AMALAWI LIMBANI MTIMA BASI ~ LEROTU CHAKWERA WAKANIKA KUYANKHA ZOTHESA NJALA KU MALAWI ~ EISH KOMA

  Рет қаралды 45,520

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 76
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 3 күн бұрын
Inu Amalawi chikangawa simtsogoleri wa Malawi ayi Muzimucha msokonezi wa dziko lino, kapena muwonongi wa dziko lino that's fit Mr chikangawa mfiti yaikulu mmalawi muno.
@KondwaniLimitoni
@KondwaniLimitoni 4 күн бұрын
Ife tili cheteeee ku dikila adad❤❤
@MosesYokaniah
@MosesYokaniah 5 күн бұрын
Bambo pakhomo sanganene ku banja lake kuti ndikupanga chitukuko pamene Ana akugona ndi njala
@CorneliusSande
@CorneliusSande 2 күн бұрын
@@MosesYokaniah zoona ndalama yopezayo amayenera kugula chakudya koma akuluwa akakhuta Iwo awona ngati those takhutanawo
@MemorieMwasinga
@MemorieMwasinga 5 күн бұрын
Sanati adziwaso
@WillyNyirenda-l7h
@WillyNyirenda-l7h 5 күн бұрын
2021 asanalipidwe ndalama Zao, akudya chaini Naga school fees?
@IqrahSikweya-wm5mn
@IqrahSikweya-wm5mn 5 күн бұрын
Ulamuliro oipa mdziko ukamachitika, izi ndizilango zomwe Mulungu amabweretsa mmaiko
@VincentKachingwe-c6w
@VincentKachingwe-c6w 4 күн бұрын
Jolobala woyeee
@GeorgeR.Mafambisa
@GeorgeR.Mafambisa 4 күн бұрын
Why should the fee for participation for women in politics be reduced yet the so called gender activitist fight for equality.... In my understanding, equality should mean equal participation and equal fee in as far as this is concerned😮
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u 4 күн бұрын
Pali njala ina yopangitsa munthu ngati iyi yaku Malawi Chifukwa chonsowa fertilizer Ndikatangale,Chiwelewele,Kuphedwa kwa anthu kuba kwa asogoleri kumayambitsa njala Kodi simunawelenge Baibo
@StewartGoma
@StewartGoma 5 күн бұрын
Atule pansi chakwela
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 5 күн бұрын
Prioritize .Government of National Solidarity to be constituted as we are regionalistically divided.
@YusufChikweo
@YusufChikweo 4 күн бұрын
Xul kwambiri inuyo😂😂😂😂😂
@AdamAhamad-k2i
@AdamAhamad-k2i 4 күн бұрын
Kumtumbo kwachakwera President opanda nzeru
@RaymondKaumba
@RaymondKaumba 4 күн бұрын
Distribution of maize which the government is doing is the answer
@Ericmalimelo
@Ericmalimelo 3 күн бұрын
panjatu kuyambira kare mafuso amamuvuta kuyakha kkkkk
@MeruMitha
@MeruMitha 4 күн бұрын
za pension nde ndizovutadi munthu ukhoza kufa nthawi isanakwane. ku Malawi za pension sizili bwino zimangokoma uli ndi mphamvu nkugwira ntchito ukapuma ngati walakwa inenso ndikuvutika koma sinali mmboma nde ayi zovutadi.
@AlexKaunda-w7l
@AlexKaunda-w7l 2 күн бұрын
Nyele yake chakwera
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl 4 күн бұрын
Iyi ndi nkhumbatu si msogoleli
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 3 күн бұрын
Tamuoneni bushiri maso awo akuchita kuonekeratu kuti nisataniki yayikuru bushiri ni chakwera angogwesa vula kupha anthu kufuna magazi basi
@Efellofredson
@Efellofredson Күн бұрын
Chimwendo ndamene amanamiza chakwela kuti bwsna anthu akukukondani mpomwe anthu sskumufuna
@johnkambala692
@johnkambala692 5 күн бұрын
Enanu mitu sikuyenda mu Parliament, moti President angakanike kuyankha za njala.
