CHAKWERA AMUDZUDZULA KUSELIKU LIMODZI NDI CHIPANI CHA MCP

  Рет қаралды 3,316

Malawi Extra

Malawi Extra

Күн бұрын

Пікірлер: 53
@Chikwawa
@Chikwawa 3 сағат бұрын
Ife a UTM tivotera dpp.
@AhmadIsmael-l5q
@AhmadIsmael-l5q 2 сағат бұрын
mcp ndichipani cholephela kuchokela kale mcp isazinamize ife tonse tivotela dpp dpp dpp basi nothing else
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u 2 сағат бұрын
I greed with you True spoken Misewu sitingadye Olo atamanga ngati kwa america simungawine Anthu akufuna chimanga ndi fertilizer,zipangizo za kumunda ndiye munkhoza kuwina
@IsaahLobern-x2u
@IsaahLobern-x2u Сағат бұрын
Wayakhula zanzeru bro
@AhmadIsmael-l5q
@AhmadIsmael-l5q 2 сағат бұрын
inu dpp sugar 500 kwacha fertilizer 18.000 nchele unali otchipa chimanga chinali chotchipa ife amalawi tonse tivotela dpp kufuna osafuna ife bolani dpp
@MattinGold-l9w
@MattinGold-l9w Сағат бұрын
Am agree with you
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 2 сағат бұрын
Kodi inu, ena nanu or mukuti ndi a chakwera mukunena zoona dziko li likuyenda bwino, tamawopa Mulungu inu, chakwera ndi munthu wolephera kwambiri, kuba, kupha, kumanga anthu, osalakwa, a comrade inu Mulungu wathu, akudalitsen powawuza chilungamo. awa, anthu osavawa, anthu sakuwafuna, awa, God bless bro
@mercymalenga1884
@mercymalenga1884 8 минут бұрын
Amen brother
@stuartsangaloti8461
@stuartsangaloti8461 2 сағат бұрын
Very true much respect
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g 48 минут бұрын
Ulibe zelu mbale wanga
@mabvutomichaelpanagona1949
@mabvutomichaelpanagona1949 2 сағат бұрын
Koma mwayankhula mau ogwira mtima zikomo kwambiri
@RoseKapalamula
@RoseKapalamula Сағат бұрын
Awuuuze amvesese
@TimothyNkhutembaChirwa
@TimothyNkhutembaChirwa Сағат бұрын
Tavulala A Malawi kwambila kuba to much Mcp
@SaidiMtira
@SaidiMtira Сағат бұрын
Komatu chakwera ndi bale wanu, m'chimwene wanu weniweni. Musavere manong'onong'o. Asatana. Ameneyo ndidani wanu owonekera. Muzilankhura moganizirana
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 сағат бұрын
Powerful speech auze brother
@BrazioNtondo
@BrazioNtondo 19 минут бұрын
Komatu munthu uyuyu, akuyankhula chilungamo akuluakulu.Mutatenga malangizo awawa Zitha kukuthandizani achina Kunkuyu
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb Сағат бұрын
Umakwana bg man zoona zake osamubisa chikangawa
@JosephChatha
@JosephChatha 7 минут бұрын
Voice
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi Сағат бұрын
Anthu wozungulira mutu kuti boma ndilomweli 😅
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 42 минут бұрын
Akamuna chilungumo chimamasula awuzeni.
@MayesoBikefa
@MayesoBikefa 17 минут бұрын
Mau amenewo pa ground sipali bwino
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 19 минут бұрын
Boma ili kuba ndi kupha basi ndi chomwe akuziwa
@EvasiJafali
@EvasiJafali Сағат бұрын
Ausilu ameyo sakusiwa chimene akupanga
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 минут бұрын
Ndipo uyu awona saona vote oloko imodzi
@DixonChimanya
@DixonChimanya Сағат бұрын
Uthenga wabwino kwambiri Anthu akumudzi pali pamavuto kwambiri
@PortiaDaveson-f8u
@PortiaDaveson-f8u Сағат бұрын
Awa akunama kwambili amalawi akumaona
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 32 минут бұрын
Akunamiza ndi Chimwendoyo
@AhmadIsmael-l5q
@AhmadIsmael-l5q 2 сағат бұрын
chakwera and mcp adeliver machende pantumbo
@RaffickAllie
@RaffickAllie 45 минут бұрын
Tangopereka # ya mpamba or Airtel Dollars.warankhura zibambo uyu guys
@JohnMalikebu-v5y
@JohnMalikebu-v5y Сағат бұрын
Ukumva kupweteka ndi iweyo uchedwa ndi mzere wadawe,Boma ndilomweli
@BrightZionga
@BrightZionga 40 минут бұрын
