A Boma akufuna kumugula Kalindo kuti asiye kuzudzula boma

  Рет қаралды 16,453

NZIKA TV

NZIKA TV

Ай бұрын

MCP ikufuna kuzabera zisankho in 2025

Пікірлер: 136
@JohnyJoy-vf6vq
@JohnyJoy-vf6vq 29 күн бұрын
Ndimamunyadira boni kalindo🎉
@GiftChiposi
@GiftChiposi 29 күн бұрын
Munthu ameneu akamayakhula zimaoneka ngati zopanda tchito koma sikulina tizamukumbukila
@HopeMakoka
@HopeMakoka 28 күн бұрын
Nkulu Wa MEC Mulungu akulange pamodzi ndi banja lako lonse ukufuna tipitilire kuzunzika ndi chipani Chopepera mmachitidwechi
@alickkachepa3801
@alickkachepa3801 29 күн бұрын
More 🔥🔥🔥 Bon kalindo
@PeterJanuary-lu3hc
@PeterJanuary-lu3hc 29 күн бұрын
Fire 🔥 Mr pangolini
@MaxwellMaxwell-zv9oj
@MaxwellMaxwell-zv9oj 28 күн бұрын
Bon adaima pa chirungamo mulungu azikutetezera nthawi zonse
@NomalaJessie
@NomalaJessie 23 күн бұрын
God bless you brother
@user-nn2mj1gt3f
@user-nn2mj1gt3f 27 күн бұрын
Ngat chilima akufuna tikhulupilireso ndye atithandize mcp isabeleso ma vote
@JuliusChipondaEphraim
@JuliusChipondaEphraim 29 күн бұрын
Mene ndimaziwila pangolin sizingatheke kumugula bare wangayi
@GodsonLindan-hn4kp
@GodsonLindan-hn4kp Ай бұрын
Layton mangochi wagulidwaditu , the DC mumayankhula zanzeru, akukunamiza anthu aupanduwa , cholinga apitilize kunzuza anthu m'ziko muno. Mulungu awakantha ,asamasewelese anthu amulungu.
@mauricetayali8041
@mauricetayali8041 Ай бұрын
Boni kalindo kutokota, akamuna,. GOD protect you
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 Ай бұрын
I love this one
@user-rd4ft9nd8t
@user-rd4ft9nd8t Ай бұрын
Congrats bro we are proud of you bro mumatimira God bless. you.
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba Ай бұрын
Keep it up bro, boma ili ndilausilu kwabas
@HajaSande
@HajaSande Ай бұрын
Mundu wakulu ukuyamgula zondigwila tima
@dontreybanda278
@dontreybanda278 Ай бұрын
Good job boss
@JimsonChisi
@JimsonChisi Ай бұрын
The DC president waife anthu Osauka ndinu mbambande boss❤❤❤
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg Ай бұрын
The DC boooooooooooooooooon kaliiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiidooooooooooooooo
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r 26 күн бұрын
Ada inuyo ndinu Daniel muzenje ramikango ayi ndithu ambuye azikhara mbari yanu abro kukana ndarama mmene wavutira marawi panopa sichinthu chopweka akuru inu mma opadi chauta sure
@AlinafeChimoto-pp7wp
@AlinafeChimoto-pp7wp Ай бұрын
God bless you
@user-rd2td7bg4c
@user-rd2td7bg4c Ай бұрын
The DC❤❤❤❤ timakudalilani god bless you
@user-ni4nw1ee2f
@user-ni4nw1ee2f 28 күн бұрын
Yhooo boooon
@MaxwellChidothe
@MaxwellChidothe Ай бұрын
Continue brother mumatiimilira
@user-mi2xf3sw1i
@user-mi2xf3sw1i 28 күн бұрын
The Dc❤❤
@GeoffreyMaulana-rh5rx
@GeoffreyMaulana-rh5rx Ай бұрын
You are the best mr Bon Kalindo keep it up we love you ❤❤❤❤❤❤
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl Ай бұрын
Keep it up mr born kalindo ❤
@EdwardGeorgeKasabola
@EdwardGeorgeKasabola Ай бұрын
The DC osalora zoputsa za anthu oputsa amenewo
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt Ай бұрын
Mbambande Inuyo Mr Dc mumakwana
@bensonmughandira
@bensonmughandira Ай бұрын
Tango tchulani dzina la munthuyo .
@user-hh4wn4vf9e
@user-hh4wn4vf9e 25 күн бұрын
DC ❤
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g Ай бұрын
We're proud of you bwana DC
@FOSTERLUPIYA-zc1xv
@FOSTERLUPIYA-zc1xv 26 күн бұрын
MCP is a matured party with mature leadership than any party.Bon kalindo is not matured to be wanted in MCP.
