Clement Kahiya - You shall surely die

  Рет қаралды 4,359

Charles Shonga

Charles Shonga

Күн бұрын

Пікірлер: 19
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 Жыл бұрын
Very powerful sermon indeed he's given that gift from above our heavenly father.May God bless and protect him
@yaobleestelle2513
@yaobleestelle2513 6 жыл бұрын
40. Abale a ku Africa, Asia, Europe ndi America! Inu mwina munali kuyembekezera Uthenga wa Mateyu 25:6 mwinamwake mu dziko lanu koma Mulungu anachita izo mosiyana. Kumbukirani Ambuye wathu Yesu Khristu! Pokhala mkulu wa ansembe Melkizedeki, achirabi ndi alembi anaona kuti Iye adzachokera ku fuko la Levi. Koma Iye adachokera ku fuko la Yuda. Ndiye, Uthenga Wake ndi ntchito Zake zinatsimikizira kuti Iye anali Mesiya. Ndipo lero pa nkhope yonse ya dziko lapansi, ngati iwe uli mwana wa Mulungu, malo ako awa ali pano ndi m’neneri wa nthawi yako, M’neneri Kacou Philipe. Ndipo amene ali ndi makutu akumva amve.
@nouratana6463
@nouratana6463 6 жыл бұрын
Ndipo lero pa nkhope yonse ya dziko lapansi, ngati iwe uli mwana wa Mulungu, malo ako awa ali pano ndi m’neneri wa nthawi yako, M’neneri Kacou Philipe. Ndipo amene ali ndi makutu akumva amve.
@lydiebayard3812
@lydiebayard3812 6 жыл бұрын
8. Uthenga uwu ukunena kuti bungwe la mipingo ya dziko lapansi, mabungwe a mipingo, mayanjano, migwirizano, zitaganya ndi migwirizano ya mipingo ... Chikatolika, mipingo ya chilamulo chakale, mipingo ya Chimethodisti, Eckankar, timagulu ta Horus, mipingo ya Chiluthera, mipingo ya Chianglica , Mahikari, mipingo ya Chibapiti , chi Rosicrucian, chiNazarene, chi Scientology, chi esotericism, mipingo ya chi Anabapiti, chivuduu, mipingo ya Chiadventi , makampani a yesu, mamishoni a chi Emmau, chi Inner Life, mboni za Yehova, mboni za Yesu, mipingo ya chi Foursquare. 9. Chipembedzo chotchedwa Freemasons, mipingo ya Chipentekositi, kulambira milungu ya Inca , mipingo ya Chipurotesitanti, chi Krishna, mpingo wa chiKhristu, kusinkhasinkha kwa chi transcendental, za chi Grail, aza mizimu, mipingo ya chiEvanjeriko, chiMormon, chiGuru Maharaja, Chisilamu ndi Chiyuda ndinso yonse mipingo yotchedwa yobvumbulutsidwa ndi yobwezeretsedwa ...misasa yopemphera, nyumba zokumanirana amuna, zokumanirana azimayi, mamishoni ndi mautumiki kuphatikizapo a Achibranham, uku ndiko kunena kuti, anthu amene adakali akutsatira Uthenga wa William Branham, ngakhale mu chiyero chake chonse, ndi puligatorio ndiwo makoka a Satana, otumizira anthu ku gehena ndipo mizimu yomwe imatumikira mumipingo imeneyi si Mzimu Woyera, koma ziwanda zodolola. Mizimu imeneyi ndi ziwanda zimene zinali mu mitsinje, zinkapezeka m'madzi, zigoba, vuduu, nkhalango ndi mitengo yopembedzedwa, zikhalidwe ndi miyambo ndiponso ndi imene inaukitsa ansembe a nsupa achikhalidwe.
