Hope the Malawi government improves the infrastructure and the equipment in the MDF
@chrisbanda85203 жыл бұрын
I wa waiting for this thanks Joabo mwana olimba mtima ngat mthiko 😅
@johnsong21183 жыл бұрын
I just love the part of reserved soldiers Ayililimbikile imeneyo otherwise aliyense akhale soldier for self defense
@JumaBirliat Жыл бұрын
Good job koma ndimayifuna mwava .....a general
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Itayi Nundwe nimudziwa tinali kuphuzila limodzi school pa mpondagaga community day secondary school ku nkhotakota ndipo tinali class imodzi komaso tinayenda tili 4 Ine, Ernest, john Kaunda ndi itayi nundwe.
@georgemsangu2 жыл бұрын
Hi Joab I just listened this just now , Mmmmm I'm a Malawian but you can't understand I educated my son in a very difficult situations my son he is looking for a Job in Malawi defence force from a very poor place can you please help my son to get a chance to Malawi defence force please am struggling .I have no wife ,my wife passed away long time but I thank God cause I managed to educate my son I'm here in South Africa for Goeld purpose please help me Joab
@DICKSONJACOB-g4l3 ай бұрын
Kkk
@clementMuyafula5 ай бұрын
Good question
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Ndi tsiku limodzi ndinajambula picture ndili pa Honda pambali panali Mr watch
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Ndi phone no yomwe ili pakati phone no ya anthu awa : bright, Mr Mwale, Phenson Bwale, sister Katete.komaso ipezeka kumapeto kwa phone no ya Mr Mwaza
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Ndinajambula picture ndili pahonda
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Ndi phone no ya apongozi anga ku Palabana ku chipalesa (ngingiloni).komaso mulamu wanga Nelson Chongwe
@emanuelbanda94484 ай бұрын
KOMA UMALAKHULABWINO MR COMANDER
@ganizaninkhambule34053 жыл бұрын
I am proud
@MartinMajola11 күн бұрын
Balibe chazelu pooo
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Ndi phone no ya uncle chilanga komaso ipezeka pakati pa phone no ya mulamu wanga Derick
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Ndi phone no ya Mr Mwale garden house compound
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Kuli ine palibe chilichose nidziwapo pa phone no timatumilana chabe foni ngati anthu ochokela kumodzi ngakhale iye mwini wake no angavomeleze zomwe ine nikamba nizachilungamo chokhachokha.
@GraceLimani-zw7dx4 ай бұрын
A Bambo inu mulungu akukhudzeni
@limbanimwasinga34693 жыл бұрын
Good job
@kamwendoderek6567 Жыл бұрын
KOMA AJOAB MUKUKHALANGAT NANU MULI NDI MILITARY CONCEPT AND BACKGROUND
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Identification number vaccination register COVID 19 yomwe ndinayenda ine .komaso ndi phone no ya achemwali anga omwe ndikhala nawo ku garden
@AlicePaulo-r5b Жыл бұрын
Anthunu apapa mukuyamikira chani? Zomwe akuyankhula sizikumveka; akungodzikolakola, akungodzichita contradict. to say the truth he is MCP.
@doriskatute87862 жыл бұрын
Mumakwana Mr chakhaza ulemu wanu
@ZecaCornelio5 ай бұрын
Nde ndíchifukwa chani amamenya apolice
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Kwa lero sinikamba zambili ndili mu station mawa ndiyenda kumudzi kwawo kwa atate kukalongosola nkhani ya reg.
@FrynessMoyo-to2du Жыл бұрын
Pa atumbuka ose ichi ndi chatulo look at burkina faso small boy kungokhalira yes bwana 😂😂
@johnsong21183 жыл бұрын
You must come to Cape Town to meet Song The President of DUFA Malawi Funeral cover
@kool2493 Жыл бұрын
Who is that?
@elliotchisalanga122 жыл бұрын
He never killed a human being? Aaaaaah I don't think so ma mission onse aja guys.
@YOMALO.2 жыл бұрын
The Big Man
@paulchifukwa46763 жыл бұрын
Thumbs up Joab
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
No ili pakati pa phone no ya jack Ngoma
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Phone no ya Joseph phiri ndi Amake vini
@SydreckMphamba8 ай бұрын
Koma Joab ukupapilatu bwanji ludzu kwambiri iweyo??🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@isaacmbewe55852 жыл бұрын
Tsiku lomwe ndinayenda kumudzi ku Katete kukatenga reg
@AlexKaunda-ir6rz Жыл бұрын
Zoona akumuthokoza uyu wationongesa dziko uyu
@g_deonm57933 жыл бұрын
The commander seems to be personable. I just want to know what drink was in the cups that made Joab out drink the commander during this interview...