BON KALINDO LERO PA 09 OCTOBER WAULURA ZINSISI ZA BOMA NDIPO WANENA MOSAOPA KUTI CHAKWERA AYALUKA

  Рет қаралды 7,594

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 63
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 2 сағат бұрын
Iwe utha kupulumutsa dziko lathu more fire
@EdsonMulendo
@EdsonMulendo 52 минут бұрын
Mafiyaa kkkk
@AutonChalion
@AutonChalion 36 минут бұрын
Umakwan mesa the DC💪💪💪💪umatiyimilira
@VictoriaBakuli
@VictoriaBakuli Сағат бұрын
Ulemu wako the DC iweyo sangakumange akuziwa kuti olo ukhale mundende Koma voice yako izamvekabe
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 38 минут бұрын
Kalindo mzeru zamuthera kkkkk guys, Ben Longwe wamupepelesa
@TameeraInglis
@TameeraInglis 51 минут бұрын
Mr DC Winiko more faya
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 2 сағат бұрын
Boma .....iliri Ayi ndinthu yatikwana .....the dc inuyo ndi 1😂😂😂
@BrianJoe-z7u
@BrianJoe-z7u 22 минут бұрын
Boooon kalindo DC inuyo inuyo
@MarcyKamaga
@MarcyKamaga 2 сағат бұрын
the dc ukunena zowona ukuwonera patari ndipo usazafe uzangosowa koma uyu chikangawa akuti pweteka mtima ukuwawa kwambiri m'mene anaphera skc mzimu wa sauros uwuse mwatendere
@calvinjamal7117
@calvinjamal7117 21 минут бұрын
Bonon Kalindo mwana oopsa kwambili iwe dolo
@IssahAluba
@IssahAluba 56 минут бұрын
😂😂 wayitulukira Dc 🙌
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 2 сағат бұрын
Koma Mr born mwamva!!!,apuletu ayamba kufa ziwalo,moti pano mkono siukugwira ntchito.moti week yamawa timva afa mkabudula😅😅😅😅😅😅
@MosesMottah
@MosesMottah 2 сағат бұрын
Akulu mukhaliketu
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 сағат бұрын
Eya nkono waku manzere wapanga paralyse😅😅😅😅😅
@VictoriaBakuli
@VictoriaBakuli Сағат бұрын
😂😂
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Сағат бұрын
Kalimdo sukunama nkhondo yafikapo panopa Iran Hezbroh Labanon ndi Palestine akuti akufuna kubwezera znse zomwe Israel yachita ku Gaza ndye kutha kwa Israel kwafika ndye anthu aja zoti Netanyahu angatumize anthu aja kunoko ndakaika mutu sukugwira Netanyahu panopa ndye zioneka
@ArchangelBanda
@ArchangelBanda Сағат бұрын
Israel shall stand forever Let's talk about zinazo koma osati kutha kwa Israel
@vittazomba
@vittazomba 20 минут бұрын
Hahahahaha koma ziliko
@FatiwelloKatema
@FatiwelloKatema Сағат бұрын
Tirimbikire kugwirantchito yotithandiza zikorathu
@BlessingsChipetuka
@BlessingsChipetuka 51 минут бұрын
Ulemu upite kwa my president the DC koma mlungu ashamed nanu
@BlessingsChipetuka
@BlessingsChipetuka 46 минут бұрын
Mlungu akudalitseni the dc
@Andygoz21
@Andygoz21 2 сағат бұрын
Zikachitika timamvera Kwa iwe DC
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 22 минут бұрын
Tiyen teyen kwacha pamsei
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 58 минут бұрын
Born Kalindo the DC
@OwenYobe
@OwenYobe Сағат бұрын
KKkk koma DC Koma nde tiyamule ma truck awiri tikangulitse feetilizer tiwaone ngati avomele
@SostinMatchado-z2o
@SostinMatchado-z2o 2 сағат бұрын
Koma DC umaseka momukweza munthu BP ase power
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 2 сағат бұрын
Koma The dc 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@DavidKadewere
@DavidKadewere 3 сағат бұрын
Mr chakwela kkkkkkkk kom ayi zikom 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@BoscoJosaya-u3r
@BoscoJosaya-u3r 2 сағат бұрын
The DC ❤
@PulayaKalaka
@PulayaKalaka 2 сағат бұрын
Proper Ganda
@JamesLongwe-qz9fd
@JamesLongwe-qz9fd Сағат бұрын
Ndiwe wa chikangawa 😂😂
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 2 сағат бұрын
Mwamnyooooo auzeeee
@MosesDicostar
@MosesDicostar 2 сағат бұрын
😅😅😅😅😅 born kalindo ndlibe nawe mawu paka ukusaka ndende kkkkkkk😅
@Thewarrior7093
@Thewarrior7093 2 сағат бұрын
No wonder nkono wake wathyoka galu wa munthu
@MarcyKamaga
@MarcyKamaga 2 сағат бұрын
ndipo akayiati mwatikhumudwitsa kwambiri ndipo murungu akuyendereni zowonadi mayi zukani mama chipani chathu chikutiwawa kwambiri koma chakwera murungu akurange koopya
@NoohNowa
@NoohNowa 39 минут бұрын
❤❤❤❤
@ChikupizgaKajawaMkandawire
@ChikupizgaKajawaMkandawire 48 минут бұрын
Za ziii
@kennedybanda
@kennedybanda Сағат бұрын
Wa MCP tatsutsatu apapa tikuone.
