Comrade Ntanyiwa Pa Limpopo Fm Lelo Pa 28 Jan 2025 "Michael Usi Samamukonda Saulos Chilima"

  Рет қаралды 34,485

Malawi Extra

Malawi Extra

Күн бұрын

Пікірлер: 77
@kampirabrendah9990
@kampirabrendah9990 6 күн бұрын
Antanyiwatu pena koma eti. Mumabebetsa timakunyadirani koma musamayerekeze za Yesu Kumwa mowa ayi ndithu. We are proud of u koma zinazi ayi mudzibweza moto.
@AubreyMatiasgamaenock
@AubreyMatiasgamaenock 8 күн бұрын
😂😂😂😂😂 dziko lapansi ndiziko loyipaa limakonda muthu alimoyo adani osekerela😅😅😅 akukusungila mpeni kuphasa
@RitaKainga
@RitaKainga 8 күн бұрын
Ambuye Mulungu watha chonde mnchitilen chifundo mwana wanu Don't Trust kut achile mwansanga,chepetsan ululu omwe mwana wanu akuumva,chonde Mbuye wathu,timvelen
@ChimwemwePhiri-y7o
@ChimwemwePhiri-y7o 5 күн бұрын
Continue it's the best program
@clairelewis5309
@clairelewis5309 4 күн бұрын
Ambuye Atiyendere DJ Don't trust.Ndimikwingwilima Yake pamtanda ndinachilitsidwa.Quick recovery Don't trust🙏🙏
@DanielHolla-v9s
@DanielHolla-v9s 8 күн бұрын
That's true and we put mr don't trust in prayers 🙏
@CharlesJames-f1w
@CharlesJames-f1w 8 күн бұрын
Ndi.ndi.chocho Mauu.ameneo.ntanyiwa❤
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 8 күн бұрын
Otchuka ku Mulanje ndi mai Kaliatitu ndiye mai ake ndindani😮😮😮
@TimexKaufa
@TimexKaufa 8 күн бұрын
Mulekeni Usi ameneunja nd Mavutchetche omangolowerera zilizonse. Chifukwa balewake wamwalira yeunja mkumakalandira utsogoleri. Yeunja nsi Wa UTM. Amangofuna ndalama. Ndipo ku UTM nsitikufunanso wachitabwino walowa dzakemu.
@ElizabethPhiri-m4e
@ElizabethPhiri-m4e 7 күн бұрын
That's true Mr comrade God the Lord guide you 🙏🙏
@GloriaKamwendo-w2h
@GloriaKamwendo-w2h 8 күн бұрын
Mai kaliati mungoononga mbiri yanu,koma mcp Ku Mulanje singawine,mark my words
@chrissyamanda5510
@chrissyamanda5510 8 күн бұрын
Amayi okhumudwitsa kwambiri Amenewa ndi silent killer ali ngati cancer sure😢
@GiftChilanga-u3c
@GiftChilanga-u3c 6 күн бұрын
Kariati nayeso ndichisiru cha mnthu iye sizinamuyendere m mene adaluzira za presdent
@ChimwemweSauka
@ChimwemweSauka 8 күн бұрын
Welcome antanyiwa tinakusowani big man takulandilani, Mulungu akutetedzeleni mu chiwembu chomwe chakwera wachikonza
@SaidiAbeck
@SaidiAbeck 8 күн бұрын
Dzanja ramachiliso lichilise Don't trust
@MathewsMakalan-l6v
@MathewsMakalan-l6v 8 күн бұрын
Mulungu chilisani Mwana wanu dont trast in jesus name power
@JoelTchuma-g3s
@JoelTchuma-g3s 8 күн бұрын
INU ZIPANI ZO TSUTSA TAKOMANANI BWANJI MUKUONA NGATI MUKUOPANA.TAMVANI ZOMWE AKUNENA NTNYIWAZI.KUZENGEREZA SIKWABWINO,NTTHAWI IKUPITA.WINA ASADZIMVE KUTI AYIME PAYEKHA AMENEYO AMALAWI,MUSIYENI ATIPWETEKETSANSO.
