I agree with you, I have been a victim of corrupt lawyers, they take your money and run away without helping, the so called senior councils
@RheggieIssahКүн бұрын
Am proud of you. Keep it up.
@ethelmkonkha69214 күн бұрын
I like that qoute" Good people need to meet and discuss" because Evil people also meet to discuss their evil plans. Oh God bless our land of Malawi keep it a land of peace.
@JonesChingaya-yf4gg2 күн бұрын
One thing, Kamangira you should do is to choose a language. To present your this program. Zomayankhula chizungu ndi chichewa pena sizikumakhala bwino.
@SolomonMumba-i5n3 күн бұрын
I like your views coz you put them as they are. Big up grootman
@BrightPhiri-bt6ev4 күн бұрын
Iwe ndi munthu wankulu simply you are the best ❤❤❤
@LufeyoMlumbe4 күн бұрын
That's our men,can't wait to see you bcomin our chief of justice to take out this nyakanyaka in dis country, we salute you sir
@gracem-y8p3 күн бұрын
Been watching this for the longest. Based on lived experiences, and when you hear this you wonder whats left of the country. It looks like there is competition to be the most corrupt and this goes all the way to ground level. Private individuals, all the way to the village, are now culturally corrupt. The question is, with this level of thiefocracy, who will turn things around?
Well done kamangira, you are an honest and brave man to lecture every one of us
@geofrybanda46014 күн бұрын
May God Almighty bless you, protect you and give you energy
@StevenMasiku-xe4zx4 күн бұрын
You need to be sober so that you understand this man, otherwise uzingotukwana
@AlickMDayi4 күн бұрын
We are be hide you brother AK keep up good work💪🏼💪🏼❤️
@moffatbanda-p3z2 күн бұрын
Osapanga zachipani ai Imani mbali yanu ija ya judge corruption not kumati ine ndiwa mcp ai
@DavidPhiri-o6w4 күн бұрын
Government of the people for the thieves by the thieves😂😂❤❤ng'alula don't keep one in the under pit.. aliyese must be checked
@kondwanienock4 күн бұрын
True fighter osat ojiya,,kutchaya mbali zonse sizandale koma chilungamo basi
@UnjiunjiGeneral4 күн бұрын
Mudzina la tate. La mwana ndi mzimu oyera. Amen
@EmmanuelGordon-q9s4 күн бұрын
Channel iyi ili bho❤❤
@nelsonarthurphiri990111 сағат бұрын
Wachamba iwe . U r more of Chikangawaism guard
@Saeed-r3z4 күн бұрын
I igree with him coz chilima anali ndi katangale yooopya angakhale akanakhala Ali moyo sakanakalandira ulemu nziko muno LA malawi
@ErnestGwelema4 күн бұрын
What a genius lawyer 😅😅
@funghiemw4 күн бұрын
As evil people meet and discuss ways of doing evil to particular people or society, indeed good people should also meet, strategizing on how to do good. The world remains in trouble today, not because of the people who are actively committed to do evil, but rather because of the people who are tolerating evil.
Even amene anafa ul😂ula, asazitenge ngati Iwo anali ayera mutima mbavwa ndi mbavwa If chilima was sizina nitole yankhula, ngati Chakwera ndi mbava yankhula Yaya bingo , Peter Joyce Banda ndi muluzi wonse aponye poyera tiziwe chowonadi... chilima usamuwope Poti dzina lake ndi Champaign wa UTM... Ulula chilichonse
@OmegaChingamuka4 күн бұрын
Ndimankonda uyu koma zonena munthu oti anamwalira ayi apa pokha akulakwa munthu wakufa sakamba nkhani tiyeni tizinena amene ali moyo kuti ngati kuli kukhamba nkhani tikambe ndi amenewo or kayima pa khothi zitheka koma munthu wakufammmmmm kulakwan
@AndrewKadammanja4 күн бұрын
Ofcourse, kaya ukunena zoona za SKC, kmno szngatithandze chfukwa wakufa saimbidwa mulandu, and udalikut pot Chilima adali mu court? Munthu akapezeka olakwa pa milandu yakatangale chilango chake ndkuphedwa? Ndchfukwa chan munasankha kumupha? Mot onse akutibelawa tikuenera kudzawapha? Uyankhe zimenez Kamangila please 🙏
