A MICHAEL USI KUYANKHULANA MOZEMBERA

  Рет қаралды 4,598

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 29
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 42 минут бұрын
Amene kupanga za size make gather here kkkkkkkkkkkk koma malawi izi ndiye iti
@stanleykundembo7765
@stanleykundembo7765 Сағат бұрын
Mulungu simunthu a malawi mwanva verse limene Michael usi wamaliza nayo mulungu akufuna kutichenjeza kuti tichenjere nalo boma ili la chakwera chifukwa ndilamwazi wangomaliza ndi verse limeneli mosazindikila popeza mulungu akafuna kuyankhula ndi ana ache amadzela munjira zosiyanasiyana ina mwa iyo ndi imeneyi koma Michael usi sakuzindikira.
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 47 минут бұрын
Awusi inuyo sitikukulupililani ndinu ofoila , kodi iweyo bwanji wangoti ziiii pakafufuzidwe a report laifa ya chilima
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb 23 минут бұрын
Andale mumakonda kubisala mwa mulungu pamene simuchita zamulungu.
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Сағат бұрын
Manganya akuyesesa kuti aziwe mau a Mulungu koma akulephera kutuluka munyumba ya falawo
@GiftMusorola-l2o
@GiftMusorola-l2o 49 минут бұрын
Kodi mchifukwa chani mbuli zina Zama socials media Ku ma Facebook amalimbana Ndi manganya mukutaya nthawi bambo Ake Ndi mai ake anamupitisa Ku school mbuli inu zinakukanika mzanutu Sazasauka Vice president siudindo wamasewera azadya pashoni yake mpaka Kuga iwe ukukukuta mano
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 44 минут бұрын
Tilibe nazo tchito zokukuta Mano ifeyo koma tufuna ulamulilo wa bwino, uli iwe atakhupela bambo ako ungalakhule zimenezo
@sydneysitima5093
@sydneysitima5093 2 сағат бұрын
The talk of no relevance today,the government & leadership no one has trust with
@tasmania527
@tasmania527 10 минут бұрын
You don't have trust in the government and leadership, but others like myself do have trust in the leadership and its government. Do not generalize your dislike of the current regime because some of us see a future prosperity being laid as a foundation now. We were in Malawi when companies were closed by the previous regimes. We were in Malawi when irrigation schemes and cattle ranches were left in shambles. We were in Malawi when the Capital City was neglected. We were in Malawi when roads wore a new face of potholes. We were in Malawi when MDC was rendered unnecessary by the regime after Kamuzu...the list is endless. Those who hate Chakwera do so due to tribalism and not due to his failures. Musamakhale anthu amkwiyo popanda justification. Play a role as a citizen of the country to help feed your family or develop the country. God hates laziness and anger plus pride.
@Patrick-kambala
@Patrick-kambala Сағат бұрын
Km munthu ngt akukanika kumanga church chitukuko adzachita bwanji?.. ndatchula dzina ngt😂
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 58 минут бұрын
THIS IS JUST A NOISE MAKER.THE SHORT DEMON
@saidimwanyali8969
@saidimwanyali8969 Сағат бұрын
Kodi David mbewe ndi kuyambisa chipani kuja akupita Ku MCP
@Mafosayilesi
@Mafosayilesi Сағат бұрын
Galu iwe Pali mfundo apa
@FidesChandama
@FidesChandama Сағат бұрын
Usamale iwe a gift ponde ponde ali mmodzi ngati iwe koma adamusowetsa ndiye iwe ndindani
@VitumbikoKaunga
@VitumbikoKaunga 54 минут бұрын
Ukanakhara wachifundo bwenzi ukupha anzako mbuzi iwe
@YusufLiffah
@YusufLiffah 2 сағат бұрын
Kod mpakana ma verses Bible kkkkkkkk
@SaidSamuden
@SaidSamuden Сағат бұрын
Ikuthandiza mesa inu mukumazivela pomwepo
@HassanTwaibu-c6h
@HassanTwaibu-c6h Сағат бұрын
usi uli patunda dikila sasakasi yikufikila inshallah
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 сағат бұрын
Usi iwe ndi mbuzi yamuthu
@GiftMusorola-l2o
@GiftMusorola-l2o 46 минут бұрын
Iweyonso ndiye galu weniweni osawuka uhule wamakolo ako unakupangisa kuti jkhale osawuka manganya is VP WA dziko la Malawi ngakhale kwazungu akuziwa kuti kumalawi VP Ndi manganya
@GiftMusorola-l2o
@GiftMusorola-l2o 45 минут бұрын
Umafuna adankhe vp mbuli yakumuzi zosaphunzira ngati banja lako
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 41 минут бұрын
Kape iwe usanditayise thawi yanga iweso ndi crocodile team wamva
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 41 минут бұрын
@@GiftMusorola-l2o kape iwe usanditayise thawi yanga iweso ndi crocodile team
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 35 минут бұрын
@@GiftMusorola-l2o voice president wakuphayo anapha nawo chirima manganya ndi crocodile wakoyo wamva iwe kumayenda ndi dziko ase
@SEEJSHJEFFREY
@SEEJSHJEFFREY Сағат бұрын
Palibe chamzeru akalankhula awa
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 Сағат бұрын
Mbunzi iyi usi
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika Сағат бұрын
Chikangwa
@ShuqItwa
@ShuqItwa Сағат бұрын
Usi ndi munthu oipitsitsa uyu, mavesi ngati munthu opemphera
MICHAEL USSI KUYANKHULA MOZEMBERA DAVID MBEWE KU MACHINGA
21:48
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 1 М.
Сюрприз для Златы на день рождения
00:10
Victoria Portfolio
Рет қаралды 2,6 МЛН
Cool Parenting Gadget Against Mosquitos! 🦟👶 #gen
00:21
TheSoul Music Family
Рет қаралды 33 МЛН
Wait for the last one 🤣🤣 #shorts #minecraft
00:28
Cosmo Guy
Рет қаралды 14 МЛН
Kluster Duo #настольныеигры #boardgames #игры #games #настолки #настольные_игры
00:47
ENGLISH SPEECH | PALKI SHARMA: India's Right Path (English Subtitles)
14:44
Highlights: Mighty Mukuru Wanderers 1-2 FCB Nyasa Big Bullets
9:49
Nyasa Big Bullets
Рет қаралды 13 М.
Prince Of YEMEN Meets President TRUMP!
12:23
Dulla Mulla
Рет қаралды 337 М.
Usauver S10E01   MULA
23:34
Piksy TV
Рет қаралды 41 М.
LUNTHA TV  |  CDEDI PRESS BRIEFING - LILONGWE |  27  OCTOBER, 2024
Luntha TV official
Рет қаралды 24
Сюрприз для Златы на день рождения
00:10
Victoria Portfolio
Рет қаралды 2,6 МЛН