Anyamata wa ku Airport wayamba kuulula zomwe anauzidwa ndi Boma

  Рет қаралды 80,116

Jay Kawere TV

Jay Kawere TV

Күн бұрын

Пікірлер: 279
@MuhammadSamson-yz1kl
@MuhammadSamson-yz1kl 3 ай бұрын
Mwayakhura bwino Koma vuto umadziwa chiwembu chonse osaulura mukuulura Pano chilima wapita 😭😭😭 sangabwelelenso
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 3 ай бұрын
Amangidwe ameneyu amadziwa zachiwembuchi ndye iyeyu ali m'gulu
@stephanongalaukabanda2step867
@stephanongalaukabanda2step867 3 ай бұрын
Eti 😢
@EllinaBitto
@EllinaBitto 3 ай бұрын
Ndipo inu osanena anthu asananyamuke Chilimaaaaaaaaa😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@MussaKukada-mt9rv
@MussaKukada-mt9rv 3 ай бұрын
Mumunvesese munthuyo akuti anali odabwa osati amaziwa akanati anene then boma likanamufinya kt abwerese umboni nde zikanamuvuta ndiyeyo​@@EllinaBitto
@SinyoroMoyo
@SinyoroMoyo 3 ай бұрын
Mwina anauzidwa tsiku lonyamuka akanatani nanga .koma ngati anadziwa kale nde Naya amangidwe
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 3 ай бұрын
amwen inuso mboza pitan ku nkhoti gt mukunena sowona mumafuna munkhale ndi maviews bas amalawi zopanda zeru😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@Ishmael376
@Ishmael376 2 ай бұрын
Pitani Kaye classe Mr man
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o 3 ай бұрын
Mkudikila chan abale ingoyankhulan.kumutundu wa Malawi kt anthu amve km mkamakhala chete chonchi mkudikila chibanz
@martinsailesi1731
@martinsailesi1731 3 ай бұрын
Nkamwa mukuchita kumveka kuti chiyawo chikulemera. And malongosoledwe akao akuchita kumveka opanda confidence. School yochepa koma kukhala wodziwa kwambiri , ndinakuuzani musalekele standard 3
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 3 ай бұрын
Tisayakhule zambiri tiyeni tidikire tidzave zambiri muthaw yake
@DanielGeorge-l4h
@DanielGeorge-l4h 3 ай бұрын
Ndiye iweyo umadikila anthuwo kuti afe kaye😢
@EnelessLundu-sn8om
@EnelessLundu-sn8om 3 ай бұрын
Iwe opusa kwambiri...ukuulula anthu atafa kale ndiye ukufuna titani ..ngt mizimu ikukuzunza usatinyase ife apa
@LeonardMhone-cg1tk
@LeonardMhone-cg1tk 3 ай бұрын
Mulungu ndiwa mkulu,zonse zikuturuka praise God 🙏
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 3 ай бұрын
Anauzidwa,ndege isananyamuke,mpaka kuyisiya ndegeyo mpaka kunyamuka.ambwiye,mwazi wa a chilima uli manjamo.soka,kwa iye,amene anaziwa za chiwembuchi,koma kusiya osanena kathu.moto,wa sulufule ukhale pa mitu pawo,ndi ana awo.
@MaxwellChiwaya-tv7kn
@MaxwellChiwaya-tv7kn 3 ай бұрын
Inu inu musakhale ngat boma simulidziwa munthu anakawauza ndani poti oyenera kuwauzawo ndi aboma omwewo or muli inu mungatani tiyeni tidzingoziona choona chenicheni chidziwika athu ndi maso
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 3 ай бұрын
@@MaxwellChiwaya-tv7kn munthu yu anali pamenepo ena ndikumuudza chinali chisisi cha anthuwo koma kumeneko kunalibe wa UTM, kapena,onse ogwila ntchito pamenepo amaziwa,za ichi,nanga bwanji osanena kwa munthu,opangidwa chiwembu yo kuti bwana musakwele,umu,pamene mulungu anamunong'onedza,kudzela mwa wina.uyutu,angofana ndi Judas,opasidwa, ndalama kukaziponya,pa kachichi.chifukwa,zizamuwawa paka Kale.
