GWEDE-GWEDE PA 27 June 2024🙌🙌🙌

  Рет қаралды 17,881

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 60
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 3 ай бұрын
Ma demo amenewo akufunika ku Malawi, zimagalimoto zodula zonse zigulitsudwe...
@JacobMsukwa-q6v
@JacobMsukwa-q6v 3 ай бұрын
We're living in the world where the book of smouldering charcoal is still working.Chilima,,, John Phombe magufuri gone some few months/yeas ago NB:there legacies remained unshakable
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 3 ай бұрын
Su Chakwera ma constitution ndi abakili muluzi....koma we pray munthu wamulungu azabwera malamulo onsewo azawathese
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 3 ай бұрын
kungoti kuyambira chakwera 'apolice' army ndi nduna zonse ndi zitsiru zokha zokha mbava zigawenga
@ChawasoMlotha-ys6bf
@ChawasoMlotha-ys6bf 3 ай бұрын
Under mcp government, chilungamo ku mzuzu mnthu kumtenga kupita ku lilongwe kuononga mafuta ma orders za ziiii.
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 3 ай бұрын
boma ili lolamulila zigawenga zokha zokha zitsiru mbava chakwera ndi chitsiru chotheratu chigananga
@MirriamKambale
@MirriamKambale 3 ай бұрын
Ngati kuli mbatama za anthu mmalawi ndie a police ndipo ngati kuli anthu ophwanya komanso osaziwa malamulo ndie a police ndipo galu ameneyu mukuti president wamalawwiyu Kaya mukuti chakwera wapepelesa kwambiri a police amenewa
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 3 ай бұрын
Zimene mwanena stive banda ndizoona a police akupanga zopupuluma chikwa cha ndale ena.vuto boma ili ambiri zeru alibe chifukwa chopana cheru ndichifukwa amapupulumisa a police. And munthu walakwa ku mzuzu makhoti alikoko police ili koko basi bwerani naye kuno ku lilongwe kuli chani ku lilongwe.
@faroukakwah291
@faroukakwah291 3 ай бұрын
Chilungamo plus❤ twapukene amagwetu
@LemosBanda
@LemosBanda 3 ай бұрын
Vuto Malawi Police inatha panopa ndi MCP Police.
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 ай бұрын
Kuyambila chakwela ndi kabineti yonse apolice army zonse ndi zitsilu za kuba boma la mcp ndi la manyi
@EstherShaba-fh8ib
@EstherShaba-fh8ib 3 ай бұрын
BOMA lopanda nzelu iri
@greymasha838
@greymasha838 3 ай бұрын
Chilungamo
@emberbotoman1613
@emberbotoman1613 3 ай бұрын
Mulingo omwe wamuyezera mzako nawenso adzakuyezera omwewo
@nasibukombo4302
@nasibukombo4302 3 ай бұрын
Cyber act will not yield anything, freedom of speech is enacted in our mother law( Constitution).
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 3 ай бұрын
Uchigawenga wachuluka kwambiri mmalawi.
@MatthewsJohn-kv8fj
@MatthewsJohn-kv8fj 3 ай бұрын
Chadwell chinsiru kwambiri
@EliasKawuwa
@EliasKawuwa 3 ай бұрын
Ngati wa Mpingoyo anapalamula nde asamangidwe,iyeyo ndi munthu, aaaaaaa ,munakangodzudzula zolakwikwazo,osati mpingo ,mpingo nde chiyani, Mesa mpingo ndi anthu,nde munthuyo ngati walakwitsa nde lamulo lisangwire Ntchito
@ThomasiSalijeni
@ThomasiSalijeni 3 ай бұрын
Useless police of malawi
@MarvGerald
@MarvGerald 3 ай бұрын
Kumibawa inu nokha ndiamene ndimakufilan mumanena chilungamo boma ili ndilofoira
@KayangeNicholas-vl6nu
@KayangeNicholas-vl6nu 3 ай бұрын
Ine koma chomwe ndikuona chimalakwika mdziko muno ndichokuti:Civil servant akalakwila munthu/anthu,nkhuluza mulandu,chipepetso chimachoka ku boma.Monga a waterboard kumwetsa anthu madzi onyasa(uku ndikunyalanyaza chabe,just lack of seriousness) Anthu onyalanyazawa pa ntchito bwenzi akuwadula salary nkhupanga compensate ma victims.
