BRIAN BANDA KUWERENGA NKHANI ZA LERO, KOMA INU MUKUTI IZIZI A PRESIDENT CHAKWERA AYANKHURADI ZOONA?

  Рет қаралды 36,895

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 163
@GeraldChilundu-e3v
@GeraldChilundu-e3v 22 сағат бұрын
Uyu ndiwolakwitsa tikamutukwana adzitimanga koma mutu sukugwira
@McshonWilliam
@McshonWilliam 21 сағат бұрын
Nde funso mkumati akufuna 5yrs again, abraz chokani ku state house ko bas nanga za nyanja ya lake Malawi amayikonzaso
@StandwellNjoka
@StandwellNjoka 20 сағат бұрын
Vinyo watha
@MelusiMwali
@MelusiMwali 16 сағат бұрын
Ineyo ndimangokumbukira kuti anatiuza kuti iyeyo sadziwa chiri chonse !!
@ussimasi2458
@ussimasi2458 22 сағат бұрын
Hiiii 🤔 achakwela asatilakwise mayakhulidwe
@ghettodripper
@ghettodripper 22 сағат бұрын
Hahahaha anakati timva kuwawa akuona ngati akanawina??? Pansana pake ndithu che chakwerayooi
@JamesRoben-dy7bx
@JamesRoben-dy7bx 21 сағат бұрын
Kkkk ndiye ukuuza ana palibeso kulowa kawili man
@JamaniNyirongo
@JamaniNyirongo 21 сағат бұрын
Chonde podzafika pa 14 september achakwera ndi ma minister okuphawa adzakhale ali house arrest. Asazathawe zisankho zikatuluka koma ku maura prison basi
@JoshuaJuwawo
@JoshuaJuwawo 22 сағат бұрын
Koma ndatopa kutukwana ambuye chitani nayeni kapolo wanu
@AubreyChirwa-v9h
@AubreyChirwa-v9h 12 сағат бұрын
Ndizokhumudwitsa kwambiri the whole president kumalankhula zopusa ngati zimenezi, kodi mukumatitenga ngati zitsiru kapena bwanji? Mwatiwonjeza kwambiri mmene zinthu zakwwleramu mungalankhule zimenezo tikuwonani popezaso nthawi yakuthelani kale.
@Enock-gu5ff
@Enock-gu5ff 22 сағат бұрын
Acakwerawa kuwanvera ukhoza kumwarira ari ndi nkhaza kwambiri
@BrianNkhata
@BrianNkhata 22 сағат бұрын
kkkkkkkkkk
@JudieBanda
@JudieBanda 19 сағат бұрын
Kkkkkkkkkk koma ndaseka kkkkkk that's true broh
@frankcassim
@frankcassim 21 сағат бұрын
Kma nditukwana kwinaku
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 22 сағат бұрын
Chakwera mutu wake sukugwira mizimu ya anthu 9 ikumubalalitsa.
