MALOZA!! UTM YAVOMELA KUYENDA NAYE MANGANYA LIMODZI ~ MPAKA UTM YATOKOTA IZI KU PRESS BRIEFING LERO

  Рет қаралды 28,350

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 101
@ShadreckThomson
@ShadreckThomson 17 сағат бұрын
You have done good.. that's one good move, way to go. Don't mess up nor give in to external pressure. Be focused and determined. Some talk to confuse others family unity and peace. Good luck to you all.
@StevenMilward
@StevenMilward 17 сағат бұрын
Aaaaa nonsense
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 2 сағат бұрын
Watching you from Pretoria South Africa,wishing you a great day during your preparation for your convention which is going to be on 17th November this month
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 18 сағат бұрын
Musamalenaye usi gyz pls pls ndi ng'ona imeneyo
@LeonardNdhlovu-x4t
@LeonardNdhlovu-x4t 18 сағат бұрын
Timakunyadilani asogoreli athu msalore kuti afisi azipani zina kuti awononge chipani chathu we still love you all God be with you all ❤❤❤❤❤
@PeterMaida-r8d
@PeterMaida-r8d 5 сағат бұрын
Uku nde kulankhulatu komwe timayembekeza Kufotokoza tsatane tsatane mot aliyese avesese Koma mwanjira ina Mayi Patricia kaliyati Mmmmm uyu ndikatundu ndipo ndaimika manja❤❤ Kulankhula mopanda nkhawa. Kulankhula mosajejema. Kulankhula kuposa Mphongo Ulemu wanu mama mumatimirira
@mansonchinkhuzi
@mansonchinkhuzi 20 сағат бұрын
Bola A Dr Usi atetezedwe
@mkhulukinyata5198
@mkhulukinyata5198 19 сағат бұрын
Mmm..Ayi ndithu CHULE wadabwa m'madzi muli mwake ,Ine ngati member wankulu wa UTM, Ndinene zowona ,,Akulu akulu a UTM Mwandikhumudwitsa pomva kuti mwagwirizanano ndi Yuda Eskarioti yemwe ndi Micheal Usi , Koma sindikudziwa mwina mukungokamba poti idzi ndindale , Koma naa ngati mukunenadi zowona kuti mwagwirizanano ndi Satana Usi" , Dziwani kuti ma Suppoter ambiri basi tikukusiyirani UTM Yanuyo muziyiyendesa ndi Biziwick wanuyo, Ife apa njira zathu ndi ziwiri basi,, DPP kapena ALFORD basi. Inu monga titenene kuti zoti Usi anali mugulu lodziwa kuti CHILIMA akuphedwa mu chaka chinochi monga inuyo simukudziwa ? .Pali ma umboni ambiri woti Usi ankadziwa bwino lomwe dza upandu womwe adawukonza a MCP kumukonzera CHILIMA ..Ndiye lero basi iwe chitsilu Patricia ndi Felix mungamabwere pa podium mopanda manyazi nkutiwuza Zopusa zanu zokhudza USI Wanuyo ..Ayi ndithu mwandinyasa ndipo ndakwiya nanu..
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 17 сағат бұрын
Iweyo Siwa UTM. Why hating Micheal Usi
@joelbanda1551
@joelbanda1551 16 сағат бұрын
True ​@@ancientnkhata1137
@joelbanda1551
@joelbanda1551 16 сағат бұрын
MUNTHU SADANA NDI KHOLO AMENEYO NDOTEMBELELEDWA
@StanleyDama
@StanleyDama 8 сағат бұрын
Manganya wawonetsa utsogoleli🇲🇼🇲🇼🇲🇼💪
@patkuipa284
@patkuipa284 Сағат бұрын
UTM is my party but with this Manganya......mmmmmm???!!!
@Chaula-km1eo
@Chaula-km1eo 17 сағат бұрын
Nice Teem ZBS
@mayachikadewa7551
@mayachikadewa7551 21 минут бұрын
Akudziwa chomwe akuchita,atambwali sametana😅
@GanizaniBishop
@GanizaniBishop 5 сағат бұрын
Ine ndili Ndi Funso Inu munachoka mugwilizano president wanu Ali mugwilizanomo ndiye apa Inu mwabwelelanso mugwilizano ?
