DALITSO KABAMBE ANAKAMUPANGA SUPPORT NTHANDA LERO PAMENE AKUCHITA MA DEMO A EKHA KU LILONGWE KWAVUTA

  Рет қаралды 30,647

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер
@usherjamson174
@usherjamson174 10 сағат бұрын
Kabambe for president 🎉
@Kenmoney-xp7tz
@Kenmoney-xp7tz 8 сағат бұрын
This is great I support this hundred percent ndipo nane ndiyamba pan dekha komaso kujoina anthu ngati chinchi... Bravo nthanda bravo kabambe bravo fredokis and everyone who joined
@FredKanyerere
@FredKanyerere 7 сағат бұрын
My president Mr kabambe watching from Cape town.
@RebeccaChikalenda
@RebeccaChikalenda 8 сағат бұрын
Ndinari wa udf kma ndarowa utm tsopano❤❤
@PreciousMaulidi-ry8om
@PreciousMaulidi-ry8om 8 сағат бұрын
Ndidari wa MCP km kabambe my vote sopano 🎉🎉
@blackcobra-b2y
@blackcobra-b2y 6 сағат бұрын
Wabodza iwe ,wa MCP sapanga masanje!!
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l 2 сағат бұрын
😂😂
@gracemnenula2518
@gracemnenula2518 10 сағат бұрын
My vote kabambe❤❤
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 10 сағат бұрын
Eeeesh mtsikana ameneyo eti 😂😂😂😂. We are fixing this country in kamangila's way
@IBRAHIMCHIPASULA
@IBRAHIMCHIPASULA 9 сағат бұрын
Walking the talk, I respect you Mr president.
@ShavickMzula
@ShavickMzula 10 сағат бұрын
Kabambe wabwela kudzakhala mundale koms mu freedom fighter
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 9 сағат бұрын
Kabambe nde muli ndi mfundotu your a great man kabambe may the almighty be with you wherever you shall go❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@LLOYDMWANDIRA
@LLOYDMWANDIRA 32 минут бұрын
It sounds great DK, work with all without creating boundaries as always you are doing ❤❤❤
@DannyKalumbaWaBanda-q7o
@DannyKalumbaWaBanda-q7o 7 сағат бұрын
Ndili nanu nganganga!osasintha zochita ayi bwana;proud of you Dr.kabambe osati yudas iskaliot uja bwezi atachigulitsa kwa chikangawa chipanichi koma inuyo aaaa kwanilitsani masomphenya a skc
@MosesDzonzi-em5px
@MosesDzonzi-em5px 9 сағат бұрын
Kabambe my vote Zinazi zatitayitsa thawi
@PatrickMatemba-x6q
@PatrickMatemba-x6q 5 сағат бұрын
Uyu munthu akunena zoona, mosayang'ana komwe akuchokera tiyeni a malawi tonse oganiza molikonda dziko lathu, timpatse support. Ena onsewa tinawayesa kale palibenso chanzeru angatibweretsere. Viva Kabambe viva.
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 4 сағат бұрын
Azipusisa makape omwewo
@FracksonMadani
@FracksonMadani 8 сағат бұрын
Sindikusamala kuti mukulankhula zoti simudzachita kapena mudzachita koma vote yanga ndikukaponyera inu basi, adalamulirakowa, akulamulawa ndilibe nawo cholowa mu vote yanga
@Staphelsavimbindhlovu
@Staphelsavimbindhlovu 7 сағат бұрын
Exactly kabambe ❤❤❤❤❤
@LLOYDMWANDIRA
@LLOYDMWANDIRA 29 минут бұрын
I see you mr Fredokiss🎉🎉🎉🎉 Work hand in hand with apule Ife tili nanu pamodzi ndiinu💯✅
@LevisonChapweteka
@LevisonChapweteka 2 сағат бұрын
Kabambe for presidency 🎉
@ObsterAdam
@ObsterAdam 9 сағат бұрын