@sallyouattara8390
@sallyouattara8390 6 жыл бұрын
33. Kuyambira ku kam’badwo kwa kam’badwo, Choonadi nthawi zonse chimakhala ndi m’neneri wam’thenga m’modzi wamoyo pa dziko lapansi. Iye ndi yemwe amakhala ndi mafungulo a Ufumu; Iye ndiye yemwe ali njira, choonadi ndi moyo mu nthawi yake. Ndipo pamene inu mutsegula Baibulo, inu mukuwona Yesaya, Yeremiya, Amosi, Ezekiele, ndi zina zotero. Iwo ndi mayina a aneneri. Choonadi, chimakhala ndi m’neneri wam’thenga wamoyo, osati mu mpingo. Koma kodi inu mumachita chiyani ndi Baibulo lomwe liri m'manja mwanu? Ngati sichoncho, kodi inu mumamupita kumpingo chifukwa cha chipulumutso? Ndipo komabe, ngati Mulungu apulumutse wa chibapitisiti, wa Chipentekosite, membala wa mpingo wa chitsitsimutso kapena wa assemblies of gods, Iye ndiye angathe bwanji kutsutsa Afarisi, Yudasi ndi Kaini? #ProphetKacouPhilippe #PKPCHANELTV
@alimakone961
@alimakone961 6 жыл бұрын
#ProjetKacouPhilippe Mawu Achiheberi kwa m’neneri ndi nabi, mawu awa akuyimira: “woyankhula”, osati ochita zozizwitsa kapena wonyamula kudzodza koma wolankhula. Inu mukuwona? Mneneri wam’thenga ndi chikhumbo ndi chiwonetsero cha Mawu a Mulungu mu kam'badwo Kake.
@leblancdegesco8321
@leblancdegesco8321 6 жыл бұрын
#prophetkacouphilippe PKP CHANNELTV 1. Ine ndikufuna kulalikira pa phunziro: utumiki wa m’zimayi. Choyamba timazindikira kuti Mulungu adalenga mwamuna pa tsiku lachisanu ndi chimodzi komanso kumapeto ndipo panalibe mkazi. Ndiye Iye anapumula pa tsiku lachisanu ndi chiwiri, momwe ife tiyenera kumawona zaka ndi zaka. Ndipo, pakuwona kuti mwamunayo ali yekha, Mulungu adaganiza kupanga womuthandiza. Apo ayi, mu dongosolo lapachiyambi, Mulungu sanapeze kuti chinali chofunika. Ichi chili chifukwa chake kuwerenga bwino kwa Genesis 2:18 kuli: "Ndipo Ambuye Mulungu anati: Sikuli bwino kwambiri kuti munthu akhale yekha; Ndidzam'patsa iye wothandizana naye mwakufuna kwake." 2. Kotero mkaziyo sanali mu dongosolo lapachiyambi la Mulungu koma iye ndi chochokera kwa mwamuna. Agalu aakazi, nkhuku ndiponso zazikazi zina ndizo zolengedwa zoyamba za Mulungu, koma sizili choncho ndi mkazi. Icho chili chifukwa chake, mu mtundu wa nyama iliyonse, kukumana kumachitika mu nyengo yobereka, mosiyana ndi munthu. Ndipo inu simudzawona galu akukwera chachikazi chamimba. Inu mukuwona? Izi sizili choncho mwa anthu. Ngakhale mayi wachikulire amene anasiya kusamba kale iye amakhalabe ndi ubwenzi wa kugonana. Inu mukuwona? Chifukwa chake ndikhoza kunena mwaulemu kuti mkaziyo ali wotsika kwambiri mu chilengedwe. 3. Ndipo Mulungu mwiniwake wamuika iye pansi pa ulamuliro wa mwamuna. Kotero, pamene iye sali pansi pa ulamuliro wa abambo ake, iye amakhala pansi pa ulamuliro wa mwamuna wake. Bambo ake kapena mwamuna wake ndi amene ali ndi ufulu wothetsa malumbiro. Onani Numeri 30 ... Inu mukuona! Ndipo Ambuye Yesu Khristu sanabwere kudzachotsa zinthu izi. 4. Momwemo ife timamvetsetsa, malinga ndi Genesis 2, kuti mkaziyo panalibe pamene Mulungu anapereka malangizo kwa Adamu m'munda wa Edene. Pali chifukwa chake! Panalibe pomwe Adamu adazitcha nyama, mbalame ndi zina maina! Inu