Deus abençoe a falecida Grace Chinga. Foi muito forte não é fácil
@Chitani100Ай бұрын
My malawi dziko likutha ili cos kupereka ma ganixo kukubvuta anyway mulungu atisogolere❤❤
@JosephKasamukaАй бұрын
Palibe cholakwika nkhaniyi is really true
@VitumbikoKaungaАй бұрын
Nde ena aziti bushiri Ndi munthu wa mulungu 😭😭😭😭 grace continue R I P
@ShamimuBisaniАй бұрын
Akhale munthu wa Mulungu akuopa kubwera ku South Africa bwanji kudzayankha milandu kd munthu oti sunalakwe umaopa munthu wa Mulungu amabera bwanji anthu
@ShamimuBisaniАй бұрын
@@VitumbikoKaunga m'bale wanga bas tingodzingodalira Mulungu yekha panopa bs
@DannieChimenyaАй бұрын
Ambuye kumwambako
@spargomwАй бұрын
Grace Chinga anali Munthu owopa Mulungu❤❤❤
@MiddayDelezaАй бұрын
That's what is happening in Malawi now, God have mercy upon us
@ShamimuBisaniАй бұрын
Bushri adziwe 2025 tidzanyamula kukampereka kwa president Ramaphosa ku South Africa
@basheerkachelenga9198Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@blessingsmkata7645Ай бұрын
Kuchita kukoka nanga akuopa Chan ngat Ali osalakwa😂😂😂
@ShamimuBisaniАй бұрын
@@blessingsmkata7645 dziko la Mulungu ili anagona ndi Adam koma Mulungu sanagone
@SAMUELNKHOMA-y3u7 күн бұрын
nice one mr sam mavita
@MadalitsoStevenАй бұрын
Zonse akudziwa ndi amwiniwake namalenga ndiye ndizovuta kwa athu amene tiliko amoyo kt tingayakhule kt chani
@RexonKamwana-c2rАй бұрын
Chipani chake ndi cha MCP(muziona momwe akuphera athu komaso ngozi zosaziwika bwino)