@BakhePaliso-h8h
@BakhePaliso-h8h 4 күн бұрын
Mulungu atisalalila atisungabe ndi moyo sitifa ndi njala mu Zina layesu
@GraceBanda-t4r
@GraceBanda-t4r 2 күн бұрын
Abale aMalawi ano ndi matsiku osiliza ngati muwelenga baibulo Mateyu 24 kuzakhala njala , nkhondo , matenda azazinthesa ndi ma president kodi ? why titaya mau a Mulungu alipafupi kuza mwini wake ziko azanthesa ZONSE AMEN ZAMBIA
@GuejendraMk
@GuejendraMk 4 күн бұрын
Apa achimwendo Banda ndie kut amawauza za bodza kut a president, anthu akukhuta. Apa angonama za nthawi . kulibe njala
@abgi.doctor.august
@abgi.doctor.august 5 күн бұрын
Ndiye anapita ku parliament kukataniko akudziwa kuti alibe choyakha Kwa a Malawi? Analekeranji kungokhala ? Zamanyazi Ndipo sizinachitikepo
@billylazaro6529
@billylazaro6529 5 күн бұрын
Chumacho chikugwira ntchito yanji?
@CharityChirwa-v8v
@CharityChirwa-v8v 5 күн бұрын
Kozekani Malawi kuluza myoyo yambili kusokhano waameneyu magazi sanakwane akufuna ena only God amenya khondo
@PhilipJulius-fm6mx
@PhilipJulius-fm6mx 4 күн бұрын
Stop judging what u don't know focus on ur own salvation leave judgement for God plz mmene munayambira kumunena kuti akupha anthu Church ikupitilirabe simukuchitako manyazi yet Sunday likakwana umanyamula baibulo lako mkupita ku church iwe wekha basi ndiamene umapemphela za amzanu ndiye zoyipa basi be smart n learn to leave other things for God abale mmmm God have mercy ndithu
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 4 күн бұрын
Tidikire wabakili muluzi
@PatrickLongwe-yc9il
@PatrickLongwe-yc9il 4 күн бұрын
Inu amwene mkutukwana muzitamba mwatukwana Kaye abambo anu musanatukwane president
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 3 күн бұрын
Inunso musabereke munthu uyu.
@CorneliusSande
@CorneliusSande 2 күн бұрын
Njala sikutha imangochepa osatikutha ndani adathetsako njala mudziko muno .Ngakhale iyeyu chaponda mesa adakanika kuphetsa ndalama zogulira chimanga atanyopola .
@user-ii9ch7oz8n
@user-ii9ch7oz8n 2 күн бұрын
Chapondaso ndiye anabaso chimanga mbava kkkkkkk😅
@Mustapher-fb4qp
@Mustapher-fb4qp 4 күн бұрын
Chakwera ndi kalulu
@Hambalisphiri
@Hambalisphiri 3 күн бұрын
Kkkkkk banja lolanda ndi chonchotu kkkk ukalowa umayiwala kt umanyoza mamuna mwini wa nkadzi
@PriscaMussah
@PriscaMussah 4 күн бұрын
Ngat alibe mayankho asamapiteko
@OdettaLowrence
@OdettaLowrence 5 күн бұрын
Atule pansi udindo
@KingsleyLawrence-b8o
@KingsleyLawrence-b8o 5 күн бұрын
Atsogoleri amene akulamulira maiko alibe mphamvu yothetsa njala mmaiko yawo . Mulungu ndiamene adzathetse njala imeneyi.or atalowa amene tikumuganizirayo sikuti njalayo idzatha ai. Chofunika kuchita ndichakuti tikhalenacho chkumbu mtima kut yesu mwini adanena kut mukadzamva za njala, nkhondo dziwani kt mwana wamunthu alipafupi kubwera, tisamaiware zimene yesu adalankhula.
