APOLICE AYAMBA KUPONYA TEAR GAS KWA ZIPANI ZONSE ZOMWE ZIKUYAMBITSA ZIWAWA PAMENE KALIATI WAMANGIDWA

  Рет қаралды 10,064

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 70
@josephjana695
@josephjana695 Сағат бұрын
Akuti mulanduwake amafuna kupha ndani? Khalani serious guys kodi amene anapha nzake ndi ndani?. Ndiolose ndikakutafune #TRAESON mugwadi ndi bp chaka chino
@Biath-m4b
@Biath-m4b 2 сағат бұрын
More 🔥 a Malawi tisafooke mpaka chilungamo chioneke
@hesbaluku7281
@hesbaluku7281 22 минут бұрын
Km raster uyoyo Ali nd confidence 😊atha kuthibura koopsa
@AnganilyEKNyirendah
@AnganilyEKNyirendah Сағат бұрын
The country has really changed mulungu chitaniponi kanthu
@ChifundoThomas
@ChifundoThomas 32 минут бұрын
Boma Ili tinaliyika tonkha tichotsaso tonkha Chaka cha mawa
@FalesMdemba
@FalesMdemba Сағат бұрын
Utm my vote osaopa osafoka osatopa anyani a mcp anthu ankhaza chipani chakupha
@RaphaelKatimba
@RaphaelKatimba 2 сағат бұрын
Bravo UTM and UDF Aford. God Bless
@MbiNauli
@MbiNauli Сағат бұрын
Yeah Ralph
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 Сағат бұрын
Sukunama Raphael........🔥🔥🔥🔥🔥
@VincentMapira-h1f
@VincentMapira-h1f 10 минут бұрын
Ine ndimafuna nditatero km vuto ndikibe lawyer komanso kabunthabuya
@TimeAbilu
@TimeAbilu 47 минут бұрын
Wanted woman can not be in custody for long time, which means can happen something
@AgnessKaliza-f8i
@AgnessKaliza-f8i 54 минут бұрын
Osaopa osafowoka osatopa 💪💪
@natashamathala8715
@natashamathala8715 Сағат бұрын
Kodo apolice amathamangila kuponya utsikamba ka chani koma anyani awawaaa?
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga 56 минут бұрын
Lilongwe wake uti wavutayo.aa.omwewo osowa zochitawo ndamene ali wekaweka.atoziwana.Lilongwe business usual.
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 2 сағат бұрын
Zoonadi the DC ifeyotu timakunyadilani
@SuzanVictorMadengu-k6v
@SuzanVictorMadengu-k6v 25 минут бұрын
Osatopa osafowoka osaopa dziko ndi lathu ili a Malawi wo nde ndifeyo nde asatiopseze ngati ndife obwera ayi
@BerthaMkwinika
@BerthaMkwinika 2 сағат бұрын
Dzikoli ena azimangidwa ena ayi chonsecho onse alakwa sizoona, aliyense akaphwanya lamulo azimangidwa
@OwamThoko
@OwamThoko 2 сағат бұрын
Ngati apolisi akuphulisa usi munseu amalawi pitani mukhaphulise usi ma office am.boma
@StevenGJohn
@StevenGJohn 55 минут бұрын
Manganya akuona ngati 2025 azakhabe vice president galu kufupika
@masingatichilumba8263
@masingatichilumba8263 Сағат бұрын
Muthamangitsa bwanji anthuwa pomwe akufuna amvere mtsogoleri wao ndipo sakupanga ma demo ayi,
@FionaKhoma
@FionaKhoma Сағат бұрын
Chakwera amangidwa lit zaimfa yachilima
@StevenGJohn
@StevenGJohn 56 минут бұрын
Imeneyi ndi plan ya Micheal Usi munthu oyipa uyu Manganya
@FionaKhoma
@FionaKhoma Сағат бұрын
Chakwera anapha chilima bwanji mlandu sakuyakha or kumangidwa a police osamakondera pomangaathu
@FrankMsiska-i9j
@FrankMsiska-i9j 2 сағат бұрын
UDF igawanikaso pompano 😂😂😂
@shaddaimaonga5832
@shaddaimaonga5832 Сағат бұрын
Koma ndikutha kunvetsetsa, umangotolera zomwe anzako ayika kale
@ZioneMkangadzula
@ZioneMkangadzula 2 сағат бұрын
apolice musatero asiyeni anthu averere milandu mumaziyamba daratu
@MercyMjima-tv5py
@MercyMjima-tv5py Сағат бұрын
Nanu muziponya khuni za Moto ayake amenewo omawaopa athu amenewo
@SolomonAmiduh-y6x
@SolomonAmiduh-y6x Сағат бұрын
Dpp bwanji sinabwele kumeneku?😊
@FestonYona-r9t
@FestonYona-r9t 56 минут бұрын
Mwatizuza kwakwana tsopano muweluzidwa inu a mcp
@MercyDzonzi
@MercyDzonzi Сағат бұрын
Kodi ndekuti ndi one party system
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI 36 минут бұрын
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
@LOKAMJ
@LOKAMJ Сағат бұрын
Nkukuyu sakumumanga bwanji,,,,
@KentWilliam-r2v
@KentWilliam-r2v Сағат бұрын
Let's go DC more fire
@EthelOsman
@EthelOsman 2 сағат бұрын
Koma chilima ayi Zikomo kwambiri mulungu analola kuti mupite dziko lidziwe wabwino ndi oipa
@JohnBanda-e5x
@JohnBanda-e5x Сағат бұрын
Aone nyekweeeee!!!!!!!
