Amayi Tokotani - Kukongola ndi mbina, sizisunga banja

  Рет қаралды 21,052

Mibawa Studios

Mibawa Studios

Күн бұрын

Amayi Tokotani - Kukongola ndi mbina, sizisunga banja

Пікірлер: 16
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 3 ай бұрын
Zoona azimai ena amazimva kwambili mchifukwa chake azimai ambili sakhala mabanja pozitenga kuti iwo ndi wokongola
@ChalresDausi
@ChalresDausi 10 ай бұрын
Kukokongola koteloko umalowa nadzo phwando mbinatu ndi nsalu akakubvula latha chimene amangokufunila kapakatiko akangokagwila sudzamuonanso wakukwatilayo amafuna ulemu khalidwe labwino ndilokhalo limaitanitsa chikondi cha mamuna wako paiwe ndi ana ako nzimene zidzakubweretsere ulemerero wa banja zikomo anakubala kip it up
@user-yk1dt1vj2x
@user-yk1dt1vj2x 11 ай бұрын
Zinali kuti izi banja langa litha chifukwa Cha zomwe muli kunena apa ma ladies sustain like you're program thanx
@mathewsmakina7845
@mathewsmakina7845 10 ай бұрын
Ndazionapo ine kuno ku south Africa chimodzimodzi zomwe mukukambazo akazi achimalawi amadzimva kukongola kwambiri amaiwara komwe achokera
@alfredjass
@alfredjass Жыл бұрын
Keep up the good work I like this program too much
@YAZIDU-l9s
@YAZIDU-l9s Жыл бұрын
It's a great program continue ccters ❤
@doreenmhango1202
@doreenmhango1202 Жыл бұрын
Inu ndi number one
@alisumani7936
@alisumani7936 11 ай бұрын
Good advice ndithu
@chirwatanyazi7024
@chirwatanyazi7024 Жыл бұрын
Mumadutsa mu mutu wa azimayi mokwanila yapa mwa ndi gometsa
@syliviatembo3071
@syliviatembo3071 Жыл бұрын
Iiiiiiii koma azimayi inu mmmmm mumandimvetsa kukoma anankungwi anga .
@elizamalikebu
@elizamalikebu Жыл бұрын
Kodi mungonena azimai okha nanga azibambo oyela naonso amaziva kuti akazi sangaakane
@samuelmanda8785
@samuelmanda8785 Жыл бұрын
Azumayi motto
@gelitofernandojose6654
@gelitofernandojose6654 Жыл бұрын
Mumayitha Azimayi inu!
@MoffatMzumala-r3f
@MoffatMzumala-r3f Жыл бұрын
Keep up azimai ambiri samadziwa kt banja ndi kuoneka bwino zosiyan tokotani bas ambiri asiyanitse
@MrsClement-ce3us
@MrsClement-ce3us Жыл бұрын
Ndinali ndi kazi anabwela wopanda mbina ndamdyesa kunyumba kwanga wakongola tinasiyana amandinyoza wafupi zambili tu kuyamikilidwa kinja kubwelesa nyumba
@ahhobebamw7365
@ahhobebamw7365 22 күн бұрын
😂😂😂😂
Amayi Tokotani
56:30
Mibawa Studios
Рет қаралды 4,1 М.
Bend The Impossible Bar Win $1,000
00:57
Stokes Twins
Рет қаралды 49 МЛН
Секрет фокусника! #shorts
00:15
Роман Magic
Рет қаралды 110 МЛН
💩Поу и Поулина ☠️МОЧАТ 😖Хмурых Тварей?!
00:34
Ной Анимация
Рет қаралды 1,3 МЛН
CCAPYUM SERVICE
42:33
MVAMA CCAP NKHOMA SYNOD (Rev. Yassin Gammah)
Рет қаралды 227 М.
CRUISE5 WITH MAYI NAYERE
1:30:20
Zodiak Malawi
Рет қаралды 7 М.
Bwalo la alakatuli with Wezie Lucky Nyirenda
27:52
Wezie Lucky Nyirenda
Рет қаралды 6 М.
Moda Fumulani
17:02
TEAM ENTERTAINERS MW#
Рет қаралды 71 М.
BANJA  EP2
29:30
AskMuviTV
Рет қаралды 17 М.
Kusanthula Bible ndi Quran
27:55
Jimmy Chimera
Рет қаралды 31 М.
Zifukwa zolowera Banja -Program ya za M'banja pa Mzati TV
46:14
Mzati Radio&TV
Рет қаралды 13 М.
Kusanthula Bible ndi Quran
27:58
Jimmy Chimera
Рет қаралды 21 М.
Bend The Impossible Bar Win $1,000
00:57
Stokes Twins
Рет қаралды 49 МЛН