🔥 fire Nana and Mr kabambe ❤ my vote
@jogechawa6192
@jogechawa6192 8 сағат бұрын
Kabambe is the main man timuvotele guys
@HaroldFodya
@HaroldFodya 10 сағат бұрын
Proud of u my sister we want railway from nsanje to bt
@leviticusnkhoswe360
@leviticusnkhoswe360 6 сағат бұрын
Well done mr kabambe good job
@VeroMaster-lo1mu
@VeroMaster-lo1mu 10 сағат бұрын
Watiimilila nana more fire
@AsiyatuAkila
@AsiyatuAkila 2 сағат бұрын
Suliwekha nthanda mulungu ndi amene akuziwa zayiwe sis ❤❤❤❤
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 9 сағат бұрын
Nana ndiwe munthu wolimba mtima Mulungu atitsogolere kudzera mwa iwe ❤❤
@WilliamKawaza
@WilliamKawaza 4 сағат бұрын
Visionary leader brings solutions, DK my vote 🔥
@DEEDMUSICIAN
@DEEDMUSICIAN 10 сағат бұрын
Kabambe aphweteka anthu uyuu
@ThomasSalaka
@ThomasSalaka 7 сағат бұрын
Shame on you , the heater of truth
@mollymasangano473
@mollymasangano473 8 сағат бұрын
Ku lower shire Valley too much PROMBLE S yes they need to fixed the road and solve so many problems Thanda Great job we are behind you ❤🎉❤ Akabambe Great job for support ing her..move 👏 👍 👌 🙌
@BakhePaliso-h8h
@BakhePaliso-h8h 9 сағат бұрын
Ndazikonda fundo zanu Mr kabambe zangovuta kut ndinagwa mchikond ndi DPP koma ayi mukuitha ndithu
@WedsonZuze-n1o
@WedsonZuze-n1o 3 сағат бұрын
😂😂😂😂😂muli muchikondi Kodi????
@DysonKamwendo
@DysonKamwendo 10 сағат бұрын
Kabambe nilinawe 2025 bomaaaaaa
@ToweraGama
@ToweraGama 5 сағат бұрын
Ambuye kufuma kwanu kuchitidwe momga kumwamba chomwecho pansi pano pa dziko la malawi Amen
@KossimasiMaluwa
@KossimasiMaluwa 10 сағат бұрын
Kabambe timakunda ife tikufuna munthu olimba mtima mwina Dziko lathu lizafika polemela
@RasheedKhamanga
@RasheedKhamanga 6 сағат бұрын
Amasuleni athu bwana❤
@ShaibuKambani-lh6vu
@ShaibuKambani-lh6vu 9 сағат бұрын
Ineyo nthandayi ndnamudziwa kale kale ndmunthu opanda zbwana I support her
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 сағат бұрын
My Vote ❤
@ChimwemweZuze
@ChimwemweZuze 4 сағат бұрын
Kabambe mofaya🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@ThomasSalaka
@ThomasSalaka 7 сағат бұрын
Mr kabambe the coming President 2025 ,thanks for your support to Thanda a concerned cetizen❤
@MrBone-zj1wq
@MrBone-zj1wq 4 сағат бұрын
Kabambe wasala pang'ono kuziswela yekha tsogolo lake la ndale pofuna ukulu bola ku DPP ku konkuja,APM my vote
@HassanJimmy-r1n
@HassanJimmy-r1n 2 сағат бұрын
Kathryn Maulid thank you so much you are so hard working
@ColbyNkhambala
@ColbyNkhambala 10 сағат бұрын
100% agree with this olemekezekawa mwachitsanzo bridge yapa museum 4 , mukadutsa pa kamuzu bridge pakumagwidwa ma kalavati awiri koma zaka ziwiri koma osatha
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 10 сағат бұрын
Zoona mr kabambe
@CharityChirwa-s4j
@CharityChirwa-s4j 7 сағат бұрын
Ndikaona uyu ndawona skc❤❤❤❤
@FelicitasKanthiti
@FelicitasKanthiti 6 сағат бұрын
Inenso ndikuona choncho. This man has great vision, I tell you!
