This man is stupid. Akuona ngati akuyankhila ndibzitsilu. He is my friend koma apartment this is stupid
@charlesmlangeni99483 жыл бұрын
Amkaka kukanika kuyankha mafunso...Shame
@jameskadete21963 жыл бұрын
Malawi ili ndivuto ma embassy amaika Madera oti nzika zake sizingakwanise kukapeza thandizo why for example in SA maiko ochuluka anakhazikisa ma embassy Pretoria komwe ndi capital pomwe Malawi imakhara munzinda wa johberg komwe nkovuta ndi umbanda Nde amister chonde popanga ziganizo kumaganizira aphawi