@MirriamKambale
@MirriamKambale 3 ай бұрын
Chakwera nzeru alibe muzamuona chipumi bilubilu kaluka panga nawo participate pa function ya CCAP after all this ndikuti ndi galu ndithu
@NedsonKanjira-qj2ig
@NedsonKanjira-qj2ig 3 ай бұрын
Onsewa mubomamo ndi zisiru za anthu panali azanu akamanga anthu , kupha anthu uzifuse kuti ali kuti
@MarcFelson
@MarcFelson 3 ай бұрын
Umakhala uchitsilu wa boma pamodzi ndi umbuli wa apolisi Koma ka pay kang'onong'ono
@WillyMajiya
@WillyMajiya 3 ай бұрын
A police athu amalephera kugwira ntchito yawo mwa professional chifukwa cha ma politicians ena ake a nkhope ngati manyi
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 3 ай бұрын
Chakwera afuna axiophyeza athu ngat anayamba kulamulila ndiiye
@innocentkapachika6591
@innocentkapachika6591 3 ай бұрын
Nanga training ya ntchito umapanga 6 months and think you can get quality staff
@VictorAmos-my8ne
@VictorAmos-my8ne 3 ай бұрын
Mayi Aja mukuti wankula wapolice ndiwankhunyu
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 ай бұрын
Steve ndayamika pa nkhani yomaliza, President ndi nduna azidzipangila okha zonse osati zaulele m'mene zilili pano. Anthu akuvutika ku midzi. Ndicho chifukwa kudzikhala ma Demonstrations osonyeza kukwiya.
@RashdShalos
@RashdShalos 3 ай бұрын
AMwene program ya gwede gwede musamayi phonye pilizi bulasa 🎉wanu
@lonjezompaso9512
@lonjezompaso9512 3 ай бұрын
mukhoza kumaiona pa official page ya mibawa nthawi zonse
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 3 ай бұрын
You two God bless you speaking honest ❤❤❤❤
@marryphili5419
@marryphili5419 3 ай бұрын
Apolice akumalawi ndi mbamva chifukwa chake alowesa ndale pa ntchito yawo shame on you
@HazwelMangazao
@HazwelMangazao 3 ай бұрын
Mr S banda mukunena zoona bwana
@emmanuelchirwa3420
@emmanuelchirwa3420 3 ай бұрын
More 🔥🔥🔥🔥 kodwa Banda umuwalero big man
@PreciousElias-lx2pz
@PreciousElias-lx2pz 3 ай бұрын
God bless you boss mwayakhula
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana 3 ай бұрын
Anakangosiya kulamulira awunikire bwino ndithu chakwera chitsiru aribe nzeru kwao kwatha garu ameneyo
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 ай бұрын
God bless you guys 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
@GladMarawaMsowoya
@GladMarawaMsowoya 3 ай бұрын
Walephera chakwela akambe church
@RazackMofart
@RazackMofart 3 ай бұрын
Big up family,,Nothing but chilungamo
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 3 ай бұрын
Chimwendo wadya1 pa nkhaza ku mcp
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 3 ай бұрын
And ziko la Malawi litha kutukuka chachikulu kuchosa mbava zikuononga misokho yamalawi. Nduna president asayendere zinthu zaulele ndichifukwa akupanga matama kutenga ngati ife amalawi ndizisiro
@gibbohtrust6118
@gibbohtrust6118 3 ай бұрын
Komaso akumanga bwanji anthu Ma umboni aupeza bwanji mene zinakhalila kuchikangawa
@MarvGerald
@MarvGerald 3 ай бұрын
Tikupempha program iiii achisili Achawezi asazalowelere
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 3 ай бұрын
A police chitani manyazi mukulephera ntchito yanu
@CliffNankumba
@CliffNankumba 3 ай бұрын