@polesanamakwenda6932
@polesanamakwenda6932 6 сағат бұрын
Thats the spirit. VP is a good person. Ololelana❤
@GrivinBanda
@GrivinBanda 10 сағат бұрын
Nkhope zawo honestly zuoneka zokugwa like anthuwa achita zinthu mokakamizika
@BlessingsNyirenda-ru7ss
@BlessingsNyirenda-ru7ss 20 сағат бұрын
Kaliyati she is already a leader
@MeriaNdalama
@MeriaNdalama 6 сағат бұрын
Anthu andale musamatipusise ife mwava iyaaaaa😮
@StellaMichael-d9d
@StellaMichael-d9d 2 сағат бұрын
Usi woyeeee
@andreabanda7838
@andreabanda7838 Сағат бұрын
On the face of it dr Usi appears to be a good man. Koma kuseliko kuli ka mpeni. He is still masterminding the break up of utm. Mungobisa zoona. Just to pacify malawians.
@aligrayjeo1071
@aligrayjeo1071 18 сағат бұрын
Iyai sanavomere pali zosokonekera nzambiri and remember manganya is the party president nde sakufuna zosokoneza chisankho koma wait for convention
@StellaMichael-d9d
@StellaMichael-d9d 2 сағат бұрын
Usi anamusakha ndi achilima mulungu anawatuma kusakha usi
@IkibaluAfick
@IkibaluAfick 17 сағат бұрын
Awa sangawine oloko atagwilizana ndi a VP wo,Boma ndi DPP basi
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 16 сағат бұрын
Kod mumafuns adane onsetu ndi a UTM
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 20 сағат бұрын
Mrs god papa nsanje kwambiri
@StanfordMNthali
@StanfordMNthali 19 сағат бұрын
Akaliati siyani zibwana mai
@ArnoldUnjika
@ArnoldUnjika 16 сағат бұрын
Is Monday 10th or 11th?
@AiwaMedia-sh6vx
@AiwaMedia-sh6vx 18 сағат бұрын
Mwachita bwino kuchita resolve ma issues between Usi ndi party koma kungoti Manganyayo mudzimuyang'ana ndimaso a Nkhwenzule
@JohnFrank-cg1yh
@JohnFrank-cg1yh 17 сағат бұрын
Kkkkk
@CatherineKatsonga-f6z
@CatherineKatsonga-f6z 7 сағат бұрын
Ndiye iwe amzako akupephera iwe Uli byz pa 4n Malawi umankhala bwanji
@FRANCISKAMPIRA
@FRANCISKAMPIRA 7 сағат бұрын
Apap nde phaka achelekeze musinjilo bas
@jomochirwa
@jomochirwa 19 сағат бұрын
Akweni dziwani kuti atolakhani akumalawi ndiwoyambanitsa ndipo iwo amangofuna kuti anthu andalenu muziyambana ndiye mitima yawo imasangalala.nchifukwa chake dziko lathu umphawi ukutikakamila.
@BlessingsLigwese-m6i
@BlessingsLigwese-m6i 8 сағат бұрын
Ndale ndikanyama koipa tiwona kuti ubale umenewu utha bwanji
@kunjemangandale1118
@kunjemangandale1118 20 сағат бұрын
Ndiye ndalezo akudziwa kuti a gwa ku conversion musadandaule
@AgnesChirwa-n4u
@AgnesChirwa-n4u 17 сағат бұрын
Ndale izo
@JamiesonKaunda
@JamiesonKaunda 19 сағат бұрын
Za mpeni ku mphasa izi
@MosesDicostar
@MosesDicostar 17 сағат бұрын
Koma mene amayakhila kaliyati mu atakhala president kuipa ndthu
@adamashrafi5875
@adamashrafi5875 8 сағат бұрын
UTM could be better without Kaliyati
@Elizabethmanda-es7se
@Elizabethmanda-es7se 5 сағат бұрын
thats a liar
@StanfordMNthali
@StanfordMNthali 19 сағат бұрын
UTM chenjelani dpp amakupusisani Chilima amanyozedwa ndi pitala Inu aKaliati mumaimba nyimbo pitala wapeleka mimba kwa Jen Ansa
@MzadziWanga
@MzadziWanga 16 сағат бұрын
Bola ankangomuzuza sanamuphe akwao anali akumuona mkumamudalirabe Inu a MCP mesa munapha nde oyipisisa ndani poti Inu munamusowetsa
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 19 сағат бұрын
AWAWA ADAKALIBE KU MCP CHIFUKWA MANGANYA NDI WA MCP WHAT A SHAME SKC MAY YOUR SOUL REST IN PEACE
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 19 сағат бұрын
Pajati Born kalindo wakhala akunena,akufuna azitiputsitsa,let's go back Kwa adad.amai awawa amadabwitsa daily
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 18 сағат бұрын
Ndiye amatulukiranji mu mgwirizano? Kufuna kupusitsa anthu basi
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 17 сағат бұрын
@VictoriaWilliam-ms2ft ndipo atitolatu agalu amenewawa
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 16 сағат бұрын
Umbulidi sizithu
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr 20 сағат бұрын
Aaaa zopusa ine manganya aaaaaaa anandidesa kukhosi
@CarolineChingwanda
@CarolineChingwanda 18 сағат бұрын
Busy pa phone anthu akupemphera?