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g Ай бұрын
Otsutsa BOMA akugona zedi
@felixbanda8356
@felixbanda8356 Ай бұрын
Mmesa umati a Malawi si anthu owafera. Maloto awa satheka. Continue with your drama. Wauponda. Osamatchula dzina la mulungu pachabe.
@user-oe1lg4xo7w
@user-oe1lg4xo7w Ай бұрын
My brother Kalindo zikomo poyika zinsisi za mcp pa mbalambanda awatu achera kumwezi nkhanga zawona. Mulungu akuyankhulanso ku buku LA Amosi 3 v ya 7 sazachita chinthu kwa Anthony are osaululira chinsisi atumiki are. Ndiwe ntumiki wamulungu the DC .
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Ай бұрын
100% DC carryon
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf Ай бұрын
Waooooooooo Bon kalindo
@JumahMchikoma-lt1lu
@JumahMchikoma-lt1lu Ай бұрын
DC president wa anthu osauka❤❤
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Ай бұрын
Koma mcp ili ndi chintchito chachikulu ay bpp u d f yazivera yokha
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t Ай бұрын
Kod osusa boma alipo
@user-nc1uv3be1v
@user-nc1uv3be1v Ай бұрын
Bone for the youth
@redsonmunlo6460
@redsonmunlo6460 Ай бұрын
Za drama izi zauchitsiru zenizeni
@user-ol3qi1kd5u
@user-ol3qi1kd5u Ай бұрын
You mas be the president of Mangochi
@Moses51
@Moses51 Ай бұрын
The DC bon kalindo we done ✅💯 note
@BrianZenengeya
@BrianZenengeya Ай бұрын
Zikomo bwana DC
@chifunirosaka9077
@chifunirosaka9077 Ай бұрын
Amen God is good
@redsonmunlo6460
@redsonmunlo6460 Ай бұрын
Mkazi wake uti? Uli ndimkazi iwe? Ana ake ati, umatha kulora ana iwe, ulibe mwana ophunzira ndimmodzi yemwe. Ana ako onse akuba iwe.
@user-yi4oc4xz4v
@user-yi4oc4xz4v Ай бұрын
We need pipo like u
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w Ай бұрын
Koma pitilizani kutiyimilila bwana DC
@user-xj9uy6wz7b
@user-xj9uy6wz7b Ай бұрын
The dc mbambande
@SmilingFishingRod-zc4wx
@SmilingFishingRod-zc4wx Ай бұрын
Wina ndiye amugula kale LYSON MANGOCHI
@user-hy5fm1ph7f
@user-hy5fm1ph7f Ай бұрын
Mbuli ngati imeneyo agile ndani poti chakwera wamaliza ma term ake kale
@TonicBeza
@TonicBeza Ай бұрын
Bodza renileni
@KanduloTauzi
@KanduloTauzi Ай бұрын
Musamavutitse anthu ngati dzikoli munasonkhelana ndi mulungu,, mulungu athana nanu
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w Ай бұрын
Akakuthyolani kholingo ,mukupanga zibwana ndi MCP eeti , si anthu a Mulungu tu awa ,wosamapanga chibwina ndi MCP ayi
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m Ай бұрын
The DC ❤❤❤❤
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q Ай бұрын
❤❤❤💪💪💪💪
@MatthewsJanuary-wr3rf
@MatthewsJanuary-wr3rf Ай бұрын
Noted
@mauricetayali8041
@mauricetayali8041 Ай бұрын
Osapitako, kumeneko ali ndi chiwembu amenewo
@YughozMaonga-ft2ny
@YughozMaonga-ft2ny Ай бұрын
Where is Mtambo😂😂😂
@linleybisani5856
@linleybisani5856 Ай бұрын
Koma tsitsilo mmmmm ayi
@user-gg6uh2wo4x
@user-gg6uh2wo4x Ай бұрын
The dcccccc
@BrianZenengeya
@BrianZenengeya Ай бұрын
Zikomo bwana
@lovenesskampira
@lovenesskampira Ай бұрын
Ndiye tingazithetse bwanji poti ndife anthu wamba
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Ай бұрын
We're with you forever Booooon Kalindoooo
@AffickChaona
@AffickChaona Ай бұрын
The DC Bon kalindo
@jangiya03
@jangiya03 Ай бұрын
Ooooo anthu ndiopsa awa
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga Ай бұрын
kusalima kuja udapitako bwanji uzinamiza ana apa ukuopa chani
@user-uv3lo3mx3v
@user-uv3lo3mx3v Ай бұрын
Don't ever try to go, angakakupweteke
@user-rm8jd9mu8r
@user-rm8jd9mu8r Ай бұрын
Bwanji umaleka kupanga recording call yo? Tikhulupilira bwanji popanda umboni?
