KOMA NGATI AKULU AWA KULANKHULA KWAKE KUZIKHALA KOTERO, BASI KU MCP ASAZALOWESO CHIFUKWA AZAMUSWA

  Рет қаралды 61,435

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 131
@johannesmorutha6842
@johannesmorutha6842 25 күн бұрын
Dpp🔥🔥🔥🔥 we still ❤❤❤💪💪
@GraceMuthema
@GraceMuthema 28 күн бұрын
Olo munene bwanj koma ife we are the Blues for good 💙💙💙
@MaxwellNdiwo
@MaxwellNdiwo Ай бұрын
Zaziii
@JosephLahaji
@JosephLahaji Ай бұрын
Abwana kumaganiza.,vuto si Inu koma nsanje,musaiwale tinali mmomo,anachita kutithamangitsa,kukamba za munthu zitichedwetsa,tiwauze amalawi zomwe tidzachite
@SandikondaIsaac
@SandikondaIsaac 22 күн бұрын
Uyuyu akukwanira
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 23 күн бұрын
Osamaiwa a enatu lelo alowa mcp koma ankalankhulatu za mcp molapitsa koma lelo bwa dalo konko ayambanso kulalata za apm ndi dpp asiyeni alalate basi
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness Ай бұрын
Koma pamene ndikuwona uchitsilu wanu enanu adpp ndiyapa mukuti mukufuna anthu akuvoteleni mukuwanenaso pansonkhano kuti sakukuwa chifukwa alindinjara kukhala ngati mukuwanyoza bwanji ngati mulindinzeru anthu anu mukufuna akuvotereni osabwelesa lore yachimanga ndikuwapasa kuti akuvoteleni bwino koma mukunyoza boma pamene boma bolani anthu limathandiza vuto ndilakuti chakudya choyesa kupasidwa sichingathe njara pamuzi boma limayesera kupeleka koma inuyo osathandiza koma basi kukhalira kunyoza anzanu basj zaziii
@ManuelyacobntimuniYacobnti-i1q
@ManuelyacobntimuniYacobnti-i1q Ай бұрын
20025 dpp mboma
@ChikumbaLenzo
@ChikumbaLenzo Ай бұрын
ineyo ndikukuuza kuti kubela sikuzatheka mulungu alinafe azayika chidima macomputer akewo obilawo
@SandikondaIsaac
@SandikondaIsaac 22 күн бұрын
Suleman wabwera
@AusteenSumael
@AusteenSumael 22 күн бұрын
Ndy mwat leave in peace not peices😂😂😂
@VictorMaluwah-u3q
@VictorMaluwah-u3q Ай бұрын
This is true pastor ad my God answer this prayer
@SettyPhiri
@SettyPhiri 26 күн бұрын
Hi
@NosparPalamelagee
@NosparPalamelagee Ай бұрын
Zilibwino dpp my team
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness Ай бұрын
Koma iweyo ukulankhura mopusa kwambiri suleman walankhura ngati mawa kulibe zimenezo mawa uzapanga nazo manyazi ngati anthu akufa ndinjara iweyo wanzeru wapangapo chani zeru mulibe ndalama zija munali kuba muboma zilikuti mukunyozaso anthu kuti njala inu mukukhuta bwanji anthu anuwo osapasa chakudya kulankhura mopusa
@SankpA-t9
@SankpA-t9 Ай бұрын
Mesa Prophet Bushiri anayifuna island koma not possible so now yaperekedwa kwa mulendo mmmmmh
@LiahRestoration
@LiahRestoration Ай бұрын
💙💙💙Apm my vote🥰
@RashidiRashidmwemed
@RashidiRashidmwemed Ай бұрын
pieter❤❤❤
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h Ай бұрын
Chitsiru iwe galu, DPP singabweleso Boma, Nyani afisi inu okuba inu okupha ma Albino.
@ebinazielkandomo7803
@ebinazielkandomo7803 Ай бұрын
Kodi chimanga chomwe chabwera kuchokera ku Ukraine chabwera ndi boma liti? Zinazi pa podium azilakhula zomwe adzachita.
@michaelchimwala-x8t
@michaelchimwala-x8t Ай бұрын
God bless Dpp to win 2025 Election
@AbdulIssah-l1e
@AbdulIssah-l1e Ай бұрын
Dpp woyeeeeeeeh 2025 boma.
@herbertmsunje
@herbertmsunje Ай бұрын
Palibe fundo apaa, boma sayendetsa ngati mmene akuganizira. Mudali pomwepo osanamiza anthu. Palibe chomwe chimachitika. Ingonenani kuti kunja kwa boma kawawa. Ine sindingakhulupire zimenezo.