@AfunikaMafotetsa
@AfunikaMafotetsa 21 сағат бұрын
Speech ya zaka zoyamba za ululuzo tiimvere. Asamatitenge ngati zitsiru munthu ameneyu
@BrandonKanseka
@BrandonKanseka 21 сағат бұрын
Awa zawo zada basi,akawone mawa ku BT mmene kutayakire moto
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 22 сағат бұрын
wakupha iwe ulibeso manyazi chikangawa
@cuthbertjafali6059
@cuthbertjafali6059 21 сағат бұрын
Uyu ngotukwanitsa kulankhula kolakwika ngat zamuvuta osangopanga resign bwanji
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 21 сағат бұрын
Mmmmm chakwera usatichimwitse wamva Mesa unkati zaka ziwiri ukadzalephera kuyendetsa udzatula pansi udindo iwe mchiwandadi
@GeorgeMartin-z7u
@GeorgeMartin-z7u 6 сағат бұрын
Chakwera kodi wapenga kapena kupepetulidwa?😢😢😢😢God help us uyu atipha tonse
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 22 сағат бұрын
Umuuze iyeyo adapha Biyeni , akukambazo za chamba , chakupha
@NeemaMkandawire-e5c
@NeemaMkandawire-e5c 21 сағат бұрын
Kabambe akufuna kumuyipisila mbili koma muona alamulira Malawi DK2025 BOMA APM ali ndi umboni adzamupasa ma vote ake coz iye wakalamba.. Mark my words
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 21 сағат бұрын
Ndipo wayakhula chilungamo gwilako🤝🤝🤝🤝🤝🤝🤝🤝🤝🤝
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 21 сағат бұрын
Ndipo DK chaka chino akutenga boma ndipo mulungu adzidzimutseni Adani wo kut achite manyazi
@PetrusTlhokwane
@PetrusTlhokwane 20 сағат бұрын
Ndipo DK adzawina sindikukayikilaso ayi naneso
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 21 сағат бұрын
Maboma ambiyomu zithu zikachipa koma chiliweleni chakwela mabvuto 2 much kuiwalaso kuti kuno ndikwathu
@JuliourMussi
@JuliourMussi 9 сағат бұрын
Mulungu atikhululukile chifukwa chimene tikulakhula tikukhala ngat tikunamiza ana
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u 22 сағат бұрын
Iyeyo akudutsa mululu waukulu ngati ifeyo Ameneyo ndi gulukunyenda eti
@MaxwellTilika
@MaxwellTilika 21 сағат бұрын
chakwera osadandaula bola walako kuyendetsa BOMA.... kkkkkkk kumulimbitsa mtima nanga nonse mungomuukira
@johnnyirenda5848
@johnnyirenda5848 21 сағат бұрын
Amafuna azilemeletse Kaye wokha kenako Kupaka mafuta pakamwa Anthu ngati akupanga chilungamo koma Apha Malawi
@MariamLajabu
@MariamLajabu 21 сағат бұрын
Mapwala awo apre
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 21 сағат бұрын
Chakwela is just hiding behind the desk he must come out and face the music.is really understand how John chilembwe fought this country. But he and his mcp ministers he is taking away all of that.here we are now we don't have freedom.
@GiftMitochi
@GiftMitochi 22 сағат бұрын
Chakwera mboro Yako ukauze amako zimenezo.
@NgomaRaheem-k2t
@NgomaRaheem-k2t 21 сағат бұрын
Kod Galu ameneyu akamat zaka zna zubweraz tisangalala akuuza ana? Nyero yake ndithu
@blessingssaiti
@blessingssaiti 7 сағат бұрын
Aaaaaa zawusilu izi anthu kumafa ndi njala kukoza kwake Kuli pati kumeneko
@RajiKassim
@RajiKassim 21 сағат бұрын
Achakwela akufuna ndalama sopangila kapeni chifukwa akungomanga andu 😂😂
@Kamwachale
@Kamwachale 21 сағат бұрын
Achakwera nfi a bodza kwambiri ngati akuti zaka 5 zinali zowongola mafupa asanayanbe kukonza zomwe boma la DPP lidaononga. Nanga bwanji Inu achakwera siimunawapase a boma la DPP mpata WA zaka 5 owongola mafupa omwe boma la mayi Joyce Banda lidaononga
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 22 сағат бұрын
Mizimu ya Anthu anja akukudikilani.....mwatizuza mokwana
@henryphiri6100
@henryphiri6100 22 сағат бұрын
Akuona ngati angapusitse anthu galu ameneyu otchedwa Chakwera, chosangalatsa ndi chiani panopa popeza tikuvutikabe mpaka pano
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 22 сағат бұрын
Chakwerayo akudutsa mu ululu waukulu? M'mene ankapanga campaign 2019-2020 anatiuza kut 5 yrs yake tidzadutsa muululu? Chakwera ndiwe otukwanitsa kobasi....