@DistonShombe-n5f
@DistonShombe-n5f 7 күн бұрын
Goden smoke koma Ntanyiwa mumaipasa moto 😂😂😂
@SydneyKhazika
@SydneyKhazika 8 күн бұрын
Even a Usi ananena okha kuti a Chilima anampeza kuti agwire nawo ntchito limodzi osati kukondana ai, iyeyutu kachipani kakeka kanalipo kale so vision yake sanafune kuti iyime ai, 𝐎𝐝𝐲𝐚 𝐳𝐚𝐤𝐞 𝐚𝐥𝐢𝐛𝐞 𝐌𝐥𝐚𝐧𝐝𝐮
@SinsaKachale
@SinsaKachale 8 күн бұрын
Koma kaliyati 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅 uchita mistake yomwe Malawi azakuda koopsa
@ChifundoFrazer
@ChifundoFrazer 7 күн бұрын
Michael usi Ake ndi ma drma basi 😂😂
@TimeAbilu
@TimeAbilu 8 күн бұрын
Mcp kuti idzalowe m'boma kachikena eeee!!!! Padzakhala povuta, kungoti ma lamulo asindidwe Apule wa dziko ngati sakulamula bwino zaka zitasala pang'ono akuchipani asankhe munthu wina podikilira chisankho (chifukwa chuma chikuonongeka akamaona kuti anthu anditopela)
@GetrudeBanda-sd1yf
@GetrudeBanda-sd1yf 8 күн бұрын
Ambuye apitirize kumukhuza
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 8 күн бұрын
Awatu akagawa mavoti a ku Mulanje central omwewo not the whole mulanje, ndani sakuwaziwa ma khuluku amenewa ma paln awo?
@JosephMakatha
@JosephMakatha 8 күн бұрын
Koma golden smoke watchuka😂😂😂
@laurentbutao4084
@laurentbutao4084 8 күн бұрын
Mkulu opoila kwabasi ameneyu
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 8 күн бұрын
Ambuye amukhuze ndi zanja lake la Machilitso.......satana ndi olephera
@MartinNice-z9n
@MartinNice-z9n 7 күн бұрын
Agwilizana ND chakwera kt anamidze anthu ngat Sali limodz cholinga choti azapange alayace
@MaxwellChaminju
@MaxwellChaminju 8 күн бұрын
Ummm zosaenda wish him every quick recovery Dj
@YoungsterKubuli
@YoungsterKubuli 7 күн бұрын
Dolo kwambiri
@ChristopherChakanza-y4t
@ChristopherChakanza-y4t 7 күн бұрын
Osazakhulupila munthu
@KasimuJasitin-n3z
@KasimuJasitin-n3z 8 күн бұрын
Manganya pamtumbo Pake mboli yake
@SamuelMoyenda-p6k
@SamuelMoyenda-p6k 8 күн бұрын
Komabe tinakakonda mutafotokozabwino kt watani muthu wadwala kapena ndi mcp yomwei yachita chipongwe komabe ambuye akumane ndinyengo zake don't trust 🎉
@MariaJaya-s9b
@MariaJaya-s9b 8 күн бұрын
❤❤❤❤❤
@Malani41
@Malani41 8 күн бұрын
Why are you guys scared? If Chakwera is that unpopular why do you need an alliance or coalition to beat him????
@joempesi
@joempesi 8 күн бұрын
Get well soon ndipo Ambuye akuchepetsere ululu wa mabala ako
@GomanKazembe
@GomanKazembe 8 күн бұрын
Zioani zambiri koma ziko losauka,kkkkkk Kodi andale akuti bwanji?
