BREAKING NEWS - GREZEDA JOEFREY WATULUKA DPP NDIPO WALOWA CHIPANI CHA MCP NDIPO WAYANKHULA LERO

  Рет қаралды 6,404

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 69
@MabushPaulo
@MabushPaulo Ай бұрын
Ndale Zaku Malawi ,Mmmmm ukhoza kuchimwa ndiweyo wotukwana , Chifukwa kutukwana ndi tchimo , Ndiye ndale sikutukwana ,
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Mayi wopusa kwambili mmesa anachita kuchosedwa ku dpp .....akuti watuluka osauza anthu chilungamo bwanji
@ChikondiChimwaza-i8l
@ChikondiChimwaza-i8l Ай бұрын
Wathapo ameneyo,amapusisana ndi mwamuna wake nankhumwa
@austingsmaganizo
@austingsmaganizo Ай бұрын
2025 palibe omaka.Bodyguard ndi mbale wake wayamba kampeni chifukwa agogo sangakwanitse.Takulandilani Mayi ku chipani Cha makolo .DPP kulibe democracy kwao mkuchotsa anthu ndiye kaya adzavotera ndani.Chipani chabanja chopanda maziko.
@MiracleDamiano
@MiracleDamiano Ай бұрын
Nosense 🚮🚮🚮🚮🚮
@JohnNdala-tv7gm
@JohnNdala-tv7gm Ай бұрын
Nose amene mwapita ku mcp ndinu anthu omwe munaphsnawo chilima chifukwa likanakhala azelu dimukanapita kukalowa ku mcp pamene kulizipani zambili koma mwasankha kupha ndikuziwa amalawi omwe akudya chitezi mulungu akuwoneseni nkwiyowache ndi mizimu yonder inaphedwa ku chikangawa kuja
@eddiesilika618
@eddiesilika618 Ай бұрын
panyini yake mmene anthu akuvutikilamu kundya chiteze kumati chakwela ,chakwela panyopako ife ndi ADaDi basi
@JusticeKawilira
@JusticeKawilira Ай бұрын
Kodi watuluka dpp.kapena anachotsedwa ku DPP sigulu lija linalembedwa ganyu yothetsa chipani lija
@zayedmitawa8345
@zayedmitawa8345 Ай бұрын
MCP ikungotoleza zofumbwa zokhazokha. DPP inaona patali,anthu awa siokhala nawo mchipani.
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 Ай бұрын
Mayi opusa iwe ngati unalephera kuwina u mp ndiye ungawawuze anthu chani apa Dpp inachina kukuchosa osati uwanamize anthu kuti wachita kuchoka ayi
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc Ай бұрын
Anthu akulowera Kut akapeze ndalama basi zaphweka ku chikangawa
@JamaniNyirongo
@JamaniNyirongo Ай бұрын
Anachoka ndikale awo mesa linali gulu la nankhumwa limenero.
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Ай бұрын
Opusa nda amako uyu waganiza bho kulowa MCP ndiye kopita kumeneku
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td Ай бұрын
Joker wa DPP walowa MCP basi DPP yaguluka Mai ndikatundu uyu
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx Ай бұрын
Hule uyu kutha kwamuthu kumakhalakomweku dziwani kut chipani ichi cha chikangawa chikupita komwe chinali samalani amalawi
@MiracleDamiano
@MiracleDamiano Ай бұрын
Zaziii 🚮 🚮
@hopesato
@hopesato Ай бұрын
Malawi has became as a drama
@jomochirwa
@jomochirwa Ай бұрын
Esh koma zinthu zake esh vuto dpp alomwe akuchitenga chipani kuti ngati cha kumtundu wawo.
