ATUPELE MULUZI 2025 AKUTENGA BOMA WINA AFUNE ASAFUNE - CHINANTINDI CHA WANTHU KU MANGOCHI UDF

  Рет қаралды 9,212

AM TV MALAWI

AM TV MALAWI

Күн бұрын

Пікірлер: 38
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 4 күн бұрын
Atupele my vote ❤❤❤
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 7 күн бұрын
AMENE MUKUWAONAWOTU NDI ANTHU SI MAVOTI VUTO ATUPERE ALI NGATI MADUNDE PANYANJA AMAPITA KOMWE MPHEPO IKUPITA , SANGAWINE UYU NGATI AKYFUNA KUWINA ASIYE KUBISALA KWA CHIKANGAWA UYU NDI MPENI OKUTHWA KONSE KONSE AKUCHEKANI
@MayimunaZuber
@MayimunaZuber 5 күн бұрын
Ndipo atupele ndimunthu osazikweza
@StevenDastan-f5y
@StevenDastan-f5y 9 күн бұрын
Aaaaa osayerekeza ndi Apm ndikuchikweza
@KeffasiJonathan
@KeffasiJonathan 9 күн бұрын
Mmm awa ayii awa
@StevenThanila
@StevenThanila 5 күн бұрын
Bvuto home ground imapusitsa, and all these paties akusewela in their own half.. How can they score ?
@JamiraJamirashaime
@JamiraJamirashaime 7 күн бұрын
Sanga wine uyu ndiwa Mcp tinamutuluka 😅😅😅😅😅😢
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 9 күн бұрын
Uyutu or atapada kuvoteledwa mkuvoteledwaso chakwela yemweyu sikuti yeyu angagone ndinjala pakjolo pake,,,sikuti angosowe fuel ovutika ndife uyutu alindindalama pomwe enawa anabwela alibe kalikose akalowa m'boma angaganize chiyani choyamba,,,,,sikuba basi,,,,timanyoza munthu emwe alindi tsogolo koma mmmm amalawife okanika tiyeni tivoteleni omwewa achakwelawa basi umphawi kuvutika kunatikakamila amalawi,,,sikuti angakoze zose 100%sizingatheke nayeso ndi munthu,,,,koma wagwilako ntchito m'boma wapangoso ndale wayimilakoso u mp kudela kwake,,,,pomwe enawa or unduna wakumudzi sakuwudziwayi kugwila ntchito ku Chipiku tikumusankha kukhala president 😂😂😂😂😂😂komaso malawi yovetsa chisoni kobasi
@abasikazembe892
@abasikazembe892 8 күн бұрын
Leave them yakula ndi jerous basi ngati angamake pa atupele
@HanifaMussah
@HanifaMussah 8 күн бұрын
Atupere akutenga boma 2025
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 9 күн бұрын
15, year's ali MP anapanga chani kumachinga Nselema,,0,pa 100,, uyutu ndiwozikonda amane simukumudziwa muzichiwombera manja koma ine ayi 😏
@QueneteCatundulo
@QueneteCatundulo 9 күн бұрын
Boma dpp
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 8 күн бұрын
Tupere wosangalala kwambili
@MoneyTiririMgwagwa
@MoneyTiririMgwagwa 8 күн бұрын
Awina ndipo muzavomeleza
@IssahBwanali-i8w
@IssahBwanali-i8w 9 күн бұрын
Atupele sangawine olo pavuta bwanji
@isaaczuze
@isaaczuze 9 күн бұрын
Munthu oti iweyo si mp atupele palibe angachite ndi mwana kwambili ....tiyeni opposition tigwilizane .....atupele payekha palibe angachite
@MayimunaZuber
@MayimunaZuber 5 күн бұрын
Ndipo UDF 2025 Boma ufune usafune
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 7 күн бұрын
Machinga ndi Mangochi ndkwao kwa UDF and izizi sizodabwisa Kut kwazaza anthu chochi Koma boma sangatenge
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h 9 күн бұрын
UDF ndidzina lonyansa kwambili kwaine nsimafunaso ndidziliva olo
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 8 күн бұрын
Simat matiki ili popo?iiiii komat ngat khaniy akuyitengera ize...mm athuwa azazion
@HaleemaAllie
@HaleemaAllie 7 күн бұрын
Kayazasawina akuziwandi mulungu potion mulungu amaziwa mutima MWA munthu koma so abale chomwe mungaziwe chakuti munthu yemwe muma chodza ndi amene amakala wa wino pazogolo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 9 күн бұрын
Ngt Mulungu avomereze atenga boma koma koz Mulungu amasankha yemwe amudalitsa kudazadxa kumsonkhano kusakupusisen