@ChristopherKamphanje-o8l
@ChristopherKamphanje-o8l 2 ай бұрын
Ok abwana mukunena zimenezo munthu atamwalila kale bwanji mukudziwa kuti kubisa chinsisi kumakhala kuti iwenso ukuvomela zoyipazo kuti zichitike basi inunsu muzigugude pamtima mwapambaso pachimenecho
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 2 ай бұрын
Ndiye awa asamabwele,pano kumanena,zoti wina anawaudza kuti,ndege,igwa,ndipo kumamuona Vic president akulowa,mundegemo,kumaziwa pasi pa mtima akukamwalila,koma osachita kathu ndiye akubwela,pano,kumatiudza zitithangata chiyani.akufuna,kundiudza, kuti kumeneko kulibeko wa UTM ogwila ntchito pamenepo? kapena nonse ogwila ntchito ndi MCP?chinabvuta ndi chiyani kukaudza mmozi wa UTM bwana asakwele.kodi,olo unganaona bwana chilima galimoto yawo ikubwela koteloko,ndikukaima ku sogolo,sakadaima?akadafona aziwe,kuti chikuchitika ndi chani.olo,unganalemba pa katoni.akadawelenga.
@EdsonNjonjo
@EdsonNjonjo 3 ай бұрын
Chindele iwe, ndiweso one of them sanakupase ndalama eti
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb 3 ай бұрын
Kalikonse tikaona pamene papita mzimu yaathu ndizovuta. Kwathu kulila abiyeni
@BestMtawali
@BestMtawali 2 ай бұрын
Zachambazo ndege snafikeko kumzuzu
@natashamathala8715
@natashamathala8715 3 ай бұрын
Utadziwa za chiwembucho, sunawauze anthu bwanji chilimayo asanamwalile kuti awone njila yina yomutetezela? Nde apa adzuka mukamaulula zanu ataphedwa kale?
@dysonfysonchifundo2284
@dysonfysonchifundo2284 3 ай бұрын
Koma chomwe tingadziwe chakuti pali zina zimayendela ma level, zikanatheka iye kulankhula koma remember osauka alibe mbalume or zomwe akunena zili zothandidza sidzimaphula kanthu. Words of God imfa iliyonse Mulungu amalola koma, Tsoka wakubweletsa imfayo.
@ChifundoChiwanda-ru3pg
@ChifundoChiwanda-ru3pg 3 ай бұрын
Nde chomasiya osanena mpaka ndege inyamuke ndi chani? Osatiuzaso basi coz miyoyo ya anthu ofunika inatayika kale ungangotikwiyitsapo l
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke 3 ай бұрын
Eti eti wandibowa bwanji ameneyu
@MosesKalenge
@MosesKalenge 2 ай бұрын
🤯🤯🤯💔💔💔💔💔💔💔💔💔midzim ya anthu onse, 9 ikusowetse mtendele ndinthu ulape😌 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@JohnMeleka-s1t
@JohnMeleka-s1t 3 ай бұрын
Akanika kukulipila kd uwulula lelo aaaaa km amalawi tulo take
@elias.m.chunga
@elias.m.chunga 3 ай бұрын
Mbuli simasowa, failing even to speak English clearly😂😂😂
@cynthiataulo5211
@cynthiataulo5211 3 ай бұрын
Inunso muli part yachiwembu, you knew and you stayed quiet and now you're busy telling us, where is your conscious. You'll guilty for rest of your life. Zamkutu basi
@GiftGift-d6u
@GiftGift-d6u 3 ай бұрын
How came you kept all this inform before the aircraft depart,,,, 9 life's lost here...
@chrispinmlambamalemboc3228
@chrispinmlambamalemboc3228 2 ай бұрын
Fooolish guy who follow the checks on a military plane.cant we justlet the souls rest in peace.Lets not just focus on VP but other families list their breadwinner's
@AliJack-e6r
@AliJack-e6r 3 ай бұрын
Mwalowesa chibwanatu guys
@MalawiPage
@MalawiPage 3 ай бұрын
Eti...
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 3 ай бұрын
Ndipo inu anthu akungokhulupilila zilizose koma ambuye atithandize ndithu
@wezzieneba9238
@wezzieneba9238 3 ай бұрын
What is it going to benefit now? We have lost a legend, a father of many, a husband to someone, a future leader in whom we had hope. You should have been in the forefront kupulumutsa moyo wa a VP ndi anzawo enawo. At least, kulolera kuchotsedwa job and save them. I wish you would have broken the protocol, run and kneel in front of the VP as he goes to board the plane and then talk to him so that he doesn’t board the plane. Guys this is painful, indeed.