@MathewsMakalan-l6v
@MathewsMakalan-l6v 8 күн бұрын
Ndipamene muziwe kuti maikol usi mutu mwake munazaza masewelo
@ZuufZuuf
@ZuufZuuf 8 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤🎉
@RoseRose-w8r
@RoseRose-w8r 8 күн бұрын
Inu ndinu mulungu wa anthu onse amene Munamva kulira Kwa ana a Israel pamene anali kuzuzika Kwa mfumu Faraoh ndipo munawatulutsa chonchoso tikupempha mukhale naye don't trust amene Ali mu ululu owopsa Ambuye tambasulani dzanja lanu lamachilitso NDI kuchiza mabala onse Kuti akachira adzachitire umboni Za dzina lanu Kuti ndinu mulungu wakutha muzonse palibe chosatheka NDI mulungu🙏
@AmosBandula-up4yb
@AmosBandula-up4yb 8 күн бұрын
More fire comrade t
@jamesFoster-dx4ur
@jamesFoster-dx4ur 8 күн бұрын
Vuto a opposition akukulilana mtima komatu nde mukafatsa kwambiri mutipweteka
@Timothy-r8l
@Timothy-r8l 8 күн бұрын
Good one
@JosephMwadzama-f4u
@JosephMwadzama-f4u 8 күн бұрын
Big up ❤❤❤❤
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 8 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 8 күн бұрын
Komatu nzimayiyo asankhale mai kaliya
@LosanThawale
@LosanThawale 8 күн бұрын
Ndithudi
@anniedennis7127
@anniedennis7127 8 күн бұрын
Get well soon Mr don't Trust
@YaxedyAlast
@YaxedyAlast 8 күн бұрын
Mtanyuwa ndikatundu
@OneziaMalemia
@OneziaMalemia 6 күн бұрын
Sono inu mumati apange bwanji pomwe anthu a ku UTM sakumufuna sasangalisidwa naye oipa ndamene akutulusa anthu wooo chifukwa anthu akanati asalowese sakho bwezi chili bwino bwino chipani chija sibwezi usi atatelo chifukwa momwe zinachitikila muja akuluakulu a UTM akanavomeleza kuti tiyeni president wathu ndiuyu ndikupanga chimozi bwezi pano chili ndiphavube koma chongoyamba kunyozananyozana zosatila zake ndizimenezi ndiye titha kuona ngati usi walakwisa koma munthu sungapilire ukupya ndi moto chosatila chake ndikuchokapo pamene pali motopoo kuti. Ine sindimuda usi koma ndimada comit ya UTM kuti inapanga chinganizo cholagwika. Akanakhala kuti panalibe kutozana tozana ndikuuza kuti UTM ikanalowa boma this year. Koma chongotosana tosana mistake ina kutenga munthu oti sanachizuzukile chipani kumuika pa pando mistake ina ndiimeneyo.
@SadrackTseka
@SadrackTseka 8 күн бұрын
Koma nyimboyi achakwera akudziwa? amene muli nayo mundigaire km akudziwa kt azaola zaka 65 atsala madzi angat apple Moto mundipeze uthengau kwa bwana olo utsogoleriwo ukome kuja adamsogoza chilima kuja azapitako afune asafune
@JoyceMoyo-mp3de
@JoyceMoyo-mp3de 8 күн бұрын
😢 chikangawa
@Patience-d8q
@Patience-d8q 8 күн бұрын
Repeat the number for Malawi
@HassanMillion
@HassanMillion 8 күн бұрын
Km iweyo tanyiwa iweyo ndi pangolin wa boma iweyo bc kkkkkk
@MartinMajola
@MartinMajola 7 күн бұрын
Goldeni smoke mbavaa
@fosterkandiero2660
@fosterkandiero2660 8 күн бұрын
akumenya kampeni wa APM amenewo
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 8 күн бұрын
