Chakwela wavomeleza kulephela koyendesa dziko Koma nduna zake zikukakamiza

  Рет қаралды 8,659

Nthambi Malawi

Nthambi Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 109
@HabiboZimba
@HabiboZimba 7 сағат бұрын
Chipani chamagazi ichi chikukoka posachegwa ❤❤❤❤
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 6 сағат бұрын
Manganya ofupika ndi nzeru zomwe kape wa chabe-chabe
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 12 сағат бұрын
More fire comrade osaopa osatopa osafooka Allah alipo mpaka aturuke basi
@PetroHerman-z5g
@PetroHerman-z5g 11 сағат бұрын
Chikuni chachikulu chimasunga Moto ndi zoonadi amenewa ndi mau akulu kwambili
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 11 сағат бұрын
Chakwela ndi farao😂😂😂😂
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 7 сағат бұрын
Ndipo Pharaoh wake oyipisitsa kuposa Pharaoh wa mu Bible
@VeraChirwa-c5n
@VeraChirwa-c5n 6 сағат бұрын
Taona ma president ife Osati manyaka zi iyaaaaa
@PeterKainga-e3h
@PeterKainga-e3h 13 сағат бұрын
Uku ndiye kuyankhula, chikangawa kwake kwatha
@WilliamMajiwa
@WilliamMajiwa 5 сағат бұрын
Ndiwe wanzeru Mani , ziuzeni mbudzi zaku MBC
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 11 сағат бұрын
Awona tayika Mulungu wathu patsogolo atimenyera nkhondo tili chete
@HendrixChaputa
@HendrixChaputa 16 сағат бұрын
Ineso Manganya sindimamuona Bwino😢😂...
@Maxielyies
@Maxielyies 16 сағат бұрын
That's the definition of talking the truth
@AllieMwedini
@AllieMwedini 12 сағат бұрын
Yes a mcp mbolo zao
@FavourAmos-rx5fl
@FavourAmos-rx5fl 10 сағат бұрын
Well explained
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
Thanks
@VeraChirwa-c5n
@VeraChirwa-c5n 6 сағат бұрын
Zakukanikani abusa achakwera .just accept
@LissaNezala
@LissaNezala 12 сағат бұрын
Ndipo ineso or chakwela waononga dziko Koma naa manganya yokha eish amandinyasa ndipo or ndimamuonela chabe poti ndimaso amaona
@CricyHaroon
@CricyHaroon 7 сағат бұрын
Chakwela walephela
@cmsanyama200
@cmsanyama200 16 сағат бұрын
Ndiye zimadanatu ndikuziuza chilungamo kuteroku ziyamba kukusaka
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
Kkkkkk azisaka okha
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 16 сағат бұрын
Kupha chilima adapanga mistake yayikulu infa idawawa ija bro 😢
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 6 сағат бұрын
Ndipo chi mistake cheni-cheni Chakwera galu wachabe.
@JamesPhiri-h7p
@JamesPhiri-h7p 9 сағат бұрын
Inde nzanga iwe u kunena zooona
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o 9 сағат бұрын
Zoonad big apakile chikangawayo
@EthelKspito
@EthelKspito 13 сағат бұрын
Ndpo tiwapasa thawi adad mopanda mademo ndpo wa MCP asazayelekeze kuti eeehhh APA simukulondola cz dziko mwaliononga kuti APM kuti abwenzelese pomwe rinali dziko lathu it's not easy
@VeraChirwa-c5n
@VeraChirwa-c5n 6 сағат бұрын
Chikangawa akalamulire ku kasiya basi
@jonathanmbewe4246
@jonathanmbewe4246 11 сағат бұрын
😂😂😂😂😂kamajekete chigawenga chachabechabe
@daviechannel8603
@daviechannel8603 13 сағат бұрын
Good b,ale wanga ukhale siku labwino
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 7 сағат бұрын
Thanks
@FaizalKhan-gx8eg
@FaizalKhan-gx8eg 11 сағат бұрын
Chonena ndilibe ine mulungu 😂
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 12 сағат бұрын
Ngati alipo amene akuti Chakwera mcp yalamula bwino 5 years ameyo ndi galu ndikanyimbi onunkha daily
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
😂😂😂😂😂
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 6 сағат бұрын
Ndi zitserekwete zonse za MCP
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 6 сағат бұрын
@ ndipo mbalame zeni zeni
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 6 сағат бұрын
@@Nthambi-zg4nu Ndipo pa 16th September pakuchedwa
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 6 сағат бұрын
@ ndipo fumbi kobooo
@bonwelllinyenga871
@bonwelllinyenga871 11 сағат бұрын
Inu mwafotokoza Zoona zokha zokha
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 7 сағат бұрын
Thanks
