A VP chitanipo kanthu pa uyu nzanuyo tamulondoreni mukamuone nzanu kut alibwanji
@IbrahimRajab-nh3rl3 ай бұрын
OK vice president asikono
@WezzieChimuzi-ek7bk3 ай бұрын
Kkkkk koma ndiponsoo
@MercyNyachi3 ай бұрын
Koma inutu bambo asikono inu zanu zomwe zimakukhalani ndi zamasewelo basi not uko mwapitako ayi akumphaniso nanu kokonda ndalama nanu inu mfa
@andyngola35423 ай бұрын
Odya zake alibe mlandu, yes off, anthu akhale osapepha akhale ozidalira. Bwanji inuyo andale mukalowa m'boma mumakabweleka ndalama kwa IMF instead of kuzidalira?
@ElizabethKazambwe3 ай бұрын
Mwandiwazatu kobasi mwakamba mwanzeru
@mthawisakaunda3 ай бұрын
Manganya nd wa ku Zimbabwe. Galu
@EdwardSande-w8x3 ай бұрын
Musatelo kuti ndiwaku Zimbabwe ai ndiwakumalwi sibwino kutelo kt zoti ndi wa ku Zimbabwe mwaziwa lelo eti
@cynthiakananji16083 ай бұрын
God is still watching.ok munayambila kale kukambilana?😂hee pali zinthu zina umangoona waziyankhula poyera kkk
@bilalisipikini80613 ай бұрын
Ok Bambo asikono timve
@FauzaTabu3 ай бұрын
Koma zomavina zija musasiye plz
@RhoydNyandule-qr2ug3 ай бұрын
Choka iwe ! Udakapanga zokambilana ndi chakwera malilo atangochitika ...amalawi siopusatu ayi
@magretvizi3 ай бұрын
Do u knw kut interview yi ndi ya kalekale? Akungobweleza za 2019
@sharrifgwape71693 ай бұрын
Ndikupanda lawyer ku mawu akungothera kukhosi amwene
@RadsonTimoteo3 ай бұрын
Awa mau kuthera kukhosi sangayankhule zanzerui
@VictoriaWilliam-ms2ft3 ай бұрын
Amakambilana ndi chakwera chilima akuthatha ndi imfa ku chikangawa munthu opanda chisoni Iwe Mulungu akuone
@WezzieChimuzi-ek7bk3 ай бұрын
Ndikukumbula last week wina wake nthawi ija ya malilo adayankhula kuti a Dr Usi manganya akuwa yang'ana a President ndi diso lammbali mcholinga awasankhe kukhala VP wao pasadadutse masiku zinachitikadi Ambuye atichitile chifundo
@Allieshaibu86123 ай бұрын
uyu ndi m'bale wake wa julius malema zulu uyu si m''malawi amalawi simuziwa anabadwa mapasa manganya ndimaxiwa uyu