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Сағат бұрын
Nthawi imene chilima ali moyo adamangidwa izi kudalibe tinene kuti zikuchitika chifukwa chani
@shaddaimaonga5832
@shaddaimaonga5832 Сағат бұрын
Iwe kapolo tazingoyika osati kulankhuliralankhulura. Ukalemba zakwana basi
@JosephGabriel-y7w
@JosephGabriel-y7w 42 минут бұрын
Moto kuti booooooo😂😂😂😂😂😂🎉
@VictorPhodogoma
@VictorPhodogoma Сағат бұрын
Ukanenetsa kwambiri akutengeta ku chikangawa ohooooh
@StaffordNgalande
@StaffordNgalande 21 минут бұрын
Koma Mulungu sangalole kut athu ake azivutika chifukwa cha M C P Mulungu akatha Chakwela posachedwa a Malawi khulupililani pepani a Mai Kaliati
@JeremiahKapundu-j1p
@JeremiahKapundu-j1p Сағат бұрын
Osaopa osafoka mpak chimbaz adyacho asaze
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 2 сағат бұрын
Dziko ndi anthu ake
@MbiNauli
@MbiNauli Сағат бұрын
Kuipa mtima kotani uku
@LovelyAntenna-rs4pz
@LovelyAntenna-rs4pz 33 минут бұрын
Khaza
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h 6 минут бұрын
Osatopa osaopa osafooka
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 Сағат бұрын
The dc 🔥❤️
@MosesDicostar
@MosesDicostar 2 сағат бұрын
More 🔥🔥🔥 DC
@MaloneFundo
@MaloneFundo 2 сағат бұрын
DC wenwen
@BillyBentryMunthali
@BillyBentryMunthali Сағат бұрын
Mkutaya nthawi
@MagretSaizi
@MagretSaizi 2 сағат бұрын
Aponyeranji tiregus aaaaa
@JabulanKelvin
@JabulanKelvin Сағат бұрын
UTM for life
@JoyceGondwe-ve1zu
@JoyceGondwe-ve1zu Сағат бұрын
Athireni usiwooo. No future
@gmxplayboy6559
@gmxplayboy6559 Сағат бұрын
Osaopa, osafooka n osatopa, it's fight for real democracy as real nation don't fear anyone just fear i will fight for and de reality will set Patricia kalita will set her free in Jesus name
@ChristopherTheu-y3r
@ChristopherTheu-y3r Сағат бұрын
Kwaola hvy
@StevenPhiriJoshua
@StevenPhiriJoshua Сағат бұрын
Osaopa, osafoka,osatopa
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 59 минут бұрын
Koma pamene mwayima apo ndipa chitukuko Cha chakwera misewu yikubeba
@MalickMkweche
@MalickMkweche 30 минут бұрын
Iwe chakwera wakokoyo ali ndi ndalama zomangire nsewu wasowa zokamba eti
@Edson-sj8vn
@Edson-sj8vn 29 минут бұрын
Misonkho sindalama zachakwera wakoyo galu ngat amenei
@trynessmsowoya4187
@trynessmsowoya4187 2 сағат бұрын
Koma dziko lanthu likupita kuti esh
@Twayaibrahim
@Twayaibrahim 56 минут бұрын
Kkk latchena kwambiri het? 😂
@EusterGoliath
@EusterGoliath Сағат бұрын
Sizona
@KalongaWhy
@KalongaWhy 2 сағат бұрын
Moto buuuu
@AbdulMalik-o7n1q
@AbdulMalik-o7n1q 2 сағат бұрын
DPP Kodi sonabweleko lelo
@MzadziWanga
@MzadziWanga Сағат бұрын
Mwina apita kukavelera mulandu wa ku mec paja amati chigamulo chiliko lero
@LOKAMJ
@LOKAMJ Сағат бұрын
Aliko,,achina sulemani
@chrisboyce2
@chrisboyce2 2 сағат бұрын
apapa ma demo ndiye ayamba mpaka pa 30 OSAOPA💪 Alunta Continua 💪 (SKC💔)
@FrankMsiska-i9j
@FrankMsiska-i9j 2 сағат бұрын
Anthu mukusowa zochita et 😂😂😂
@BettieKamija
@BettieKamija 2 сағат бұрын
Iwe uli nazo zoopha anthu
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 2 сағат бұрын
Osaopa osafooka osatopa
Как не носить с собой вещи
00:31
Miracle
Рет қаралды 1,7 МЛН
小丑家的感情危机!#小丑#天使#家庭
00:15
家庭搞笑日记
Рет қаралды 36 МЛН
Flipping Robot vs Heavier And Heavier Objects
00:34
Mark Rober
Рет қаралды 59 МЛН
didn't manage to catch the ball #tiktok
00:19
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 34 МЛН
COMRADE FRANK -TAMVANI ZENI ZENI ZOMWE AMUMANGIRA KALIATI UJA AMALAWI.
9:04
Как не носить с собой вещи
00:31
Miracle
Рет қаралды 1,7 МЛН