@CharlesBanda-kv8bh
@CharlesBanda-kv8bh 20 сағат бұрын
Anthu oyipa mnzawo akupemphera china busy pa foni what ashame
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 17 сағат бұрын
Kaliat wangovomelela choncho kut ayende ndi manganya koma sakusangalala nazo angowopa malalamulo
@EvansEgra
@EvansEgra 20 сағат бұрын
Kupusa uko, chizungucho ukuwerengera ndani? Nonse a Malawi pamenepo, zibwana basi.
@SiphamandlaNcaphayi
@SiphamandlaNcaphayi 4 сағат бұрын
Anakuuza ndani Kuti usapite kusukulu ambuzi inu
@EvansEgra
@EvansEgra 4 сағат бұрын
@SiphamandlaNcaphayi Sukudziwa nchomwe ukulankhula, nkhala chete zikuthandiza
@KelvinMandelaChirwa
@KelvinMandelaChirwa 19 сағат бұрын
Kodi mzimayi wakhala pafupi ndi Hon Njawala Dzina lake ndindani?
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 19 сағат бұрын
Ndi WA MCP uja
@oskidooscar7468
@oskidooscar7468 5 сағат бұрын
Mwadya chi banz sife Ana Manganya munadana nawo kale kale mukungofuna za convention akuthandizen... Mwaluza a utm . Muli kut kut kod
@ignatiuslowe6852
@ignatiuslowe6852 19 сағат бұрын
Anthu amaganizo oyipa awa, akungophimba mmaso anthu koma aaaaaa zabodza izi
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 17 сағат бұрын
Nde pemhelo lilinkati koma enawo sizikuwakhuza
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 17 сағат бұрын
Koma njawala ndimulumikizisi ndipo Muli usgoleli
@ehinsupport3217
@ehinsupport3217 20 сағат бұрын
Tili mu nthawi ya god papa
@peterbyson6269
@peterbyson6269 17 сағат бұрын
Atola nkhani akumakhala anthu oyambanitsa guys apitenso ku school anthu amenewa
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 16 сағат бұрын
Ndipo zoonadi mwava mmmm
@peterbyson6269
@peterbyson6269 7 сағат бұрын
@@ElizabethMulinde amafunsa mafunso osathandiza nkomwe amalawi koma kubweletsa nkangano adziti auje ati inu mwakuti inu mukuti bwanji zanzii
@shaleefabada8267
@shaleefabada8267 7 сағат бұрын
Ndikuuzan ndionere kae
@MosesDicostar
@MosesDicostar 18 сағат бұрын
Koma nawo atolakhani mafunso awo
@andreabanda7838
@andreabanda7838 59 минут бұрын
What the account number ya UTM. I WOULD LOVE TO DONATE Something.
@IssahMussah-d4t
@IssahMussah-d4t 7 сағат бұрын
Zabwino zonse
@IseckNkhoma
@IseckNkhoma 19 сағат бұрын
Zovuta kwabas
@HacksonRuReKabwitama-s6v
@HacksonRuReKabwitama-s6v 20 сағат бұрын
Kuli kanthu uku
@josephleman8756
@josephleman8756 17 сағат бұрын
Mukanakhala kut munalibe ming'alu bwezi madam S G mutawawuza azanu kut asamavale makaka a chipani ku function ya boma a mayi musamatinamize ife
@HenryKamanga-q7w
@HenryKamanga-q7w 10 сағат бұрын
Winawe umat Usi wako alepheresa zakuvuta apa
@GomezganiMkandawiretikatik-l1f
@GomezganiMkandawiretikatik-l1f 20 сағат бұрын
U can't get back in government again they main key 🗝️ it's gone u shift all quiet 🤐 🤫 kaliyati makutu apaphasa kkkkkkk achewa inuyo u can't Evan farm anthu akudya chiteze 🎉bayamba mwamvapo mzuzu agona ndinjara we always well ❤️‍🩹 kept
@eliasemmamoyo8225
@eliasemmamoyo8225 19 сағат бұрын
Iwe nawe osachuluka zelu nge wanthu wose kumpoto mbochita makola cha
@GomezganiMkandawiretikatik-l1f
@GomezganiMkandawiretikatik-l1f 9 сағат бұрын
@eliasemmamoyo8225 ukhalira izo azikutuma zoousa
@tiyesemawindo-c5x
@tiyesemawindo-c5x 18 сағат бұрын
kod usi mukufuna aonenge chipani
@GoefryNyilongo
@GoefryNyilongo 18 сағат бұрын
Chuma chamasiye chavuta uku
@RichardAlick-o8k
@RichardAlick-o8k 19 сағат бұрын
