GWEDE GWEDE | 23 JANUARY 2025

  Рет қаралды 13,063

Malawi News Update

Malawi News Update

Күн бұрын

Пікірлер: 23
@HastingswaLyson
@HastingswaLyson 9 күн бұрын
watching from Johannesburg
@HirikerJose-v7r
@HirikerJose-v7r 9 күн бұрын
Watching from Lusaka Zambia
@HassanIzaya-y1p
@HassanIzaya-y1p 9 күн бұрын
Gwede gwede mumakwena kwabmili tafika live south Africa Cape town 🔥🔥💪
@QspyKtmSlmn
@QspyKtmSlmn 9 күн бұрын
Following 🎉
@DuwaAdam-r2x
@DuwaAdam-r2x 9 күн бұрын
Watching from durban
@geofreydzinyemba6107
@geofreydzinyemba6107 9 күн бұрын
Good news keep it up guys chilungamo chiziyenda ngati Madzi
@EsnartMkunda
@EsnartMkunda 8 күн бұрын
Madzi onyikila mphale amachita kumveka mfungo 😂😂😂😂😂
@VictoriaMukhova
@VictoriaMukhova 6 күн бұрын
Akatolika anzathu mmwatichitisa manyazi zi apa..chilango Cha bwanji chimenecho
@chikondiphili5144
@chikondiphili5144 10 күн бұрын
Ndipo amalawi tilindivuto tikamagula zithu pa shop ,sitikonda kuwona expired date, Ndimawona ngati ziziyambila Ku school kumuuza mwana kuti chithu chilichose chomwe wangula aziyamba waona expire date,makolo komaso ma lediyo tizilimbikitsa kuuza athu kuti azipanga check chilichose chomwe agula❤
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 9 күн бұрын
Ndalama angogula mankhwala mzipatala anthu akufa , iwowo angisiya kunvela zabodzazo
@DennnisGogoda
@DennnisGogoda 9 күн бұрын
Moni bambo Banda ndi Mayi Dumbula
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 9 күн бұрын
Katengeni Ibrahim Traore azakonza Malawi
@ChifundoKaphirikwete
@ChifundoKaphirikwete 9 күн бұрын
Ndipo inu ndiye ukhale ndi ana oti nawonso akukwela min bus mpaka munthu kumapanga spend 10,000 per day ,ayi ndithu nenetsanidi pamenepo it's too much
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 9 күн бұрын
Kungosintha bomalo basi
@CourageBanda-d1g
@CourageBanda-d1g 9 күн бұрын
Chilungamo chabwino
@christopherchapuma6484
@christopherchapuma6484 9 күн бұрын
Never spare ma institutions a boma, simulinso bwino.
@ChristopherMakamo-ky4pq
@ChristopherMakamo-ky4pq 9 күн бұрын
Chigayo kkkkkkkk yoh
@BrianZimba-nn6sn
@BrianZimba-nn6sn 8 күн бұрын
Za ndare zimenezo
@ChifundoBeston
@ChifundoBeston 9 күн бұрын
Amabugwewo ndi aSatana, ndichifukwa chani akudana ndichilungamo. Amalawi tatopa ndindale zabodza. Leader of opportion it's obvious kuti sangagwilizane ndi machitidwe omwe angazetse chilungamo. Machine agulidwe ndipo amalawi yatisangalatsa tikufuna tochoke muuchimo wabodza. Dziwani kuti bodza pamaso pa Mulungu otilengayo nditchimo. Amalawi tisazalangidwe chifukwa cha Tchimo labodza la kamachende uyu mukuti wa bakili tv or mtanyiwa ai. Yense wankhani zabodza amangidwe akalowe kundende. Mumalamuro aMulungu amakana bodza kamvuzi chaponda ndindani pamaso pa Mulungu? Oti akakanene kuti bodza ndilofunika? Amalawi timaopa Mulungu ndipo timalimbikitsa kusunga malamuro aMulungu.
@JustinMakoka
@JustinMakoka 10 күн бұрын
Ukunso kumachinga kasimonje phunzitsi 1 akudzunza ana mupiteko
@mauricesande9661
@mauricesande9661 9 күн бұрын
Km guys aah these people why always em?
@ChristopherMakamo-ky4pq
@ChristopherMakamo-ky4pq 9 күн бұрын
Chigayo kkkkkkkk yoh
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH RICHARD CHIMWENDO BANDA
1:13:46
Zodiak Malawi
Рет қаралды 52 М.
Malawian Cameras Kukumana maso ndi maso ndi Dennis Thanthwe Khang'a Mahata
29:51
-5+3은 뭔가요? 📚 #shorts
0:19
5 분 Tricks
Рет қаралды 13 МЛН
Military trial tug of war | NBS Morning Breeze
27:52
NBS Televison
Рет қаралды 95
January 30, 2025
13:07
bambo a Sapesa
Рет қаралды 727
Apapa ndayamba kunvesetsano anthu akamati bola Peter Mutharika, Ben Longwe.
29:10
Citi Breakfast Show: Monday, 3rd February, 2025
Citi FM
Рет қаралды 428
MKULU AMENE ANAKULA MODABWITSA AMENE AKUDZITI NDI MULUNGU
34:14
Factory265 Media
Рет қаралды 13 М.
Meyiwa murder trial resumes | 3 February 2025
eNCA
Рет қаралды 1,4 М.