Comrade Ntanyiwa On Limpopo Fm "Alfred Gangata Amumanga Ku Area 3 Police Ku Lilongwe"

  Рет қаралды 6,062

Malawi Extra

Malawi Extra

Күн бұрын

Пікірлер: 50
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 26 минут бұрын
Boom apsa machine mulibe kubwela ma vote, Comrade Mtanyiwa man of the mach❤ .
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 3 сағат бұрын
Ikubwera nthawi nafe tizamanga kuyambila nkulu wa asilikali , wapolice ndi ena onse a MCP
@BORNFACESIMBOTA
@BORNFACESIMBOTA 2 сағат бұрын
Straight 🤞
@ShillaShamil-v2y
@ShillaShamil-v2y 2 минут бұрын
Ambuye azikudalitsani aMtanyiwa
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 Сағат бұрын
Comrade Ntanyiwa.....moto buuuuuuu
@leonardmarkmasamba3862
@leonardmarkmasamba3862 3 сағат бұрын
Chipan chochitisa manyazi...mxm
@Rasheedissa-f3q
@Rasheedissa-f3q 4 сағат бұрын
Shisullo shanjanje it's mtanyiwa on lipopo fm redilo lives in sautha Africa 🌍
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 3 сағат бұрын
Ndipo MCP sikumva kudzudxulidwa Kaya bwanji agalu amenewa apenga kodi
@kingssalema3364
@kingssalema3364 3 сағат бұрын
Anthu mukuwamangawa mukuwapangilaa camping pliz,Tanzimvani Inu a emusiphiiiii. Tasovan mavuto omwe Ali pa ground, njala ,kusowa kwa gaso komanso forex. Eeeee koma agothiiii inuuuuu.
@WhyteSmart
@WhyteSmart 2 сағат бұрын
Malo momapanga ma plan wothesa mavutowa akulimbana ndikumanga anthu eeee zithandiza chani zimenezi.
@ChrissyScot
@ChrissyScot 14 минут бұрын
Kusowa zochita
@MaulanaIriyasa
@MaulanaIriyasa 3 сағат бұрын
Kodi mukuti akupalamula ndi adpp okha okha kumalawiko kodi??
@JohnmjigoMalinda
@JohnmjigoMalinda 2 сағат бұрын
Mcp zisiru zaathu
@ShillaShamil-v2y
@ShillaShamil-v2y 8 минут бұрын
Agalu eni eni
@DuncanRashid
@DuncanRashid 3 сағат бұрын
Koma this party ai ndithu apa ndipomwe ndikuonadi zinthu zomwe makolo angakhala akutiuza kuti MCP ndiyoipa ndithu apa ndiye tikuziona
@DanielJuwawo-s5n
@DanielJuwawo-s5n 2 сағат бұрын
Adalakwanji anthu adpp inu a mcp
@BORNFACESIMBOTA
@BORNFACESIMBOTA Сағат бұрын
Akunama eeeeee!!! Akunama eeeeee! 😂😂😂😂Your dys are numbered
@JoefreyGongoni
@JoefreyGongoni Сағат бұрын
Osangomanga Amalawi tonse pakuti ifeyo ndife tikuchotsani muboma osati amene mwamangayo
@bhowazpindani7755
@bhowazpindani7755 Сағат бұрын
Aaaaaa!! Koma boma ili esh?
@mavisChit-j5r
@mavisChit-j5r 2 сағат бұрын
Kiss wanu Mr ntanyiwa 💋💋💋💋💋💋💋💋💋💋💋Yokhayo ya stop working machine 😂😂😂😂😂😂😂
@IsabelLuka-i8f
@IsabelLuka-i8f Сағат бұрын
Comrade nde mwasekatu 😂😂😂😂
@Rasheedissa-f3q
@Rasheedissa-f3q 3 сағат бұрын
What's going on with MCP please
@ConnexShawanda-t3b
@ConnexShawanda-t3b Сағат бұрын
Tiphulitse zithupsa ndikuongola mafupa
@lilianprince661
@lilianprince661 2 сағат бұрын
Koma ndalowa chakachi DR ntanyiwa woyeeeeeeeweee ndipo ndumva kukoma posepose tiyeni nawooo agalu awa azipita kwawooooo
@RhodaPhili
@RhodaPhili 3 сағат бұрын
Kodi nthawi yonsei anali kut .kut aziyamanga anthu..chifukwa talowa 2025.
@RabbeccaChitimbe
@RabbeccaChitimbe 3 сағат бұрын
Chakwera uziwe kt nawe uzamangidwa munthu opanda nzeru iwe chiziwa iwe ndi kumanga anthu komatu nditukwana wamva iwe
@Biath-m4b
@Biath-m4b Сағат бұрын
