Iyi ndi mbiri ya mpingo wa Seventh Day Adventist padziko lonse lapansi.
Пікірлер: 75
@user-sh5wq4uf6r2 күн бұрын
Good history keep it up
@bakhtullah51543 жыл бұрын
Thanks for the best video.
@mukatitchulebrand92443 жыл бұрын
Good jod done mr ,,,,,continue doing it
@ishmaelbilali5742 жыл бұрын
Wow brother still following, keep it up
@bkelly30533 жыл бұрын
keep it up boss tikuziwa zambili kamba ka inu ulemu wanu💪
@bestonjoseph21933 жыл бұрын
Good job Mr 🙏🙏
@chinsinsikundiya11715 ай бұрын
Great history 🎉
@dorikakamwendo69703 жыл бұрын
Nice church
@cephasnkhoma2301 Жыл бұрын
Now did you have the books of those history's? .because this is my food to study those things.
@djsishimanemunena6785 Жыл бұрын
Big up bwana mumandivetsa kukoma in Munena sandram.
@umaliisah69203 жыл бұрын
Thanx man
@blessingchirwa86832 жыл бұрын
God bless our sda
@lusayomkumbwa2113 жыл бұрын
Good stuff, keep the good work
@basiliojeremias62002 жыл бұрын
Ambuye apitilize ku peleka Nzelu ndi Mavumbulutso. koma ndimati ndipemphe kuti pa Chito yanuyi ikufunika mutenge Yesu akhale mbuye ndi pulumusi wanu chifukwa amagelasi ndi ambili pakufunika chitetezo chochokela kumwamba
@user-zc9wb4dj4q4 ай бұрын
Man of God,let me talk with you,I have so many questions
For God so loved the world , that he gave his only begotten son, that whoever believes in him should not perish but have eternal life (John 3v16)Let not your hearts be troubled , Believe in God believe also in me ,in my father's house are many rooms ,if it were not so,l would have told you that l go to prepare a place for you.And if I go and prepare a place for you,l will come again and will take you to myself , that where l a'm you may be also.(John 14v1)"l a'm the way ,and the truth ,and Life,No one comes to the father except through me"(John 14v6)
@franciskhundi93353 жыл бұрын
Ambuye akutsogoleri pantchito yomwe mukugwira
@ThokiseWiriyam-ws1ec11 ай бұрын
Ame
@prosskaymw99533 жыл бұрын
Nkhan yabwino ndithu
@cephasnkhoma2301 Жыл бұрын
Koma inuyo muli ndi zida ndithu, mulugu akutsungeni. ndi inutso mumu kuluphilire.
@johnstonumali5881 Жыл бұрын
Aah koma adha mumatha ulemu wanu
@ezakidalitso65232 жыл бұрын
Bola muzikamba zowona kamba anthu sakhulupilaka
@chippiephiri4505 Жыл бұрын
To God be all the glory
@sanlakedickson67803 жыл бұрын
Tipangileni mbiri ya charlies chaplin
@johnbauya17943 жыл бұрын
Nkhani yopatsa chidwi
@user-pg4pt9bl6n Жыл бұрын
Amen 🙏🙏🙏 to God be the glory 🙏🙏
@spiwejafal72683 жыл бұрын
Kodi aulutsi a program imeneyi ya kafukufuku wa mbiri za maiko Muli mpingo wanji
@osmank.milanzi8836 Жыл бұрын
Man inuyo mumatha
@husseinsamuson51733 жыл бұрын
Mumakwani tikudzindikila zambili kuchokelakwainu
@kholwanigondwe9086 Жыл бұрын
Kufotokoza kwabwino
@gabrielatanasiopessulane12792 жыл бұрын
Mwalankhula zoona...coz nkhaniyi ndikuidziwa
@kuziririzaisabatosiitegeko7088 Жыл бұрын
😆😆😆😆😆
@nditumenichagunda4192 Жыл бұрын
Anthu a sda amazitenga ngati oyera mtima namanyoza anzao chikhalirecho background ya mpingo wao it's from fake prophet komanso ziphunzitso za mpingo wao zikuchokela munthu wachabechabe otchedwa Ellen g white osatinso mulungu
@memorylipenga20697 ай бұрын
Ine ndi mmodzi wa seventh-day adventist koma sindinamveke akunyoza mpingo wa munthu aliyense amangolalikira kuti yemwe alinalo khutu amvee chifukwa chipulumuso aliyense ndi chayekha ndipo momwe amayakhula apa sananyozepo seventh-day adventist wangonena za mbiri ndi chiyambi chake
@thembaphiri45233 жыл бұрын
Welcome to muslim truth religion in the world mark 13:21 quran 3:19 from blantyre
@truthtellerlastonk.m.p49853 жыл бұрын
Zoona mzoti kulibeso munthu otchedwa Jesus amene adzabwere kuchoka kwamwamba,,,,, I was Jehovah's witness Christian,,, but I quit it,,,, please next time tell us about history of Jehovah's witness
@truthtellerlastonk.m.p49853 жыл бұрын
@hope saiden zabodza izo
@truthtellerlastonk.m.p49853 жыл бұрын
@hope saiden don't waste my time with your Jesus,,, he's nothing for me 🤷🤷,,, and the story of Jesus it's not real so I don't want to talk about it
@truthtellerlastonk.m.p49853 жыл бұрын
@hope saiden mapeto achani inuso zongotaisana nthaw I was one of those people they preach this so called good news,, but it's just waste of time,, ndinali mkhristu wa mbon za yehova, not just a witness ai I was minestrial servant ( Mtumiki othandiza) ndalalikira kwambiri, koma am telling you mzachabechabe zongotaisana nthaw,,, open your mind brother and see the truth,,, now am just regretting for the time I wasted when I was Christian,,,,, but am happy coz I know the truth now,, and it was not too late,, even for you it's not too late
@truthtellerlastonk.m.p49853 жыл бұрын
@hope saiden thanks for understanding don't waste your time for nonsese thing,,,,,,,
@truthtellerlastonk.m.p49853 жыл бұрын
@hope saiden all of Christianity issue
@andrewmaluwa2713 Жыл бұрын
Ine always ndimanena kuti chimphuzitso cha seventh day Adventist, sicholongosoka coz anthu omwe adayambitsa mpingowu amatsogoleledwa ndi munthu wabodza fake prophet, mpovuta kuti omutsatila ake adzikamba zoona
@yamikansintala4178 Жыл бұрын
Exactly ndithu
@patelaysha7752 Жыл бұрын
yese amene akuti kulibe Jesus amene adzabwere uli ndi tsoka chifukwa iwe otchedwaso kristu koma osadziwa Yesu, uwelenge chivumbulutso 1 vest 7 komaso machitidwe 1 vest 11, khalani nchocho mumuona posachedwa akubwela
@olivechikwindi9126 Жыл бұрын
Asaaaaaa kuyankhula kwabwanji uku?
@francisevalleygama2984 Жыл бұрын
U shall know the truth and the truth will set u free. There were others who were spoken like u but today they are members of SDA Church after knowing the truth. May good LORD help u
@johnsoko70983 жыл бұрын
Amen
@patelaysha7752 Жыл бұрын
ndikutanthauza mpingo owona ndiuti
@patelaysha7752 Жыл бұрын
kapena ungandiuze iwe khristu zanga malamulo a mulungu Ten anja lilipo or limodzi lomwe linatha mphamvu koti tisaligwiritseso ntchito nde ngati ukuti ai ,nanga ndichifukwa chani la mulo number 4 sumalitsata? akuti uzikumbukila tsiku lasabata,motani,ungandiuze?