KALEMBELA ANAYAMBA BWINO UYU ZIMENEZI NDE ZITI? MPAKANA MWANAMVEKA WAKWIYA NAZO KWAMBIRI LERO PA 21

  Рет қаралды 5,551

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
#MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

Пікірлер: 12
@StaffordNgalande
@StaffordNgalande 13 күн бұрын
Koposa ziko Asilikali alitenge kae
@LucksonChipofya
@LucksonChipofya 12 күн бұрын
Zimene akupanga a mec ndizauchitsiru asatitenge ife amalawi kupusa
@marryphili5419
@marryphili5419 13 күн бұрын
Ndiye masiku awiri wokha mikanangosiya basi
@SostenSambani
@SostenSambani 12 күн бұрын
Matsiku awili ndiochepadi kaswiri pandaleyo nayenso alindizifukwa zake koma chilungamo ndichomwe akunena a mwanamveka
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 13 күн бұрын
Zipani zosusa boma pitani ku khothi
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 13 күн бұрын
ANTHU SANGALEMBETSE CHIFUKWA CHA UCHITSIRU UNENE MUKUPANGA AGLU INU A MCP
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 13 күн бұрын
Palibe chimene mwachita masikuwodi ndi ochepadi kotero anthu ofunikilawo Salembetsa.
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 13 күн бұрын
MCP IKUYESETSA NJIRA ILIYONSE KUFUNA KUBERA NDIPO AZIPANI ZOTSUTSA MUKUYENERA MUDZUKE CHISANKHOCHI CHIKUYENERA ALIYENSE AKAVOTE BOLA M'MALAWI ZAUTSIRU ZIKUCHITA MCP
@Jaymore265
@Jaymore265 13 күн бұрын
Mwachulutsa ma strictions simukufuna kulemba anthu....nanga poti ambiri cha NRB alibe so how can you say tikulemba okhawo ali ndi chauzika? That's nonsense 😢
@JoyLuwanika
@JoyLuwanika 12 күн бұрын
Ena sanalembese ana udzidwa kuti kunja kwanda lero akuwakwana
@EliasKhofi
@EliasKhofi 13 күн бұрын
Adziwa bwanji kut atsala anthu ochepa kut alembese a NRB.anthu mudziko tilimo 25 millions olembesa ochepa kwambili.iwo sakufuna kut anthu ambili alembese a NRB ndizomwe agwilizana kut adzasokoneze mavoti omwe anthu ama ID Anawaika kale mu system yawo yodzabela.aona kut akachuluka ndi figure yawoyo akamadzalengeza kut wawina ndi chakwela,awa adzawasokoneza kut abera adzagwidwa ndi figure yomwe ikulembesa pano yomwe sanaike mu system.
@AnishaMoosa-ej7yr
@AnishaMoosa-ej7yr 12 күн бұрын
eshh km boma iri iii
USAUVER S10E08 - CHAKA CHATSOPANO
23:00
Piksy TV
Рет қаралды 72 М.
UFC 287 : Перейра VS Адесанья 2
6:02
Setanta Sports UFC
Рет қаралды 486 М.
Ful Video ☝🏻☝🏻☝🏻
1:01
Arkeolog
Рет қаралды 14 МЛН
Жездуха 41-серия
36:26
Million Show
Рет қаралды 5 МЛН
Prophet Uyu Walosera Zoopsa Pa Zisankho Zikubwerazi ... Tanvani
27:34
Nkhani ya mulandu wa A$AP Rocky
12:19
The Jaki Show
Рет қаралды 15 М.