Ndakukondani kwambiri ndifundo zani zabwino koma VUTO ndi implementation moment mukadzalowa mu office ,otherwise you will take my vote keep it up bwana
@JohnKalembo9 күн бұрын
Kodi ndiwakuti ameneyu eeish sindingamuvotere munthu osamudziwa ine Dpp my vote❤
@MackenzieAlfred-l6z8 күн бұрын
Thanks 👍 Mr.President.
@RobertJere-p9u2 күн бұрын
I will follow you 😎
@MakayikoNdhlovu8 күн бұрын
My vote and very ready to work with you. Festus Gondwe from Rumphi
@NOKIAMalawi6 күн бұрын
100/%ndimbambande ndioganiza Ngati bingu💪💪💪💪
@mussakapalamula19909 күн бұрын
Wauka kwa akufa Kamuzuyu
@MaxwellMbesa9 күн бұрын
Good Dreams go ahead brother bravo❤ GOD BLESS YOU and guide you
@lovenesschimombo3887 күн бұрын
🔥🔥🔥
@FaroukSaliem8 күн бұрын
Ichichi Ndichipani cha mcp. Bon kalindo adanena kuti tiyembekezere ku badwa zipani zosiyana siyana zomwe a mcp azatsegule pofuna kuwasokoneza mitu amalawi. Kumapetoko onsewa adzakumana pamodzi. Ndine Farouk saliem from kasiya in Lilongwe kwawo kwa chakwerayo. APM is my vote 2025 ndipo sindikusintha. Bwana Tobias, zikalimani kumunda basi. APM moto kuti bhuuuuu!!!!!!!!!!!!! ❤❤❤❤❤❤❤
@yasiniKalonga8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 exactly 💯
@HellenChejohn-n6o8 күн бұрын
Yes! Yes! Ndankumbukirad the dc
@Alice-z7t4z8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤
@PeterJackson-o2n8 күн бұрын
Awa asatipusise ayi
@MadalitsoLuhanga7 күн бұрын
Adad woyeeee 2025 bomaaaaa 🎉🎉🎉🎉
@miraclejohnphiri76878 күн бұрын
PA moto wanga ode sindinamvepo munthu wa Neale akupeleka manifesto ngat awa big up mr
@MisheckMalichi-k3y8 күн бұрын
Mapaziako iwendiye ndani
@MaxwellMangamba8 күн бұрын
Anzanu aja anali owonda chonchi ankavala majekete amatakisi, masukumba ngati vendor wamatemba Ngati ine. Ngakhale nkhope ikuchita kuoneka kuti nanunso mukudutsa mu nyengo zovuta. Mwachidule ine sindingavoteyere anthu a sweet talk ngati angelo. APM my vote.
@ThomasmosesMoses9 күн бұрын
Azanuso anayakhula bwino kuposa zanuzo km tinagojezela mavuto ositha dziko NDI adadi bas amalawi tiyen tisakhe dpp pofuna kutukula dziko osat kutukula mu2
@georgeaiwa86619 күн бұрын
Am impressed. Iwe ndiwe Vote yanga. You deserve presidency
@HarrisonMwanga-xy4sc9 күн бұрын
Tobiasi from Mozambique,tidzalamulidwa,ndi wobwela.malawi,ndi ziko lobvetsa chisoni kwabasi.lotoledwa
@RodneyKapere9 күн бұрын
Olongololanso ngati skc anthu otelewa aMalawi tawaona takumana nawo kale and aMalawi tkudziwa mwabwino ndi moyipa mwawo
@beatsbymcstevens9 күн бұрын
Nde zokanikazo, Obama atalamulira America kenya inkalamulira nawo? Every Malawian is a foreigner kafunseni agogo anu ngat ndinu amalawi
@HarrisonMwanga-xy4sc9 күн бұрын
@beatsbymcstevens ndi chifukwa, malawi lingobedwa mwala ya mtengo ya patali olamulila,ake kumangokupopani magazi.obama,mufufudze,kholo lache limodzi ndi la ku america,kuja.pomwe,ku Malawi kuno,tinalamulidwapo,ndi ena,osakhala,akuno.ku,zambia mufufudze from Kaunda ndi wa ku nkhata bay.onse,ankhaza mukuwaonawa ngati ali mmalawi ndiye kuti,kwao anali phawi.ndikukula,mobvutika.