Komano inuyo a John kunena zoona munthu uyu wanyoza kapena wangonena zomwe zikuchitika? Wakamba mopanda mbali ngakhale DPP waikamba umunthu wanu udachoka eti tiziti kwanuko anthu akunjoya ndimmene zinthu zilili you must be ashamed of yourself
@khasimMusa-d3w
@khasimMusa-d3w 2 сағат бұрын
Mulungu akudarisen uthenga wabwino kwambili mulungu azisalilani amwene
@RoseThindwa
@RoseThindwa Сағат бұрын
Zoona n boma ili likuononga dollar kugula anthu ,kuba Malo mopanga fix mavuto ochuluka mdziko lathu
@SaniJonathan
@SaniJonathan Сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂 awuzeni
@emmanuelmukondia3568
@emmanuelmukondia3568 2 сағат бұрын
Mtima wakuphweteka .UDF is a party with peolple.
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 24 минут бұрын
Ndipo live mawu abwino awa
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 2 сағат бұрын
Manganya ndi wa chipani chake chimanchedwa kuti wodya zake alibe mulandu ndie chipani chake Manganya
@AdizzMadizo
@AdizzMadizo 2 сағат бұрын
Awuzeni sakuziwa amenewo
@AlexanderKamanga-i2l
@AlexanderKamanga-i2l 2 сағат бұрын
Chakwela simunthu
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 3 сағат бұрын
Kodi APM.akalowa m'boma sadzayambiranso nkhanza zakezo zija ankapanga zija **ngqti akupanga Holy Jihad"?
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 2 сағат бұрын
Palibe wabwino padziko pano sure
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 3 сағат бұрын
Ife DPP yi ikutipatsa maganizo a àMalawife tonse..tatopa nazo izi .APM anaphunzira nkhanza ku India chifukwa mkazi wake woyamba amene anabereka naye ana awiri aakazi.aja ..Peter ÿo anaphunzira nkhamza za Asilamu .muhamadan Holy Jihad.crueties .in Africa historically
@ZaidDaiton
@ZaidDaiton 2 сағат бұрын
Mmmm ndiye kuti chani?? Zopanda nzeru basi.
@UseniMailosi
@UseniMailosi 2 сағат бұрын
Inu kumayangula bwino mn nkhasa sachakwela olo satana akuchepa paka kupha chilima yemwe anakanga kuti alowe m boma
@spargomw
@spargomw Сағат бұрын
Nanu mwalemba ma comment awiri koma opanda nzeru. Kutenga thelere kuthira mu Thobwa. Lembes sms imodzi yoti tive
@ThandiShandu-l6w
@ThandiShandu-l6w Сағат бұрын
Osapanga chako chipani udzapange utsiru wakowo azako alipa ground iwe basi unyani awine asawine vuto ndilako alemera kaya Kadett moyo kuwawa ndiye tikuti bomaaa ndilomweli ndipo sitikusintha secure our brothers alubino
@DysonTummiesSajiwa
@DysonTummiesSajiwa 2 сағат бұрын
Enafe ndi a chakwela ndipo muva ukweche chaka chino
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 сағат бұрын
Crocodile ndi muthu Oyipa kwambili ngati idya amin
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 сағат бұрын
Sakufunikaso kuyendesa dziko basi angoba ndi kupha basi zimenezo ndizimene amaziwa crocodile
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 сағат бұрын
Komaso miseu akumanga ndi achima urereso basi
@HannahNtenda
@HannahNtenda 2 сағат бұрын
Mmmm inu Chakwela akukupatsani chani?tikuvutikila limodzi apa akukugailani ndalamazo dololo
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 20 минут бұрын
Mbunzi yamunthu imeneyo ikumvutikaso kwambiri namapwala ameneyo
@RoseThindwa
@RoseThindwa Сағат бұрын
Zoona n boma ili likuononga dollar kugula anthu ,kuba Malo mopanga fix mavuto ochuluka mdziko lathu
SABIN MURUNGI ASUBIJE ABAMUKUNDA BYA NYABYO|ISIMBI TV 01
1:01:48
黑的奸计得逞 #古风
00:24
Black and white double fury
Рет қаралды 17 МЛН
This mother's baby is too unreliable.
00:13
FUNNY XIAOTING 666
Рет қаралды 39 МЛН
Liberal Hypocrisy is Fueling American Inequality. Here’s How. | NYT Opinion
14:21
Visiting NSCN Unification war Cemetery at Dimapur
6:26
Wangyen Vlog
Рет қаралды 152
Funeral service of former Minister Tito Mboweni
SABC News
Рет қаралды 8 М.
How Israel Eliminated Yahya Sinwar#israel #yahyasinwar
9:37
AiTelly
Рет қаралды 1,2 МЛН
How the Most Elite Spy Agency Operates
22:42
Newsthink
Рет қаралды 1,9 МЛН