@alexsumani6823
@alexsumani6823 16 сағат бұрын
Ulemu wanu basi anthu amenewa atizunza mokwanira bwino
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 7 сағат бұрын
Mau Brother.....👏👏👏👏❤❤❤
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 7 сағат бұрын
Thanks
@isaaczuze
@isaaczuze 13 сағат бұрын
My vote is Apm osati mbuzi iyi akuti chakwera ....waononga ziko ......taonani njala nanga kusowa kwa mafuta ......chakwera ndi munthu wolephela ....ineyo ndiye sindingavotele chisilu ine ayi ...chakwera ndi mbuzi ya munthu
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 14 сағат бұрын
Joyce tidzinena cilungamo zinavuta ndi kashigetiyo basi koma zonse zinali bwino. Kasakula ndi mbuzi ya munthu tisadandaule cake cino mbc yonse tiphasula, wina afune,usafune yemweyo nkhalambayo ndiyemwe timvotele caka cino APM ndiyemwe tagwilizana a malawi kuti tivotele ndikakhala ine ndi a zangawa tingodikila kulumbilitsa cifukwa awina kale program sikusintha. Comrade tili pambuyo panu mcp ipakile palibe ca mzeru ciliconse akucita olo amange a dpp sizisintha kanthu angotaya nthawi panopa kafukufuku wawonesanso kuti dpp 1, utm 2, udf 3, cikangawayo ali pa 5 cifukwa no 4 ndi aford mwaona! 💙💙💙💙💙boma, APM boma,DPP oyee! Caka cake ncino Adad boma! Comrade takunyadilani cifukwa cowauza a malawi chilungamo
@AdamJames-x7x
@AdamJames-x7x 15 сағат бұрын
ndipo thawi ikubwera , zinsinsi zonse zizabwera poyera one day is one day ,
@BanetLuka
@BanetLuka 16 сағат бұрын
Zoonadi bro more fire !
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 15 сағат бұрын
Manganya simunthu wabwino ndipo Chilima uja anapanga mistake kumutenga Manganya ngat vice wake.
@mabvutomichaelpanagona1949
@mabvutomichaelpanagona1949 15 сағат бұрын
George kasakula ndi chitsiru kwambiri ngati pali dzitsiru dza dzitsiru ndi George kasakula ndi ombwambwana
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 10 сағат бұрын
CHAKWERATU AKUDZIWA KUTI ZINTHU SIZIRIBWINO NDIPO MOYO WAKE ULI POFUNA KUPANGA RISING KOMA ACHINA CHIMWENDO NDAMENE AKUMUNAMIZA
@ernestphiri5507
@ernestphiri5507 16 сағат бұрын
Chilungamo chimenechi brother
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
Thanks
@SannahAbdulAzizi
@SannahAbdulAzizi 13 сағат бұрын
Mwana watembo achoke palibe UDF kusakanikezana ndi MCP olo atati faila Doom mkamwa sizingatheke
@alexsumani6823
@alexsumani6823 16 сағат бұрын
Munthu wake ndi Kasakula mpala uli nyezi nyezi ndi misonkho ya a MALAWI 😠😠
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
Kkkkkkk
@ishmaelimedi7363
@ishmaelimedi7363 4 сағат бұрын
Well said sir,,,, zomba maximum ndende yamanganya
@phillgatoma4857
@phillgatoma4857 6 сағат бұрын
Dzoona Brazz Auze akunama Anthu woopi kwambiri
@mariawachesterweluzan
@mariawachesterweluzan 7 сағат бұрын
Zoona atsogoleri ❤❤❤❤❤
@rashidadan2533
@rashidadan2533 13 сағат бұрын
Kuchoka ndikuchoka basi , mcp ikuchoka mopanda chikaikiso , ndipo ngati ndilimoyo ndizaonesesa kuti mbava za mcp zonse zikafele kundende without mercy .
@jumaatibu787
@jumaatibu787 3 сағат бұрын
Amwene mwatiankhurira bwino zikomo kwambiri ndithu
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl 5 сағат бұрын
Ndipo ineso ndikudikiraso kut kod azizati chani pa campaign😂😂 anyatu amenewa ohooo asiyen
@daviechannel8603
@daviechannel8603 13 сағат бұрын
Ndipo inu zoona chimwene wanga ambuye akufungatileni ndip Dpp ndizipani zina zikanagwilizana kt apange chimodzi agwese ng,onayi ndipo kodi nyamatayo akupanga chani
@daviechannel8603
@daviechannel8603 14 сағат бұрын
Ubwino wake pitala yo samamanga anthu
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 14 сағат бұрын
It's madness R70,000 a bag of maize it has never been happen in the history of malawi poor leadership.
@JoshuaJumah-l4n
@JoshuaJumah-l4n 2 сағат бұрын
Kkkkkk mwayakhulatu tikumane kuseriku
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 7 сағат бұрын
Alephera or kubera sangathe attaaa
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 6 сағат бұрын
Awuze Brother amvesetse, manganya amawoneka maso mwa!! mwa!! mwa!!