@RealNation-k7s
@RealNation-k7s 6 сағат бұрын
Vote for our freedom fighter MR KAMBAMBE 🔥🔥🔥
@HabelGuwende
@HabelGuwende 9 сағат бұрын
Ulemu wanu Mr President
@GiftZuze-ge1ne
@GiftZuze-ge1ne 9 сағат бұрын
Kabambe my vote
@ChristopherKanzere
@ChristopherKanzere 10 сағат бұрын
Umatimilila more fire mwana wakwathu
@JumahIssah-d2n
@JumahIssah-d2n 6 сағат бұрын
DR KAbambe pls itanitsani mademo achimachine chi coz people we love you
@hesbaluku7281
@hesbaluku7281 6 сағат бұрын
Tsono mukazumura muthu wamatewe wa chihipi Why😂😂 bravo thanda
@fredgabrielnyangulu
@fredgabrielnyangulu 10 сағат бұрын
Awa ndie a makosana tsopano amachotsa voice ya munthu ndikuyika ka background kawo kumamveka zopusa zeni zeni
@ElisaNyirongo
@ElisaNyirongo 9 сағат бұрын
Anthu a ndale zimatere , mwina tidzaona koma mfundo zake ndizomveka bwino
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd 5 сағат бұрын
Dkkk my vote ❤❤
@RosinaPatel
@RosinaPatel 7 сағат бұрын
Well done Mr Kabambe
@Daisy-w1m4r
@Daisy-w1m4r 9 сағат бұрын
More fire my daughter,🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@MadamSimba-v1t
@MadamSimba-v1t 10 сағат бұрын
Osaopa osatopa osafooka tiye nazo ndiufulu kulankhula zakukhosi
@JosephyChithope
@JosephyChithope 5 сағат бұрын
Zoonad ndipo malawi ngat idzayambe kutulutsa katundu wambiri currency yathu idzakwera
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 5 сағат бұрын
Keep it up Nthanda am with you ndikufuna nambala ya nthanda share me
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f Сағат бұрын
Ma donors anathawa muno iweyo uli governor wa reserve bank chifukwa cholephela kuendetsa chuma. Lero ukufuna kutinamiza chiyani?
@ChikhuNamate
@ChikhuNamate 10 сағат бұрын
Tazatikonzereni bridge ya mkango kumulanje...
@MavutoFodya-p1u
@MavutoFodya-p1u 10 сағат бұрын
Mukukambatu za nzeru ngt mene amakambila DR chilima ndi chikangawa kma Palibe chinachitika kuyakhula sizivuta kma kuchita ndi Pali vutolo anthu andale ndimadabwa nanu
@lacksonsiyadi943
@lacksonsiyadi943 9 сағат бұрын
Ndipo andalewa,malawi wangosanduka ngati dimba lawo basi kumangotinamiza
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 4 сағат бұрын
Kabambe the pangolin, chiphona ichi
@AnnaElisha-b4h
@AnnaElisha-b4h 9 сағат бұрын
Kodi inu amakosana simungamachose Kaye sound yanuyo zomwe akuyakhula munthu sizikuvekayi
@RedsonSuwed
@RedsonSuwed 8 сағат бұрын
Kabambe must be a president
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 8 сағат бұрын
Kabambe pitilizan kmaso mtsikanayu timpase support
@I-Qz265Beats
@I-Qz265Beats Сағат бұрын
Bravo 👊
@WilliamNuludin
@WilliamNuludin 10 сағат бұрын
First
@yassinn5634
@yassinn5634 7 сағат бұрын
Uyu ndi Kamulepo Kaluwa wakale sakusiyana. Chifukwatu Kamulepotu ankapanga mademo ayekha osalandira ndalama iliyonse
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 4 сағат бұрын
Wamisaka uyu wasala pang,Ono kupenga
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 3 сағат бұрын
👏🏾👏🏾👏🏾👏🏾👌🏾
@JosephyChithope
@JosephyChithope 5 сағат бұрын
Cotton akunenay ndiuja amapangira zovara,
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri 8 сағат бұрын
Roads authority itipweteka panseu our roads are not fit ndipo COF ija tingosiyaso kukhoma nzopanda phindu
@mayachikadewa7551
@mayachikadewa7551 9 сағат бұрын
Mutsegula naye kamwazi kabambe ndithu
@RichardKumbambe
@RichardKumbambe 10 сағат бұрын
❤ 👏🏽👏🏽👏🏽👏🏽👏🏽👏🏽👏🏽
@chancyphiri
@chancyphiri 7 сағат бұрын
Ine ndikuona ngati tikuchedwa ku vote kapena ka vote card adzatenge azikasunga yekha
@maxwellmajawa6091
@maxwellmajawa6091 7 сағат бұрын
Tisamapange like page ya ada amenewa kaya background sound yo amaikiranji aaah samamva,
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 7 сағат бұрын
Akabambe mudsbweradi kuzakhara ku UTM palibeso okugwedezani mudsgwetsa mizwanya ku Comvention
@malvinhusted6245
@malvinhusted6245 6 сағат бұрын
Zomwe mukunenazo mukanati muzachite ayi ndithu malawi akanafika pena koma ndimabodza awa
@EffieletMagombo
@EffieletMagombo 9 сағат бұрын
my vote🎉
@WanangwaGobede
@WanangwaGobede 7 сағат бұрын
Atsikana zomatumidwa pliz chonde samalani !!!
