Takumvani pastor Moses Shumba.May the Almighty God bless you
@saidimwanyali89695 күн бұрын
Atupele ndi tsogoleli wabwino anawawaza anthu akalembese sopano funso ndilakuti mukawafookesa anthu lelo mukwawusa Kuti akalembese kalembila Ali kumapeto
@AgnesNjikho5 күн бұрын
Ndipo amupweteka chifukwa amarepheresa anthu muzenena zawo atukwana pano akt kalembesen nthawi yantha ndiye piter yo akavotera ndichiyani poti salembese
@chipilirolikatho35725 күн бұрын
Who is Ntanyiwa munthu ongokhalira kubisala, bwanji sabwera poyera, zomwe amalankhula ndi maboza okhaokha, inunso a Shumba ndinu m,busa wachinyengo, Mulungu salowerera zandale za ma ulamuliro adziko lapansi ndi za satana, inuyo ashumba ingolowani politics
@gilamwelekedwa48895 күн бұрын
😂😂😂😂😂 you discouraged your voters not to register how do you expect to win this election? Do you know this poll was just an example that was taken by barometer and was taken by only 1000 people? mukanadziwatu poyambilira pompaja mu August a MEC akuyamba kulembetsa anthu muja ma voters munakamalakhula chonchi but munachultsatu mantha kwa anthu anu ovotera a AMP .panopa Munthalika yo sangawinenso pepani kwambiri 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😂😂😂😂😂