ANTHU AMBIRI ANALI ODABWA DZULO RICHARD CHIMWENDO BANDA ATAYANKHURA IZI ZOKHUNZA PETER MUTHALIKA

  Рет қаралды 3,719

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 79
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 3 сағат бұрын
Inutu zikuoneka kt mukuchita mantha ndi dpp. Nkhani ya ndege simukuinena bwanji?
@JackElias-ty2tt
@JackElias-ty2tt 59 минут бұрын
True
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 2 сағат бұрын
Anthu akuona kuti ndiosakondwa😂😂😂😂
@WatsonMalanga
@WatsonMalanga 2 сағат бұрын
A chimwendo munthu wolemela sangalimbane ndi munthu wosauka ngati inuyo a mcp ndinu wolemela koma simukugona nayo turo dpp.
@IshmaelJuma-x1f
@IshmaelJuma-x1f 2 сағат бұрын
Tapelekani mfundo zoti anthu ave
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr 46 минут бұрын
Tambala timugwira pakhosi 2025 sazaliranso. Kodi mukuti nkharamba kodi a ntaba ndi nyamata?
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl Сағат бұрын
Nkhani ikungokhla ya Peter cfkwa chan ? Mtengo omwe umagededwa ndye kut muli zipaso
@imranhopewell-yv4zc
@imranhopewell-yv4zc 3 сағат бұрын
Kodi mukuiopa Dpp ati? ndikudabwa nanutu Dpp oyeeeeee
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx Сағат бұрын
Milomo ngati usandilakwitse chisilu chimwendo chaka cha mawa ukuchoka ndipo uzakakhala kudende iwe
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma 2 сағат бұрын
Sakunama chimwendo
@isaaczuze
@isaaczuze 2 сағат бұрын
My vote is Apm asati zisilu tikuziona apazi ayi ndi mbuzi chakwera
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 3 сағат бұрын
DPP NDIY MUKUIOPAT KOD A OPPOSITION NDI ADPP OKHA MALAWI MUNO? WAMUTU WAUKULUYO DAILY ANGOYAKHULA KUSOKHANO ZA PM UKUMUOPAT IWE NDIPO UZIOPADI 2025 UKAFERA KUMAULA IWE APM MY VOTE
@rozertmbale9545
@rozertmbale9545 2 сағат бұрын
Dpp ikuwaopaso a mcp tisanamizane
@alexsumani6823
@alexsumani6823 2 сағат бұрын
Tikungodikila mwa chete kumva kuti anati ndege yadzadza ndindani
@AvideOfficial
@AvideOfficial 2 сағат бұрын
Chimwemdo amaopa DPP sorry for you My Brother chimwemdo 😂😅😢
@Lushaka
@Lushaka 3 сағат бұрын
Guys Chakwela please don't allow this people take advantage with people we tried with ndale just build country please 🙏
@GertrudeKamoto
@GertrudeKamoto 2 сағат бұрын
Dpp my vote
@MakabaBauleni-c2i
@MakabaBauleni-c2i Сағат бұрын
Kkkkk Chimwendo akamva zina loti Peter Muthalika amadwala ,chaka ici nde udwalatu chimwendo ife pheee kudikilira kugwa kwa Mcp 2025 September
@RodgersNtambalika
@RodgersNtambalika 2 сағат бұрын
Garu kunyasa nkhope thyolo stadium akumanga ndi chakwera???mboli yamako chimwendo miseu ya China aid ndi ya mcp
@SteveKanongwa
@SteveKanongwa 2 сағат бұрын
Ine maona ngt unanena kuti uyamba kugawa chimanga pa 1 October nde chomwe umapangiranji kuyamba dzulo anzanu akupanga zao sichisokonezo chimenecho
@imraanJafal
@imraanJafal 35 минут бұрын
Tikufuna tidziwe za imfa ya chilima osati Dan lu Ai chilima🥺🥺🥺🥺🥺🥺🥺🥺
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 2 сағат бұрын
Takonzani ndende is waiting for you chimwendo
@lestainmatenganya9850
@lestainmatenganya9850 2 сағат бұрын
Chipani Cha zitsiru za kupha anthu
@kingtiles-g6q
@kingtiles-g6q 2 сағат бұрын
ndiye kuti kwanuko kulibe akazi okongola eti
@SydneyNyasuli
@SydneyNyasuli 2 сағат бұрын
Kwanthu chawezi muzimuvesesa a Richard akunena zowona
@simonpaul6567
@simonpaul6567 2 сағат бұрын
Mr chimwendo Banda amene anakuuzani kuti ndege yazaza ndani
@MartinMpoya
@MartinMpoya 2 сағат бұрын
Mukunama achimwendo zanu zinada basi
@NiccoGama
