Good Malawian, really promoted likes of many by creating them jobs God bless Thom
@EthelOsman3 күн бұрын
Presedent wathu my team wanders
@MarthaSunday-y9oКүн бұрын
Zilibwino
@JosephyMakunganya6 күн бұрын
How about Triphonia Primarly,Secondary and University xull??
@YasinMmadi6 күн бұрын
Tileseko pang'ono Mr mpinganjila anabadwila ku Zomba not Blantyre ndipo fdh inayamba ndi anthu 6 osati 9 ndipo pa anthu 6 po MMODZI anali massager ndipo inayambila mu umoyo house ku Blantyre komanso maina a anthuwo anali madaliso Winie Phiri Steve Ritch komanso Stella NDATI tingokonzapo pang'ono pamenepo Amenewa ndi amene anayamba nawo fdh KOMANSO business anaphunzisidwa ndi malemu bambo awo kuzomba komweko chifukwa nawonso anali akupanga business moti kumwalila kwa bambo awo kuzomba anamwalila chifukwa Cha nkhanza zimene chipani Cha mcp chinkawapanga Mwachidule ndi mmenemo
@OrtonKabbichi6 күн бұрын
Akanati anthu ngati mkuluyi ku malawi apezeke 10 ndikulemba ntchito anthu aliense oposa 2000 bwenzi tili patali God Bless
@JosenMhangomlowoka-og9es6 күн бұрын
Big amemewa
@SebastianSauwa6 күн бұрын
I will create my accban with FDH bank
@edsonnyasulu53946 күн бұрын
Pa dziko la pansi palibe amene anganene mumene anapezela ndalama amangonena maboza basi
Vuto amakana kulowa ndale tikanawavotela kuzakhala president Malawi akanatukuka chifukwa ndi munthu othandiza anthu
@ChimwemweSauka6 күн бұрын
Nkhani yabwino kwambiri
@TrebuMalunga-sr2rz6 күн бұрын
Munthu wamkulu
@jennyx69146 күн бұрын
akhoza kubeleka ndikale paja anakwatirana palibe chovuta olo atamabeleka each and every 6months no problem kkkkl akhoza kudyetsa ana awo mskobidi ali mbwe mbwe mbweeee like bushiri joyce banda muthalika ndi ena ambiri mu malawi 🤣🤣🤣🤣🤣🤣