@LuciusMowa
@LuciusMowa Ай бұрын
Iyeyo anachotsedwa kale ku chipani cha Dpp alibenso ntchito
@FranksonKennethChipande
@FranksonKennethChipande Ай бұрын
Koma cadet alimba????? Tingovota basi a satana asiye kumunamizira Chakwera
@LameckBanda-gk6ri
@LameckBanda-gk6ri Ай бұрын
Tikuti za Baja asiyireni abanja ,lowani chipani Cha ufulu osati za family ,wina daily azingolira , MCP imakodzetsa munya muwona
@henryhenry6632
@henryhenry6632 Ай бұрын
Akutsugula mpwelele Peter munthalika 😂😂😂😂
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Ай бұрын
zazi mahule azimayi a mcp
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Ай бұрын
Aaaa uwu nde uchisilu munthu ati anachita kuchotsa lelo mudzina kuti watuluka aaa ndalama za boma kumangogulila ndidzisilu dzomwe akanakhala dolo nde DPP inalephela bwanji vote uchisilu wa MCP ukutola dzisilu mahule amwano 2025 DPP ibwelatso MCP anthu akudya chitedze inu KUMAMVA kukoma inu agalu kwabasi
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu Ай бұрын
Zamkhutu za ziiiii!
@BlessingsLuclus
@BlessingsLuclus Ай бұрын
Amayiwa ndi hule angofuna ndalama bas
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u Ай бұрын
Chitukuko sitikufuna Tikufuna kudya katatu Chifukwa magalimotowo achitukukowo tilibe
@PatricaTchuwa
@PatricaTchuwa Ай бұрын
Waboza uyuu wasowa kolowela
@AdamKay-q1l
@AdamKay-q1l Ай бұрын
Wasigulitsa ameneyu Ku mcp
@adamadbilaal1674
@adamadbilaal1674 Ай бұрын
Kod kweni kweni MCP chitukuko chomwe yapanga ndichitiii posakhala kumangonamizira nkhond ya ku ukraine nd covid 19? Kuba mkatii
@JohnFrank-cg1yh
@JohnFrank-cg1yh Ай бұрын
Kodi linali banja???
@ChimzyWesley
@ChimzyWesley Ай бұрын
Anachosedwa ku DPP osati wachoka ayi
@NoreenNaituri
@NoreenNaituri Ай бұрын
MCP yatenga Malo basi
@JohnFrank-cg1yh
@JohnFrank-cg1yh Ай бұрын
Nsewu akukonza koma ndrama za fertilizer anabesa zija simukuwakumbusa bwa nji
@prettytambala5687
@prettytambala5687 Ай бұрын
Ndale zapa mpanje
@lovenesskampira
@lovenesskampira Ай бұрын
Akhale wabwino lero?
@LawrenceBelson
@LawrenceBelson Ай бұрын
Wapitilako uhule
@MonicaKafunya
@MonicaKafunya Ай бұрын
Nkhalamba yanuyo ndiye yofunbwa
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Tikuonelani agalu inu ngati mungaduse pachisankho
@kaitanokagalu
@kaitanokagalu Ай бұрын
Eeeew koma MCP ndi moto
@ellahmwams831
@ellahmwams831 Ай бұрын
Akufuna ndalama ameneyo
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n Ай бұрын
Anathamangisidwa
@SallahSallah-i3i
@SallahSallah-i3i Ай бұрын
Ife tikufuna chakudya ndi fertilizer ochipa izo ndi sako
@MosesDzonzi-em5px
@MosesDzonzi-em5px Ай бұрын
Otsutsawe nde lilongwe ndi imeneyo paja imavotera mopweteketsa mtima wotsutsa, kungokumbutsana lilongweyo 2020 idapereka 680000 votes ku MCP only ndiye Ulendo uno muyembekezere million plus votes mulimba, aaaaa mwachepa ingozolowerani kotsutsako bayi koma bomali zoti mulanda Mmmm mwalemba mmadzi, ngati ukufuna kusitha ulamuliro ingopitani dziko Lina koma kumalawi kuno boma ndi lomweri
@franciscochiwandah1191
@franciscochiwandah1191 Ай бұрын
Olo boma litakhala lomweli palibe kanthu bola mavutowo akutikhudza tonse
@JustinLipipa
@JustinLipipa Ай бұрын
Mmmmmmmm pajatu munapha chilima nde mpomwe mutadziwe kuti kuchuluka kwa anthu pansonkhano sikanthu , chuma mukulephera kuchiyendetsa bwino, munapha chilima inu mutuluka bac.