@peterbyson62698 күн бұрын
i love the points but in action we get different
@zechariahphiri12878 күн бұрын
Mr. Tobias, if this is not a mere sugarcoated manifesto, Malawi can really develop under your leadership.
@MercyKziphondo8 күн бұрын
🎉ndangotha data Yanga aaaaa bola gogo uja dpp
@KennedyBaton8 күн бұрын
Dennis mahata my president
@EmmanuelGordon-q9s2 күн бұрын
My vote😂😂😂
@EliamKaponda-pi9cv8 күн бұрын
Mukunenazo bwana Tobi tamva koma tatiuzeni kaye malonje anu tingayambe kuombela mmanja alendo
@MpasulavisaSonjo9 күн бұрын
Good analysis, but easier said than done. One maybe fitting Presidency but bitting corrupt systems and egocentrism remains a challenge Winning presidency as an independent, a hustle
@richardarmittage16937 күн бұрын
❤
@HastingsBwanali-q9b8 күн бұрын
Akulu ndinu achinyamata ndi wanzeru tiyeni ku UTM kwa afana oganiza boo
@LLOYDMWANDIRA8 күн бұрын
Exactly 💯 this guy may join UTM, My vote 2025 UTM.
@AndrewMachemba-j2u6 күн бұрын
Tiyeni ku dpp musazipusise gyz
@MasChisi-v4lКүн бұрын
UTM inagulitsidwa
@edsonnyasulu539422 сағат бұрын
Exactly anyamata ngati inu tangopitqni ku utm mukathqndize malawi utm ndi chipani chopanda banja la munthu kapena mutundu
@edsonnyasulu539422 сағат бұрын
Anagulisa ndi ndani
@lottiethamanga8 күн бұрын
How shall you reduce the gap between the rich and the poor? If given the post, how much will be monthly perk and your cabinet?
@FanuelManesi9 күн бұрын
Umu muli dzeru ....my vote
@MathewKalinkhu9 күн бұрын
Anzako onse amakamba zomwezi, koma palibe chimene akuchita. Ungolowa DPP kuti ma ideas amenewa ukatulutse kumeneko.
@abdulsalammkwepu33218 күн бұрын
Maina achina tobiyasi wa penapake aaaaaa😀
@millionsenenje50109 күн бұрын
The guy ndi machine , way better than bambo a vaileti
@SamisonLevison-z5p8 күн бұрын
Samalani maina a Tobias ndi akathyali.Uyu atha kudzaba zochuluka.Mumuonesetse akuwoneka kuti ali pa dzuwa.
This is not strange and outrageous campaign promises , not all that gritters is Gold
@Amos-h8g4 күн бұрын
Harrison Mwanga ndiwe wabodza Milward Tobias ndi mmalawi from Kalumba Village, T/A Makwangwala ku Ntcheu. Primary yake waphunzira pa Mpotola LEA School. Ineyo ndaphunzira naye timapikisananso MKALASI. Musanamize wanthu.
@AlbertGoffat-jo8et8 күн бұрын
Waukayo Ameneyu Kwinaku aah nditha kubweza mkwiyo kudzela mu Pansana panu kom ndisatelo Zikomo
@DONNEXKhama-bk1gy8 күн бұрын
It will be not easy for you Keep it up
@lastonkamanga40728 күн бұрын
If chakwera and Peter hear that how do they feel😢
@StevenDastan-f5y9 күн бұрын
Ma sweet talk ife ayi
@JoyceKasongo-s8k7 күн бұрын
Ndinu akuti
@MaxonKambazithe9 күн бұрын
You better be activists wava
@JoelTchuma-g3s8 күн бұрын
Mulungu sayankha zoipa ayi koma amavomereza chiysankho za anthu monga adasankhira Sauli mmalo molamuliridwa ndi Mulungu.
You would be surprised that Chakwera doesn't have all those details. The dude is lost ,crueless
@PiassDayit8 күн бұрын
Kodi akuruwa anali Kut ndawi yoseyiii
@Mazizi268 күн бұрын
Mufuna VP ngat ndilipo
@JoelTchuma-g3s8 күн бұрын
Nyanja ya Lake Malawi yagulitsidwayi mukuiganizira motani chifukwa tamva kuti yagulitsidwa.
