I'm impressed by Chihana's humility and wise answers to questions.
@mauricechembe14 күн бұрын
I admire this guy. He always say the truth
@osamabinraden93913 жыл бұрын
Anafanana nawo kwambiri Mr chihana💞💞💞👍👍
@masanathindi93273 жыл бұрын
Joab pano malawi ngati ali ndi mtolankhani wabho ndi iweyo enawa timafunso tawo ndikhonza kuwaposa ngakhale ntchitoyi sindikuyiziwa keep it up
@smithelectro-plumb29943 жыл бұрын
This good man to be a president
@Calycious_Loves3 жыл бұрын
Joab umayitha. Sometimes kukhala ngati kuopa kuti koma fuso limeneli eish I might get a slap but you still go on and ask kudos to you. I really enjoy this program.
@SheenahMwalabu-iz3pr Жыл бұрын
💙💙💙✌✌✌
@AlvinJnr-rm6pe Жыл бұрын
Chihana yemweyo kuti wawa❤
@davidgutsu34923 жыл бұрын
Joab ukhale ndi ulemu munthuyi uli mnyumba mwake 😂😂😂
@chassemlangeni47063 жыл бұрын
He is Grt man...Chihanna
@rossbank72483 жыл бұрын
Enock chihana is half chewa and ATUPELE MULUZI is half chewa too...most of politicians used to marry chewa ladies in those days
@Camdenkazunguza3 жыл бұрын
hahaha interesting observation!
@MichaelpenielPhiri23 күн бұрын
This guy amandiwaza
@chesterphiri75233 жыл бұрын
Kodi chilipobe Chipani cha AFORD?????
@chesterphiri75233 жыл бұрын
Mumatenga Katapira posachedwa pompa kumapinyoritsa Magalimoto ndiye ndalama ziksngobwera poyerayera? MCP statergy yaeo imeneyo koma alembic kumwezi nkhanga zawona. Resurrection ya AFORD will need more than a miracle & Chihana Enoch can not inspire that. He doesn't have what it takes
@yusufmapata67213 жыл бұрын
Mr chihana kwa munthu woganiza mukuyankha bwino mafuso yineyo ndi wa kumachinga Ku liwonde yine ndi wa afford
@stanleydamalekani23983 жыл бұрын
Alephela kuyankha mafuso ku mapeto komabe ulemu wanu achihana
@HandsamPhiri9 ай бұрын
Malawi ikufunika munthu okhwima mutu ngati E chihana