TONDE WADULA DRAMA SERIES  - EPISODE 115
29:24
Adyesedwa nyama ya galu
0:32
Күн бұрын
TONDE WADULA EPISODE 113
27:54
14 күн бұрын
Michael Usi Vice president of Malawi
5:42
Funeral June 2024 Recap
3:25
Ай бұрын
MBIRI YA LUCIUS BANDA
6:19
Ай бұрын
MBIRI   HISTORY   MR  MAKANDE
56:40
2 ай бұрын
NKHANI YA IMFA YA EDSON CHILEMBA
17:06
DOUBLE SHOT Muzik NDICHANI
2:48
2 ай бұрын
Пікірлер
@Felixcanadad3j
@Felixcanadad3j 2 сағат бұрын
Mr usi mukuoneka Kuti munatuluka ndithu mukukana mukudziwa
@PaulRobertKamanga
@PaulRobertKamanga 3 сағат бұрын
Gaga ndi mlamu ndi 1 lv it
@user-bq2zb1pc8m
@user-bq2zb1pc8m 4 сағат бұрын
Mutengele Ku khoti mwana wachibwana😂😂😂😂😂😂Mr Zimveka😂😂😂
@Christophermoh430
@Christophermoh430 9 сағат бұрын
Koma nzimveka sazatheka 😅🤣🤣😂🤣
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 10 сағат бұрын
Usi usadandaure ayi iweyo bola ukudya ndarama zako zayenda koma kumbukirani kuti ife anthu tikuvutika tikugonaninjara
@NancyBanda-g2j
@NancyBanda-g2j 11 сағат бұрын
😂😂😂😂😂kma usi anakonza eish
@FraserNamaona
@FraserNamaona 12 сағат бұрын
Character ya Makwale imandibowa kwambili
@Linly-w2k
@Linly-w2k 12 сағат бұрын
Manyiwa ndi anga kma mikodzoyi siyanga huuuuu Zimveka zamuvuta
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 13 сағат бұрын
Nde zauchtsilu tu izi chamba chani ndi ndalamatu izi apapa siposewelatu apa timaphunzilapo zambiri
@chibambarichard22
@chibambarichard22 14 сағат бұрын
GAGA ALEMEKESEDWA SOPANO 😂😂😂😂😂😂
@MunimushyJumbo
@MunimushyJumbo 18 сағат бұрын
Tisiya kukutamangilanitu
@user-qs2tx7wt6g
@user-qs2tx7wt6g 18 сағат бұрын
Mwayamba kusowa zoponya etiiiiii
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani 19 сағат бұрын
Mr Muthintha mumatimirila
@jimybashil5350
@jimybashil5350 Күн бұрын
Izinso nde ziti aaaaaaa
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o Күн бұрын
Zaziiii
@Chikwayakalongolo
@Chikwayakalongolo Күн бұрын
Am watching in Zambia, at kasumbalesa
@TrishBanda
@TrishBanda Күн бұрын
Too bad
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi Күн бұрын
Watching from pretolia nice❤
@user-ju4uf5ht4y
@user-ju4uf5ht4y Күн бұрын
RIP 😢am from Zambia 😢
@BensonChilundu
@BensonChilundu Күн бұрын
Ndiye wina mkumati chipani cha Malawi Chikangawa Party ndi chabwino simwaona ochitsatilawo momwe akuchitila kupha mzawo ngati nyama yet munthuyo amamudziwa,ayi ndithu sichilungamo ndipemphe kuti chilungamo chidzawoneke uyu ameneyu akadzachoka pa mpando.Ndi odala padakali pano komano popeza mlandu siwuola and mawumboni onse alipo ndizotheka ndipo omwe amapha nawowo adzakalowa limodzi pangachedwe pangafupike
@AfickDaud
@AfickDaud Күн бұрын
Amuthinda ingomkwatirani Shameela atha kukhala wife material ndpo mutha kutukuka naye ndthu
@user-pq5bo5ch3m
@user-pq5bo5ch3m Күн бұрын
Ndipo nde ili nyatwa
@patrickzembani4315
@patrickzembani4315 2 күн бұрын
Koma Gaga ndi Zimveka ayi zikomo boza mumalikwanirsa😂