@YoungMwacho
@YoungMwacho 3 ай бұрын
Waboza uyu. He seems not Malawians from his chichewa accent. If he new why did he let the people perish like that. This is stupid narration.
@nenaningola
@nenaningola 3 ай бұрын
Ati ndudikira investigate😂 aah
@smithh.njirayafa5847
@smithh.njirayafa5847 3 ай бұрын
I have stopped to support MCP because of this
@andsenJeke
@andsenJeke 3 ай бұрын
Skc has gone forever inu mumadziwa ndithu God should intervine malawi wants to know the truth of what was actually happened
@ChimwemweMuhelliwah
@ChimwemweMuhelliwah 3 ай бұрын
Ndie ndiwe chitsiru,,ukuti umadziwa kt ndege sibwelera..mbuzi iweyo,,bwanji sunanene ku U TM members... ndie chilungamo chanji uwuze aMalawicho?
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 ай бұрын
Chilima Munamupha Uja Nzimu Wake Ukukudandaula Iwe Chichakwela, Chinchewa Chakupha Iwe Umanama Kuti Ndiwe M busa , U president Wanji Okupha Naye Nzako? Iweyo Suzafa? Sitikukufuna 2025 Chitsiru iwe
@madalitsomorris6566
@madalitsomorris6566 3 ай бұрын
Why now, how do we know it's true what you are saying, Osati pusisa pano, Malawi will never be the same,
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 2 ай бұрын
Palibe chifukwa chodikilila kunena,, iwe waphesa nawo anthuwa,, ukhala utachedwa usazatiuzenso
@PatrickMailos
@PatrickMailos 3 ай бұрын
Iweso ndiokupha bwanji sunamuuze chilima kuti asikemo
@francismungu7749
@francismungu7749 3 ай бұрын
Koma anthu ndi olimba ntima kumapanga zinthu ngati sakuziwa. Ambuye mutichitile chifundo
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 3 ай бұрын
Zaboza izi bwanji sunapange kuthekela kopulumusa anthuwa ngati umaziwa zimenezi ndiwauza a Zikhale akusaketu iwe
@OssmanAbubaker-st7pu
@OssmanAbubaker-st7pu 3 ай бұрын
Mulungu ndi wamkulu .brother mwachitabwino kunena tiyenitidikile kut MCP ikambachani paifa ya anthu 9 amenewa
@MateyuKamwani
@MateyuKamwani 2 ай бұрын
This is all fake..Dude is too ileterate to work at the airport.." tudikira investigate" whats that?
@YamieManda
@YamieManda 3 ай бұрын
Kodi athu inu munakhla bwanji?lmeneyi ikuyakhulayi ndimbuzi yotheratu
@giftkanjuchi-qm8hf
@giftkanjuchi-qm8hf 2 ай бұрын
Ndiwe opusa ukuwulura lero? Ulibe nzeru anzako ukuwawona akukafa bwanji osaiphedura nthawi yomweyo kuti chilima atsikemo? Opusa iwe nchawa
@paulinekayuni1621
@paulinekayuni1621 3 ай бұрын
Nkhani zovuta ngati mulidi ogwira ki airport komaso ngati muzalankhule report ya mdf ikatuluka
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 3 ай бұрын
Mwazi wa chilima sungapite pachebe mulipo gulu muulura ndipo mzimu wake ukusowetsani ntendere
@LilyMbewe
@LilyMbewe 3 ай бұрын
Aaà video ndinasiya ine koma ndimadabwa kuti zikukhala bwanji😢😢😢
@FrankKambwani
@FrankKambwani 3 ай бұрын
Ulibe chikondi ayise,chiwembu umachidziwa koma osadziwitsa mmodzi wa okwerawo bwanji nawenso ndiwakupha basi
@LindaKaunda-t7z
@LindaKaunda-t7z 3 ай бұрын
Total lie why you allowed them to board a plane knowing something will happen to them, so just stop if not you are evil too
@languitoneelias9972
@languitoneelias9972 3 ай бұрын
Wabodza kape uyu zomwe ukukamba sizikumveka chiwembu ngati ichi sangauze iweyo ukunama kwambiri
@shupikayintuwaluwa-5899
@shupikayintuwaluwa-5899 3 ай бұрын