Ndipo ife ana athu timalipira tokha fizi bwanji
@Pangolinimw
@Pangolinimw 3 ай бұрын
Kom iweyo umaganiza bwino bwino kobasi
@WysonBilly
@WysonBilly 3 ай бұрын
Kondwani umayankhula. Bwino
@emmanuelchirwa3420
@emmanuelchirwa3420 3 ай бұрын
Point take big man .komaso aziganiza kuti kunyumba kapena kulokecheni kulibe police officer,tisatenge malamuro pamanja azanja lathu. Ndi ye tiyeni tigwilentchi to kulingana ndimalamo , komaso Pali mwambe wakuti ukakhala pabwino lero usayiwale zamawa,chawonamuzakochapita mawa hilipayiwe..ndangoyimapamenepo, amoyo salekana,
@tamarajoycemalata
@tamarajoycemalata 3 ай бұрын
😊
@awardjafar2928
@awardjafar2928 3 ай бұрын
JB uja sakumalakwisa akamatukwana msogoleri ndinduna zake
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 3 ай бұрын
Nanga akamatukwana amalawi nose amalondolaso
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 3 ай бұрын
@@NancyNyirenda-v9oof course. Ndifedi anthu ogona ambirife
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 3 ай бұрын
JB amangotukwana chamba kwambir alibe fundo
@NoreenNaituri
@NoreenNaituri 3 ай бұрын
Azibusa asiyenso kulowelela ndale
@BrendaJailosi
@BrendaJailosi 3 ай бұрын
Alowelera bwanji iwo akunena chilungamo inu multi mbali iti? Anzathu?
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 3 ай бұрын
Ndipo zowona mumalo mokalalikila uko timadabwakuti ku zolozolo bwanji kwabuka ndeu mu church chawoneka kuti niwachinyengo mubusa uyu
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 3 ай бұрын
Inunso ngt muli opemphera nde musiye zomalimbana ndi anthu
@BrendaJailosi
@BrendaJailosi 3 ай бұрын
@@NancyNyirenda-v9o mukamva kupenga nde uku kd zigandanga zilipo gulutu kd za Infa imeneyi sidzinamukhuze ndindani km anthu akanike kulira fukwa nda zibusa nonsense
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 3 ай бұрын
Chigamulo changa chiyende moteremu chilimat waphedwera agree ment yake ndi chakwera komaso mlandu wasatar , choncho ngat achakwera amupha chilima kuti asale ndiudindo sizitheka , ngat agreement yalephereka pomupha chilima ndibwinoso achakwera aduse aliyese asakhaleposo muthu chilima amalakwa chani ? Nsupa zatulukat taombeza achakwera mwaphat chilima dala inuso mudusa udindowo aliyese asatenge chilima mwapha ife amalawi tiphaso inu bas 50-50 chilungamo titero
Players vs Corner Flags 🤯
00:28
LE FOOT EN VIDÉO
Рет қаралды 69 МЛН
规则,在门里生存,出来~死亡
00:33
落魄的王子
Рет қаралды 16 МЛН
Крутой фокус + секрет! #shorts
00:10
Роман Magic
Рет қаралды 20 МЛН
One-on-one with Zimbabwean President Emmerson Mnangagwa
27:48
CNBC Africa
Рет қаралды 52 М.
PAMTETETE
59:48
Mibawa Studios
Рет қаралды 4,3 М.
චන්ද්‍රසේනට වැඩ වරදියි..?
7:28
BON KALINDO LERO KUTOKOTA
16:05
HOT 265
Рет қаралды 11 М.
TIKUDZIWENI - 13 AUGUST -  ABITI MANICE WILLIAM DAUDI
28:46
Times 360 Malawi
Рет қаралды 52 М.
prophesy about 2025 presidential election
26:15
Senior Prophet Rodrick Mtupa SC
Рет қаралды 47 М.
Dan Lu sanalemekeze malemu Saulos Chilima
7:31
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 61 М.
Amalawi tidzameta maliro a Chilima 2025
7:57
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 56 М.