Dikilan tibweza inu ndye simudzatulukaso mukaza mangidwa yobwenzera imawawatu
@SamsonChitezi-o6g
@SamsonChitezi-o6g 4 сағат бұрын
Kodi mwasowa zochita agaru inu amcp mkupanga mantha
@smt7036
@smt7036 2 сағат бұрын
Pitilizani kutipulumusa
@Rasheedissa-f3q
@Rasheedissa-f3q 3 сағат бұрын
Mtanyiwa nanga yoshossa mbendella sa dpppppppp wooooooyeeeeeee silliphati nkulimbi mwaiphesa 🤛🤛🤛🇿🇦🇲🇼
@HajieMtenje
@HajieMtenje Сағат бұрын
Please mokuphemphani umuwunze ntanyiwa azishula date akamayanga VN please
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 3 сағат бұрын
KODI INU A MCP MUKUONA NGATI MUWINA CHIFUKWA CHOMANGA ANTHU NDALE ZA UCHITSIRU ACHAKWERA NDI NDUNA ZANU MUDZIWE KUTI CHAKA CHINO CHISANATHE NANUNSO MUKHALA MUKULOWAMO NDIPO INUYO SITIDZALORA KUTI MUZATULUKE MUDZATHERA KONKO
@BORNFACESIMBOTA
@BORNFACESIMBOTA 2 сағат бұрын
Mcp your dys are numbered 🤞
@CathrineRamseyJafaal
@CathrineRamseyJafaal 3 сағат бұрын
Rlp chakwela chikangawa party chithupya party rest well
@AmosFrancis-c5w
@AmosFrancis-c5w 2 сағат бұрын
Malawi wavunda
@MemoryMteketi
@MemoryMteketi 2 сағат бұрын
Koma kod MCP bwanji mwamanga wolakwika zopusa eti
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n Сағат бұрын
Mcp yaukape
@ChibakuliKaisi-cm3hn
@ChibakuliKaisi-cm3hn Сағат бұрын
MCP PHOLO ZAKHE NOZE
@johnyonas5021
@johnyonas5021 3 сағат бұрын
Koma agalu amenewa aonjezano
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 сағат бұрын
Agangata alakwaso chani boma osowa zochititsa ili mweee....
@MemoryMteketi
@MemoryMteketi 2 сағат бұрын
Mbuzi inu
@DavieDulani
@DavieDulani 3 сағат бұрын
Galatasaray wooye wooye mcp chitseko chawapana
@CharlesJames-f1w
@CharlesJames-f1w 7 минут бұрын
Mumanga.angati..mcp.achakwera.mwalusa
@BORNFACESIMBOTA
@BORNFACESIMBOTA Сағат бұрын
Matatizotu Mcp boma lonukha hvy ili
@blessingsmofat
@blessingsmofat 2 сағат бұрын
mumakwana bwana
@JohnmjigoMalinda
@JohnmjigoMalinda 2 сағат бұрын
Koma tinene kuti onse amene ali ku mcp ndizisiru kwambiri anthu amenewa ndiagalu kwambiri mix chakwera walephera kulamulira dziko lamalawi
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 45 минут бұрын
Ndipo mcp anthu ake osamva kudzudzulidwa chipani chokupha
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 2 сағат бұрын
Koma zitsiru za mcp muli ndi ntchitotu manyazi olo mulibe? Mukuwamangilanji anthuwa are you holly you yourselves? Nthawi yanu ikubwela yozamangidwa and nobody will be sympathized you
@rashidadan2533
@rashidadan2533 3 сағат бұрын
His exllence professor Peter muthalika The president of the republic of Malawi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 🌹The winner of 2025 general election 🌹
ANC supporters slowly arriving in Khayelitsha
7:48
Newzroom Afrika
Рет қаралды 1 М.
“Don’t stop the chances.”
00:44
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 62 МЛН
coco在求救? #小丑 #天使 #shorts
00:29
好人小丑
Рет қаралды 120 МЛН
99.9% IMPOSSIBLE
00:24
STORROR
Рет қаралды 31 МЛН
ANC January 8 Statement
SABC News
Рет қаралды 1 М.
Assista na íntegra o FM Podcast 11/01/2025
MIRAMAR
Рет қаралды 294
LIVE: ANC January 8 statement
Eyewitness News
Рет қаралды 115
“Don’t stop the chances.”
00:44
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 62 МЛН