Km2 mukungobwata ayao inu! Shiiii umagwila ku airport yake ya usku or kapena zomwez tuziziwazi . Zsyen this z serious issue, uyu ndwaboza.mboli yakonxo
@ClementAnusa
@ClementAnusa 3 ай бұрын
Iwe munthu opusa maganizo kwambiri, you think anthu angakhale ndi chidwi pa mfundo zakozo , what do you think will this silly information help us? Never do such a mistake wamva
@VictorKachulu-y3n
@VictorKachulu-y3n 3 ай бұрын
Five moba yaku Malawi ili pa social media pitani ku Court mukanene umboni wanuwo because anthu opusa akumverani koma ozindikila kuti Satana akugwilitsa ntchito social media sakhulupilila zonena zanuzo ndiye ngati muli a nzeru pitani ku Court musawope, Ngati mukuwopa kutenga mabodza anuwo ku court mukuwopa chiyani mudiwuza mbuli zimenezo inetu ndine wa DPP koma si zonse kumangowombera mmanja ndi nyasi zomwe ayi ndinu omvetsa chisoni manyazi bwanji DPP wooyeeeeeee Mulungu amayika munthu pa mpando wotsogolera komaso amachotsa yekha ndi cholinga ndawonera a Dad (APM) koma savomereza kuti Mulungu analanda ndilo vuto lili ndi atsogoleri athu 😊😊😊😊awa ndi maganizo anga ndimmene ndikuwonera work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die
@dumisanimoyo3152
@dumisanimoyo3152 3 ай бұрын
Tsopano wapinduranji ukana ulula nthawi yomwe yija ukanapulumutsa mutsogoreli wamawa bwezi nawe zako zayera
@ArchraphNkhoma
@ArchraphNkhoma 3 ай бұрын
Umbuli wauchisilu Moti mukanapulumusa Miyoyo yaAnthu ochuluka basi umafuna uzizapereka umboni anthu afe Kaye opusa iwe Munthu Oipa otembereledwa mizimu yaAbale amenewa ikuone
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 3 ай бұрын
Bwanji sunakangon'goneze Chilima ndi anzake zazomwe unauzidwazo? Lero ndiye ukunena anthu aja ataphedwa kale, ndiye ukuti ife titani?
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 3 ай бұрын
Mpaka mwandilembeza zozamveka APA chifukwa mandiwontcha ntima kukonda ndalama kotani Koti mpaka kulolela anthu awonongedwe ndiwe mbusi yamunthu nde mwapindula chani ?
@MaprinceKasiyah
@MaprinceKasiyah 3 ай бұрын
Anthu ndinu olimba mtima kuwalora anzanu kuti anyamuke mukudziwa kuti sakabwera amoyo padziko lapansi palibe chisisi
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke 3 ай бұрын
Zikundiwawa kwambiri mukamaulula pano pomwe mumadziwa chilichonse anthu asanamwalire inunso munatengako gawo pa imfa ya anthu aja
@johnmalupia1754
@johnmalupia1754 3 ай бұрын
Ndiwe chitsilu usapusitse anthu sugwila ntchito ku Airport komaso ndiwe galu, kodi achawa bwanjinu bwanji mumachuluka mbuli? Osamangopita ku mzikiti ku ka swala bwanji a galu mi dyomba inu dzitsilu
@AgnessKavalo
@AgnessKavalo 3 ай бұрын
Ndipo kumeneku timati ndikupusa inu ngati mumamvana anthuwo asananyamuke why munatani kuwakokera pambali ndikuwadziwitsa anthuwo kuti asakwere ayipqnge check everything inetu zandinyqsa
@AgnessKavalo
@AgnessKavalo 3 ай бұрын
Ndipo kumeneku timati ndikupusa inu ngati mumamvana anthuwo asananyamuke why munatani kuwakokera pambali ndikuwadziwitsa anthuwo kuti asakwere ayipqnge check everything inetu zandinyqsa
@mussahalfraid6395
@mussahalfraid6395 3 ай бұрын
Koma anthu akupekatu eeee. Mukulipidwa zingati kodi? Anthu ndiye tili busy kugwirizana nazo zoyankhula za makapewa atangokupeperetsanipo apa. Palibe choona ngakhale cha mzeru wayankhula uyu.