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 21 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@CassimMeleka
@CassimMeleka 12 сағат бұрын
Galu ameneyu
@LimbikaniTambala-z1y
@LimbikaniTambala-z1y 21 сағат бұрын
Dziko lina liri lonse limakhala ndi malamulo komanso china chimene ndi nganene wina akakulakwira si bwino kubweza koma chimafunika ndi kukambirana. Anthu akumangidwa pena achita kuziyamba dala ndi cholinga chofuna kuipitsa mbiri ya chipani cha Malawi Congress Party.
@SamboRuphan
@SamboRuphan 18 сағат бұрын
Mwapenga
@DeavncKapesi
@DeavncKapesi 20 сағат бұрын
Chakwera pantumbo pako ndithu🙄🙄
@CassimMeleka
@CassimMeleka 12 сағат бұрын
Zoonadi
@HopeMakoka
@HopeMakoka 21 сағат бұрын
Chakwera ukumayankhuratu ngati Mwana wanva
@McDonaldbeketeNkhata-n4l
@McDonaldbeketeNkhata-n4l 21 сағат бұрын
Achakwera kapumeni choti munene kuziko lamalawi
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 21 сағат бұрын
Kodi athu omwe amafuna kupha chisale anawatuma ndindani koma zikuyambikazi ayi iyi ndikhondo one maso anga kwachauta
@WestonRoben
@WestonRoben 22 сағат бұрын
Ukanama sikuchedwa kutcha mawa limafika
@MadalitsoIbrahim
@MadalitsoIbrahim 22 сағат бұрын
Kodi chakwelayu ufiti satanic chani? Angoyankhula zopepela alipheee
@giftkhomani
@giftkhomani 21 сағат бұрын
Kodi paja president uyu dzina lake ndi ndani?😂😂
@mkandawirem610
@mkandawirem610 20 сағат бұрын
Dzina lokhalo dziko lonse chilichose kukwerelatu
@HestingsChibalo
@HestingsChibalo 20 сағат бұрын
😂😂😂😂
@BrieMajoni
@BrieMajoni 9 сағат бұрын
Amalawi tikuseweresedwa ndithu 😢😢😢😢
@HestingsChibalo
@HestingsChibalo 20 сағат бұрын
Koma chomwe ndachiwona tikumupasa matama ndi ife kuti aziyakhula zoduka mutu zakezo chifukwa tikanakhala kuti akamayakhula ife kuseka makutu mwina atasiya
@Yanjanani
@Yanjanani 22 сағат бұрын
Pa chakuti pake asankhe yekha
@lloydchikumbutsochizinga1429
@lloydchikumbutsochizinga1429 21 сағат бұрын
Bwanawa asatupusitse awona kuti zawo zada Iwo adati atipatsa Malawi wokomera tonse osati 5 years yazowawa. Asatitenge ngati tonse ndi ana oti atha kuwanamiza mmene angathere
@PeterMakaika
@PeterMakaika 21 сағат бұрын
Mmmm koma Chakwera umunthu wako uli kt?? 😢😢😢
@JamesJana-z1i
@JamesJana-z1i 22 сағат бұрын
Ambuye akuwona
@HamiltonSachokeraKamende
@HamiltonSachokeraKamende 21 сағат бұрын
Aaaaaaaaaaa koma Boma iliiii!!!!!!!! Yehova musatifulatile
@KelvinBandah-o5v
@KelvinBandah-o5v 19 сағат бұрын
Kodi mudzingomanga nzika zadziko lino Malo mwachitukhko
@PaulNkhata-c3b
@PaulNkhata-c3b 16 сағат бұрын
Chakwera ambuye anamuchotsa pamaso Pao koma mulungu wamoyo sangalole kuti anthu 22million avutike chifukwa chaanthu 1.7 million
@josephalfred5138
@josephalfred5138 21 сағат бұрын
MCP chomwe ikuchita sakuchisziwa
@AleCloset
@AleCloset 21 сағат бұрын
Koma uyu mmati chikangawa yu Pena ngat ndingokuwa kuti zautsiru basi
@AtupereSadiki
@AtupereSadiki 10 сағат бұрын
Chakwera ndilibe Lawyer ine usandiyakhulise pa mbali
@HenryKatopola
@HenryKatopola 10 сағат бұрын
Chakwela wapenga chikangawa😂😂😂😂
@MariamLajabu
@MariamLajabu 21 сағат бұрын
Then go lawo ape woooo
@MusahAkim-p3h
@MusahAkim-p3h 20 сағат бұрын
Kodi ife amalawi chikutisangalatsa ndi chiyani popitilinsa kumulola kupitilinza kulamulira dziko lino, mbuzi imeneyi yalephela enough is enough, president opanda tsogolo uyu.
