AND LIMPOPO FM WITH COMRAD NTANYIWA HAS DISCLOSED THAT @ BLACK BOX A CHAKWERA NDI NDUNA ZAO AKALISUNGAKU KASÙNGU .KU NYUMBA YA KAMUZU .YA NGULI YA NAWAMBE*** PAMODZI NDI MAVOTE OMWE A MCP ABERA KALE AJA NDI MEC NDI NRB
@StarchJonas7 сағат бұрын
Kafukufuku wa ndege popanda black box palibe chimene chingadziwike. Uku ndi kupusisana chabe. The whole inquiry report tikumva kuti palibe olo point imodzi yokhuza black box why?
@AdamJames-x7x6 сағат бұрын
Manyi a report awa , tizapanga inquiry MCP ikazachoka m'boma Chaka cha mawa, onse okhudzidwa azamangidwa including amene anapanga kafukufuku ameneyu.
@NearBanda5 сағат бұрын
Mmmmmmmm chilungamo akuchiziwa ndi mulungu
@LeonardChawinga5 сағат бұрын
😊😊😊😊😊😊😊😊😊
@bridgetmajor36464 сағат бұрын
😮😮😮
@MauriceMukona3 сағат бұрын
Ai akuchidziwa ndi ndi Mr chikangawa Dr lazi
@GuejendraMk6 сағат бұрын
Ndikukhulupira kut Mr President wakhutisidwa ndiripotiyi. Koma ndinakakhala ine ndikanafuna mudziwa 1. Anapopa magazi mkodzo ndi màlovui awanthuwa ndani and why 2.kodi ànaendesa ndege kukasia thupi 17:10 ku nkhatabay y a kasambala ndi ndan
@waniamwale6 сағат бұрын
Nanu tangopelekani black box bsi
@mussakapalamula1990Сағат бұрын
Nonse amene mukupelekera umboni wa report la bodzali mudziwe kuti muli gulu la anthu omwe anapha Chilima ndi anthu 8 ku Chikangawa ndipo Mulungu achita nanu kanthu. Nthawi yanu izakwana popeza iye Mulungu sachedwa komanso safulumira la 40 lizakwana.
Kutseka pakamwa Kwa Amalawi sikuti ndi anthu osaganiza ayi koma kuganiza mozama monga anthu oganiza bwino
@TamikaKaponya2 сағат бұрын
Nde akumabanjawo alandira nyasizo?ngati ndicomco tu n ndekuti akuvomerezano nazo za report yo cos sanayenereka kutero
@mabvutomichaelpanagona19496 сағат бұрын
Kodi papita dzaka dzingati nkhalangoyi ilipo ndege sizimadutsa dela limeneli? koma Black box anachotsa ndindani pakuti munalibe ndipo mpaka pano Black box mulibe mu ndegemo
@AlfredJuliusTemboh6 сағат бұрын
Komatu kunena zoona zikuti Wawa kwambiri
@HamuzahBamusi4 сағат бұрын
Izi nde zapatumbo izi nde munena bwanji zimenezo pomwe black box palibe muzanya mukachopa boma
@RoseMkandawire-e2g4 сағат бұрын
Ok nyanja mwagurisa ku songeya ija mdarama zake nizimene mukupangira zopusazo
@LashidBenardi3 сағат бұрын
Km mene inarili ngodzi ija mayakho ake akukhara amenewa mulungu Ali nafe😢😢
@shadreckMphambo-mt9pu3 сағат бұрын
et et
@AlihIbrahim-s7v5 сағат бұрын
Koma guys ku Malawi ndiye basi sikuzathekasoyi ndithu palibe obwela poyela mkulifusa or Boma ngati akhuthila ndi report lomwe lapangidwa popanda Black Box,,,kodi zoti oyendetsa ndegeyo analephela kuyendatsa bwino anadziwa bwanji popanda Black Box,,,,koma ndithu basi zatha izi eeee komaso malawi
@RuthChilobwe5 сағат бұрын
MIKODZO YONSE NKUSOWA .NOT NKUSWA
@alexsumani68235 сағат бұрын
kutitenga a Malawife ngati zitsilu