@Rodrick-m8h
@Rodrick-m8h 3 ай бұрын
Nde inuyo bwanji osatiuza zoonazo
@mussahalfraid6395
@mussahalfraid6395 3 ай бұрын
@@Rodrick-m8h aaaa kuteroku inunso ndi mmodzi okhulupilira mbwererazi? Vuto lake mu mtima mwanu mwakhazikika zoti Chilima anachita kuphedwa ndiye kamba ka zimene zili mmutu mwanuzo chilichonse chokambidwacho chikumakhala choona kwa inuyo. Mudziwe kuti kagulu kambiri kamene kakupanga mislead anthu ngati inu sikalinso Ku Malawi kuno anthu ake ali kunja akungopeka nkhani inu muzikhulupilira mabodzawo.
@MasegoModukanele-xg2hj
@MasegoModukanele-xg2hj 3 ай бұрын
Umbuli wa athu ena ndiumenewu mosemuja pano uzikati kati mwango funa kuthila mchele kuti zikome ndiye simunazitenge bwino mwaphonya
@TemboMedison
@TemboMedison 2 ай бұрын
sizikupindula chilichose zimene ukulankhulazo Bola ukadalankhula kale
@andrewkalima
@andrewkalima 3 ай бұрын
Ase khala chete ulibe thandizo lililonse pano siposewelera ndikumatchula maina a anthu zikuchita kumveka kuti ukungobwebweta potengera zomwe anthu akulankhula samala usatisokoneze tinatopa nazo za anthu oziikamo ngati akuziwa zomwe zimakhalira yet you are totally blank,If you had more evidence you could come the very same day.Be carefully
@MjombaMjuba
@MjombaMjuba 2 ай бұрын
Pamtumbo panu inu, wanthu wazungulira mutu. Bwanji mukulankhula lero, munali kuti nthawi yonseyi. Munthu adapita basi. Zapachimtumbo
@anoldkapolo4493
@anoldkapolo4493 3 ай бұрын
Bwera poyera usamanamize anthu ngati akunamuza agalu akowo ingokeanitsa kuwadtera zomwe akupatsazo. Ndimtere line lija ndiye lero vuziti nyooonyoonyoo ?wamisala galu iwe
@eunicethokomanda8911
@eunicethokomanda8911 3 ай бұрын
Abale Pena tamaopani Mulungu pofuna kuyankhula zinthu
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 3 ай бұрын
nthawi yonseyi mumatani kuulula?? mumadikira kuti munthu afe then muzibwera apa kuzapotoza amalawi??? ndalama anakigailani a MCP zija zatja or anangokulonjezani osakuoatsani???Amalawi ndife oganiza moperewera?? inu mukifuna mundiwuze kut kwa neba wanu kwabwera wakuba inu mkumawone kenako akubawo athawa then muxikabwera mkumati ndinawona akubawo koma mafikira kut anthu muyakhure kaye then ndiwulure??? bwanji simumakuwa nthawi yomweyo kut wakuba anthubapulumutse??? Amalawi ngat tizikhala tcheru kumamvera izi ndthu tizakhaka anthu odanisana..