@alstonemagombo2377
@alstonemagombo2377 2 күн бұрын
Mphunzitsi uyu eeeh
@user-zj5dm7il2z
@user-zj5dm7il2z 2 күн бұрын
Akut ndizikupasa moni yekha
@user-wc7hf7wg1d
@user-wc7hf7wg1d 2 күн бұрын
Achswa samb😂😂😂😂😂
@user-wc7hf7wg1d
@user-wc7hf7wg1d 2 күн бұрын
Emmah nda Adad awo amanjoyatu
@wilsonkuyere9554
@wilsonkuyere9554 2 күн бұрын
achiswa mukuyiyendesa udyo nkhani kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
@clalesschisale3792
@clalesschisale3792 2 күн бұрын
Set up yanu munaiphonya mukanalola mkaziyo alowe mnyumba then Dora ndikuzatulukila zikanabebaso 😂😂😂
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 2 күн бұрын
Koma gaga gaga bodza iiiiii🙌
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 2 күн бұрын
Nyc ❤
@clalesschisale3792
@clalesschisale3792 2 күн бұрын
Chiswa kukokera kwake cholinga azidya shamiiru 😂😂😂😂😂😂
@FrankJoshua-zr9pw
@FrankJoshua-zr9pw 2 күн бұрын
😅😅😅😅Good drama koma muzipanga everyday not once a week ,Kodi ife akumalawi tikusalila pati? Za once a week zamakezana muma 80th ngati pamajiga
@nkhalangomultimedia
@nkhalangomultimedia Күн бұрын
Nkhani ndi ndalama bwana, Episode imodzi kuti itheke imafuna ndalama zosachepera 650,000 normally
@patriciatembo3095
@patriciatembo3095 2 күн бұрын
Achiswa muli ndimabodza paja inunso mumamfuna shamilayo 😂😂😂😂
@nkhalangomultimedia
@nkhalangomultimedia Күн бұрын
Amadya osati kumufuna chabe
@user-dx5dc4sm5v
@user-dx5dc4sm5v 2 күн бұрын
Watching from America
@JoelSawasawa-h1e
@JoelSawasawa-h1e 2 күн бұрын
...
@FraserNthewa
@FraserNthewa 2 күн бұрын
Achibiriti anamwalila pa 16 June 2024
@dytonmoyo4629
@dytonmoyo4629 2 күн бұрын
❤❤
@IbrahimAdam-pb7rn
@IbrahimAdam-pb7rn 2 күн бұрын
Watching from kraaifontein, Cape town
@user-sz2lv3xm9q
@user-sz2lv3xm9q 2 күн бұрын
Gaga ati mlamu uli ndima dress ambiri 😂😂
@user-sz2lv3xm9q
@user-sz2lv3xm9q 2 күн бұрын
Zimveka ku khothiko uzikati chani iwe😂 akugwira red handed 😂😂
@user-zd2ne1ic2v
@user-zd2ne1ic2v 2 күн бұрын
Atonde arikut koma
@CalebPhiri-mi3me
@CalebPhiri-mi3me 2 күн бұрын
😂😂zimveka ndi one😅
@user-hs8px9mp8g
@user-hs8px9mp8g 2 күн бұрын
more fire 🔥 mmatimvesa kukoma mabwana inu,,, Pitilizani kutisangalasa
@user-hs8px9mp8g
@user-hs8px9mp8g 2 күн бұрын
mr Chiswa musanamize mzukulu wanu kuti mkazi salibeuno 🤣🤣🤣🤣🤣🤣 mpaseni mpata akwatile
@user-hs8px9mp8g
@user-hs8px9mp8g 2 күн бұрын
mr Zimveka mmatha kuthawa mnkhani kkkkkkkkk ulemu kuyitembenuza nkhani pompo pompo 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@MathewsBanda-s4s
@MathewsBanda-s4s 2 күн бұрын
Shamira wavuta
@AlinafeMoses
@AlinafeMoses 2 күн бұрын
Achiswa ingoululan musamuipisile mbili tsikanayo
@CassimabdulEreven-i3u
@CassimabdulEreven-i3u 2 күн бұрын
May phiri kuteng mary kumudzi chisakhare chiphidyo. Mukuteng mary ngt wantchito
@enockmsakatiza1683
@enockmsakatiza1683 2 күн бұрын
Zimveka my actor 😂😂😂