@MjombaMoosa4 сағат бұрын
Kodi kunkuyo uyu adapatsa mpando umenewo ndi ophutsira kapena ndi pa chibale pawo zomwe amayankha sindipakhutilisidwa naso
@AndersonChimwala-hz4so5 сағат бұрын
Muzayanga inu imfatu ndichitu chowaea
@jamessheki42934 сағат бұрын
😢
@shadreckMphambo-mt9pu3 сағат бұрын
inu report limeneli mwati anthu ena akulimvetsa bwino bwino mwati eeeeee koma Mulungu ayi zikomo kwambili ndiumbuli wangawu koma ambuye abwele azatenge dzikoli basi
@masianobrighton4 сағат бұрын
Abale maganizo anthu siomwe ali mulipotilo ifeyo tisunge maganizo anthuwa bcoz mwai oti tipite tikapereke maganizo anthu unalipo palibe anaipitako kukanena zomwe ifeyo timafuna kuti zikhale mu repotilo kuti likhale loona sibwino amalawi tiphunzire kugwiritsa ntchito mwai omwe tapasaidwa ndipo amachita kunenesa kuti amene akuziwapo zangoziyo apite akafotokoze koma inuyo ndi ine sitinapiteko it will be of no use kumalubwanso apapa imfa ija inatililisa ambiri bcoz its first of this kind mu democracy ndiye otsutsa olamula aliyense zinamukhuza ndithu
@TrizaGeorge-q8w2 сағат бұрын
Mumafuna muthu akapita kukanena chilungamo akamuphe uweso kapena eti ndati nose mumaikila kumbuyo boma lakuphali muli ndi tsoka lalikulu kwambili ndipo simuzapeza m, tendele
@johnjoachim38206 сағат бұрын
Achita bwino report lopanda zeru ngat limeneli
@PhlipsPhi5 сағат бұрын
Mulungu akuziwa Ife siana
@MakufaTrading4 сағат бұрын
Where is black box
@andrewmtendere31672 сағат бұрын
Apapa mai chilimayo nde ayakhulapo?
@ThomasShuga-z5p40 минут бұрын
Ndopenga awa😡😡
@Eliezer-vg1nx3 сағат бұрын
Ine ndikuonangat, nose amene mukutsutsa report mungolemba lanu, on top of that ankafuna anthu mukapeleke umboni, koma simudapite nde apapa muziti chan, lilani bac mukatopa mutiuza😏
@MaulidiAtibu3 сағат бұрын
Akupasa zingati coz ukuwoneka kuti nawe akugawila
@Eliezer-vg1nx3 сағат бұрын
@MaulidiAtibu do I look like a needy, who am I need of money, 😏
@MaulidiAtibu3 сағат бұрын
@@Eliezer-vg1nx walandila.zingati tangoyankha mayankhulidwe akowo akuwoneka.kuti walandila no black box where you can get report?
@Eliezer-vg1nxСағат бұрын
@MaulidiAtibu inuo are you sure kut mu ndege munalibe black box 😂
@MaulidiAtibuСағат бұрын
@Eliezer-vg1nx Mesa mwayibisa inuyo ndi anzanuwo
@JanetNyamayalo-f4r4 сағат бұрын
Koma ndalamazo sizikukuyanjani a Moses
@GiftMuyungu2 сағат бұрын
Ndiwodwala😅😅😅😅
@mercymalenga18845 сағат бұрын
Iyi sinali ngozi abale anga
@bridgetmajor36464 сағат бұрын
Live
@SliviaJosephyСағат бұрын
Anachita kukodza izi
@jeremiahmwawembe6 сағат бұрын
Kafuku fuku umayamba ngat mwanvela zomwe zili mu black box thus all
@LawrenceNdalaСағат бұрын
Let Njawala commission his party's Commission of Inquiry for the plane tragedy. He seemingly has some special interest apart from what we as Malawians have been informed on the catastrophe.