CHIPANI CHA UTM SOPANO CHAKONZA KUTI CHIFINYE MANGANYA ~ NDE APANGA MOTANI?

  Рет қаралды 13,436

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 12
@MerryWayson
@MerryWayson 2 күн бұрын
❤❤❤❤❤ mumaipasira bwino nkhani kkkkk
@DuncanBanda-r9l
@DuncanBanda-r9l 2 күн бұрын
Usi ndi mthira kuwiri ndipo asapezekeso akugwiritsira katundu aliyense wa utm komanso atha ngati katani ndipo ndi mbuli pa ndale akulimbikira mtunda opanda madzi
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 күн бұрын
Delays has destroyed many things in utm including the coming out from tonse alliance which resulted into chilima s death. Usi was almost be fired in early days but its not too late to fix the party.
@IyshaBakali
@IyshaBakali 3 күн бұрын
Achedwetsa kumuchotsa palibe wamkulu kuposa chipani Ausi asamatenge anzawo ngati zitsilu
@MikeTwaibu-i1h
@MikeTwaibu-i1h 2 күн бұрын
Usi ali ndi vuto, ndi wa nsanje osamadya zake bwanji , mulandu wa usi ndi kudya za mzake
@MosesTangwe
@MosesTangwe 2 күн бұрын
Ka usi ndikopatsa manyazi kwambiri
@RaphaelKweve-u5s
@RaphaelKweve-u5s 2 күн бұрын
Usi ndi Ogiya wa Chikangawa Party
@DixonChimanya
@DixonChimanya 2 күн бұрын
Usi ndi kape
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 2 күн бұрын
Manganya nfiti ya munthu iyi
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 2 күн бұрын
Usi anaoneka shasha kwambiri chifukwa usi anadziwa kt chipani chagulitsidwa
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 2 күн бұрын
Mukulimbana ndi usi second person adzadya pension mpaka kufa inuyo mukagwira tchito akakudulani mtsonko azikadya ndi usi mufune musafune
@TakalaniGlenda
@TakalaniGlenda 2 күн бұрын
Akaswiriwo akamba zakafukufuku atumidwanso ndi MCP awona kuti ma concerned leaders of church ojiya aja alephera😂😂😂
Michael Usi - Akanaziwa sakananena izi
5:36
Malawi Top Talent
Рет қаралды 17 М.
So Cute 🥰 who is better?
00:15
dednahype
Рет қаралды 19 МЛН
Qualification ya nduna yasanduka beansness 🫘 m'boma la Chakwera
8:58
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 19 М.
DPP SENDERA SISTERS, AKUFUNA NDANI
4:03
nyimbo zama choir
Рет қаралды 57 М.
Nkhani Madzulo | 2 JANUARY 2025
20:16
Malawi News Update
Рет қаралды 710
ACHAKWERA AWAZUZULA PA ZOMWE APANGA__2 January 2025
15:08
HOT 265
Рет қаралды 10 М.
Sameer Suleman - Kwake kwatha
24:34
Malawi Top Talent
Рет қаралды 10 М.
BON KALINDO LERO KUING'ALULA __1 January 2025
18:04
HOT 265
Рет қаралды 70 М.
So Cute 🥰 who is better?
00:15
dednahype
Рет қаралды 19 МЛН