Why guys kuyenda ndi munthu wa mcp? Mukuzuzatu mzimu wa Malemu inu ukukanthani Banja langa lonse linali la UTM koma apapa basi waku Dpp basi muzipangako zopusazo bwino.😢😢😢😢😢😢😢😢
@LucyKamala
@LucyKamala 17 сағат бұрын
Iyiyi nde goof movie amwene ,kuopa pa mawa ku ma court, Apapa akuyendera malamulo a mchipani, Usi akukamalozidwa pa 17 basi, Zidzakhala zathapo😂
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 6 сағат бұрын
Iwe Khala ku dpp uko
@peterbyson6269
@peterbyson6269 17 сағат бұрын
Zilibwino pamenepa guys umenewu nde utsogoleliwo❤❤❤
@tiyesemawindo-c5x
@tiyesemawindo-c5x 18 сағат бұрын
ifetu ovota sitikumufuna
@GomezganiMkandawiretikatik-l1f
@GomezganiMkandawiretikatik-l1f 20 сағат бұрын
Why u gays 😢 u can just have peace ✌️ mini wachipani wapume bwino wewewe 😮😅 leave these shift mkulephera ndikuwelenga kkkkkkk more over ndinu nokhanokha achewa kkkkkk
@ChimwemweLimbe
@ChimwemweLimbe 19 сағат бұрын
😂😂😂
@josephleman8756
@josephleman8756 17 сағат бұрын
Amati atani mwini thiko wawoneka nsopano
@LinlyMatheweKufakwina
@LinlyMatheweKufakwina 10 сағат бұрын
Aaa nde mwini nthiko wataninkufika apapa?komanso Usi zoti apereka 20 mita hmm kuumira uja😂😂😂
@HenryKamanga-q7w
@HenryKamanga-q7w 10 сағат бұрын
Chilibe mwini
@AdamMakala
@AdamMakala 19 сағат бұрын
Kkkkkkk
@LemsonManyowa
@LemsonManyowa 19 сағат бұрын
Anthu awa asatipusise adya kale ndalama awa
@AdamMakala
@AdamMakala 19 сағат бұрын
Akweni
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 18 сағат бұрын
Usiyo gyz awonongazinthu ndikazitape ameneyo anamupeleka skc
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 16 сағат бұрын
Inu musadandaule ndi usi tikukamutsitsa pa 17 pano trust me
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 16 сағат бұрын
@ElizabethMulinde kamunthu koyipitsitsa kamenekaja ndinadanzko kukhosi
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 16 сағат бұрын
@@NovemberMmangathayo kwambili mwava mmmm
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 16 сағат бұрын
@ElizabethMulinde zamveka eeeee ineyo utm ndimayikonda kwambili ngakhale ndimamudandawula chilima
@MalawiMalawi1580
@MalawiMalawi1580 19 сағат бұрын
Ine membala wa utm ndagwilizana nazo pofuna kugonjensa dani khalangati wayiwala chipogwe kenaka suvutikana naye kugwetsa awa ausi ndiulendo pa 17 novembala
@JosephElliam
@JosephElliam 17 сағат бұрын
Edale zonyozana nzachikale
@macleanwazalanyirenda4994
@macleanwazalanyirenda4994 16 сағат бұрын
Usi is smart sakaima nawo ukuuu
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 16 сағат бұрын
Mau oveka bwino ndithu pa 17 usi kwake kwatha
@andreabanda7838
@andreabanda7838 Сағат бұрын
On the face of it dr Usi appears to be a good man. Koma kuseliko kuli ka mpeni. He is still masterminding the break up of utm. Mungobisa zoona. Just to pacify malawians.
SADC Heads of State to meet over Mozambique elections
5:37
SABC News
Рет қаралды 7 М.
UFC 308 : Уиттакер VS Чимаев
01:54
Setanta Sports UFC
Рет қаралды 933 М.
🕊️Valera🕊️
00:34
DO$HIK
Рет қаралды 20 МЛН
'They call us terrorists': Inside the Palestinian resistance forces of Jenin, West Bank
13:29
Starmer and Badenoch CLASH on Trump, farmers and defence
9:58
The Independent
Рет қаралды 36 М.
We Want To Patronise Dangote But Nigerians Must Not Suffer - PETROAN
28:26
Channels Television
Рет қаралды 10 М.
US Elections | In conversation with Prof David Monyae
14:42
SABC News
Рет қаралды 1,7 М.