@AlexDaniel-m4t
@AlexDaniel-m4t 2 сағат бұрын
Komatu ndiye zafikapo ndiye fertilizer Chaka chinoso kulibe aaaaaaa yeah koma tiziwona
@AllanBinali
@AllanBinali 2 сағат бұрын
Akuti ma Mafia kkkkk
@PrivilageMpasiwa
@PrivilageMpasiwa 2 сағат бұрын
Ponyani tima video anyamata ku Gaza ko tione ngati muli moyo
@samsonjgareta6144
@samsonjgareta6144 Сағат бұрын
Boma lipusa ili
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Сағат бұрын
Kalindo muuze Chakwerayo kuti dzulo lomweri Iran yayankhul pa Aljazeerah kuti yakonzeka 100% kuphulisa Israel ndye kutha kwa Benjamin Netanyahu kutha kwake kwafika panopa
@ArchangelBanda
@ArchangelBanda Сағат бұрын
Kkkk maloto chabe amenewo Israel shall stand forever
@AmosCup
@AmosCup Сағат бұрын
Mamafiya
@MussaZakeyu
@MussaZakeyu 3 сағат бұрын
Kkkkkkkk boon kalindo 😂 the DC
@SurprisedDarts-di6fs
@SurprisedDarts-di6fs 2 сағат бұрын
Umakwana
@WestonGawaza
@WestonGawaza 2 сағат бұрын
Achinyamata mulipo eeeee azimayiiiiiii mulipo eeeeeee Timange boma ili achinyamata azimayi makolo anthu azitiphuzisa nchito sitiwataya ayi kapeni azimayi ndi achinyamata osanena Zamariro ayi zamariro mukalowa muboma mukaphonya apa chipani mugulisadi
@kennedybanda
@kennedybanda Сағат бұрын
Anaftu mafana amenewo
@RoseThindwa
@RoseThindwa 2 сағат бұрын
Boma ili more tricks😂😂
@EvanceGilmon
@EvanceGilmon Сағат бұрын
Zazii
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v Сағат бұрын
Boma la mamafia
@RebeccaFinias
@RebeccaFinias 3 сағат бұрын
Bambo nyoooo tsopano
@WestonGawaza
@WestonGawaza 2 сағат бұрын
UTM ikalipo ndi mphavu chaka chino osasintha maudindo zinkhale mene zinaliri .MARRY chilima president Anenekuti tipange History malawi ziko lose lapasi
@FionaKhoma
@FionaKhoma 2 сағат бұрын
The dc
@KayceeBrighton
@KayceeBrighton 53 минут бұрын
😢
@RuthBanda-p9k
@RuthBanda-p9k 51 минут бұрын
😂😂
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo Сағат бұрын
Propaganda akalindo anthu sitingamakuvere manyaka akowo
@BrightZionga
@BrightZionga Сағат бұрын
Khalani choncho malume
@SelinaNamagowa
@SelinaNamagowa Сағат бұрын
Sungamumvere wenkha ife timumvetatu ameneyu
@chilembwekanjirawaya4296
@chilembwekanjirawaya4296 24 минут бұрын
Iweyo uzingopusa uzazindikila uli wekha
@ThomGentle-xf4mc
@ThomGentle-xf4mc 2 сағат бұрын
Mukava ndafa ndi uyu basi pulezidenti woipa
@NoohNowa
@NoohNowa 39 минут бұрын
❤❤❤❤
Mlaka Maliro - Chilungamo (Official Music Video)
5:57
Mlaka Maliro
Рет қаралды 3,4 М.
Watermelon magic box! #shorts by Leisi Crazy
00:20
Leisi Crazy
Рет қаралды 92 МЛН
1 сквиш тебе или 2 другому? 😌 #шортс #виола
00:36
Man Mocks Wife's Exercise Routine, Faces Embarrassment at Work #shorts
00:32
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 6 МЛН
Rivers Crisis: One-On-One With Nyesom Wike + More | Politics Today
54:46
Channels Television
Рет қаралды 118 М.
Fubara To Wike: Let Go Of Rivers, You Can’t Win All Fights
20:28
Channels Television
Рет қаралды 109 М.
Rivers LG Poll: APP Wins 22 Out Of 23 Chairmanship Positions
9:42
Channels Television
Рет қаралды 53 М.
22. Mai 2024 - Regierungspressekonferenz | BPK
1:03:02
Jung & Naiv
Рет қаралды 22 М.
Watermelon magic box! #shorts by Leisi Crazy
00:20
Leisi Crazy
Рет қаралды 92 МЛН