mukuwona? Mulungu adachita izi zonsezi kuti mkaziyo adzindikire modzichepetsa malo ake. 5. Ndipo poyankhula za utumiki wake, ngati munthu sanabwere padziko lapansi kudzagwira ntchito ngati Yudase Iskariote, sangathe kuvomereza mkazi pa guwa; Ndipo ngati wina si mbuzi, wobadwa kudzanyengedwa, sangakhale pansi kuti amvetsere mkazi akulalikira kapena kusogolera kuimba panthawi imene amunawo ali pamenepo! Ngakhale iye atayigwira iyo bwino, ndi mdiyerkezi amene amakhala ali kumbuyo kwake. Chikhalidwe mwachokha chimatiphunzitsa ife kuti mkazi sali wonyamula kwa mbewu. Choncho iye sangathe kulalikira ndi kubweretsa Moyo Wamuyaya. Ndipo m’nyamata m’modzi pakati pa amayi chikwi amapanga "iwo" kusintha kwachikazi ku "iwo" chifukwa cha ulamuliro wa mwamuna. 6. Mwana wa Mulungu sangathe kutsutsana ndi zomwe Mulungu adakhazikitsa; ngakhale popanda Mzimu Woyera, iye adzasokonezeka! Baibulo silingadzitsutse lokha. Ngati Yesu akadakhazikitsa mtumwi wamkazi kapena wophunzira ndiye kuti iye sakanakhala Mesiya. Ngati Paulo akanalola mkaziyo kuti azilalikira ndiye Paulo akanakhala wabodza. Zirizonse zozizwitsa zake, zikanakhala zodabwitsa zonyenga. [Mawu a Mkonzi: Msonkhano unati, "Ameni! "] 7. Utumiki wa akazi ndi ukwati wa amuna kapena akazi okha-okha zili zonyansa zazikulu kwambiri za nthawi za mapeto. Ndipo munthu yemwe amalowa mu mpingo kumene amayi amalalikira ali ngati munthu amene akuchita nawo chiwerewere cha amuna kapena akazi okha-okha. Zaka 2000 zapitazo, anthu sankadziwa kuti tsiku limodzi, amuna kapena akazi okha-okha adzaguba ku Yerusalemu. Zaka 2000 zapitazo, anthu sankadziwa kuti tsiku lina mkazi, ngakhale iye mukusamba kwake, adzapita kukalalikira pamaso pa anthu m'mipingo [Mawu a Mkonzi: "Amen!] 8. Mu Chipangano Chakale munalibe wansembe wamkazi. Ngakhale mu dziko lapansi panalibe mtumiki wa chimayi. Ndi kumasulidwa uko komwe kunaika mkazi kumeneko! "Mtumiki" wachikazi kunalibeko. Ndipo ife tikudziwa kuti amayi anabwera ku zochitika za amitundu kupyolera mwa kumasulidwa. Mkazi woyamba womasuka padziko lapansi anali Naama, mwana wa Kaini. Ndipo mkazi woyamba yemwe anali womasulidwa mu Israeli anali Yezebeli, obwera. Koma pachiyambi sizinali choncho. Ndipo tinawona akazi akumenyera ufulu wovota ku Ulaya ndi ku America, koma pachiyambi mu Chipangano Chakale, mu Israeli, mwachitsanzo, akazi samawerengedwa. Ndipo mu Africa, mkazi sangakhale mtsogoleri wa mudzi. Ngakhale anthu akamakumana m'midzi, amayi alibe ufulu wolankhula. 9. Chimene Mulungu adawapatsa kwa Ayuda mu cholemba, adachipereka kwa amitundu pamitima yawo. Kodi ndi inu mudawaphunzitsa amitundu kupereka lobola la ukwati, zipatso zoyamba, kapena kupatsa dzina la tate kwa mwana woyamba? Ndinso mu machimo aakulu kapena migwirizano, kupereka nsembe ya magazi? Uyu ndi Mulungu amene anachita izi! Ndipo kotero Mulungu anawaululira iwo udindo wa mkaziyo. Ngakhale popanda kuphunzitsa, iwo amadziwa mwachitsanzo kuti tchimo la pachiyambi liri kugonana. Popanda kuphunzitsa, mwana weni-weni wa Mulungu amadziwa mumtima mwake kuti kugonana ndi tchimo limene Adam ndi Hava anachita. Koma pamene iwo amapita ku mipingo, mdierekezi amachotsa izo kuchokera kwa iwo. Ndipo mdierekezi yemweyo amamuyika mkazi pa guwa. Mpingo umayenera kukhala mkwatibwi wa Khristu. Ndipo mpingo umene umalandira mkazi pa guwa ndi mpingo wa wokwatirana akazi okha-okha. Ndipo akazi onse omwe amapita paguwa amakhala ndi ziwalo zachimuna m'maloto awo ndipo ambiri amavomereza zimenezo. 