@GreyShadreck
@GreyShadreck Ай бұрын
❤❤❤
@AliceMpango
@AliceMpango Ай бұрын
MCP zao zada basi or atachita motani
@FrankMankhokwe
@FrankMankhokwe Ай бұрын
Kulirauku
@FulumoFulumo
@FulumoFulumo Ай бұрын
Amezing
@AndrewKaira
@AndrewKaira Ай бұрын
Dpp mzapanga chan mkawina mkungotukwana koma fundo palibe.... Anthu opusa kungoombera mumanja zilizose
@DouglasDimingu
@DouglasDimingu Ай бұрын
True saying
@AlumakioChingalu
@AlumakioChingalu 26 күн бұрын
Asiyeni alomqe ndi. DPPyawo yofoirayo
@DaveChinomba
@DaveChinomba Ай бұрын
Kupatula ine Dpp sindimaifuna olo pang'ono ndinali mphawi ngakhale ndimalima koma pano chakwera wandikweza ndagula njinga yamoto kanthawi kochepa kuzera kuulimi omwe ndimalima😂😂😂.
@AndrewKaira
@AndrewKaira Ай бұрын
Oroso ine boma ndilomweli
@usumanidaudi
@usumanidaudi Ай бұрын
Kubera ma vote mcp 2025 tizayambisa nkhondo yowospa kwambiri
@GreshamKadzembe-tn8cq
@GreshamKadzembe-tn8cq Ай бұрын
Inu mukaba mavote amayambitsa nkhondo ndindani
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness Ай бұрын
Zaziii mukuyesa nkhondo ndimasewera inuyo mwina mumangomva nkhondo nthawi zambiri munthu akati iwe ndiwe wakuba uzewe kuti nayeso ndiwakuba wandiziwa bwanji sopano adpp ayika kwambiri panzero yoti amcp azaba mavote akuganiza zija anali kupanga iwowo zakuba zija panopa boma liri ndanzawo zayamba kuwapweteka panopa
@DinhLawck82
@DinhLawck82 Ай бұрын
Ife ngabhobho Ku DPP nkwathu basi..
@BlessingsmChiipira
@BlessingsmChiipira 28 күн бұрын
Kungodzivuta agalu inu
@EmmyYafete
@EmmyYafete Ай бұрын
inuyo ndiamene munasiya DPP ,ife timaikondabe kwambili ndipo tilowa boma, nyau ukoo!!!
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke Ай бұрын
Ndipo straight win 2025
@PreciousDzonzie
@PreciousDzonzie Ай бұрын
Malawi wake uti iwe ukudzinamiza sitingalore kt muzayambireso kupha azathu acalubino zausatana tinakana zotetherana maofes tinakana Malawi wake uyu simudzalamuliraposo munatenga tsoka athu akupha inu
@bs-malawi
@bs-malawi Ай бұрын
Kkkkk koma kumeneko
@Okalekale
@Okalekale Ай бұрын
DPP munapatsidwa mpata munalephera,m'mangopha ma albino ndi anthu ena ambiri mapeto ake mumaba ma votes,ulendo uno sizitheka kuba ma votes.DPP inapita ndi Bingu,DPP ya Peter ndi ya alonwe okha.Ngati munthu suli mu lomwe uwonongapo vote yako,votela zipani zina zoyimila aMalawi onse osati chipani cha kwa Muthalika,azalemeletsana okha okha ngati m'mene ankapangila kale lija iwe ukuvutikabe.Chenjera Malawi. Ma passports anasiyidwa kupanga nthawi ya Peter,ndalama inayamba kugwa kwambiri nthawi ya Peter,tikudziwa zimenezo ndi chifukwa chake Malawi sinafunenso DPP ndipo sitikuyifunanso or 2025.