@ChriKezi
@ChriKezi 3 ай бұрын
mutadabwa simunauze amalawi bwanji?mukamafuna kunama kumaona even english yanu ikuonesa kuti or ntchito simungagwile boma
@YamikaniKamphero
@YamikaniKamphero 3 ай бұрын
Km amalawi mukadanena nthaw yomwey mukunena pano km mtsogoleli kulibe
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga 3 ай бұрын
ndiwe waboza ojambula anamangidwatu lwe ukufuna ktchuka
@FunnyPhiri-ky2ib
@FunnyPhiri-ky2ib 3 ай бұрын
Osangoneneratu bwanji iweee Usatipsyese mtima aaaaaa zikutiwawa enafe tuuu
@NicksonMoffat
@NicksonMoffat 2 ай бұрын
Wachibwana uyu , Munthu wafa kale olo utawulura ndiye abwera, iwe ndi mbudzi ya munthu
@AlfredMtukula
@AlfredMtukula 3 ай бұрын
Murungu popanda njira amaika njira zobisika zidaonekera nkuwara
@Floranyimbiri
@Floranyimbiri 3 ай бұрын
Mphaka weniweni iwe. Ndiwe chisilu wanva? Umadziwa kuti imfa imene ija imatiwawa kwambiri? Vuto ndiloti ambilinu mumangowona pa a Chilima basi koma enafe pano tilibe potsamila. Ndiwe galu kwabasi
@judithchaima
@judithchaima 3 ай бұрын
Umadikira anthu afe, pano ukudikira report? Imfa ya a Chilima ndi anzawo inatipweteka kwambiri ife ngati mzika za malawi ndipo ndi imfa yosaiwalika choonde osaseweretsa maliro Mulungu akulangani inu
@mustaffahhemmad
@mustaffahhemmad 3 ай бұрын
No evidence how can we trust this. Why you don't want to mention your name..komanso tatolapo chayani pa video imeneyi.. muziponya ma video opanda chikaiko apa
@MosesPhiri-l6e
@MosesPhiri-l6e 3 ай бұрын
Uvek ngt mwa law signal bwanj edit or wat If u know the damn truth umbon wak uli kt mwin ufun more comments
@MeliaDivala-sl5yk
@MeliaDivala-sl5yk 2 ай бұрын
Nde kungouzidwa kt musaipange check iwe nkuziwa kale chomwe chinachitika,mutu wako ndthu.Ukamangiwa ukuona ngt amalawi akhala nawe ntchto
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 3 ай бұрын
Unatani uwauza anthuwo kuti asakwele ndegeyo, moti uri serious kumapeleka uthengau anzako atataya abale awo ndwe chitsilu iwe
@EnockNgozita
@EnockNgozita 3 ай бұрын
Zidalizovuta kuti alimbane ndi boma nthawi imeneyo komaso sadaliko yekha kumeneko akadangoyelekeza kuyankhula kanthu akadaphedwa kapena ndiiyeyo muziyamba mwaganiza mutsadayankhule
@paulinekayuni1621
@paulinekayuni1621 3 ай бұрын
Ndizoona kuti uja analankhula ndi Zodiak anaona ndege ku Chikangawa wapezeka atafa? Penatu musamangotero mwinadi anthu amaopa zotsatira akaulula pajatu anthu andalewa amadalira zozimitsa aliyese ofuna kuwasokoneza. Ndiye uyuyu conscious ikumuvuta ngati zili zoona
@TeciaKumpitah
@TeciaKumpitah 3 ай бұрын
Kma zomaulula munthu atamwalira kalezi ndizopusa .taluza miyoyo yambili ngoz imene ija, kuculutsa umasiye nde mukamapatsidwa ma plan a ziwembu muziyamba mwalingalira atakhala achibale anu.. kma Ambuye acite nanu nose kuyambira kulikuluko poti amadziva ngt ndiamuyaya😢
@AmujeMwamad
@AmujeMwamad 2 ай бұрын
Aaaa, inu muulura anthu atafa, bwanji simudauze kut asanyamuke? kma mmapemphera inu 🤔
@RhulaniMukasi
@RhulaniMukasi 2 ай бұрын
Ndipo namachende winaaliyese yemwe anaziwa zachiwembuchi alinawo mukuphamo ndipo ngati sanakupasen ndalama ndizoenera akupasa ndalama bwanji pamene ngakale achakwerao akuziwakuti azindikiridwa kut anapha komaso zot anapha ndiiyeyo zinaziwika asanaikidwe Manda chikara sizinaziwike kut anapha iyeyo bwezi pano mutapasidwa ndalama zachiseka pakamwa ndipo galuiwe sukanaulura iweyo ndichakwera ndiamoz ndipo izi musaganize kuti mukuulura chakwera koma mukuziulura nose ndipo 2025 kuyanbira namachende iwe ndi MCP yonse mulimmazi
@MollenMponya
@MollenMponya 3 ай бұрын
Osanena Ndege isananyamuke bwanji, tikati ndwe modz mwa Iwo ukana
@KhebranConnections
@KhebranConnections 3 ай бұрын
Aaaa kkkk wokhulupilira izi ndi zoba wenweni a dpp mwapezela mwai koma simungawine chisankho
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 3 ай бұрын
Zazi munasiyirangi kuurura poyamba paja mukuurura rero chirima wapita kare ndarama munadya kare ingokharani chete apa
@antonsam40
@antonsam40 3 ай бұрын
Ndinu wopusa Inu kwabasi bwanji simunanene ndege isananyamuke anthu akanapulumuka onse aja,muli gulu lopha anthu khalani chete basi muzidya ndarama za magazi
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 2 ай бұрын
Aaaaaaaa ndiwenso wakupha bwanji sunaulule zisanachitike unalola kuti anthu afe then udzibwera ndi mabodzawa musatenge ngati chotchukirapotu iyaaaa ukanakhala wanzeru ukadaulula kuti anthu asakwere ndegeyo
@AlufeyoBanda-cv2we
@AlufeyoBanda-cv2we 3 ай бұрын
Choka iweyo ndiye mfiti yotheratu ngat sulapa ukapsa iwe,why kunenana pano satana weniweni iwe
@noelcheonga8247
@noelcheonga8247 3 ай бұрын
Mwakhuta chani kodi kapena mungofuna kutchuka chabe?