@HawaHussein-o5k
@HawaHussein-o5k 21 сағат бұрын
Kodi olankhula zotelezi ndio okha nkhani ndi za ndale basi azipani zolamula amalalata koma samamangidwa bwanji?
@GiftChalunda-ss9qu
@GiftChalunda-ss9qu 20 сағат бұрын
Chakwelayu sakuyenela kuzalandila compasation tikamuchotsa 2025
@MusahAkim-p3h
@MusahAkim-p3h 20 сағат бұрын
Aaaaa koma anankhumwawo ndeee palibe iliyonse.
@VioletDambolachepa
@VioletDambolachepa 22 сағат бұрын
Thawi yonseyi anali kut kungofuna kuziphimba akhau
@DOLADAUSI
@DOLADAUSI 22 сағат бұрын
Chiiiiiii😅
@LAZARUSCHAPAMBA
@LAZARUSCHAPAMBA 20 сағат бұрын
Mwanjira yina ndiyekuti a pule athu avomeredza kuti zawakanika kwa zaka zomwe tidawapatsa from 2020. Mwanjira yina akutinyengelera kuti tiwayesenso zaka zina 5 zikubwerazi.😂😂😂
@ChrisEnos-to5uv
@ChrisEnos-to5uv 22 сағат бұрын
Chakwera mbuzi yeniyeni
@MacdonaldMajohn
@MacdonaldMajohn 21 сағат бұрын
Panyapako galu iwe chakwera iwe mfiti kwabasi tikulabe ife dzakodzi sitinadzione
@ResterKabudura
@ResterKabudura 22 сағат бұрын
Bola boma lomwelija la dpp uyu angoonga
@Chancy-ry4tw
@Chancy-ry4tw 21 сағат бұрын
Chakwera is a Joke
@emmanuelnyirenda3289
@emmanuelnyirenda3289 6 сағат бұрын
Utm yachilima sikadapanga umve uwu
@KondwaniChaponga
@KondwaniChaponga 21 сағат бұрын
Kodi achakwera mukuona ngati tinaiwala zomwe munanena mutangowina kumene? Mulungu akuchitireni chifundo
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 21 сағат бұрын
Ngalu ameneyi chikangawa alibiletu Dzelu
@HappyAutumnTrees-cd9ye
@HappyAutumnTrees-cd9ye 21 сағат бұрын
Izi zitha kundichimwitsa kumeneku kuuza ana,,ai km amukhululukire sadziwa chimene akunena,,
@estonmnthali3719
@estonmnthali3719 21 сағат бұрын
Nonsense
@MphatsowisikiWisiki
@MphatsowisikiWisiki 20 сағат бұрын
Kkkkkk zomangan zavuta muchokab this September
@RebeccaChikalenda
@RebeccaChikalenda 22 сағат бұрын
Kma abare zinna
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 20 сағат бұрын
Inuso mulibe manyazi muzawina inuyo akondwan 😂😂😂😂 ayi
@SamboRuphan
@SamboRuphan 18 сағат бұрын
Anakhumwa nanu kagoneni chabe za ziii ...mungamake kwa adad inu
@MeruMitha
@MeruMitha 21 сағат бұрын
kodi tatiwerengerani total number ya ma presidential candidates ndi angati kuli 50 plus 1
@GabrielMzich
@GabrielMzich 22 сағат бұрын
CHIKANGAWA ANAPHA CHILIMA SITIKUNFUNASO
@frankcassim
@frankcassim 21 сағат бұрын
Kukanika kuvomeleza kuti zamukanika
@ChifundoMakuta
@ChifundoMakuta 18 сағат бұрын
Nditukwane?
