Gulewamkulu akuonongeka ndi MCP; Verbal war between Mutharika & Chakwera

  Рет қаралды 17,795

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

27 күн бұрын

Пікірлер: 84
@HusseinMachemba
@HusseinMachemba 25 күн бұрын
Nde kukhala wa DPP ndi vuto komaso chakwela amandibhowa kuyakhula ngt samawona zomwe zikuchitika galu ameneyi
@user-fk7cn6wl7r
@user-fk7cn6wl7r 25 күн бұрын
Big up Bakili Muluzi TV everyday we are checking your update to know what really happening across the globe
@christophermkhize1991
@christophermkhize1991 25 күн бұрын
Big man ndiye munatipatsa matenda yoyang'ana phone kuti any update from bakili muluzi tv we love you big man❤
@user-jd9yz5hp7y
@user-jd9yz5hp7y 25 күн бұрын
Ine sindinawonepo munthu ophuzira komano ndikukhala nkhuku yeni~yeni ndawonera Chakwera ndithu akuti ndi ophuzira komano zoxhitika zake ngati nkhuku yeni~yeni bolaninso mzimayi wa cash gate anali dolo
@webstermbewe8395
@webstermbewe8395 25 күн бұрын
Very good analysis malawibyavunda mu mcp
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 25 күн бұрын
Adad woyeeeeeee ❤❤❤❤❤❤
@LukaAron-el5qh
@LukaAron-el5qh 25 күн бұрын
Inde ndi zoona ukupanga tsogolo la ana ako omwe ukuwapasa ma contract aboma,kodi zomwe udayakhula zija kuti ukalephera boma uzatula pasi udindo osatulapasi udindo bwanji?iwe kukhala busa kodi udali busa wanji?amalawi akuvutika ndi kudula kwazithu iwe ungodya ndalama ku state house ulipheee Koma kunja kumacha patalike patani amalawi siopusa ai nkhani zonyasa zomwe zakhala zikuchitika boma lako la mcp ndizambiri kudula kwazinthu kusowa passport,koma chomwe ukudziwa iweyo ndi bodza basi pena amalawi akumachita kudabwa kodi dzikoli akulamurila ndi mwana wako kpn ndina zako.Tikamati walephera iwe ukukana,police imene yaonongeka akulephera kuwagwira anthu omwe adakhapa anzawo a dpp kuwaphwanyila ma galimito awo mpaka pano kuliziiii ikawafusa apolice akowo ati akufufudza Kodi afufuza mpaka riti?pomwe chilungamo chikuchitika kudziwika bwino koma chakwera tsiku lizafika panali ena pompo pano adachokapo
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 25 күн бұрын
Munthu woyipa chakwera wawononga dziko..
@thomasnkhomarangopicturesp8944
@thomasnkhomarangopicturesp8944 25 күн бұрын
Ma cadet akhapa anzao kangati?? Kungokhapidwa kamodziko mxieww musatinyase,ma cadet anaotcha banja pa area 24 pompa anthu atatu anamwalira makolo ndi mwana nde musamatinyase nazo,bwezera kamodziko
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 25 күн бұрын
Brother pitilizsni kiwulula zimene zikuchitika, Chakwera ndi boma lake la MCP azidziwa.
@innocentchirombo2073
@innocentchirombo2073 25 күн бұрын
Ipondeni fadah ❤❤❤
@kubengovender6996
@kubengovender6996 25 күн бұрын
Keep brother man!!
@user-dv8xd3qz6d
@user-dv8xd3qz6d 25 күн бұрын
Boma ilili ai zikomo😢 chabwino sakukwanila ndithu koma mulungu aziwakhululukila ndithu
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd 25 күн бұрын
I wish I was hme to vote this mcp out......
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 25 күн бұрын
APM my vote ❤❤❤❤
@user-pg9yl8jq8p
@user-pg9yl8jq8p 24 күн бұрын
Achimwene apapa ndiye mwatipatsira phala lopanda tchere.
@user-ix7pb6hk2w
@user-ix7pb6hk2w 25 күн бұрын
Anyamata osalora zopusa zomwe akupanga a MCP tiyeni tithane nawo
@user-nj4ob8jw6y
@user-nj4ob8jw6y 25 күн бұрын
Kukadakhala kuti anyamata wonse ndi akumweratu kapena, nanga ungoti anyamata ngati ukuwuza Wana wako basi. Pali anyamata ambiri m'Malawi muno
@yusufbanda4980
@yusufbanda4980 25 күн бұрын
Nkoptka nd2 ngat munaagonjetsa nkhondo ya miyala inabuka ija. Musaonetse kufooka a dpp
@user-pl8kw3dc9d
@user-pl8kw3dc9d 25 күн бұрын
Chakwera zakukanika dziko lino silako lokha
@MasterAkidu-cz4fb
@MasterAkidu-cz4fb 25 күн бұрын
Kodi ndikaikapo ndemanga chakwera awerenga ? Ndikufuna galu ameneyo...tandipezerani njira Yomwe ndingaonese nyenkhwe
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 25 күн бұрын
Akugwa nayo chakwera chaka cha mawa
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 25 күн бұрын
massage to mcp party .ngati mukufuna kuti centre region murowe nkhondo yapachiweniweni pitilidza kutuma nyaudzo kuti zizipangira nkhadza anthu osapota zipani zina..Centre region ili ndi anthu ambili Ma million ochekera kummwera and amasapota UDF and DPP nde zomwe mwayambadxi muphetsa anthu osarakwa ..ndipo siku ndilimodzi anthu azatopazo ndipo azabwedzera
@chipi892
@chipi892 24 күн бұрын
Mr Chakwera stop sweet talk n do the work
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 25 күн бұрын
Kukamwa kobwafukako chakwera
@SmartAdack
@SmartAdack 21 күн бұрын
Ati zose zakwela chifukwa cha chakwela 😂😂😂Ai zikomo
@emmamolande8193
@emmamolande8193 25 күн бұрын
Zonse zakwera chifukwa Cha chakwera😂😂😂😂😂 adad adha!!