@charlesmuwanya7845
@charlesmuwanya7845 4 күн бұрын
Njala imene amanena mbuye wathu Yesu Kristi idzakhala ya dziko lose lapasi osati Ku Malawi kokha ayi. Please read the Bible between the lines.
@YusufChikweo
@YusufChikweo 4 күн бұрын
Inuns nda zoba yesuyo abwera ku Malawi konkuno basi?Nanga maiko Ena? Takawelengenins Bible then mubwerenso
@georgezikabuma9396
@georgezikabuma9396 5 күн бұрын
Bible limati mmasiku otsiriza kudzakhala njala wina wake akuti akhoza kuthetsa njala palinzeru? Nthawi ino si yothetsa njala ayi ndi yokhala maso ndi mawulosi a mmasiku otsiriza. Ndikupusa kwambiri anthu ophunzira kumaganiza kuti wina angathetse njala. Anthu andalenu kupusa kumeneku bwanji?
@symoldicky
@symoldicky 4 күн бұрын
inuyo bible lake liti mukufanizilalo? kod bible lidat njala yake idzakha yopanga dalayi izozo nde zopepelazo kumapanga zopusa kut muzibisalila kut bible? njala iyi its man made hunger sizopusisanazo
@FelicitasKanthiti
@FelicitasKanthiti 4 күн бұрын
Kodi zoti dziko likutha zinayamba liti? Munabadwa munazipeza ndipo mudzaziyiya!
@FelicitasKanthiti
@FelicitasKanthiti 4 күн бұрын
Exactly!
@andrewmbilinte4589
@andrewmbilinte4589 5 күн бұрын
Koma abale nthawi ya masiku ano,tiyeni tikhale chitsanzo patokha.Kumabanja kwathu tikuchokera ngati kulibe njala; ndekuti tikhonza kuyithesa.Tikukanika kudyesa makolo athu njara itha bwanji.Maso ali pa boma mwanokha mukukanika,
@EllenKapinga-rm9zm
@EllenKapinga-rm9zm 4 күн бұрын
kodi a Chakwera ndi Mulungu? aaa wabweretsa njala ndi Chakwera?
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 4 күн бұрын
Koma inu musatilakwitsepo apa mwamva eti
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 3 күн бұрын
Kkkkkk mudziwerenga bible muone kuti atsogoleri omwe amachita zofuna zawo amakumana ndi zotani?
@CassimJafali-g4l
@CassimJafali-g4l 5 күн бұрын
Athawa sanayambe kuthawa akungoyelekeza
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 5 күн бұрын
Aaah bushiri chuma mukudya nokha ndi azanu a mcp kobili zanuzo sitikudzifuna dzikoli ndi zako cikangawa mwaliphasula. Iwe ndi zako mcp tisiyeni mulungu aona mocitila mwake. Iweo bushiri ukumpusisa ndani? Mavuto ali dziko munowa iwe ndi zako cikangawa mwacita kuwapanga mukuona ngati sitikudziwa aaah za ziii this is nonses
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 4 күн бұрын
Awa ndi a president oti mulungu sanawalole onani kumwamba zuwa no 1 njala yosatha chiloweleni 2020 Pana pano nde Kumari 2025 boma ndilomweli cholinga athu angofamo
@EllenKapinga-rm9zm
@EllenKapinga-rm9zm 4 күн бұрын
mmalo moti muzipemphera kwa Mulungu kuti sgwetse mvula muli busy kunyoza Chakwera,
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 4 күн бұрын
Agent ofuna kut anthu azitukwana cz ov mfundo zako zopanda nzeru zo. Kodi mukuona ngt anthu sakupephela???