@matthewsmuwa7645
@matthewsmuwa7645 Ай бұрын
Ing'aluren a DC
@user-lw4hw9ce4w
@user-lw4hw9ce4w Ай бұрын
Tipemphere zenizeni zikomo kwambiri a DC
@lloydmalinga1198
@lloydmalinga1198 Ай бұрын
Mbwiye ntchito mukuyigwira.
@EvanceMakuluni
@EvanceMakuluni Ай бұрын
Kodi nanga nkutani? Kuti zimenezo zisachitike
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v Ай бұрын
Fuso kodi aboni kalindo muvomera kugulidya
@DylesMtenje
@DylesMtenje Ай бұрын
Winiiko umatiimilila well dan
@SniperWonder
@SniperWonder Ай бұрын
The pangolin
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z Ай бұрын
NO PAIN NO GAIN THE DC BON KALINDO
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Waboza iwe wadya ndalama zingati zochokela kuboma komaso waanthu andale .ndani amene sakuziwa uzinamiza alomwe anzako wo chisilu galu
@user-sw8bb3iz7x
@user-sw8bb3iz7x Ай бұрын
Yabaya
@Dysonkhofi
@Dysonkhofi Ай бұрын
Chisiru ndi iweyo machendeako,wakongiresi nyani,Bon Kalindo Viva!
@nellietchuwa9913
@nellietchuwa9913 Ай бұрын
Ukanapita kut pakhale umboni nanu
@user-fe7fb3nw5h
@user-fe7fb3nw5h Ай бұрын
Emena mwayakha bwino ambuye akundarisen mulungu ndiothekera tipambana musaderekhawa mulungu akupambanisani
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 Ай бұрын
Koma ndiye kulamula MCP anakufunisisatu
@yankhofreemansomanje6433
@yankhofreemansomanje6433 Ай бұрын
U wish 🤣
@user-wi9hz8fk8i
@user-wi9hz8fk8i Ай бұрын
Vuto ndiwe wa chipani kalindo
@godfreyalberto7425
@godfreyalberto7425 Ай бұрын
Chenjere akupha
@JosephJosab
@JosephJosab Ай бұрын
2025 MCP thithithiiiiiiii kumenya kugwetsa
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
Eeee tili pa mavuto a Malawi..
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
Munthu wa mkulu kwambiri The DC'S
@marygoza1205
@marygoza1205 Ай бұрын
Tsitsilo bwana kalindo silibwino ayi.
@mamulemathekga
@mamulemathekga Ай бұрын
Eee mavuto alipo kumalawi chakwera
@user-sw9ov2yt7b
@user-sw9ov2yt7b Ай бұрын
Mmaitha bwana kalindo
@johnkambala692
@johnkambala692 Ай бұрын
Mabodza pano ai
@VincentNyabanga-dw9uj
@VincentNyabanga-dw9uj Ай бұрын
APM vote,
@JosephJosab
@JosephJosab Ай бұрын
Mcp 2025...thithithiiiiiiii kumenya kugwetsa
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba Ай бұрын
Sono tinkhulupilile ndan pot amekioo ndiamene timadalila kwambiri?
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
Mulungu alipo sagona tulu ndipo saozela atimenyela khondo ndithu
@FOSTERLUPIYA-zc1xv
@FOSTERLUPIYA-zc1xv 26 күн бұрын
Drama at its best.
@philipmgbebig165
@philipmgbebig165 Ай бұрын
Mulungu azikuyan g'anilani aboni
@user-wi9hz8fk8i
@user-wi9hz8fk8i Ай бұрын
A kalindo chamba chakupwetekani. Bwanji osapanga record ngati umboni. Wamisala iwe ndithu
@ApocheC.
@ApocheC. Ай бұрын
osamapusa, private # siimatheka record
@meltonMumba-dc4pf
@meltonMumba-dc4pf Ай бұрын
The DC
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o Ай бұрын
Bwinotu angakakupheni kokumanako
@RCFAKI-mx4dv
@RCFAKI-mx4dv Ай бұрын
Malawi wabvuta
Grote aardverschuiving in Papoea-Nieuw-Guinea
1:59
NOS Jeugdjournaal
Рет қаралды 15 М.
NEW CALEDONIA | A New Insurgency?
14:07
Prof James Ker-Lindsay
Рет қаралды 65 М.
Zo ontruimde de ME het bezette pand van de Radboud Universiteit
2:43
Omroep Gelderland
Рет қаралды 4,7 М.
Restaurant ingestort op Mallorca, zeker vier mensen omgekomen
1:33
NOS Jeugdjournaal
Рет қаралды 34 М.
Jongeren voelen zich slechter over hun gezondheid
4:26
Omroep West
Рет қаралды 1,1 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51