@HolickLemajomo
@HolickLemajomo 25 күн бұрын
Chakwera wasowa chonena
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l 25 күн бұрын
Iweyo chakwera ndi mbuzi iwr ndi nyau zakozo
@samdiverson9733
@samdiverson9733 15 күн бұрын
Apm ndi machine
@RabsonTambula-fe5sx
@RabsonTambula-fe5sx 25 күн бұрын
Mbambande big mani 💙💙💙💙💙
@samdiverson9733
@samdiverson9733 15 күн бұрын
Bakili muluzi tv ndi kawawa
@user-cp7hu6xu8h
@user-cp7hu6xu8h 25 күн бұрын
Nyau zimeneso ndikwanukokho zikoli zi lakwanu anthu ozola manyi Mene kanayerere kunjakuno wins kumazola manyi Ake uko kumauza zochita anthu muzamare dzikoli zla Manu
@PhillipAcquaron
@PhillipAcquaron 25 күн бұрын
Ulenje umasimba wako
@user-ln3zx6wo4w
@user-ln3zx6wo4w 24 күн бұрын
Asiyeni nawiso asavale makaka a mcp tizabweza zomwezo
@dumisanimoyo3152
@dumisanimoyo3152 25 күн бұрын
Usanene zakumpoto wapangako chani
@user-dx4zu1wv4q
@user-dx4zu1wv4q 25 күн бұрын
Timakunyadila 😂
@user-sw2hc6we5e
@user-sw2hc6we5e 25 күн бұрын
Chakwera kwache kwatha
@thomasnkhomarangopicturesp8944
@thomasnkhomarangopicturesp8944 25 күн бұрын
Yankhulani Ma guys kuvota savoterana aliyense amavota yekha km ineyo sindingataye voti kwa APM....magetsi ngwee ndikavotere mdima?amalawi anazolowera kukhala ndi atsogoleri oyambitsa ntopola like APM,self centred,arrogant,and stupid president...zitukuko za 2kwacha kupanga lero mawa chagamuka
@user-yz5bq8rj9w
@user-yz5bq8rj9w 24 күн бұрын
Mmmmmm
@shideshidex5679
@shideshidex5679 25 күн бұрын
Atii Zonse Zakwera Chifukwa Cha Chakwera 😂
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 25 күн бұрын
Gogo iyiso ndi kapeso bwanji
@ibrahimbamusi109
@ibrahimbamusi109 25 күн бұрын
Mcp ndi worse mwaononga malaw sure
@robertrichman9376
@robertrichman9376 25 күн бұрын
Zoona amugwesere munthu nyumba coz he's a DPP fan ? That's total nonsense
@ChiyanjanoKhweleriwa
@ChiyanjanoKhweleriwa 25 күн бұрын
Eee
@DuncanMasina
@DuncanMasina 25 күн бұрын
Zoona
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 23 күн бұрын
Chakwera ndi Manyi
@yamikanimkanthama4354
@yamikanimkanthama4354 25 күн бұрын
Zinthu zake eeee
@user-is5dl7np9g
@user-is5dl7np9g 25 күн бұрын
MCP yankhanza kwambiri
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 24 күн бұрын
Koma ambuye
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 25 күн бұрын
Inekunenaso ona achisilu achakwera alindimtima oipa wangasa ndipoine ndantukwna pamachende akedziko linali bwino bwino mbusi achakwera aliononga ndekumamti paka 2030 asilamulila Malawi kapena akasiao kodi achakwera zelumulipe mutumwanumo kodimuma ganisabwanji chivukwa kunamakwani kopandana komanyasi kodimuma nganisakumti ivendiana aachatap machende ako kape ondina iwala kunenaakumti muvine musavine 2025 you go
@user-nj4ob8jw6y
@user-nj4ob8jw6y 25 күн бұрын
Kodi nanga Atupele alipodi koma? Bwanji simukupatsa moto Atupele, mukuganiza kuti ulendo wuno awupeza u running mate? Kkkkkk mukusewela ndi a Llomwe, mukhawula.