@eddiesilika618
@eddiesilika618 Ай бұрын
iwe kholo yamako. Meme akuvutikula anthu kumalawi kumakamba za chakwela chikangawa
@MosesDzonzi-em5px
@MosesDzonzi-em5px Ай бұрын
@@JustinLipipa iweyo chimakanika chuma cha m'banja mwako ana akowo amakudandaula kuti zithu suyendetsa bwino yamba wakoza katangale wapakhomo pakopo ndiye uzidzayasamula bwino pano
@MosesDzonzi-em5px
@MosesDzonzi-em5px Ай бұрын
@@JustinLipipa chilima adafa pangozi ya ndege even Germany experts akakuwuza kuti vuto ldali ndege, sukuvetsa Pati
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Ай бұрын
MCP boma basi
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Chikamgawa woyeee galu iwe chakwera waononga ziko ili .....munthu wokutha maplan mbuzi
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Ай бұрын
Koma kunali anthu ambiri ndiye tikamati boma ndilomweli wina abooka mimba
@IshmaelJerard-u9w
@IshmaelJerard-u9w Ай бұрын
Zazii
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx Ай бұрын
Chikangawa woyeee muphatu ambiri inu
@FidesChandama
@FidesChandama Ай бұрын
Za uhule akutsata kachimutuyo
@TenoPop5-cl4zt
@TenoPop5-cl4zt Ай бұрын
Ndiwolotse ndkakulikhwe Wosaona kulandira wosaona nzawo
@NtchindiChirwa-l8o
@NtchindiChirwa-l8o Ай бұрын
DPP mukuva bwanji komwe muliko
@AbuZunairaHanafie
@AbuZunairaHanafie Ай бұрын
Chakwera anapha chilima
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 Ай бұрын
Analibe chipni uyu paja anchotsedwatu kalekale
@MenasKaliati
@MenasKaliati Ай бұрын
Musapusise anthu
@NoreenNaituri
@NoreenNaituri Ай бұрын
Aaa finish Wasala dausi atipeza
@MenasKaliati
@MenasKaliati Ай бұрын
Hule iwe
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k Ай бұрын
Zawo izo,,za ziii
@UseniMailosi
@UseniMailosi Ай бұрын
Amene akufuna kulemela apite ku MCP koma chitukuko pitani kwinako
@patricknthakomwa5613
@patricknthakomwa5613 Ай бұрын
Podyera
@DamianoNombo
@DamianoNombo Ай бұрын
Watha ndiweyo ukufunika kukhala ndi osokoneza anzako nzako nankhumwa nduyo munapusisana naye
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 Ай бұрын
Kkkkkk pano Nankhumwa Ali yekhayekha
@ErnestJohn-gp1ub
@ErnestJohn-gp1ub Ай бұрын
Paja anachoka kaletu musayiwale
Это было очень близко...
00:10
Аришнев
Рет қаралды 7 МЛН
Wait… Maxim, did you just eat 8 BURGERS?!🍔😳| Free Fire Official
00:13
Garena Free Fire Global
Рет қаралды 9 МЛН
КОГДА К БАТЕ ПРИШЕЛ ДРУГ😂#shorts
00:59
BATEK_OFFICIAL
Рет қаралды 7 МЛН
GWEDE-GWEE YA LERO PA__ 5 November 2024
28:21
HOT 265
Рет қаралды 19 М.
Это было очень близко...
00:10
Аришнев
Рет қаралды 7 МЛН