@Katengezayobu
@Katengezayobu 7 сағат бұрын
Dalitso Kabambe my vote
@yassinn5634
@yassinn5634 7 сағат бұрын
Nthanda ndiye President wa amphawi osati kudikira kuti alandire ndalama ngati anthu enawa
@JephterBanda
@JephterBanda 5 сағат бұрын
Akabambewo akhala mm'boma nthawi yoseyi anapangako chiyani??zimaneneka ndi zamkotu
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem 5 сағат бұрын
eeeeetu osati kuma demo kupita chigulu ndikukukanikaniso kkkkkkkkkkkkkkkkkk😂
@BlessingsNyalugwe
@BlessingsNyalugwe 10 сағат бұрын
Cathy uziyenda ndi dk
@JoaquimElidioChiwisse
@JoaquimElidioChiwisse 42 минут бұрын
good job nthanda
@MatiasSakha
@MatiasSakha 7 сағат бұрын
Nthanda our pangolin from Nsanje
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 6 сағат бұрын
Osati Malawi yonse bwanji?
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 6 сағат бұрын
Chifukwa palibe mtsikana olimba mtima ngati uyu.
@jozyomar5361
@jozyomar5361 10 сағат бұрын
Mr Kabambe your a good man to be a leader but you can not be a president. Maybe take something better that you can change Malawi as your ideas.
@MayaChimpokosera
@MayaChimpokosera 6 сағат бұрын
Never give up 💪
@Wilsonianfacebook
@Wilsonianfacebook 7 сағат бұрын
Uyu apweteka anthu#Fredo I see you
@Amina-gg5gr
@Amina-gg5gr 8 сағат бұрын
Kodi chakwera yu osangopotokola khosi bwanji?????? Athokoze ndiribe ufiti nkanamulodzaine
@khwimaBanda-s3u
@khwimaBanda-s3u 8 сағат бұрын
kabambe kulankhula bwino kwambili koma kulowa m'boma uzapeza akupanga zao andalewa umakhudwisa bwanji i think 2030 kabambe tizamuyese enawa tatopa nawo
@FatsanNyanda
@FatsanNyanda 7 сағат бұрын
Ulibe zeru kabambe udaonapo ndan atawina masankho nkumayenda wapasi
@ChimwemweZuze
@ChimwemweZuze 4 сағат бұрын
Koma Nthanda ndiri pambuyo pako
@BashielSalade
@BashielSalade 9 сағат бұрын
Good man
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 6 сағат бұрын
Kabambe kabambe kabambe
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 3 сағат бұрын
☄️🔥🇲🇼👏🏾👏🏾
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 10 сағат бұрын
@mphompho6652
@mphompho6652 7 сағат бұрын
Uyutu Ali ndi nzeru zopoa Chikangawa uyu
@MasautsoMkunika
@MasautsoMkunika 8 сағат бұрын
Kabambe ndi machine
@BennettNjedza
@BennettNjedza 9 сағат бұрын
God bless you
@ChimwemweZuze
@ChimwemweZuze 4 сағат бұрын
Tili munyengo ya mademo ayekha yekha anthanda
I was just passing by
00:10
Artem Ivashin
Рет қаралды 18 МЛН
Accompanying my daughter to practice dance is so annoying #funny #cute#comedy
00:17
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 26 МЛН
Quando A Diferença De Altura É Muito Grande 😲😂
00:12
Mari Maria
Рет қаралды 21 МЛН
Sigma Kid Mistake #funny #sigma
00:17
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 17 МЛН
KODI MWAIMVA? NKHANI ZA LERO PA 4 DECEMBER 2024
16:32
Makosana
Рет қаралды 3,3 М.
Pastor Tobi; My Response To Solomon Buchi..
8:03
Daddy Freeze
Рет қаралды 2,4 М.
Новости дня | 4 декабря - вечерний выпуск
11:43
Euronews по-русски
Рет қаралды 6 М.
ZIMENE  PATRICIA KALIATI KOMANSO DALITSO KABAMBE AYANKHULA LERO......TAMVANI
50:54
Izindaba zesiZulu @19H00 l 04 December 2024
23:36
SABC Izindaba
Рет қаралды 4,4 М.
KUMANGIDWA KWA NTOLANKHANI WA TIMES __4 December 2024
38:56
I was just passing by
00:10
Artem Ivashin
Рет қаралды 18 МЛН