10. Ndipo sindikumvetsa kuti anthu omwe ali ndi Baibulo m'manja mwawo akhoza kuchita izi, kuyika akazi pa guwa kuti azilalikira kapena kutsogolera nyimbo za matamando pamene amuna ali pomwepo. Ndipo ngakhale zimachitika kuti akazi ena amakhala m'kusamba ndipo iwo amavala thewera pansi pa iwo amabwera kuima pa guwa. Inu amene mumakhala m’mipingo yotere mulibe chikumbumtima! Inu ndinu gawo la amuna wamba, ndinu mbadwa za serpenti, ndinu woipitsitsa kuposa Achikatolika ndi Achisilamu ndipo inu mumayesetsa kuwalalikira iwo. Ngati inu simukutsatira cholinga china, simungakhale mu mpingo woterowo. Kaya kungakhale kulalikira kapena nyimbo, ndi chinthu chomwecho. Kukhala wolakwa mbali imodzi iyi ndi kukhala wolakwa pa zonse. [Mawu a Mkonzi: Msonkhano unati, "Ameni! "]. Mkazi ayenera kukhala chete pa kachisi. Paulo akuti chowonadi chakuti mkazi sali woyenera kulalikira ku kachisi liri lamulo. Paulo akuti mu 1 Akorinto 14:34 "Akazi anu akhale chete m'mipingo, pakuti iwo saloledwa kulankhula, koma amamvera, monga lamulo limanenanso." Inu mukuwona? Lamulo limanena kuti mkazi sangathe kulankhula mu msonkhano. Ndipo palibe mkazi mu unsembe.
@carineablo2593
@carineablo2593 6 жыл бұрын
19. ChiKiristu kuzviisa pasi kuna Satani kuburikidza nebhuku rekare rinonzi Holy Bible, Islam kuzviisa pasi kuna Satani kuburikidza nebhuku rekare rinonzi Holy Quran, uye chiJudha kuzviisa pasi kuna Satani kuburikidza nebhuku rekare rinonzi Torah. Asi kuzviisa pasi kuna Mwari ndiko kuteerera Shoko raKe raakupa kuburikidza nemuporofita mupenyu wenguva yako. www.philippekacou.org #ProphetKacouPhilippe
@richardnamathanga999
@richardnamathanga999 Жыл бұрын
Amen
@adopolilianeedwige7628
@adopolilianeedwige7628 6 жыл бұрын
1. Monga aneneri a M’baibulo, mu Epulo 1993, ine, Kacou Philippe, mwamuna amene ndinali ndisanakhalepo ku mpingo, kupyolera m’masomphenya, ndinachezeredwa ndi M’ngelo amene anapereka kwa ine Uthenga wa kwa dziko lonse lapansi kukwaniritsa Mateyu 25:6 ndi Chivumbulutso 12:14. PKPCHANNELTV
@froramopiwa2138
@froramopiwa2138 6 жыл бұрын
God is good
@yaobleestelle2513
@yaobleestelle2513 6 жыл бұрын
Frora Mopiwa 40. Abale a ku Africa, Asia, Europe ndi America! Inu mwina munali kuyembekezera Uthenga wa Mateyu 25:6 mwinamwake mu dziko lanu koma Mulungu anachita izo mosiyana. Kumbukirani Ambuye wathu Yesu Khristu! Pokhala mkulu wa ansembe Melkizedeki, achirabi ndi alembi anaona kuti Iye adzachokera ku fuko la Levi. Koma Iye adachokera ku fuko la Yuda. Ndiye, Uthenga Wake ndi ntchito Zake zinatsimikizira kuti Iye anali Mesiya. Ndipo lero pa nkhope yonse ya dziko lapansi, ngati iwe uli mwana wa Mulungu, malo ako awa ali pano ndi m’neneri wa nthawi yako, M’neneri Kacou Philipe. Ndipo amene ali ndi makutu akumva amve.
@clementineahemin8086
@clementineahemin8086 6 жыл бұрын
3. Tsopano tiyeni tibwerere ku vesi 6. Kodi m’ngelo uyu wochokera ku vesi 6 akuchokera kuti? M’ngelo uyu amabwera kuchokera ku gawo la Mau omwe ali kumwamba monga mwa Masalimo 119: 89 osati m'Baibulo. Mawu a Mulungu amabwera kuchokera Kumwamba kupyolera mwa mngelo pamene mawu a mdierekezi amabwera kuchokera kuphompho kupyolera mu sukulu ya abusa. M’ngelo uyu akubwera kuchokera ku kachisi, chitsanzo cha Mpingo umene uli Kumwamba osati kuchokera ku Machitidwe a Atumwi, Vatican kapena United States. Mulungu anaululira izi kwa Mose, Yesaya, Ezekiele, ndi aneneri onse.
@nguessankacou2873
@nguessankacou2873 6 жыл бұрын
#prophetkacouphilippe #pkpchanneltv . Monga aneneri a M’baibulo, mu Epulo 1993, ine, Kacou Philippe, mwamuna amene ndinali ndisanakhalepo ku mpingo, kupyolera m’masomphenya, ndinachezeredwa ndi M’ngelo amene anapereka kwa ine Uthenga wa kwa dziko lonse lapansi kukwaniritsa Mateyu 25:6 ndi Chivumbulutso 12:14. Iyi ndi nkhani ya kutembenuka kwanga, komanso masomphenya atatu a maitanidwe ndi utumiki wanga: 2. Ndinatembenuka mtima pa Epulo 24, 1993 molingana ndi Danieli 10:4 mpaka 11 kudzera m’masomphenya amene ndinadziona ndekha nditaima pa mchenga m’mbali mwa nyanja, kenako pamwamba pa piramidi yayikulu kenakonso pa mchenga wa m’mbali mwa nyanja mu malo ena ndipo ndinaona galimoto yachikale ya ankhondo ikutuluka kuchokera pansi pa nyanja ndikulowera chakumbuyo. Nditatembenuka ndinaona kuti munali anthu amoyo ndipo anali akazi okha-okha, mmodzi wa iwo anali wosakanizika mtundu. 3. Kenako nkhunda ziwiri zinabwera moyandikira kwa ine ndikubwereranso pamadzi. Ndipo panachitika kadamsana, ndipo munthu wamaonekedwe angati Mtambo atagwira lupanga anatsika kuchokera kumwamba ndi Mwana wa Nkhosa kenako kunawalanso. Iwo anaima pa madzi ndipo Mwana wa Nkhosa anayamba kulankhula nane m’chinenero chosadziwika. Phokoso la mawu ake litabwera mwa ine, ndinagwa, ndikufa, Moyo wanga unapita kukaima pa madzi ndi iwo pamene thupi langa linagona pa mchenga wa nyanja. Pamene Mwana wa Nkhosa yo anamaliza kulankhula nane moyo wanga unabwelera mu thupi langa ndipo ndinakhalanso moyo koma sindinawaonenso. 4. Kenako khamu la anthu linabwera kwa ine kuchokera kumbali ya kumanja ndipo ndinawafunsa ngati iwo adaona Mngelo ndi Mwan wa Nkhosa. Iwo anati, "Ayi!" Ndipo ine ndinati: "Koma, kodi simunaone Mngelo ndi Mwana wa Nkhosa ndi zinthu zonse Iwo achita?" Iwo anayankha kuti, "Ife sitinamuwone Mngelo ndi Mwana wa Nkhosa ndipo sitidamve Mawu Mwana wa Nkhosa wayankhula koma ife tikukhulupirira izo kwathunthu chifukwa chimene Mulungu anapatsa ndipo mdierekezi anatenga, chabwezeredwa kwa iwe". Nditayang'ana m’mwamba ndinaona makwelero atakhazikitsidwa pakati pa thambo ndi nthaka pamwamba pa madzi ndipo angelo akumakwera ndikutsika. Ndipo masomphenya anatha ndipo ndinamverera chimene tsopano ndikudziwa kuti ndi Mzimu Woyera ndipo ndinalira ndikukhulupilira Mulungu nthawi yomweyo.
@gnagomichaeltv226
@gnagomichaeltv226 6 жыл бұрын
#PKPCHANNELTV 8. Ndipo pambuyo pa Kukonzanso, pamene Martin Luther, Ulrich Zwingli, Farel, John Calvin, John Wesley ndi ena anafa, mipingo inasaladza Mpingo woona. Mulungu ndiye anaukitsa m’ngelo wachitatu, mtumiki wachitatu ndi uthenga wa uneneri kwa onse okhala padziko lapansi. Mulungu samaukitsa mpingo kapena gulu la amuna kuti abweretse kapena abwezerezetse choonadi pa dziko lapansi koma m’neneri wamthenga. Ndipo kukana m’neneri uyu ndiko kukana Mulungu, ndipo m’neneri ndiye kamwa ya Mulungu, wolankhulira Mulungu, wonyamula Uthenga wa Mulungu, nthumwi ya Mulungu osati wina yemwe amapereka mawu a chidziwitso kapena iye wopangitsa anthu kugwa mu misonkhano ya mapemphero ndi zodabwitsa ndi mavumbulutso a kudolola, ngakhale kutakhala kuti mavumbulutso awa ali owona nthawi zonse ... [Mawu a Mkonzi: "Ameni! "].
@achillebehi1754
@achillebehi1754 6 жыл бұрын
12. Ndipo ngati Mulungu apulumutsa Mkatolika, wa Chiprotesitanti, wa chievangeliko, wa chiBranham, kapena membala m’modzi wa mamishoni ndi mautumiki amenewo, Mulungu ayenera kuchotsa gehena ndipo aliyense adzapite ku Paradaiso, ngakhale Satana. [Mkonzi: Osonkhana akuti, "Ameni!"]. Kodi munthu angakane bwanji m’neneri wamoyo wa nthawi yake ndikupita ku Paradaiso? Kodi munthu angapulumutsidwe bwanji ku Chigumula pamene atakana Nowa? Pamene Ambuye Yesu Khristu anali pa dziko lapansi, zikanatheka bwanji kumukana iye ndi kupulumuka? Dziko lonse lapansi liri ku mphompho chifukwa cha mipingo iyi. #PKPCHANNELTV
@gnoumouphilippepkp4661
@gnoumouphilippepkp4661 6 жыл бұрын
24. Ndipo inu achi Ivory, mwawonetsa pamaso pa dziko kuti ndinu woipitsitsa kuposa Congo-Kinshasa ndi Tshala Muana ... Kodi ndipemphere kuti misewu ya mafumukaziyi ikhalepo? Kodi ndiyenera kupempherera kuti mipingo ndi aneneri awo akhale ndi moyo? Ngati ine ndichita izi, lolani kuti moyo wanga usakhalepo komanso mulole kuti zipata za gehena zigonjetse pa ine. Koma ndikupempherera osankhidwa kuti madzi asawatengere iwo kutali ndipo kuti asonkhanitsidwe ku Moyo Wamuyaya ndi kuti chikhulupiriro chawo chisalephere. 25. Koma chifukwa cha tchimo ndi chifukwa cha mipingo, dziwani kuti dziko lapansi lidzachokera ku zowawa kufikira kuzowawa. Ndipo zidzachitika kuti munthu sazatha kugwirana chanza ndi m’chimwene wake kapena bwenzi lake lapamtima chifukwa choopa kuti adetsedwa ndi nthenda. Anthu adzayenda popanda kugwirana wina ndi mnzake. Sukulu zidzatsekedwa ndipo mudzamva anthu akunena kuti: "Ndikuwopa kutenga mayendedwe a pansi pa nthanka kapena basi, ndikuwopa kuti ndidetsedwa." Inu mukuona? Wolungama adzati kwa woipayo: "Pita ukawonetsere maliseche ako ku gombe la nyanja" ndipo woyipayo adzamuwuza iye: “Ine sindipita.” Inu mwaona? #PKPCHANNELTV
@gontranyao585
@gontranyao585 6 жыл бұрын