@NiccoGama 2 сағат бұрын
Kkkkkk pasanapawo mesa anthuwo akukwedza manja kut alandile ndalamadzo asawapasa chimanga bwanji anthu apusa dzeru mulibe inu
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 3 сағат бұрын
MULIBE MFUNDO AMCP
@RaffickAllie
@RaffickAllie Сағат бұрын
Kodi Mesa muli pampando ndinu .komaso munaudza Amalawi sanje to Chitipa kuti .mukazarowa Boma within 100 days muzamanga onse amapha ma Albino .lero ndi 4 years muli pampando koma or ndimmodzi yekha omangidwa .. 2022 APM anapereka report Kwa chakwera lokhuza yemwe amapha ma Albino kuti aliudze dziko .koma chakwera anakhalira Kodi muli chani katimo .nde nkhani yama Albino musatinyase
@isaaczuze
@isaaczuze 2 сағат бұрын
Za ziii ....ineyo sindingavale tshirt yojambulidwa tambala ngati chisilu ayi
@YusufuUsumani
@YusufuUsumani Сағат бұрын
Dpp ndi boma ndaona kuti Mukuyiopa ngani yandeje kuchikangawa
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 сағат бұрын
Mcp kunena chulungamo sangawine ndichifukwa akumayakhula zapita akuziwa kuti sangaduse pa peter ndichifukwa amanena zopanda mutu anthu awa
@ClementbWatches
@ClementbWatches Сағат бұрын
Tayankhulani mfundo zomanga malawi sizokamba za dpp ayi. Zakutu zomwe mukuyakhula apa. Mbolo zanu
@JimmyMhone-b5p
@JimmyMhone-b5p Сағат бұрын
Ngati kuli chitsilu chotelatu ndi chimwendo banda
@maxwellmashon4897
@maxwellmashon4897 28 минут бұрын
Takambani mfundo inu a MCP zoti zithandize dziko osati muzikamba za DPP kose mungayende
@honmitrus
@honmitrus 3 сағат бұрын
Chimwendo ukulimbana ndi nuclear weapon Adad, sisize yako
@GeoffreyChapita
@GeoffreyChapita Сағат бұрын
Agalu inu muziona chaka cha 2025 mukutuluka muzikazipwisila mumakomo
@thokozanimangoni
@thokozanimangoni 3 сағат бұрын
Mcp dziwani kuti mulungu wakumwamba akukathani ndipo adzakukathani mulungu wakumwamba adzilemekezeka chifukwa ali pa chitchito chotiteteza ana akefe
@RafickAlissah
@RafickAlissah 2 сағат бұрын
Agalu awa mchifukwa anakhala kosusa mpaka 30 years mfundo alibe awina chifukwa cha chilima uja
@christopherpetro-pen3678
@christopherpetro-pen3678 3 сағат бұрын
Nkhaza zake mukunena ziti zochita kuposa kupha anthu kuchikangawa?
@David-z9o4m
@David-z9o4m 3 сағат бұрын
Mulibe Mfundo a chikangawa inu,mulingu akukanthan
@P.Bilali
@P.Bilali 2 сағат бұрын
Kupereka moni kwa nduna zako kuyera (promised 50 pin) eti.... What does it mean
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Сағат бұрын
Ndge inagwa bwanji anakuuza kut yadzadza ndindani? Lero ukutumbwa dziwa sunadzilenge wkh ur days r numbered
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 2 сағат бұрын
Vimelezani kuti boma latikanika kuyendesa,nothing you can convince pple this time around,mumkayesa kuti 2025 mpatali,kagwere uko ndi mfundoless zakozo,sitinayiwaletu za Biyeni
@RodgersNtambalika
@RodgersNtambalika 2 сағат бұрын
Musowa mfundo mbuzi iwe anthu 9 munapha aja ai koma anthu malubino???kupusa anthu akuba inu
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 2 сағат бұрын
Bwanji osayakhula za kusowa kwa ndege , inu ndie munapha vc ndi anthu ena 8 kmaso kuonjezelapo apo sadiki Mia ujaso munamusowesa kmaso ndi ena ambili mwawapha
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl Сағат бұрын
mcp fundo alibe ndi chifkwa kwao ndikunyoza bas,mufune musafune pack and go
@victormaluwa6710
@victormaluwa6710 2 сағат бұрын
Please God, help Malawi,,,,,
@lyiemax
@lyiemax 2 сағат бұрын
Mfundoless, never again to MCP
@AubreyKabango-g8l
@AubreyKabango-g8l 2 сағат бұрын
Kukalamba ndi vuto, Inu munali chontcho?
