Inu nkhani yoti cimwendo ndi amene akulamulira osati cakwera ndinanenapo kale comrade inu mwangolasa.Ndipo ndizoona cikangawa ndi mbuzi ya munthu akulamulilidwa ndi nduna zake ndicifukwa dzikoli lasokonokela.But as u said comrade its 2 late coz mcp clorck its over.