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 9 сағат бұрын
Lero fertilizer akwezao kagoneni ma shop ati chithupsa aphulisachakwera mfiti ya cha be chabe
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 12 сағат бұрын
Akuyesera zida km akunama tu achakwera
@pilirani3536
@pilirani3536 12 сағат бұрын
Eya tinawanva aku ena kuti akugwila ntchito kwa falawo
@SannahAbdulAzizi
@SannahAbdulAzizi 13 сағат бұрын
Zowonadi manganya akudziwapo kathu
@GladysMagadi
@GladysMagadi 4 сағат бұрын
😂😂😂😂😂 zakazinazo ampase ndiambuyake
@FracksonMadani
@FracksonMadani 16 сағат бұрын
Eeeee koma Chilima mhuuuu😭😭😭😭😭
@SannahAbdulAzizi
@SannahAbdulAzizi 13 сағат бұрын
Kkkkkkk umakwana osaopaa
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 7 сағат бұрын
Thanks
@HarryThomson-n7n
@HarryThomson-n7n 10 сағат бұрын
İwe nawe wauza zoona awa ndipo wauze avese
@EmmanuelSambani-g2g
@EmmanuelSambani-g2g 15 сағат бұрын
Eeeee bro mwayakhula momveka bwino zedi ndipo mfundo zanu zamphamvu ine pambuyopo basi.
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
Thanks
@MartinNgoma-tp2jk
@MartinNgoma-tp2jk 15 сағат бұрын
Koma kulankhula kozindikila adaseka njila muulungu akuona basi apite ameneyo
@paulpaseli6310
@paulpaseli6310 17 сағат бұрын
Ulamulilo omwe sitingaufuneso ndi yachakwela. Eeee chakwela watizuza kupha athu.
@JohnPhiri-t2r
@JohnPhiri-t2r 13 сағат бұрын
😢m'bare fetereza ndi mk 117000
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 7 сағат бұрын
Iiiii wafikanso pamenepo
@JazzimBrothers-ml5np
@JazzimBrothers-ml5np 6 сағат бұрын
Fact about this story ❤❤❤
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 3 сағат бұрын
Awuze agalu amenewa athu oipa kwambili
@MariamMwalabu
@MariamMwalabu 17 сағат бұрын
Mau bro
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
Thanks
@WilsonFelix-j9n
@WilsonFelix-j9n 14 сағат бұрын
Aise ndakukonda kwambili iwe ndi mmalawi weniwenidi
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 7 сағат бұрын
Zikomo
@yusufbakali
@yusufbakali 6 сағат бұрын
Akasakura
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r 9 сағат бұрын
Akunena kuti chakwera akuziwa kuyendesa ziko chifukwa iwo amufasira kumupusisa ndipo iwo alemera azanong, one za bondo kumaso kutakuyerani chakwerayo
@FracksonMadani
@FracksonMadani 16 сағат бұрын
NPK 126pin😂😂😂
@JohnNyowani
@JohnNyowani 3 сағат бұрын
Tizapanga mademo kuti APM asachoke pa mpando u t m Afford DPP moto kt buuuuuuuuu
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 12 сағат бұрын
Well spoken
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
Thanks
@BrianKaila
@BrianKaila 16 сағат бұрын
Amen
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
Thanks
@emmanuelchikowi8786
@emmanuelchikowi8786 14 сағат бұрын
More fire
@khwimaBanda-s3u
@khwimaBanda-s3u 13 сағат бұрын
kwa ine ndikuona kut amalawi tikana choka ku udf mcp dpp akuziwana kuba kwao pazipan ndanenaz tikana thawako kuyesa ena ndikunena maganizo anga kaya anzanga dziko lathu si likumasuka pa osewa alamula wa amapanga tibwino tochepa nkumaba chuma chambili
@isaaczuze
@isaaczuze 12 сағат бұрын
Za ziiiii
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 14 сағат бұрын
I like this man❤
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 7 сағат бұрын
Zikomo
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 11 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂 Good
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 12 сағат бұрын
Akupanga dala zonsezi
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 9 сағат бұрын
Eeesh
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 15 сағат бұрын
Zoona zake big
@Nthambi-zg4nu
@Nthambi-zg4nu 10 сағат бұрын
Thanks
@johnlameck8366
@johnlameck8366 14 сағат бұрын
😅😅😅 paka mapazi ake kkkkkkkk
@alickmathias2097
@alickmathias2097 12 сағат бұрын
Eya tikamuvotelabe
@francismungu7749
@francismungu7749 15 сағат бұрын
Madela ena chimanga chafika 85
TIKUDZIWENI WITH ANTHONY MAKONDETSA - 5 August 2019
30:45
Times 360 Malawi
Рет қаралды 57 М.
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН
Enceinte et en Bazard: Les Chroniques du Nettoyage ! 🚽✨
00:21
Two More French
Рет қаралды 42 МЛН
Support each other🤝
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 81 МЛН
KULINJI ? | 14 JANUARY 2025
58:23
Malawi News Update
Рет қаралды 2,8 М.
Cde IB Dhlamini
1:13:44
Swazi Voice Of The People News
Рет қаралды 2,5 М.
Sh Abdirahman Bashiir "Side Uga Fa'idaysana Waqtika 2025"
55:30
Xogmaal Media
Рет қаралды 49 М.
Ngozi Ya Ku Chikangawa Tikufufuza Tokha   Samuel Lwara
17:07
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 300
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН