Comrade Ntanyiwa On Limpopo Fm Lelo Pa 17 Jan 2025 "Wa Police Amene Anaombela Mai Breda Wadziwika"

  Рет қаралды 10,695

Malawi Extra

Malawi Extra

Күн бұрын

Пікірлер: 45
@joycekarima6319
@joycekarima6319 50 минут бұрын
Tiomboleni antanyiwa tiomboleni timakudalilani mulungu akusungeni ❤mpaka september 16 zabwino zonse
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 5 сағат бұрын
Abusa amenewa mulungu awadalitse ife tingoti AMEN! Comrade apapa nde wayitha potidziwitsa dza chisilu chimene chinawombela ma sten kukhala iyeko tikudziwako, kugwila iye ntchito tikudziwakonso sangatipusise timupeza ndipo tikangomuona zache zada chifukwa timuwontcha tilibe nthawi yodikila polisi chifukwa palibe ikuchita. Manyaka police tipha tokha chifukwa mcp yatitola kwambiri.
@salmankhanofficiel.5018
@salmankhanofficiel.5018 4 сағат бұрын
Go koko 😂😂😂
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 4 сағат бұрын
@salmankhanofficiel.5018 yah gyz panopa basi lamulo mmanja mwathu chifukwa tilibe police onsewa ndi makape kuphatikizapo chikangawayo
@bashwhy
@bashwhy Сағат бұрын
ulemu wanu bwana
@MercyChidzombe
@MercyChidzombe 2 сағат бұрын
Comrade nthanyiwa mmakwanila koma muchepeseko nyimbo nthawi ya nyimbo imachuluka
@GetrudeBanda-sd1yf
@GetrudeBanda-sd1yf 6 сағат бұрын
Number one mntanyiwa
@FreddieKanyerere-u2z
@FreddieKanyerere-u2z 6 сағат бұрын
Comrade God bless you 🙏🙏.
@HabiboZimba
@HabiboZimba Сағат бұрын
Boom boom awululeni adziweokha😅😅😅
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 4 сағат бұрын
Jummah Mubarak to you Mr Mthanyiwa
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 5 сағат бұрын
Loud and clear here mpumalanga (SA)
@TressLuka
@TressLuka 6 сағат бұрын
Game on Mtanyiii 😅
@OwenNyambose
@OwenNyambose 6 сағат бұрын
Danco Comrade ntanyiwa ❤❤❤❤
@DanChirwa
@DanChirwa 6 сағат бұрын
Ulemu wanu Mr mtanyiwa
@HarrisonBiscuit-c8l
@HarrisonBiscuit-c8l 6 сағат бұрын
Thanks,may God see him
@petermasenti2084
@petermasenti2084 5 сағат бұрын
Comrade inuyo number one
@ChrissyScot
@ChrissyScot 7 сағат бұрын
KomA mtanyiwa ulandile ulemu kkkkkk PAKA wapeza yemwe anabudula mpunga wagulu kkkkk fire him.. from Capetown
@MillieMalakam
@MillieMalakam 6 сағат бұрын
koma 😂😂mtanyiwa wabaya ayaluse basi chipani cha mcp chazaza ndi mbuli 😂😂😂
@DanielJuwawo-s5n
@DanielJuwawo-s5n 16 минут бұрын
Ulemu wanu bg
@Nelsonmatenda
@Nelsonmatenda 3 сағат бұрын
Ntanyiwa inu ndi munthu olimba mtima ngati John chilembwe..No more mcp+ chakwera 2025 coz this is a wicked party
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 11 минут бұрын
Kodi chitsilu chamamuna chimenecho chimaphunzila kuwombera or bwanji 😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 56 минут бұрын
Bwanji nafe tikaombale amake tione ngati zinganukodweletse