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi 5 күн бұрын
tava simungatinaze inu ganyuyo apwetekesani
@dumsanmgabhi2015
@dumsanmgabhi2015 5 күн бұрын
Alepela.angochoka.palibe.apanga.ife.tikulila.ndinjala😂😂😂😂😂
@MonicaThocco
@MonicaThocco 5 күн бұрын
Chakwera angolimbana ndi nkhani ya dzitukuko basi ,ku njaraku palibe chomwe akupanga cholinga chake ndi chokupha anthu basi ,muthu akayenda munsewu wokongola ali ndi njala zipindula chiyani? Ku njalaku ayi ndithu kuthawa thawa kokha kokha, kuyambira pa chiyambi chomwe anakhala president, muwone ngati anatseka ma Admac mukuganiza ndi masewera 😢 mkulu ameneyi akudziwa zomwe akuchita pa nkhani ya njala ,pakati apa panali nkhani yoti amagulitsa chimanga ku Mozambique, pomwe ifeyo njala tiri nayo siyingalingane ndi ku Mozambique, kumapha anthu ake, kumakadyetsa anthu adziko lina pali nzeru?
@MosesYokaniah
@MosesYokaniah 5 күн бұрын
Ukakhala moyo wosadwaladwa umaona ngati kunjaku matenda kulibe enanu chifukwa choti mukudya ndi kukhuta mmawanja anu mukuonangati kunjaku vuto la njala kulibe ndichifukwa mukumalankhula motumbwa kuti mwatumidwa ndi ena amene mukudandaula za njala
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 4 күн бұрын
NDIPO WAYANKHULA ZOONA ENAO CHIFUKWA CHOTI AKUKHUTA NKUMAPITA KU TOILETI NDI CHIFUKWA CHOTI AKUKAMBA ZOPUSA , ZOTI ANTHU AKUDYA CHITEDZE IWO SAKUMVAYI
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 4 күн бұрын
NANUNSO A BUSHIRI NDIYE NDALAMAZO ZIMAPINDULIRA A MALAWI NGATI MESA ZIMAPINDULIRA KUMENE AMAKALIPIRAKO NDIYE ZIKUGWIRIZANA BWANJI,
@KingsleyLawrence-b8o
@KingsleyLawrence-b8o 5 күн бұрын
Musaiware anthu a Mulungu kuti yesu adalankhula zokhudza njala, kuti mukadza Va zanjala,nkhondo dziwani kt mwana wamunthu alipafupi kubwera . Ndiye palibe angathetse njala mdziko lapasili, angathetse zinthu zimenezi ndi Mulungu yekha. Kom munthu
@symoldicky
@symoldicky 5 күн бұрын
Aaaa akulu . inuyo yesuyo nde anat njala yake idzidzakhala yopanga dalayi? Osamabakila zolakwika pozembera ku bible. Kod nde kut masiku otsilizawo akubwerela amalawi tokhafe? Cuz mavuto ali dziko muno ambili nchifukwa kulekelera komaso dyera pachuma nkudzikonda nde musiye mulungu akhale mulungu
@MarryMartin-z6u
@MarryMartin-z6u 5 күн бұрын
Tsoka obweretsa njala
@YusufChikweo
@YusufChikweo 4 күн бұрын
Ndy yesuyo abwera liti kumalawi kuno kuzaweluza? Cz njalayitu yabuka mmalawi mommuno ku china kulibe ndy kuti qkazaweluza kuno azadikiranso ku china izayambenso njala azapitanso kkkk Kuganiza mofoira ANATI "MUKAZAMVA ZA NJALA KOMANSO NKHONDO" IZIZ ZIZAKHUZA ZIKO LONSE LA PANSI NOT KU MW KOKHAKUNO AI NDIKHULUPILIRA MWANDIVA MBWIYACHE
@FelixKChisale
@FelixKChisale 5 күн бұрын
Mukamati njala yabwela ndi chakwera kapena vuto ndi namonde daily ayi chakwera wakanika kuyankha mafuso akakuyankhani mukuti sanayankhebwino mukungosonyezelatu kut mukutumidwa et
@symoldicky
@symoldicky 5 күн бұрын
Akulu inu pamutu panu sipayenda bwino , kod tili ndi ma president angat nziko muno? Nde ngat zinthu zikudza kamba ka kulephela kwa mtsogoleri muti anthu azdiloza ndani? Zipangizo za ulimi kubwera mochedwa alipamwamba pa zose ndindan? Kukalipila ndalama za feteleza kawili konse kumalo olakwika butchale ndi famase alipamwamba ndi ndani ? Nde muka sakukhudzidwa ndinjalayi mutanthawuza chan pot iyeyo olamula gamu yose cuz namondwe sabagwere malawi yose zomwe zusonyeza kut madera omwe sakhuzidwe amayenera kukhala nchakudya chomwe chidakhatha kuthandiza madera okhuzidwawo monga mmene zimakhalira mbuyomu kut zikavuta kwina anthu amadalira kwinaku. Koma pano bzosatheka cuz production njochepa kamba lakusowa kwazipangizo za ulimi komaso kudula kwambiri
@MosesYokaniah
@MosesYokaniah 5 күн бұрын
Koma enanu mulindi umuthu? udindo wa mtsogoleli ndi kuthandiza ovutika mdziko. mukamanena nchoncho enanu mukutathauza kuti vuto lanjala kulibe mdziko muno?