@user-ii9ch7oz8n6 күн бұрын
yagulisidwa ndindani kuva moyipa nyanja atazania akufuna kudulako mbali yimozi yakwawo
@RoseThindwa9 күн бұрын
Manifest abwino koma tatopa Malawi's sweet talk pano dziko lili ndi mavuto utsogoleri power hungry
@ChristopherNamatika8 күн бұрын
Gayileniko # yanu boss ine ndamva mfundo zanu mzothadizadi kusintha malawi kuno ku mangochi
@MartinNice-z9n8 күн бұрын
Kuyankhura reality ndakukonda
@Dellingsmunthali8 күн бұрын
Wachepa I say ndiwe mwana mavuto athuwa sungathane nawo ngat ukunjenjemera poyankhura ungatani mwanawe wachepa kwambiri""
@JoshuaNyirongo8 күн бұрын
If wishes were horses beggers could ride
@Amos-h8g4 күн бұрын
Mamuna Koma uyu
@miraclejohnphiri76878 күн бұрын
Ndiiwe mchewa mbola
@JimmyIsaac-xd4ef9 күн бұрын
Ali ndi mfundo zabwino ndithu, Koma a Malawi chinatiluma chakuda
@KachingweNtaja8 күн бұрын
Angofuna ndalama awa ,kwao kut kod
@HellenChejohn-n6o8 күн бұрын
Tobiasi ndi opposite ya chakwera
@PiassDayit8 күн бұрын
koditu bozatu bola Wosasekhatu
@ElizabethMajiga9 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂 Yesu angobwela basi ndinu nomweee😅😅😅😅
@yakinidagalasi9 күн бұрын
mbavaizi dpp my vote
@EliasKhofi8 күн бұрын
😂😂😂😂 kuyankhula nkosavuta koma kuchita.taonapo manifesto a tonse alliance kubwela ndimfundo zabwino.kuwavotera kutimbenukilana koma guys mumapeka mfundo bwanji inu andalenu?mapeto ake mumatikanila manifesto anuwo.kodi bwanji zipanizi tiziwapasa manifesto ndife ovotafe kut mudzatipangile izi muzaka zitatu or 2 kulephera tikuchosapo coz walephera.kodi bwana ndi wantchito amapeleka ntchito kuwantchito ndindani?mapresident ndi antchito athu timawalemba ndife komanso opanga fire ndife which means mabwana awo ndife(managers).we voters are bosses to tell them what to do in the office not them to tell us what to do these pple.thats y they abuses us with our vote.
@PATRICKPhandaphanda9 күн бұрын
Akunama ameneyo
@beatsbymcstevens9 күн бұрын
He sounds like he knows what he's talking about, let's see akabwera pa ground
@spymhango67039 күн бұрын
he once served as advisor to SKC on economic affairs
@GoodsonLevison-o1m8 күн бұрын
Koma mukukayambe u MP bwa
@Thanthwe20209 күн бұрын
Kakmeni inu iyaaaa zaziii
@MathewsMandutu-q9l8 күн бұрын
Wachokela pati ameneyu
@LucyKulemeka9 күн бұрын
A Tobias ndi akuti?
@KasimIbbu9 күн бұрын
Mwasowachochitasopano kod akugayilani ndan makobiliwo
@RabbeccaChitimbe9 күн бұрын
Mwachoka kt man simukuziwikatu
@GoodsonLevison-o1m8 күн бұрын
Ma fundraising akuchitika pakulimbikisa chipani komanso kusonyeza kt adachoka m boma sanatenge chuma
kadziko kochepa ngati Malawi ma president opikisana almost over 6? taonani USA only two chidziko chachikulu Africa kuchepa. nde mukuti 50 plus 1 muigwira ma president nonsenu?
@Sholivid3 күн бұрын
Vuto lake mumabwela ndi zinyengelelo zolusa tikakulolani kenako muyambe kutipha,kutimana chakudya,komanso kutimanga osalakwa ,andale ndinu afiti mxoo!, Koma uli ndi mfundo za bho
@Inaciokenedimoendamoenda8 күн бұрын
Akuluwa ari ndi zelu koma afunika achite zabwino kwa wathu chifukwa ose akamayaba amabela ngat agwilo koma akalowa akalowa amasitha