@JohnmjigoMalinda
@JohnmjigoMalinda Сағат бұрын
Koma boma ili likufuna chani chakwera walephera kulamulira dziko lamalawi, chomwe nukuziwa ndikupha basi
@AchinaKellz
@AchinaKellz 4 сағат бұрын
Ok amakhala pamenepo ndapaziwa tizicheza naye😂
@Rasheedissa-f3q
@Rasheedissa-f3q 7 сағат бұрын
Mr mtanyiwa ulemu wanu bwana tili on line shifunkwa sha iweyyo umata ngani yonse ayaluseni
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 6 сағат бұрын
Chithuzi cha mayiwo si amene adaomberedwa mayi saidi amenewo ndi mayi navicha mukozetse next.
@GraceShaibu-i9d
@GraceShaibu-i9d 5 сағат бұрын
Big up
@FrancesZimbili
@FrancesZimbili 12 минут бұрын
Kom ripopo umakwan
@LouisAndrew-jr1yj
@LouisAndrew-jr1yj Сағат бұрын
Biggest one 😅
@FrancesZimbili
@FrancesZimbili 14 минут бұрын
Koma athu. Ari mmazi
@YusufAuss
@YusufAuss 6 сағат бұрын
Ulemu want antanyiwa mumativetsa kukoma ine Ausi yusufu
@JosephyHarry
@JosephyHarry 7 сағат бұрын
Inuyo ndiwakhulu man mumatha bro
@shabanitamimu7372
@shabanitamimu7372 4 сағат бұрын
Hy bhobho
@Brightkadox
@Brightkadox 7 сағат бұрын
Kodi bwanji mfutizo mukansphela anyani m'malo moombera anthu?mmmmmmmm
@FatimaMisheck
@FatimaMisheck 7 сағат бұрын
Ulemu wanu Antanyiwa
@LookmanAdamu
@LookmanAdamu 6 сағат бұрын
Mumakwana tiwomboleni ife amalawi
@HADIJAZAMBIA
@HADIJAZAMBIA 5 сағат бұрын
Mumakwana inuyo mr
@louisgolden
@louisgolden 3 сағат бұрын
Koma mayi Brenda wa ndiwokongola bwanji
@AchinaKellz
@AchinaKellz 4 сағат бұрын
Inu ndi pangolini kkkkkkkk😂chakwex walipira 3 billion chifukwa cha anthu ngati inu zizilowa zamisokho akuyendera sauli style koma yahwe wakana😂
@BashiruAdamus-l2b
@BashiruAdamus-l2b 7 сағат бұрын
Tanyiwa ndi 1 kuno kumalawi ndipo anthu awa tiwapeza ndipo aziwaso
@MillieMalakam
@MillieMalakam 6 сағат бұрын
ndipo live satifiketi yaabusa panopa akuti ndi pule wadziko koma guys chimwendo banda ndiye chizimu alibe mzeru
@bhowazpindani7755
@bhowazpindani7755 7 сағат бұрын
Ntanyiwa ndi wani basi
@MarySinjirani
@MarySinjirani 7 сағат бұрын
Ulemu wanu mr Comrade Mtanyiwa ambuye aziku dalitsani
@TenganiObety
@TenganiObety 6 сағат бұрын
Amene akudziwa anaimba nyimboyi andiuzeko pepani
Assista na íntegra o Fala Moçambique 17/01/2025
MIRAMAR
Рет қаралды 1,8 М.
Война Израиля с ХАМАС закончилась?
27:34
BBC News - Русская служба
Рет қаралды 3,8 М.
Quando A Diferença De Altura É Muito Grande 😲😂
00:12
Mari Maria
Рет қаралды 45 МЛН
Арыстанның айқасы, Тәуіржанның шайқасы!
25:51
QosLike / ҚосЛайк / Косылайық
Рет қаралды 700 М.
Grooming Gangs: Do we need a national inquiry? Feat. Owen Jones & Dawn Neesom | Storm Huntley
15:47
GWEDE GWEDE | 16 JANUARY 2025
31:11
Malawi News Update
Рет қаралды 19 М.
ZOMWE AYANKHULA MAI KALIATI 😱 😱 __17 January 2025
27:20