BEN LONGWE WABWELA KUZAFUKULA ZA NDEGE YOMWE IDAPHA ACHILIMA 🙌🙌😱

  Рет қаралды 13,716

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 43
@AliceMwakhundi
@AliceMwakhundi 10 күн бұрын
Well expounded waiting for the next episode
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 10 күн бұрын
Ben longwe simunthu omumvera kulankhura kwake,satha kubooleza ali ngati mwendo wina uli uko wina uli uko sadalirika
@WysonChilonga
@WysonChilonga 10 күн бұрын
aaaa waipa lero chifukwa akuyankhula chilungamo?😢😢,ife timumvera
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 10 күн бұрын
Kulankhura kwa Beni longwe nkofewa nkamwa ngati mwana obadwa kumene,kulankhura kwao nkokhara ngati mkamwa muli minga nde kuti amasuke atambasule lirrime ngati kuti akuopa ndi minga kuwabaya,salankhula mobooleza
@Yamikie-yamikie
@Yamikie-yamikie 10 күн бұрын
Ben longwe is regaining his senses now😅
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f 10 күн бұрын
Zoona Ben Longwe Mcp yamumanadi chibanzi
@WatsonMzava-k9f
@WatsonMzava-k9f 11 күн бұрын
From South Africa
@ThomasMaxwell-ks7yi
@ThomasMaxwell-ks7yi 10 күн бұрын
Zoonadi nkhaniyo mukambayo anthu tikutsatani ambili enawa majelas❤❤❤
@phadybaugpa3361
@phadybaugpa3361 10 күн бұрын
Very good brain storming
@PazAutomb
@PazAutomb 10 күн бұрын
Boma ili iiiiiiih lad mbuli
@WysonChilonga
@WysonChilonga 10 күн бұрын
lakupha Biyeni
@GodfreyMaliseya
@GodfreyMaliseya 10 күн бұрын
😂😅ben longwe nzeru ulibe
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 10 күн бұрын
Uladi musa Amubwilitsa dothi ku MCP, achikaulitsa chimakonda kupita ku zipani zolamula kutsata unduna Uku wakumana ndi mchewa change golo. Andale adyela chonchi kumawatelo ndithu
@KondwaniKubwalo
@KondwaniKubwalo 10 күн бұрын
Ben longwe wayamba chibwana usamale ife tikulila
@AnorldKamponda
@AnorldKamponda 10 күн бұрын
Samakutukwanani akulu Koma Kukuuzani zoona, munapepelabe pakati po, chilungamo uxhidziwa
@michaelzuze6516
@michaelzuze6516 11 күн бұрын
University of Hard knocks 😂
@victorbanda9039
@victorbanda9039 10 күн бұрын
Wachita bwino kuyamba kunyoza boma atapidwe tsopano akayankhe milandu yose amapalamula ali ku south Africa ija ananyoza majaji apolice present nduna apa ayankhe tsopano
@hagayichiluwe
@hagayichiluwe 10 күн бұрын
zaziiiiii
@moyowrobert3331
@moyowrobert3331 10 күн бұрын
just wait for 2025 chakwera ndazake akukalowa anapha chilima ndiazake this time a malawi sitikugina
@RodgersBanda-l6j
@RodgersBanda-l6j 11 күн бұрын
Koma Mayi Yolamu Aja unawakoka zokokakoka zija,,,
@PazAutomb
@PazAutomb 10 күн бұрын
This is real commission we expect to be not chikangawa
@dalitsosakwata
@dalitsosakwata 10 күн бұрын
Ndipo Chekwerayu osamangoti MR bwanji? Ine u DR opanda ntchito umandimyasa 😔
@tasmania527
@tasmania527 10 күн бұрын
Pa Malawi padzadza anthu ozungulira mitu monga a Ben Longwewa. You fail to wonder kuti peni peni wayima pati?
@LogicBowman-fk3is
@LogicBowman-fk3is 10 күн бұрын
Inu tinakutulukani kale mulibenso nfundo
@Williammkandawire-x6z
@Williammkandawire-x6z 10 күн бұрын
ali ngati Mtambo
@Williammkandawire-x6z
@Williammkandawire-x6z 10 күн бұрын
Ben, Akulu people die n if you want to achieve something unasuzgo. sanakupatse
@WysonChilonga
@WysonChilonga 10 күн бұрын
aaaa anafa anafa chani,anthu anachita kuphedwa and anthu anachita zimenezi akudziwika,musatipusitsepo apa,Ben Longwe auze
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 10 күн бұрын
Zoduka mutu zokhazokha udali kuti ndi maganizo ako opusawo anthu alira atopa kapanyo ngati iwe uzikasokosela pano uziwuza anthu pepela
@JamesMatupi
@JamesMatupi 11 күн бұрын
Ukuonesa uchitsiru wako Ben Longwe zopusa zokha zokha
@WysonChilonga
@WysonChilonga 10 күн бұрын
chifukwa akuyankhula chilungamo 😢, shame on mcp
@AlumakioChingalu
@AlumakioChingalu 10 күн бұрын
Awa angotitayitsa nthawi .ndachitsiru
@alfredpatel3984
@alfredpatel3984 10 күн бұрын
Kodi alipo akuluwa?? Amajiya za UDF kenako DPP panopo akujiya za MCP. Komatu pano sakuoneka chonchi akuluwa. Anayamba kukhala analyst waza ndege? Zotukwana IG asiya? Zotukwana Chakwera anasiya? Zotukwana APM apumano?? Anapanga ma origin andege?? Ndiye kuti chani??
@KingsleyWilliams-y1x
@KingsleyWilliams-y1x 10 күн бұрын
Inutu dyela lizakuphani man
@KondwaniKubwalo
@KondwaniKubwalo 10 күн бұрын
Wakutuma ndani usamale zopusazakozo ugaluwako
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 10 күн бұрын
Muliko mfundo mu nkhaniyi
@ChrisPhiri-s2p
@ChrisPhiri-s2p 10 күн бұрын
Ine Ben Longwe ndinamutuluka kalekale since anayamba kupanga za Mcp ndie apa or mukubweranso after kumanidwa chiguma ndi lazalo koma fanz inakutulukani man u better stick one side cos ur comfusing us ndi dyera lakolo
@WysonChilonga
@WysonChilonga 10 күн бұрын
aaaa wamutuluka ndi iwe ife nde tili nayenaye Ben Longwe and akuyankhulachi ndi chilungamo you think mungatipusitse?,imfa ya Biyeni imatiwawatu and ndife okwiya
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 10 күн бұрын
Vuto lolowa uku ndi uko Zimavuta .Timvele ndani munali Chete nthawi yonse ija abale.Any way Only God knows
@stanleychisale198
@stanleychisale198 10 күн бұрын
Nonsense. We are sick and tired of it.
@BMDMasulani
@BMDMasulani 10 күн бұрын
Ben longwe ndikape
@Williammkandawire-x6z
@Williammkandawire-x6z 10 күн бұрын
ukuzipanga contradict kwambiri. iwe info yako ili partizan. uzionela nat geo on planes. you r lyng
HOT CURRENT YA LERO NDIYE ANG'ALULA MCP__2 February 2025
50:48
The Lost World: Living Room Edition
0:46
Daniel LaBelle
Рет қаралды 27 МЛН
Prophet Uyu Walosera Zoopsa Pa Zisankho Zikubwerazi ... Tanvani
27:34
BON KALINDO WANG'ALULA ZOGAWA CHIMANGA__4 February 2025
15:50
Ben Longwe Kuyankhula Za Ku Chikangawa - Part 3
21:04
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 11 М.