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t 6 күн бұрын
Munthu opusa uyu
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 9 күн бұрын
Bomali kuti litengedwe inu a oposition mumenye nkhondo smart matic ngati simutero nde muiwale cifukwa cikangawayi wabela kale APM voti yathu 2025
@ChrissyBhima
@ChrissyBhima 9 күн бұрын
Atupere ndale zanu mukufuna muzilimbana ndi osusa anzanu zimenezo sizikuthandiza I,inu Malo momalimbana ndi chakwera Mene walisinthira dzikoli lero Kumati DPP inatibera Boma,pamenepo Pali nzeru? nanga inu munamubera ndani?ndale zanu atupere anthu akukudabwani
@arnoldchayamba4088
@arnoldchayamba4088 9 күн бұрын
Bwana is not true kuti Boma anachita kuba wa DPP?ngati ndinu achipanicho mudziwe zimenezo
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 9 күн бұрын
Boma silibacite kubedwa kunali ngatj mwana akakula banja amafunika akayime payekha eetu wamkulu dpp oyee!
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 9 күн бұрын
Atupere ndiwozikonda amazuva too much koma ndi 0,pa100
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 8 күн бұрын
Kutenga boma Atupele kkkk fodya kapena chani this guy is puppet of MCP.
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u 8 күн бұрын
Ndipo anthu a UDF mulibe manyazi penapake sure, ine ndi waku Balaka, Atupele ndimamukonda koma sindinganyoze DPP or kunena zoti DPP ili ndi mantha ndi Atupele 😂😂😂😂😂 ndaseka kuli kumva chisoni cz tikanena za APM, from nsanje to chitipa!!!! Eeeeish ineyo sindina zambiri, Tiyeni muwona PA ground and even Atupeleyo akudziwa komwe aliko kuti sangamake kwa APM, more over anthu azindikire tsopano kuti adachotsa APM munthu wabwino then mkusankva satana tili nayeyu nde anthu omwewo akufuna kubwezeletsa,koma mukati mumutame Atupele then ayime payekha, adzagwa mufune musafune adzathawanso kuti ndale wasiya 😂😂😂😂
@CleanwellPhiri
@CleanwellPhiri 9 күн бұрын
Azavota okha akumangocchi?
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h 9 күн бұрын
Uyu wachikasu anatikwana anationongela beu munda
@spargomw
@spargomw 8 күн бұрын
Maloto achumba
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma 9 күн бұрын
Azimuwopa adpp osati MCP nichipembedzo
@symoldicky
@symoldicky 7 күн бұрын
MCP inayamba yawino payokha kut Munthu ukkhale nayo ntima mwamba
@YoungMwacho
@YoungMwacho 7 күн бұрын
Arupele is a crook, he wants to divide votes for MCP to win. Atupele you have shown that you are also a failed leader ngati Chakwela. Instead of uniting with the opposition to remove MCP out of power koma ukulota zowina pawekha. Are you really serious Atupele? kukonda ndalama kuzakuphani mmene kumuphere Chakwela ndi azinzake.
@Frederick-s4h
@Frederick-s4h 9 күн бұрын
Bomalakeliti atenga angati bomali muthallka adzakhala alikut kkkkk mukunama zd
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH ATUPELE MULUZI
1:10:49
Zodiak Malawi
Рет қаралды 43 М.
Presidential National Address
17:25
State House Malawi
Рет қаралды 2,9 М.
Turn Off the Vacum And Sit Back and Laugh 🤣
00:34
SKITSFUL
Рет қаралды 11 МЛН
One day.. 🙌
00:33
Celine Dept
Рет қаралды 75 МЛН
Lamborghini vs Smoke 😱
00:38
Topper Guild
Рет қаралды 64 МЛН
Nyimbo Za Ndale - Akawina Atupele Mudzapanga Cha
5:07
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 6 М.
TIMES EXCLUSIVE| 07 DECEMBER 2024| SAMEER SULEMAN - MP
58:50
Malawi News Update
Рет қаралды 36 М.
TIKUFERANJI? | 8 December 2024
23:49
Malawi News Update
Рет қаралды 26 М.
Times Exclusive featuring Sameer Sulemani - 13 April 2024
1:00:14
Times 360 Malawi
Рет қаралды 102 М.
Turn Off the Vacum And Sit Back and Laugh 🤣
00:34
SKITSFUL
Рет қаралды 11 МЛН