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 25 күн бұрын
Chakwera you mad
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 23 күн бұрын
Mcp umburi wachulukira
@thomasnkhomarangopicturesp8944
@thomasnkhomarangopicturesp8944 25 күн бұрын
Cadet kumva pain
@TonyBanda-zh2rd
@TonyBanda-zh2rd 25 күн бұрын
Kkkkkkkk iweyo unabwera
@peterjim6810
@peterjim6810 25 күн бұрын
Mukuona mtembo pano?
@user-nj4ob8jw6y
@user-nj4ob8jw6y 25 күн бұрын
Mutharika ndi chitsiru sadziwa ndale. This old man is always emotional, he is not fit to be president.
@user-pn7cj9hb3t
@user-pn7cj9hb3t 25 күн бұрын
Chitsilu iwe eti mutu wopindikawo
@user-dv6rt6vb6e
@user-dv6rt6vb6e 25 күн бұрын
Mwanama
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 25 күн бұрын
DPP pachiongolero ❤❤❤❤❤❤
@user-nj4ob8jw6y
@user-nj4ob8jw6y 25 күн бұрын
Kutiko? Mukunya, muwonanso kuti ndale ndikanyama koyipa, timugwetsa APM wanuyo
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 25 күн бұрын
Chakwera kwake kwatha aisova
@user-my4gr1pv8h
@user-my4gr1pv8h 25 күн бұрын
Kom akulu awawq
@ShalifaJames
@ShalifaJames 25 күн бұрын
Nyapanu chakwera
@user-nj4ob8jw6y
@user-nj4ob8jw6y 25 күн бұрын
Ngakhale utukwane Chakwera adzawinanso, mark this date of today.
@robsontyg3928
@robsontyg3928 25 күн бұрын
Akulu ngati ili jealousy , pamtumbo pamako ndithu mchawa , achawa mukuiwala kuti kwanu ndi Mozambique
@noelmunthali3516
@noelmunthali3516 25 күн бұрын
Inu kwanu ndikuti?
@user-rl3ku3yo6o
@user-rl3ku3yo6o 25 күн бұрын
uyambe wanena kwanu ndiye uzinena za achawa vuto mukafika pamalo mumafuna mutseke there ma history.. mukhale ngati inu ndi zika pamalopo tchende lako kavule luzi
@robsontyg3928
@robsontyg3928 25 күн бұрын
@@user-rl3ku3yo6o machende amako mwana w mchawa chomwe umdzidziwa ndikuchapa kumatako ndi manja futseck mbuzi ya munthu
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 25 күн бұрын
Alomwe mumakana kwanu bwanji kamuzu adakugulani ndi gaga kwanu kuli njala mwatasa agaru inu omanu odakulerani mopusa vitsiru onyani ovikundu demeti kwathu Kuno simungatiuze zopusa magogo ayi Kuno manyi anuo
@robsontyg3928
@robsontyg3928 25 күн бұрын
@@JackMvura-ik2td more fire awuze
@uchizJoelMumba
@uchizJoelMumba 25 күн бұрын
Kunoso kumpoto kuno dpp kulibe ndi mcp basi
@PhillipAcquaron
@PhillipAcquaron 25 күн бұрын
Ukakhara pa bwino usamayelekedwe suziwa zapa mawa
@lusolawo73
@lusolawo73 20 күн бұрын
Chi fiti
@AaronWiniko
@AaronWiniko 25 күн бұрын
Chakwela iwe opusa
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 25 күн бұрын
mcp has failed
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v 24 күн бұрын
Very dull speech not fit to be a leadership even as a pastor
@MARTCHIBISA
@MARTCHIBISA 24 күн бұрын
Apm tulan pasi anyamata atsogolele inu
@user-fk7cn6wl7r
@user-fk7cn6wl7r 25 күн бұрын
Big up Bakili Muluzi TV everyday we are checking your update to know what really happening across the globe
@DannielOnions-fy3dc
@DannielOnions-fy3dc 25 күн бұрын
Chi mbava ichiso
Afrikaans Nuus | 09 Junie 2024
7:11
SABC Nuus
Рет қаралды 4,8 М.
Can you beat this impossible game?
00:13
LOL
Рет қаралды 63 МЛН
Китайка и Пчелка 4 серия😂😆
00:19
KITAYKA
Рет қаралды 3,2 МЛН
Growing concerns over possibility of violence in KZN
4:16
Newzroom Afrika
Рет қаралды 7 М.
What happens if parties don't reach an agreement?
3:40
Newzroom Afrika
Рет қаралды 56 М.
Kunene explains why PA wants Home Affairs
10:00
Newzroom Afrika
Рет қаралды 6 М.
MOSES KUNKUYU EXCLUSIVE INTERVIEW
56:13
Zodiak Malawi
Рет қаралды 25 М.
Timothy Mtambo wapepesa kwa amalawi powakweza Bus ya ku Bagamoyo
19:12
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 28 М.
Leonard Zhakata - Hupenyu Mutoro(Official Music Video)
5:28
Leonard Zhakata Official🎶
Рет қаралды 83
MURANGANWA FAMILY 1 SEKURU MUKOTSANJERA Karanganda TV
3:53:45
Karanganda Tv (Waiyepo ere ?)
Рет қаралды 1,7 М.