Usi ndi oyipa mtima nkhope yonyasayo anapha chilima
@MartinMajola
@MartinMajola 7 күн бұрын
Usi fiti yunda sikalioti
@ClementVincent-q1r
@ClementVincent-q1r 8 күн бұрын
Don't trust ndindani kodi
@FemiaNTalakwes-i5v
@FemiaNTalakwes-i5v 8 күн бұрын
Ok
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 8 күн бұрын
Anthu akumulanje mitu YAWO wamitsala pinganjila nankhumwa manganya otse akuthandidza MCP kuti adzitiphabe Malawi muno awa agalu KWABASI ndi MCP YANUYO
@JJ-in-the-hut
@JJ-in-the-hut 8 күн бұрын
Dyela ndilimene likuwapangisa
@Christopheryakobe1989
@Christopheryakobe1989 8 күн бұрын
Tiyeni azipani zotsutsa tigwilane manja tichonse mcp
@ElediyaWatch
@ElediyaWatch 8 күн бұрын
Ambuye amukhudze
@AlexKaunda-w7l
@AlexKaunda-w7l 8 күн бұрын
Usi pa mtumbo pake vuto kukondaso kumasankhani achewa nokhanokha ndi izo mukugulisana panya pake manganya
@NicholasMWMwale
@NicholasMWMwale 8 күн бұрын
Ntima wanzako ndi tsidya lina😮
@TimexKaufa
@TimexKaufa 8 күн бұрын
Zosakhalabwino tipephe machilitso kuti akhale bwino mwansanga
@KhirChisale
@KhirChisale 8 күн бұрын
Zosakhala bwino tingopempha mulungu kuti athandize
@SadrackTseka
@SadrackTseka 8 күн бұрын
Mmmmmm akunama amenewo mulungu simunthu ndichaka choti osakhulupilira mulungu akhulupirire chifukwa cha chodzizwa chimene mulungu achite dyeralo pangani koma achakwera achoka basi Kaya zikhala bwanji koma mulungu achita izi ingotini phee muone
@YahayaKondwan-mo8hu
@YahayaKondwan-mo8hu 8 күн бұрын
Mulungu amukhuze mwa padela
@EirdLaher
@EirdLaher 8 күн бұрын
Wapatsidwa chimanga ndindani
@MartinMwanjawanthu-dj3fw
@MartinMwanjawanthu-dj3fw 8 күн бұрын
Kalaiti
@HADIJAZAMBIA
@HADIJAZAMBIA 8 күн бұрын
km zovutat
@EsnartMkunda
@EsnartMkunda 8 күн бұрын
Mr Ntanyiwa or mutanena bwanj km a opposition sangakumvelen aliyense akupanga zake mmmmm Ndipo a MCP akulowad boma anthu adzakhumudwa Tingopempha Ambuye kt akalowa a MCP zinthu zizakhale bwino
@CharlesJames-f1w
@CharlesJames-f1w 8 күн бұрын
Mulungu.ndiwàkulu.mashar
@HassanBabujr
@HassanBabujr 7 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤
Ben Longwe Kuyankhula Za Ku Chikangawa - Part 3
21:04
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 11 М.
Prophet Uyu Walosera Zoopsa Pa Zisankho Zikubwerazi ... Tanvani
27:34
СИНИЙ ИНЕЙ УЖЕ ВЫШЕЛ!❄️
01:01
DO$HIK
Рет қаралды 3,3 МЛН
Support each other🤝
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 81 МЛН
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:32
Family Games Media
Рет қаралды 55 МЛН
CRUISE 5 WITH DENIS MAHATA
1:10:36
Zodiak Malawi
Рет қаралды 67 М.
A Ntanyiwa Mubweletse Umboni Pasanathe 72 Hrs - Agape Khombe
13:39
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 37 М.
TIKUDZIWENI WITH ANTHONY MAKONDETSA - 5 August 2019
30:45
Times 360 Malawi
Рет қаралды 57 М.
СИНИЙ ИНЕЙ УЖЕ ВЫШЕЛ!❄️
01:01
DO$HIK
Рет қаралды 3,3 МЛН