@MaryNgwira-s5z
@MaryNgwira-s5z 3 ай бұрын
Ndiye ku mafotokoza zimenezi anthu atataya miyoyo yawo sibwino a Malawi
@TimoteyoInvestments
@TimoteyoInvestments 3 ай бұрын
Iweyo ndiwe mzika yopusa zeedi ukuuzano ndani nyasi zakozo anthu anafa kale ukuganizano kuti zipindula chiyani zomwe ukunenazi foolish.
@lemanwayesi
@lemanwayesi 2 ай бұрын
Ukanakhala wanzeru ukanawaletsa kut asakwere bwenz mwapulumusa anthu
@SafariBvumbwe
@SafariBvumbwe 2 ай бұрын
Nde zipindula chani galu iwe uziwa zot chilima wanga anafa unakanika bwanj kunena isananyamuke
@TriciaMalikebu
@TriciaMalikebu 3 ай бұрын
Why didn’t you alert the team? You are then part of it if that be the case
@CinthiaThaonga-jw6er
@CinthiaThaonga-jw6er 3 ай бұрын
Za zii nde muzikaulula lero zinatani tsku lomwelo kunena 🙁☹️😡
@MtisungePhiri-te9nz
@MtisungePhiri-te9nz 3 ай бұрын
I can't believe this ,this is totally fake
@MphonoMatube
@MphonoMatube 3 ай бұрын
machende ako naweso ndiwe chifwamba galu wachabechabe
@KenDuweh
@KenDuweh 3 ай бұрын
Iwe nde pano upindula chani zinthu zinaonongeka kale sife ogona ngat iwe
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 3 ай бұрын
Hmmm mulungu akuyendere
@JOSEPHPHIRI-ve6ls
@JOSEPHPHIRI-ve6ls 3 ай бұрын
Linali ndibodza anakhala kt amadziwa akanaulula kale kwa chilimayo ngat amamukonda
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em 3 ай бұрын
Mzimu wa chilima anthu musowa nawo mtendere
@Paul-q2p
@Paul-q2p 3 ай бұрын
Uli chaboza ukuyowoya mwahuno wanthu wafwa matongo yako
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 3 ай бұрын
Ululani pano asanakumangeni mukachedwa kuwulula musanga akumangani Phone yanga data yanga ndiye nkhumba zina zizinena musayakule tikumanga ngati zinakugulira phone misala kapena cha. Boma liyambe kaye kugula ma phone ndikupasa anthu ndipamene aziyuka malamulo opepera
Help Me Celebrate! 😍🙏
00:35
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 47 МЛН
БЕЛКА СЬЕЛА КОТЕНКА?#cat
00:13
Лайки Like
Рет қаралды 2,5 МЛН
Миллионер | 1 - серия
34:31
Million Show
Рет қаралды 2 МЛН
KUNG'ALULA MOSAONA NKHOPE_BON KALINDO
16:59
HOT 265
Рет қаралды 51 М.
Oyimba Akugulidwa Ndi MCP
6:22
Sam Malvitha
Рет қаралды 38 М.
Help Me Celebrate! 😍🙏
00:35
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 47 МЛН