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 18 сағат бұрын
Chakwera ndiopusa kwambili nden wakoza kapena waononga?
@YohaneMdala
@YohaneMdala 22 сағат бұрын
Koma zoopsa kwabasi
@GiftChalunda-ss9qu
@GiftChalunda-ss9qu 20 сағат бұрын
Iweyo chikangaxy ndamene wadutsa muzowawa koma ife amalawi sitinadutse nawo chauta nda mene amatisamalila
@LottiAffati
@LottiAffati 21 сағат бұрын
koma uyu sinziwa chilichonseyi abale uyutu atilakwitsa mayankhulidwe odalawa
@SilikaMkapu
@SilikaMkapu 19 сағат бұрын
Chalakwe bizy kumanga anthu wasiya umbavawako ukuba ndalama zaboma ulibe nzeru
@petertengani
@petertengani 19 сағат бұрын
Eish. 🤦🏽‍♂️🤦🏽‍♂️.
@StewartBatret
@StewartBatret 21 сағат бұрын
Ululudi zoonazake
@SiphamandlaNcaphayi
@SiphamandlaNcaphayi 20 сағат бұрын
Mwatukwana takumvani koma Boma president ndizomwezi sizikusintha ayi
@SamboRuphan
@SamboRuphan 18 сағат бұрын
Akuvotelani anthu munapha anja,,mukawapeza pa line
@SandikondaIsaac
@SandikondaIsaac 15 сағат бұрын
Uhuu
@MelusiMwali
@MelusiMwali 16 сағат бұрын
Ali busy kuwononga taxpayers money instead of bringing fuel in the country !! Mitu yafa !!
@storytambala6088
@storytambala6088 20 сағат бұрын
Panyopako, Chakwera.
@PetrusTlhokwane
@PetrusTlhokwane 21 сағат бұрын
Bwanji kuti tingomuloza Chakwelayo chizifa chimunthu choipa icho tiyeni tigwilizane a Malawi
@AleCloset
@AleCloset 21 сағат бұрын
Ana achepa.... Njenjenjeee kunjenjemera, adad alowe m'boma..
@MayesoBikefa
@MayesoBikefa 20 сағат бұрын
Chakwera komaso kazi wake ose ugalu wawo atizolowera
@RashidKusum
@RashidKusum 22 сағат бұрын
Panyapake chakwera
@andrewlikoya7302
@andrewlikoya7302 22 сағат бұрын
Mtima suvala sanza
@ChingaipeBoss
@ChingaipeBoss 22 сағат бұрын
Koma akuluwa alibe manyazi
@MatthewKanyenda
@MatthewKanyenda 21 сағат бұрын
Amatamba ndi mfiti
@JafaliAjusa-zg2xi
@JafaliAjusa-zg2xi 20 сағат бұрын
Akuona Ngati Ali kudambwe
@KelvinWaMpozela-r5q
@KelvinWaMpozela-r5q 20 сағат бұрын
Chakwera machende ako ndiweso chisilu kwambili
@RosinaPatel
@RosinaPatel 16 сағат бұрын
Bde afuna zaka zina 5? Zikomo
VIP ACCESS
00:47
Natan por Aí
Рет қаралды 30 МЛН
So Cute 🥰 who is better?
00:15
dednahype
Рет қаралды 19 МЛН
IL'HAN - Qalqam | Official Music Video
03:17
Ilhan Ihsanov
Рет қаралды 700 М.
She made herself an ear of corn from his marmalade candies🌽🌽🌽
00:38
Valja & Maxim Family
Рет қаралды 18 МЛН
Izindaba zesiZulu @13H00 l 08 January 2025
24:08
SABC Izindaba
Рет қаралды 7 М.
VIP ACCESS
00:47
Natan por Aí
Рет қаралды 30 МЛН