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 3 сағат бұрын
Kkkkkkk matha achuluka ku mcp,,inu ndi amene mumapha ma alubino coz munkanamiza anthu mdziko muno kuti ma lubino amangosowa-si afa.
@EnerstManess
@EnerstManess Сағат бұрын
Iwe chimutu panga zot anthu akukonden osalimbana ndi munthu
@giftsululu4274
@giftsululu4274 46 минут бұрын
Boma ndilomweri stikustha
@Vascomw
@Vascomw 2 сағат бұрын
Km guys ukuku ndikuyiwopa dpp moti ayakhule zazelu km ayi
@andiwochishadreck3753
@andiwochishadreck3753 3 сағат бұрын
MCP msonkhano uliwose nkhani ndi ya DPP ndi Peter basi kkkkkkkkkkkkk
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 2 сағат бұрын
Akumuopa koopsa amene aja ndakatundu chilichonse chinali chontchipa 😂😂😂
@YunusuMaulidi
@YunusuMaulidi 3 сағат бұрын
Inu mukunena zakalekale anthu aphedwa mu June momwemu sizakalekale mukunenazo
@marryphili5419
@marryphili5419 2 сағат бұрын
Koma amalawi mavuto sazatha chifukwa ndife wotengeka chifukwa cha ndarama
@AnthonyJimmy-i4c
@AnthonyJimmy-i4c 2 сағат бұрын
😢ndegchikangawa
@GitfIobodo
@GitfIobodo 2 сағат бұрын
Iweyo ulibe dzeru chikangawa machende ako
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 2 сағат бұрын
Chimwendo tu akunama
@christopherpetro-pen3678
@christopherpetro-pen3678 3 сағат бұрын
Ntsano okamuzunoja paja onali nzaka zingat ?
@HamiltonRaphael-q2d
@HamiltonRaphael-q2d 2 сағат бұрын
kumenya kampeni wa Dpp
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 2 сағат бұрын
Kambani mfundo inu mukuopa dpp inu anthu oyipa
@LovemoreSuliwa
@LovemoreSuliwa 2 сағат бұрын
Kusowa mfundo ukuu
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 сағат бұрын
akuziwa kuti sangawine sanganene ifa yachilima anamupha basi
@ChicoBanda-kq7py
@ChicoBanda-kq7py 2 сағат бұрын
Kodi mukufunabe kumangompha munthu
@FrancisJumbe-zj4ue
@FrancisJumbe-zj4ue Сағат бұрын
Chilima anapita basi
@mailos.laisoni7001
@mailos.laisoni7001 3 сағат бұрын
Ndalama kumangogawa
@StevenFombe
@StevenFombe Сағат бұрын
Wakuba amadziwa kuthamanga
@JonesNkhono
@JonesNkhono 10 минут бұрын
Boma ilo
@DaudHassan-r4f
@DaudHassan-r4f 3 сағат бұрын
Mukuwopa apm
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 2 сағат бұрын
😂😂😂ndipo sukunama aixe
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 2 сағат бұрын
Zadziiii
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr 46 минут бұрын
Tambala timugwira pakhosi 2025 sazaliranso. Kodi mukuti nkharamba kodi a ntaba ndi nyamata?
Senzo Meyiwa Murder Trial I 07 October 2024
SABC News
Рет қаралды 4,5 М.
РОДИТЕЛИ НА ШКОЛЬНОМ ПРАЗДНИКЕ
01:00
SIDELNIKOVVV
Рет қаралды 3,4 МЛН
Стойкость Фёдора поразила всех!
00:58
МИНУС БАЛЛ
Рет қаралды 6 МЛН
Man Mocks Wife's Exercise Routine, Faces Embarrassment at Work #shorts
00:32
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 6 МЛН
Watermelon magic box! #shorts by Leisi Crazy
00:20
Leisi Crazy
Рет қаралды 84 МЛН
Senzo Meyiwa murder trial | 7 October 2024
eNCA
Рет қаралды 392
Nancy vs Che Nkope - Mkazi Biyeni
12:16
CHE NKOPE
Рет қаралды 6 М.
I SUSPECT MY LANDLORD IS THE FATHER || Justice Court EP 208
18:03
Justice CourtTV
Рет қаралды 47 М.
РОДИТЕЛИ НА ШКОЛЬНОМ ПРАЗДНИКЕ
01:00
SIDELNIKOVVV
Рет қаралды 3,4 МЛН