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh Ай бұрын
Suleman machine opangira machine anzake
@AbdulIssah-l1e
@AbdulIssah-l1e Ай бұрын
Malawi yonse dpp boma .mabro osapita kusukuluo plz achoke dpp 2025 boma❤❤❤❤
@Biath-m4b
@Biath-m4b Ай бұрын
Suleiman big boss koma tikukudaliran kwambiritu mukuoneka dziko mukhoza kusintha
@LukasiginalaLusaka-v7y
@LukasiginalaLusaka-v7y Ай бұрын
Dpp bom 2025
@AllieJonassi
@AllieJonassi Ай бұрын
Suleman nd machine omanga nd mawaya
@FrankMankhokwe
@FrankMankhokwe Ай бұрын
Za ziiiiiii
@GoldenZebediaMkandawire
@GoldenZebediaMkandawire Ай бұрын
Siku transport 😅😅😅
@winstonbelon482
@winstonbelon482 Ай бұрын
Ili ndi pemphero la a nd ale,,,,,
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 Ай бұрын
DPP Ndikufuna itadzawina komq vuto kwachuluka kudzikonda akutaya ma member ambiri Kuzikonda kwambiri
@HlamuChavalala
@HlamuChavalala Ай бұрын
A MCP muzithu zonse matengedwe aboma ziwembu Zanu zimene mumachita Ndi Mulungu adzakuchitileni chilichonse Kuti mudzadziwe Kuti athufe tilindi amene anatilenga nayeso Mulungu Ali okonzeka Kuti akudziwitse yemwe analenga malawi uwakakamila bwanji athupomwe sakukufuna ndithu ndipo ufune usafune ulangidwa ndithu chilango maso akoudzadzionela wekha ndipo ukanalowa mitima mwawathu amangokuonangati gahena mmene ukumaonekela
@RechealHarry99
@RechealHarry99 Ай бұрын
Suleman mulungu azikusungani mumakonda athu Anu
@FlorenceDouglas-x5c
@FlorenceDouglas-x5c Ай бұрын
MCP ndiyomwe izakhale Ku opposition 2070 yo 😠 Afiti a MCP mu
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs Ай бұрын
❤❤💙💙💙
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td Ай бұрын
Opempherayu siwakumalawi atate muzina ndiye Kuti chani if MCP basi DPP kulibe inatha boma dilomweli
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza Ай бұрын
Only God knows who is going to win
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo Ай бұрын
Dpp 🔥🔥🔥🔥
@ChikumbaLenzo
@ChikumbaLenzo Ай бұрын
chonde amalawi anzanga titsamangoziwa kulankhula koma tizionesa action mubvitu oyang'anila ulowa m'maso tikuona
@Giftwwiseman
@Giftwwiseman Ай бұрын
MCP woyeee
@alubisabili5188
@alubisabili5188 Ай бұрын
Need change
@alubisabili5188
@alubisabili5188 Ай бұрын
@EnockSankhylani
@EnockSankhylani Ай бұрын
Dpp bolani feteleza bolani komanso inu mitengo yazonthu zinali bwino ndalama. Inali yonkhazikika koma kupita kooda ukapeza ntengo w nte
@RargieMediaclassic
@RargieMediaclassic Ай бұрын
Kom dpp ili ndi Master of ceremony mbambande.ati chala mmwamba chamakande😂😂
@LovemoreKamoto
@LovemoreKamoto Ай бұрын
Mukati anthu sakufuna mcp ukunama ndiweyo ndi ana ako usamaphatikizane ndifetomwe
@omaligeorge4296
@omaligeorge4296 Ай бұрын
Ineso sindikuifuna
@JeniferKananji
@JeniferKananji Ай бұрын
Chakwela ayende ngat Madzi amunyanja
@bornface4786
@bornface4786 Ай бұрын
God must help Malawi
@ChimzyWesley
@ChimzyWesley Ай бұрын
Anthu akumudzi nthawi zino chakudya chinali palipose koma lelo mmmmm Malawi wanunkha
@anoldkapolo4493
@anoldkapolo4493 Ай бұрын
Bodza iwe ungagule fertilizer mkupatsa anthu. Ndikwakwera yekha akutukula dziko lino mwa nyoooo. Achita bwino kukusankhani kuti mcp ikukodzetseni limodzi ndi nkhalamba yanuyi. Simungawine muoneso 2025 mpaka 2063 woooo. Mukodza dzinamizanani Amalawi zopusa za dpp adasiya.
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Ай бұрын
😂😂
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 Ай бұрын
Amalawi ake unena ndani ife dpp isadzabwereso sitifuna ma alubino akukhala ndi ufulu
@FortunePhiri-kl7oe
@FortunePhiri-kl7oe Ай бұрын
Ulibeso nzeru kulankhula kwabwanj kumeneko
@ellardmaster1637
@ellardmaster1637 Ай бұрын
DPP 🔥🔥🔥
@RhodrickWassi
@RhodrickWassi Ай бұрын
Tsiku transport 😂😂😂
@AndryDTylos
@AndryDTylos Ай бұрын
Nde mwati ku LL anamupasa dzina ati ndi Siku transport 😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂
@janetmoses7266
@janetmoses7266 Ай бұрын
Sammy's amandifananira ndi sidik mia
@FrezaMadika
@FrezaMadika Ай бұрын
Mbava nokhanokha inu
@NadeemKhan-sh9js
@NadeemKhan-sh9js Ай бұрын
Akunyodza dpp ameneyo walandira ndalama
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo Ай бұрын
We are tired as Malawian Allah tioneni
@GiftMakowa-k9f
@GiftMakowa-k9f Ай бұрын
Pitilizani adadi ipatseni fire❤❤❤❤❤
@UmaliIshmael
@UmaliIshmael Ай бұрын
Pangolin
@kubengovender6996
@kubengovender6996 Ай бұрын
Yes my Boss man!! We definitely need you brother to take over!! You're the real thing, the poor people defender!!
