Ambuye adzikupatsani mpweya wamphanvu kuti mudzilankhula. Koma inuyo a Boni Kalindo mudzidziwa kuti mavuto amene akukumana nao a Malawi 🇲🇼 munyengo inoyo ndi boma MCP. Zonse zimene zikuchitikazi ndi chifukwa cha inuyo a Kalindo pamodzi ndi Chilima ndipo ndi anthu inuyo amene munapangitsa kuti Malawi afike pamene alipa. Zonsenzi munachita chifukwa chakuti inuyo a Kalindo and Chilima ndi team yanu imene munayambitsa UTM munkachita nsanje kapena kuti jealous ndi a Peter Mutharika. ndiye pakuti munkadana ndi a Peter Mutharika ndichifukwa chake munawapeleka a Malawi 🇲🇼 ku MCP. ndipo sindikudziwa ngati Chilima ali ndi ntendele kumene aliko. Chifukwa anthu inuyo ndi amene munawaika a Malawi pa mavuto. chifukwa chimene ndikudziwa ineyo a Malawi anathana ndi MCP 1994 ndipo sankaifunanso ndipo anada nayo kukhosi. Koma iweyo Kalindo ndi Chilima ndi amene munawakakamiza anthu kuti avotele MCP. Ndipo inuyo a Kalindo pamodzi ndi team yanu imene inachita zimenezi mudziwe kuti milandu imeneyi mudzakayankha kumwamba chifukwa mwazunzitsa a Malawi 🇲🇼 osalakwa.