ALICK MACHESO BASS GUITAR SKILLS YOU DONT LIKE TO MISS LATEST IN UK🇰🇾

  Рет қаралды 1,303

Megatvzw

Megatvzw

Күн бұрын

💣💣 *Alick Macheso*💣💣
Album: Kupa kuturika
Song: Kunditaya
(All that gliters is not Gold)
Atomic Bombaaaaa
Abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu.= My father, what You did is not a good thing indeed
Abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu.= My father, what You did is not a good thing indeed
Ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayiiiii.= It's only good for you but not to me, even to my mother
Ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayi wanga oooooooo.= it's only good for you but not to me, even to my mother
Kunditayirira ine ngati mbuzi ineee, abambo anga mulibe chisoni.= Throwing me out just like a goat, my father, without pity
-Kunditaya kunditaya, kunditayira mudzenjeee
Abambo anga ineee ndithu.....= kundirasa, kundirasa, kundirasira into a deep pit
-Kunditaya kunditaya, kunditayira muchitini
Abambo anga ine ndithuuu...= kundirasa, kundirasa, kundirasira mu Bin
Kunditayirira ine ngati mbuzi ineee, abambo anga mulibe chisoni.= Throwing me out just like a goat, my father, without pity
-munandibalira umphawi inee,kundibalira umphawiiiiiii.= You conceived me, just to face the poverty
-munandibalira umphawi ineyo,kundibalira umphawiiiiiii.= You conceived me, just to face the poverty
Abambo angaaaa= My father
-abambo anga ineee, umoyo wanga inee, umoyo wanga ine wokulira muumphawi.= my father, my life, my life is to grow on poverty
Wokulira muumphawi,= growing on poverty
Ndine mwana wa masiye inee= I am an orphan
Ndine mwana wa masiye inee= I am an orphan
Zomvetsa chisoni,= what a shame
Ndithu siumoyo wosangalatsaaaa = My life is not a joyfull one
Ndilibe chomwe ndingapange ineyo chifukwa ndine mwanaa= There's nothing I can do because I am a child
Chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi= I can't figure what made you to do this
Abambo anga inee ndithu.= really my father
Ndilibe chomwe ndingapange ineyo chifukwa ndine mwanaaa= There's nothing I can do because I am a child
Chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi.= I can't figure what made you to do this
🙏🏼🙌🏼🙌🏼🙌🏼🙌🏼🙌🏼🙌🏼🙌🏼🙏🏼#zimentertainment #zimentertainment #musician #concert #markngwazi #duet #zim #sungura

Пікірлер: 3
@NitofanySainety
@NitofanySainety Ай бұрын
Boa noite baba chero,sou eu Martinho virassone,estou aqui Moçambique,,,, Messica.
@PeterGanyiwa
@PeterGanyiwa Ай бұрын
good one
@MegaTvzw157
@MegaTvzw157 Ай бұрын
Thanks
Zvichada Hama
10:52
Alick Macheso - Topic
Рет қаралды 59 М.
Как мы играем в игры 😂
00:20
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 3,4 МЛН
Spongebob ate Michael Jackson 😱 #meme #spongebob #gmod
00:14
Mr. LoLo
Рет қаралды 11 МЛН
How do Cats Eat Watermelon? 🍉
00:21
One More
Рет қаралды 12 МЛН
Zvichada Hama (Kupa Kunopa)
10:53
Alick Macheso - Topic
Рет қаралды 78 М.
1940 Live4 at Jongwe Corner | Alick Macheso 56th Birthday Celebration
12:15
Alick Macheso ft Baba Harare 🔥🔥🔥 Baba Harare chibaba che lead Guitar
13:39
Zimbabwe Entertainment Online
Рет қаралды 42 М.
ALICK MACHESO KUTADZIRANA (LIVE PERFORMANCE) AT THE KADOMA MUSIC FESTIVAL 2023
15:00
Odyssey Entertainment TV
Рет қаралды 113 М.
Как мы играем в игры 😂
00:20
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 3,4 МЛН