewell-yv4zc
@imranhopewell-yv4zc Күн бұрын
Galu iwe chokapo ukutinyasa
@shaibuakimu6141
@shaibuakimu6141 Күн бұрын
Chisilu iwe wa mcp choka galu
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Күн бұрын
Gwilizano ulipo ndi Mcp muziwe zimenezo amakumana kuseli
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 Күн бұрын
MCP TAYEDZEKA
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 Күн бұрын
😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂yomweyo Chikangawa yakwiya ndi mizimu 😅😅😅😅😅😂😂😂😂
@gracemnenula2518
@gracemnenula2518 Күн бұрын
Kodi mayi Lilian mulikuti kusiyira ameneyu
@marthablessings1314
@marthablessings1314 Күн бұрын
❤❤❤love Comrade
@RiteRoderick
@RiteRoderick Күн бұрын
Members a UDF big up mumatha koopsa zed this is how to handle issues. MCP isapitekoyi ndithu
@RiteRoderick
@RiteRoderick Күн бұрын
Apapa kuvuta zedi ndipo zipani zotsutsa zonse zisapiteyi akangoitana MCP
@Kenmoney-xp7tz
@Kenmoney-xp7tz Күн бұрын
Kuteroko anyani anzake azikavina kumulandila pa airport including bataa manganya
@MARAWIANMEDIAFM97
@MARAWIANMEDIAFM97 Күн бұрын
NTANYIWA bakiri muruzi TV Bon karindo sitisiyana mpakana woooooo 2025
@GrivinSauka
@GrivinSauka Күн бұрын
Kuyimbaaaaaa kuyankhula??? 😂😂😂😂😂😂😂 Zomvetsa chisoni. Makape mwasowa choyankkhula
@PeterMhon-n6c
@PeterMhon-n6c Күн бұрын
Acomrade musafe awulureni mutiphure mumavuto
@jacklinenkhata
@jacklinenkhata Күн бұрын
Uku timamveleko zambiri
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v Күн бұрын
Anthu awa ndi zilombo 2025 ndipo kwatalika
@EryvinMhango-zl3oh
@EryvinMhango-zl3oh Күн бұрын
Usadzafe udzangosowa
@isaaczuze
@isaaczuze Күн бұрын
My vote is for Apm osati chisilu chimene tili nacho lelo .....munthu wosamva uyu
@pidona825
@pidona825 Күн бұрын
I like you Mr and I always pray for you
@ChimwemweSauka
@ChimwemweSauka Күн бұрын
Welcome antanyiwa
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 2 күн бұрын
Amalawi muleke kususuka ndikutengeka kuma landila ndalama za magazi zotembeledwa za satanic muzasowananzo mtendele MCP ikatula m'boma popaze pangano supangana ndi satana imafika nthawi yomwe azafune kutolera.be carefully you have warned.
@JusticeNakhaonga
@JusticeNakhaonga 2 күн бұрын
True
@Maulana-s2n
@Maulana-s2n 2 күн бұрын
You Lilian Patel if MCP will come to attend that convention don't come to your constituency here at bwananyambi because you have nothing here
@Maulana-s2n
@Maulana-s2n 2 күн бұрын
Comrade Ntanyiwa Kodi a chair a bakili muluzi bwanji osangomuchitsa a Aishah yu? Pomaliza a comrade munditumizile kanyimbo mukutumikila nakoka Kuti ikhale tone mu phone Yanga chonde
@AnthonyPhiri-e3g
@AnthonyPhiri-e3g 2 күн бұрын
Freedom is coming tomorrow continue 💪 power Limpopo
@TinoChipangura
@TinoChipangura 2 күн бұрын
Ineyo number 5
@lenardLysson
@lenardLysson 2 күн бұрын
❤❤❤wawa big man
@JamesRodrick-ym7cc
@JamesRodrick-ym7cc 2 күн бұрын
Mumakwana
@JamesRodrick-ym7cc
@JamesRodrick-ym7cc 2 күн бұрын
Kenako ineyo
@cmsanyama200
@cmsanyama200 2 күн бұрын
Oyamba ndine kuyimvera nkhanga zaona lero bwana Mtanyiwa.