@PatricaTchuwa
@PatricaTchuwa 4 күн бұрын
Awaso inu 😂😂😂😂
@YusufChikweo
@YusufChikweo 4 күн бұрын
Ndy iweyo kape utiuze lero , 1 amene akuenera kupeleka zipangizo za ulimi zotsika ntengo ndi ndani mziko muno? 2 kukwera kwa katundu amene ali ndi mphamvu yolamula kuti zitsike kapena zikwele ndi ndani? Ngati ali agogo ako angapange izi ndy tiuze tiziwayankhula iwowo kuti timusiye chakwera wakoyu.😂
@EletinaMzuwala
@EletinaMzuwala 4 күн бұрын
Palibe zot agogo amunthu apa. Inuyo mudapeza kt adalepheretsa vula kugwa ndi chakwera? Olo panopa mphepo yaonongaso manyumba aanthu omwe akuganizilidwa zanjalawo, apaso muziti chakwera cifukwa chot ndipresident? Musaiwale ufumuwu umene mukuusapoterawo umkacitika muzaka zam'buyomu zinoso ndizaka Zina. Kunyoza sikunhathe kusintha zinthu , camzeru nfimaona ine ndikupereka maganizo Anu abwinowo KUT akawerenga anthu oyenererawo azionjezera pazeru zawo. Osati kuukwana,kugemula, Kunyoza, kuweruza zimenezo mzosapindula. Zilingati munthu woti wakangana ndimunthu mzako Malo mokambilana ukukaswera kukaledzera. Mzoona achakwera alipamwamba paonse koma amagwira ntchito ndianthu ambali zose ziwiri olamula ndiotsutsa. Ena alindimaganozo abwino paudindo umene adapatsidwa ndipresident ena ayi. Tisaiwale ndizamalemba zinazi
@UniceSauli
@UniceSauli 5 күн бұрын
Osusa sogoleri want ndi munthalika kamuzeni athese niala zopusa kumalawi njala imatha
@samuelbrian3409
@samuelbrian3409 4 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@MedsonMark-m4k
@MedsonMark-m4k 5 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@DalitsoGoliath-m2y
@DalitsoGoliath-m2y 2 күн бұрын
Chikangawa azipita zamukanika
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 5 күн бұрын
Dziko lamukulira cikangawa abwelele ku kasiya akapitilize ubusa wa nyau this is bushit
Enceinte et en Bazard: Les Chroniques du Nettoyage ! 🚽✨
00:21
Two More French
Рет қаралды 42 МЛН
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:32
Family Games Media
Рет қаралды 55 МЛН
人是不能做到吗?#火影忍者 #家人  #佐助
00:20
火影忍者一家
Рет қаралды 20 МЛН
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 134
28:56
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 7 М.
Enceinte et en Bazard: Les Chroniques du Nettoyage ! 🚽✨
00:21
Two More French
Рет қаралды 42 МЛН