@AbdulsharifulKalipinde-m6u4 күн бұрын
We are suffering because of rich people Tiyeni tapase mphuma amkulu amkulu
Bwanji sunabwere anthuwa ali moyo umaopa chani. Udwalatu ndi dzindevu zako
@WilliamBanda-rw7yw4 күн бұрын
Akamangira ndimakonda kukuvetserani please ngati muli ndizithu n ndiwumboni wake please just take them kumabwaro amirandu tikuphuzira zambiri from u tikufuna tive kuti ena mulinawo kumabwaro amilandi bcz kuchokera tsiku munayamba khanizi no one was arrested or anachotsedwa ganyu wake
@HarryMsudzula4 күн бұрын
My brother please try to use chichewa when you are sharpening the eyes of vulnerable malawians chizungu munthu amene sanaphunzire ndibwino azimva nawo cos ndiamene amafinyidwa kwambiri if you use English ndi anthu ochepa kwambiri omwe angamakumvese komanso angamakutsate ndiochepa
@FracksonMadani4 күн бұрын
Ndilibe nazo ntchito kuti Chilima kaya muti anali wakatangale, koma munthu uja potential ya utsogoleri adali nayo and zolankhulazotu singandibwenze mmbuyoooooo Ine vote for DK basi
@FracksonMadani4 күн бұрын
M'malo moti uzikamba zaanthu amene akupanga katangale pakali pano your too busy kukamba zoipa zamunthu amene kunja kuno kulibe, sangayankhe kalikonse kaizi, sadzaonwkanso kunja kuno, misonzi ikanali mmaso ku family yake, tatha miyezi ingati chimwalilireni iyeyo? Khalani ndi umunthu man, kulankhula zaChilima oti kulibeko, apapa mwandinyasaaaa man
@brightben39843 күн бұрын
Justice ilibe chisoni... Justice simafa chifukwa wopanga injustice wafa aiii... His wrong doings are going to answer for him cuz his wrong doings are still alive.. Justice should save us
@gomezthera5354 күн бұрын
❤❤❤❤
@LameckBanda-gk6ri4 күн бұрын
Mbuli kwawo mkutukwana ndi mabodza basi
@DavidPhiri-o6w4 күн бұрын
Mbava ndi mbava even they died must be talked.. chilima kamuzu and Bingo please tiwuze kodi anali woyera or mbava? Chilima was thief but his courageous was brilliant...koma very thief that's why he was close to thief lawyer kasambala
Mpamtumbo Pako ndithu kare loseri umatan kuyakhula yachilima pano anapita uziti chani panyero pa omwe anakuberekawo
@BenardChilemba-k8w4 күн бұрын
Mpaka kutukwana amai inu hmmmmm
@Hdsagdf-t1n4 күн бұрын
Kung,alulesotu chipani cha makolo akocho akutuma et ukatelo wadya chi bamsi utm suithetsatu wachepa iweyo
@ManzyNgoleka4 күн бұрын
Inu mumatikankhulira nkhani zolimbisa ntima km nkhani iyiyi olo saulosiyo atakhara kuti ankapanga zonse mukunenazi km sikupanga sense clz munthuyu adafa kale kale,mukutiuza kuti mutha kumutengeraso kukhothi?,, munthawi ino aaaa nkulu ndizoona kuti sugwedezeka ndizokamba zaanthu km kukamba zamunthu okufa zitha kupeleka chithunzi thunzi choti mmutumo penapake sizikuyenda
@Nelsonmatenda4 күн бұрын
Nick chakwera zoonadi afufuzidwe
@DavidMalewa4 күн бұрын
😅😅😅😅😅 mng'aluli tiye nawo andale akutitora
@AbdulsharifulKalipinde-m6u4 күн бұрын
Let's work together brother
@EmmanuelSikwese4 күн бұрын
Kodi inu izi mukubweretsa lero izi nthawi yoseyi unali kutiko? Before the death of late SKC?? Mupindula nazo chani lero?? Mufuna kuchuka kapena??
@brightben39843 күн бұрын
Hahaha 🤣😂 before Chilima escape from Justice he was already accused of the same cases ndee osadabwa ayii all these were already there... Phindu la zonsezi is about Justice... Munthu wamzeru amadziwa kut chilungamo sichimafa even munthu olakwira chilungamo yo atafa... Thank you very much
@DavidPhiri-o6w4 күн бұрын
Tili pambuyo payiwe❤ kamangila, we need new Malawi
Useless,,man ndikakutenga ngati was zeru koma out box enieni , unali kuti thawi yomwe anali wamoyo ,amayendela kukhoti uko more than some days , mpaka kufika komupha ,, siguli lake ndinu , choncho muziti zikoli litukuka ,kifuna kunchuka chani, mvuto tili nalo mumalawi muno aliyetse akufuna aoneke ngati akudziziwa zithu ,eeee