Nyimbo ngati izi ndiye zikufunika zizifika ma million osati nyimbo zakuthupi ayi ndiye poti choonadi chimavuta kuvesesa Amen powerful mulungu apitilize ukupasani zisomo za kumwamba
@rexakalua-dd2qg3 ай бұрын
Powerful! with this song I can smell heaven ❤
@portianahkalonga3 ай бұрын
Been looking for this .. finally... Hallelujah 🎉😊
@bridgetkamutumwa9100 Жыл бұрын
This song really touches my soul. It leads me to pray
@francissimbani3241 Жыл бұрын
I'm finally saved by his grace, thank you Jesus for the salvation.
@QuelvinNicolaujoaoJoao Жыл бұрын
Ambuye akudalitseni munthu wa mulungu ndimadalitsika nanu mumatilowetsa mu dziko la wumzimu ndi mayimbidwe anu akoma Amém amen
@lyndahharah72433 ай бұрын
Nyengo zonse za moyo wanga nzadalila inu🙌
@PromiseLucky-pj6bz4 ай бұрын
He's the best .and his my favourite Allan from Zimbabwe to God be the Glory
@user-tm9ro2sm6n5 ай бұрын
Amen amen nyimbo yogwira mtima osasisimuka ndi kufuna bsi