@LovenessMagombo-t3c
@LovenessMagombo-t3c Ай бұрын
Kkkkk koma kuli ntchito
@MumbasnwaMumba-ih1xi
@MumbasnwaMumba-ih1xi Ай бұрын
When i see suleman i see bright future for Malawians
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj Ай бұрын
DPP again in 2025 mashall Allah bless everyone has being DPP
@RazackMofart
@RazackMofart Ай бұрын
Mlomwe wachizungu
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu Ай бұрын
Koma ndizoona, Mavuto achuluka ku Malawi, ili si boma ayi.
@WallyMsiska
@WallyMsiska Ай бұрын
Siku chikangawa transport kkk
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n Ай бұрын
Samia Suleiman ndinu katundu
@HaroonAlibarara
@HaroonAlibarara Ай бұрын
Koma chakwera waonjeza eeee
@AmosKapira
@AmosKapira Ай бұрын
Mnakanika kale inu Team Kabambe basi osati agogo
@FoniyalaMthamulo
@FoniyalaMthamulo Ай бұрын
Sangalandire pemphelo limeneli lazifukwa
@emonagusitafgusitafemona
@emonagusitafgusitafemona Ай бұрын
Akatundu omanga ndiwaya
@ElanjaLusiyasi
@ElanjaLusiyasi Ай бұрын
Zoon
@LovemoreKamoto
@LovemoreKamoto Ай бұрын
Azibusa mwaleka kupephela chulungamo mwakonda zandale pephero lopanda fundo
@EddenKamanga
@EddenKamanga Ай бұрын
Zaboza zimenezo mwankhuta
@courageouslondo1986
@courageouslondo1986 Ай бұрын
Ndiye ukumaweluza bwanji mesa iwe ukut tidzinvela ndiy ukut ngati mawa kulibe u means what?
@SymonTheu
@SymonTheu Ай бұрын
Ndipo live atigulitsadi
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g Ай бұрын
Chikangawa achoke 😂😂😂
@AckimKasiya-u7q
@AckimKasiya-u7q Ай бұрын
Munazolowela zaurere athu akumwela aresi
@FosterChinzimuBanda
@FosterChinzimuBanda Ай бұрын
Tsiku transport AKA, Chikangawawa.
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 Ай бұрын
koma blenac pitilizani zomwe muka Chita ZIJA izi aaaa ayi DPP tinali nalo chadzeru palibe apa
@EnockSankhylani
@EnockSankhylani Ай бұрын
Tisawamvere pomwe tikumva kuwawa iya
@LehmanManere
@LehmanManere Ай бұрын
Auze Suleiman chilungamo osaphonya zaku immigration ma passport,Road Traffic Driving Licenses
@DrianoYakobe
@DrianoYakobe Ай бұрын
Congratulations Hon suliman
@MercymithiMithi
@MercymithiMithi 25 күн бұрын
❤❤❤❤
@archangelchimaliro84
@archangelchimaliro84 Ай бұрын
kutsutsa kukuphani anyamata inu kkkk
@CharlesKachipanda-jz9jv
@CharlesKachipanda-jz9jv Ай бұрын
Mwawona makina athu not jefu wa jefu
@tracybennie7783
@tracybennie7783 Ай бұрын
Tikupita. APA basi
Каха и лужа  #непосредственнокаха
00:15
Wait for it 😂
00:19
ILYA BORZOV
Рет қаралды 11 МЛН
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 148 М.
Nyimbo iyiyi mwainvera koma?
6:48
Malawian Cameras
Рет қаралды 475 М.
Chifukwa Chimene Anthu Amamudera Miracle Chinga
11:55
Sam Malvitha
Рет қаралды 149 М.
Kucheza ndi wa Sataniki Mpakana Waziwulula Yekha
20:20
Morton Baghaya
Рет қаралды 198 М.
Chikangawa Commission of Enquiry yotsogozedwa ndi anyamata a Chakwera.
11:36
Каха и лужа  #непосредственнокаха
00:15