KACOU PHILIPPE : Ndipo ngati Mulungu apulumutsa Mkatolika, wa Chiprotesitanti, wa chievangeliko, wa chiBranham, kapena membala m’modzi wa mamishoni ndi mautumiki amenewo, Mulungu ayenera kuchotsa gehena ndipo aliyense adzapite ku Paradaiso, ngakhale Satana. [Mkonzi: Osonkhana akuti, "Ameni!"]. Kodi munthu angakane bwanji m’neneri wamoyo wa nthawi yake ndikupita ku Paradaiso? Kodi munthu angapulumutsidwe bwanji ku Chigumula pamene atakana Nowa? Pamene Ambuye Yesu Khristu anali pa dziko lapansi, zikanatheka bwanji kumukana iye ndi kupulumuka? Dziko lonse lapansi liri ku mphompho chifukwa cha mipingo iyi. #ProphetKacouPhilippe #PKPCHANNELTV
@mariusesmel3218
@mariusesmel3218 6 жыл бұрын
10. Uthenga uwu ukunena kuti Chisilamu, Chikhristu ndi Chiyuda ndizo mizimu itatu ya chule mu Chivumbulutso 16:13. Zipembedzo zitatu izi zimati ndi za Abrahamu. Zipembedzo zitatu izi zimakhulupirira mwa Mose. Zipembedzo zitatu izi sizimakhulupirira mwa aneneri amoyo koma aliyense amadzinenera kuti ndi wa mneneri yemwe iyo sikumudziwa. Aliyense wa iwo ali ndi buku lake-lake loyera. Ndipo onse atatu akuyembekezera Mesiya. Iwo ali mizimu itatu ya chule mu Chivumbulutso 16:13. Uthenga ukukunena kuti zimenezi ndi ziwanda zimene zinaukitsa Elvis Presley, Bob Marley, James Brown, Madonna, Papa Wemba zimene lero zaukitsa magulu ndi oyimba a chikhirisitu monga Tabitha Lemaire, Don Moen, Exo Eclats, Yolanda Adams ndi Celine Dion … 11. Uthenga uwu ukunena kuti Kaini, Joel Osteen, T.D. Jakes, Doug Batchelor, David Owuor, Emmanuel Makandiwa, Uebert Angel, T. B. Joshua ndi Manase Jordan ndi Satana muthupi. Uthenga uwu ukunena kuti Jesse Jackson, John Hagee, Pat Robertson, Joaquim Gonçalves, Donald Parnell, Alejandro Bullón, Guillermo Maldonado ndi Alberto Mottesi ndi Satana muthupi. Uthenga uwu ukunena kuti Claudio Freidzon, Dante Gebel, Edir Macedo, Valdemiro Santiago, Sila Malafaia, Paula White ndi Joyce Meyer ndi Satana muthupi. Uthenga uwu ukunena kuti Chris Oyakhilome, David Oyedepo, Tommy Osborn, Kenneth Hagin, Morris Cerullo, Yongi Cho, Win Worley ndi Rebecca Brown ndi Satana muthupi. #ProphetKacouPhilippe #PKPCHANNELTV
PAMENE MULUNGU ATSOGOZA NJIRA - Pastor Phiri
1:06:22
Charles Shonga
Рет қаралды 2,4 М.
LAMULO NDI CHISOMO - Pastor Frackson Kuyama// Ndirande
56:51
Charles Shonga
Рет қаралды 477
Noodles Eating Challenge, So Magical! So Much Fun#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:33
Twin Telepathy Challenge!
00:23
Stokes Twins
Рет қаралды 68 МЛН
Morning Chapel Pastor Aaron Dolan 11/19/2024
22:43
Martin Luther College
Рет қаралды 115
YESU ACHIRITSA MUNTHU WAZIWANDA - George Maganga
40:54
Charles Shonga
Рет қаралды 756
''When The Brook Dries Up, Move !'' By Pastor Brian Chimfwembe
1:21:57
Kabwata SDA Church
Рет қаралды 63
TIKUCHITANJI MU OLA LOTSIRIZA -- Elder J. Moses
32:36
Charles Shonga
Рет қаралды 381
MAKHALIDWE AMENE AKUTIPHA -- Pastor Frackson Kuyama// Ndirande
59:56
Charles Shonga
Рет қаралды 2,8 М.
ULI KUTI, NJIRA YA CHIPULUMUTSO - Pastor Frackson Kuyama
51:32
Charles Shonga
Рет қаралды 2,2 М.
ZAKEO AKUMANA NDI YESU -- Pastor Collins Manase
23:00
Charles Shonga
Рет қаралды 1,4 М.
MWINI NKHOSA -- Pastor Frackson Kuyama// Ndirande
59:01
Charles Shonga
Рет қаралды 7 М.