I greatly appreciate your awesome collection 🙏🙏🙏🙏 keep em coming bwana
@HopefulCoralReef-tx4vxАй бұрын
Ili bwino ndithu ❤❤❤
@FREEZOOM.128 күн бұрын
Zabwino zosse boss koma ndimafuna kungokudziwitsani Kuti channel yongoika nyimbo za anuwake a KZbin salipila mwina zikhoza kungokuthelani nthawi, sindikuti muleke ai koma mubakhala mukudziwa basi mwina mungayambe kutaya ntawi 🎉❤
@a1electrical82128 күн бұрын
Ife bwana sitifuna chuma from KZbin, timaziwa ndondomeko yakuti munthu apeze ndalama from KZbin. Ife tisiye kuvina nyimbo za kale pano chifukwa chowopa kutaya nthawi? Nanga poti oyimbawo amaimba kuti titaye nthawiyo pomvera ndi kuvina nyimbo zawo. Komanso ndiyetu tilipo ambiri amene tikutaya nthawiiyo, including inuyo bwana. Nanga m'ma video onse ali pa channel yanuyi ndi anu?. Kapena mwalandira kale chuma from KZbin? Ngati pali nyimbo yanu, ya achibale pa channel yangapa or ngati muli ndi ma copyright infringement claims, mukhoza kunena, tiyichotsa.