Ambuye tithandizane tikuvutika kudziko lathu la Malawi,tigweseleni nvula ambuye ,tisavutike chifukwa Cha anthu ochimws a
@YassenYasin-v6oКүн бұрын
INuyo ndimachine boss DC ❤❤❤❤
@Dellingsmunthali17 сағат бұрын
Tasekaso koma kalindo kuseka kokhako ndi ndeu kare🤣🤣🤣🤣
@JudthChisaleКүн бұрын
Kodi ndife ana kuti azititseka pakamwa achita bwino abishop kulakhula
@hamiltonsolomon3756Күн бұрын
The DC...Umakwana ❤❤❤.More Fire 🔥 ❤❤❤❤❤❤❤
@JohnfosterNkusengwaКүн бұрын
Mr bon kalindo your the voice of malawi 🎉 and bishop sakuyenera kupepesa iziz ai ndipo timpanha sapoti kuti asaope and tili nawo limozi
@Dellingsmunthali17 сағат бұрын
Wado wado ndindani koma kalindooooooo😂😂😂😂
@wonganimtabayiranyondo9880Күн бұрын
Akuti anjanjawidi kkkkkk😂😂😂😂
@MosesDicostarКүн бұрын
Koma kalindo ndwe katundu ase ❤❤❤
@CarolineSelemani-p5p17 сағат бұрын
Kkkkk katundu bwino
@WisdomMoyo-v8j17 сағат бұрын
Ndipo nd diso lathu loona patali amachenjeza zisanafike zowawa iye wati muimitse madongosolo olandila alendo kuchipinda chomatacho cos achikangawa party akukonza zokaphulitsa kabomba kawokawo kukatolikako chonde wamisala nkhondo anaiona timvere ndithu !!!!
@PatrickSomanjeКүн бұрын
We love u mr bon kalindo 😂😂😂😂
@AlexThabwani-f3mКүн бұрын
Bishop of the year msusa😂😂😂
@BreezeBarryКүн бұрын
MCP have no chance
@CheobviMasambaКүн бұрын
Innnuuuu munaza akalindo boma illoo🎉😂
@DavidMakasuКүн бұрын
A bishop alankhula mu church Sanachitise press conference. Inu ngati muli akulu amipingo bwanji osakayankhula ku church komweko? Why press conference.
@KateMunthaliКүн бұрын
Koma Winiko iweyo 🙌anakonza😅😅😅😅
@DemusterKamwimbiКүн бұрын
Zoona mcp ndiyakupha ndimakumbukira thawi ya kamuzu bishop waku Lilongwe ku Lilongwe anampanga chipogwe komanso ku Blantyre ku c I anabweretsa wall drop ngati phatso atayikamo wa payoniya koma munthu anadziwa ndipo anapephera mulimbika mpaka anafera mkati mwa wall drop mu roma ndiwopysa zinachitika mu 1993 17:08
@joychinyama305315 сағат бұрын
I can remember
@MchachaGoodson18 сағат бұрын
How long Chakwela will understand that Malawians don't need him.He Will be exposed and if that happens he will regret why he didn't resign from his presidency.
Tikachoka pano tikukatsilizila ku bakili muluzi tv
@EugeneMatopeКүн бұрын
What is wrong is wrong no matter how many abusa ojiya are pretending to be right!!!
@TakalaniGlendaКүн бұрын
Koma born kalindo umandimaliza ndimaseka ndikamamva mawu ako 😂😂😂😂
@YasinMmadiКүн бұрын
Mr born kalindo mulipo atatu dziko muno pliz musazasinthe kutiyankhulila ife osauka Mr kalindo Bakili muluzi tv Mr ntanyiwa You are the best activists in malawi
@GetrudeBanda-sd1yf22 сағат бұрын
Bon Kalindo number one
@NEBRA-lm7jiКүн бұрын
Zomwe alankhula a msusa zo nde chilungamo ena inu ndinu osochel
@MikeChimombo-n6wКүн бұрын
😂🔥🔥mbambande the DC mwachita bwino kuwasambwaza agulu amenewa akutitenga ngati ife opusa
@WilliamMachila18 сағат бұрын
Abishop Msusa zimene munayankhula ndizimene mulungu anakutumuni asiyeni anthu aziwanda mosogozedwa ndi wamkulu wa ziwanda Dr chisilu chakwela mwana opusa
@JudthChisaleКүн бұрын
Eti.ulaliki wa church umayakhidwa ?
@SylvesterSululuКүн бұрын
Ine ngati wosavela the DC sindiva bwino chifukwa zambiri timavela kwaiwo mmumalana achimwene
@vittazombaКүн бұрын
Malume ine ndemmandiwauza msaname simmanyengelera poyankhuka,ndipo abishop akuyenetekadi asamalire maka kachipinda kolapira kaja asamalandire anthu achilendo
Mulipo anthu angapo kuno Bishop Nausea Kalindo Bakili muluzi tv Ntanyiwa Ecg church Pastor shumba Lwawa Lyton mangochi
@WanangwaMfune20 сағат бұрын
Iwe ndiwe mbuzi yeniyeni...... Abutsa ose umawaziwa iwe chamba chinakupatsa ntchito yotsalipidwa et, Ndipotso utsogolero wa u president osawuka anakuvotela ndani kusowa zochita. Komatso kupanda misala Yako ndiyongolalata daily. Ndikati pheeee iwe ndiwedi openga
@DONNEXKhama-bk1gyКүн бұрын
Haye Haye 😂😂
@PiasonAndrew-t7v16 сағат бұрын
Chilungamo Kwa chilungamo
@ThokozaniBondo-em9fr23 сағат бұрын
Inuyo mukwanila Mr Kalindo
@william51448Күн бұрын
Koma Amwene ..... 2025 .....kuchema
@CosmasMkuta11 сағат бұрын
Khenge
@blessingsnyalo-rp9ko16 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@kingmireZiyazieКүн бұрын
Auzen chilungamo🎉
@BistonMachesoКүн бұрын
Ineyo ndinanena kare kuti siazibusa amenewo ndimakawalala amenewo simazibusa amene masata achakwera amenewo mcp akupita basi APM akulowa boma basi
Koma zikugwilizana nanu apa?????? Inuo or it akhala nyasi zikukukhudzani bwanji za mpingo a Ena????? Inuo kumpingo kwanu kuli angel????? Manyazi mulibe eti
@berthachithumba859322 сағат бұрын
This is a church founded by Jesus Christ of Nazareth so God will punish you wherever you go. Listen I feel bad to insult catholic church rather than other churches founded by any evil persons.